Prophetic Advice to Professor MUTHARIKA of DPP in Malawi

  Рет қаралды 2,328

Prophet Austin Liabunya

Prophet Austin Liabunya

6 ай бұрын

Пікірлер: 32
@BridgetZingani-gb8yf
@BridgetZingani-gb8yf 5 ай бұрын
Lalikani za uthenga wabwino wa Yesu inu osati za ndale
@user-wf2ii7zx5e
@user-wf2ii7zx5e 6 ай бұрын
Auzeni anthu za Yesu. Is this the new gospel?
@alexgweje8610
@alexgweje8610 5 ай бұрын
Opemphera amasiku ano Mmmmm mwataya njira ya Yesu khristu mukulimbana Ndi ndale xa
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 5 ай бұрын
😂😂😂 mwayiwala anthu awa kunthamangira ndalama basi wayiwala kalekale za Yesu . uyu
@GamaChifundo
@GamaChifundo 17 күн бұрын
Ok malawi amakhulupila utaona
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 27 күн бұрын
Kkkkk misatisrketse aku broker ndani aprophet😊
@witneymunthali8371
@witneymunthali8371 6 күн бұрын
Timusiye Mulungu mwini Mphamvu asnkhe yekha msogoleri Kwa ife ndikuponda Bondo.
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 12 күн бұрын
Apm yomweyo
@mabletungande349
@mabletungande349 5 ай бұрын
He might be telli ng the truth
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Ай бұрын
🤣🤣🙌
@ericchilinjala481
@ericchilinjala481 Ай бұрын
We need to know that mulungu akamayankhula ndiye kuti akutikonda. Olo mu bible atsogoleri amalangizidwa ndi ma prophet.izi sizachilendo..komanso ma prophet omwe ayitanidwa kulakira the pure gospel of God alipo..uyu calling yake is to give counsell to the goverment. Zinthuzi zimafunika kuzimvetsa..Liabunya sakunama.
@user-dd5kb4iv3z
@user-dd5kb4iv3z 6 ай бұрын
Mtima wanjiru, munthu wa Mulungu mabodza,mwana wa satana iwe, a professor timakonda ndife, pita ukalalikire anthu akumidima
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 27 күн бұрын
Munali so kwa chakwera pompano aprophet
@GodfreyjcBinguh
@GodfreyjcBinguh 4 күн бұрын
Chitsiru Ichi sadziwa pano Kuti mulungu akulilira Moyo wakoyo fiti iwe .do you knew Kuti nthawi yatha pompano okudzayo akudza.mulungu akusithe chifukwa yemwe ndimudziwa akuva chisoni ndi dziko
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 5 ай бұрын
Ubwino wake opemphelanu takuonani zochita zanu nde sitingamvela zakozo..iwe si Mulungu.. Auze anthu za ufumu wa Mulungu ..lalikilani kut anthu tilape pliz..mukupangazi ndi gospel ya ntundu wina..kukuyang'ana mmaso mwakomo I 've lead your mind..
@sylessmaduka466
@sylessmaduka466 16 күн бұрын
Munapereka chitsanzo cha Sauli ndi David. Nde munazatinso 2019 Peter atawina inu munkauzabe anthu kuti Chakwera ndi amene anawina mpakana 2020 zinaonekadi poti Mulungu mau ake sapita pachabe. Now tikaona za David sanakakamize ayi, sankamemeza anthu kuchita chipolowe mpakana nkutenga ufumu, ndi Sauli amene ankalimbana ndi David koma David sankabwenzera pomwe zinazi ndibwino musafananize chifukwa zinali zokakamiza. Komanso Mulungu kunena zoona mene zinthu zikuchitikira ku Malawi kuno olo munthu oti sawerenga mau a Mulungu sangavomereze kuti Mulungu anatisankhira mtsogoleri. Kodi zikuchitika ku Malawi kuno ndi mdalitso kapena thembelero? Izizi kupanda kusamala mayiko ena atengera chitsanzo pa Malawi kuti Mulungu siomuseweretsa.
@user-zm4vy5rs4v
@user-zm4vy5rs4v 5 ай бұрын
Ndizowona munthu si pitalayekhayu anzake achitepo
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 6 ай бұрын
Akunama uyu
@johnkumbanga3369
@johnkumbanga3369 6 ай бұрын
What are you trying to say mr prophet?
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 5 ай бұрын
Ukayang'anatu ndi diso la uzimu zimu koma uli mwana wa njoka,,,,,,,,,alosi onyenga inu mmodzi wa Satanism iwe mmmmmmmmmmmmm ngati mwadya ndalama za uyo mukumuti ndi ofatsayo nonse ana anjoka,,,,,,,,,,,,,,,ofatsa wake tsiluyo!
@user-qq3ip1od6i
@user-qq3ip1od6i 5 ай бұрын
Wabodza iwe,, busy wit politics rather than kulalikila uthenga wabwino,, busy kuchita predict zoipa za moyo Wa wina
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 6 ай бұрын
What he saying is not from God,he trie to be a politician
@NevesonChirwa-tt5eg
@NevesonChirwa-tt5eg 6 ай бұрын
Iwe prophet iwe ndiwe wa chamba kwambiri wamva?osangojoina ndale bwanji?Anzako a Mbewe adayambaso choncho koma pano si awo anayambitsa chipani.
@MisheckChapomba-lr8kz
@MisheckChapomba-lr8kz 6 ай бұрын
Akunenazo ndi zoona Koma osati zachokela Kwa Mulungu ayi God has nothing to do with this satanic parties
@MuhammadSamson-yz1kl
@MuhammadSamson-yz1kl 5 ай бұрын
Kkkkkkkk forsake kagwere uko iwe wasuta chamba
@user-pt2ok1kr1o
@user-pt2ok1kr1o 6 ай бұрын
Zachikunja izi auzeni anthu za yesu.
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 6 ай бұрын
Just start politics Mr prophet than Malo mumatiuza mawu a mulungu.
@EllenLuwanika-tl5ck
@EllenLuwanika-tl5ck 2 ай бұрын
Man of God stimuli kumalawi eti anthu akuvutika kuno
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 6 ай бұрын
Fake
Stop Worrying and Start Trusting God | Tony Evans Highlight
13:31
39kgのガリガリが踊る絵文字ダンス/39kg boney emoji dance#dance #ダンス #にんげんっていいな
00:16
💀Skeleton Ninja🥷【にんげんっていいなチャンネル】
Рет қаралды 7 МЛН
A Woman Gospel Minister in Malawi - prophecy
3:53
Divine Kingdom TV - Diakoneo
Рет қаралды 19 М.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 116 М.
Kodi a Chakwera Adzakhala so President Chaka Cha Mawa Chino?
22:58
Prophet Austin Liabunya
Рет қаралды 21 М.
Imam Mahdi and Muharram | al-Ghaibah (pt. 2)
35:29
After Maghrib 🌙
Рет қаралды 284
God will comfort Malawi - prophecy | Dr. Ian Ndlovu
4:43
Divine Kingdom TV - Diakoneo
Рет қаралды 42 М.
39kgのガリガリが踊る絵文字ダンス/39kg boney emoji dance#dance #ダンス #にんげんっていいな
00:16
💀Skeleton Ninja🥷【にんげんっていいなチャンネル】
Рет қаралды 7 МЛН