Subscribe For Daily Prophecies
0:58
Why Does God Test Our Faith
1:28:21
8 ай бұрын
Faith & GRACE Expose Prt02
33:57
11 ай бұрын
Пікірлер
@MathiasJoseph-xv1hj
@MathiasJoseph-xv1hj 9 минут бұрын
Man of God ndimamvesela km achakwelawo asiyad kumanga wanthu?
@user-ur8fq6ht5u
@user-ur8fq6ht5u 16 минут бұрын
Mulungu wake utiyo kodi amene mumanena inuyo akulu?
@planmalawi-sm2cw
@planmalawi-sm2cw 18 минут бұрын
Wachibwana mulungu wake uti?
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 24 минут бұрын
Mulungu yekha ndi Amene amadziwa tonse......Fake prophets....masiku oziliza.....koma mkulu uyuu akundimvetsa chisoni.
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 24 минут бұрын
Koma zomvetsa chisoni kwambili,mupalamuliranji mkwiyo wa Yehova
@ThompsonMakwakwa
@ThompsonMakwakwa 27 минут бұрын
Mulungu wambuyako and mulungu angakhale busy kuyankhurana ndi iwe!!
@user-kq6rp6hn7y
@user-kq6rp6hn7y 30 минут бұрын
Akulu inu mutu wanu sukugwira. Ungoti bwerani mwachangu aaaaa u r wasting our time
@NedsonIssah
@NedsonIssah 40 минут бұрын
Aneneli abodza akuchulukira
@RhoddensChasamuka
@RhoddensChasamuka 42 минут бұрын
Zamanyazi
@user-nt9go2fz3k
@user-nt9go2fz3k 47 минут бұрын
Rubbish
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j Сағат бұрын
Zopangana izi.zaziiiiiiiiiiiii
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo Сағат бұрын
His kingdom is not of this world........
@ChawezChinkhuntha
@ChawezChinkhuntha Сағат бұрын
Akulipilanituuu inu
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Сағат бұрын
Iweyo si mtumiki wamulungu koma umatumikira satana ndikuudze izi mulungu sangalole kt anthu ake adzingolira chifukwa ca mbusa uyu cakwera yemwe sakudziwa kuyendetsa. Dziko ndiyeno adzaonetsa ukulu wake tiyeni amalawi tidzipephera
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo Сағат бұрын
Iwe ngat uli munthu wamulungu mene akuzuzikila amalawimu ukuona km usandiyankhulise zolakwika
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Сағат бұрын
Kukacha mauneneli ndi achakwela basi mulungu adzakulangani nose ndi chakwela wanuyo tatopa ndi aneneli aziko
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Сағат бұрын
Mauneneli anuyo muzinenelelna ndi kwakwela wanu yomweo peter muthalika musiyeni salimbana nanu Kodi chilima akanakhala plesdent litili popeza m, gwilizano omwe anapanga chakwela sanafune kuti m,zake aimile komaso chomwe mungadziwe chilima amapita kumalilo samapita kuphwando
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 25 минут бұрын
Ndipo kwambili
@omarrasheed5568
@omarrasheed5568 Сағат бұрын
Wamisala uyu amayendela mizumu
@user-dh3gr2cg4o
@user-dh3gr2cg4o Сағат бұрын
Mmmmmmmm paja umadya nawo
@memaumoyo2561
@memaumoyo2561 Сағат бұрын
Uthenga wamveka a Pulo.......
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 Сағат бұрын
God is with Malawians and not with MCP which so called bloody party.
@kennedybanda
@kennedybanda Сағат бұрын
You are doing business in the name of prophet. Stop telling false prophecies.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Сағат бұрын
AAAAAAAAA MA PROPHET AKE SI AZAKAZINOWA , MA PROPHET ANALI KALE ACHINA YOHANE, DANIEL KUNGOTCHULA OCHEPA, ANTHU AMENE AMAIMA PA CHOONADI. OSATI AWA OMETA MBALIWA CHONSECHO MALAMULO A MULUNGU AKUWADXIWA , MUKAKHUTA ZAKUMIDIMA KWANUKO MIZINAMIZA A MALAWI,. MUKULANDILAKUMENE MUNTHU WA MULUNGU SAPANGA ZANDALE, IYAAAAAAA ZA U SATANIKI BASI, NDIPO NDIWE MODZI AMENE UKUTENGERA ANTHU KU CHIONONGEKO , YOU SAID PEOPLE HAVE TO TRUST YOU LIKE WHO? INSTEAD TO TRUST IN GOD, FALLS PROPHET.
@stevezulu2108
@stevezulu2108 2 сағат бұрын
Utiseketsa tu iweee 😂😂😂 .
@stevezulu2108
@stevezulu2108 2 сағат бұрын
Mulungu amaseka?????😂😂😂😂😂😂😂
@stevezulu2108
@stevezulu2108 2 сағат бұрын
Umacheza ndi mulungu? 😂😂😂
@TomDziko
@TomDziko 2 сағат бұрын
Nanga za kupha anauzidwanso ndi mulungu tatiuzani
@SimonLikwangulo-xq9oz
@SimonLikwangulo-xq9oz 2 сағат бұрын
Tayankhulabwino usathawe apanga zonse kupha Saul's chilima uyambile pamenepo tikumva udzibwelano kwinako ungofuna nthumba iwe
@user-ph1oe8ig2i
@user-ph1oe8ig2i 2 сағат бұрын
Ubwno wake sitizavota
@cynthiandekhakatundu6890
@cynthiandekhakatundu6890 2 сағат бұрын
Mwadwanawo misonkho ya Amalawi
@TrywellMakaika
@TrywellMakaika 2 сағат бұрын
Penapake ukudabwitsa kwambiri ukukamba za phone yako kuti ndi ya timamilion tingapo ife zitithandiza chani? Mulungu osamasewela nayetu ukuti umacheza naye mkumakuwuza zokhutazo, ingopemphani ndalama kwa chakwela osanamizila mulungu mukulankhula maganizo ano. Chibwana cha mchombo lende!
@Patgregorymanyumba
@Patgregorymanyumba 2 сағат бұрын
You are fake prophet
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 2 сағат бұрын
Paja azibusa ndi anthu oipa kumalawi kuno, and mazibusa amadyaso mabazi kuchokera ku government
@HarryMsudzula
@HarryMsudzula 2 сағат бұрын
Ukatelo wapasidwa ndalama aneneli asatana
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 3 сағат бұрын
Mwayankhulatu agavanala a MCP 😂😂😂
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 3 сағат бұрын
Zochokera ku midima izi
@FrancisNthache-r3l
@FrancisNthache-r3l 3 сағат бұрын
THIS IS NOT GOD
@FrancisNthache-r3l
@FrancisNthache-r3l 3 сағат бұрын
Koma ngati Ali MULUNGU WA ISAAC ,JACOB IFE TINGOTI AMEN KOMA NGATI MULUNGU WAKE SI AMENEYO AYI DZIKOMO
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 сағат бұрын
ANENERI ABODZA INU ODZITUMA NOKHA, CHAKWERA OLO ATABA SANGAIMENSO NDIWE WABODZA KWAMBIRI UNENERI WAKO NDIWABODZA UKUONETSAKUTI AKUKUDYETSA ZAZIIIII
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 3 сағат бұрын
I am very disappointed in you,i have been following you all along,koma I have now realized that I have been following a very wrong person,God almighty should forgive you.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 сағат бұрын
IWETU USANAMIZE WANTHU IWEYO UMACHEZA NDI MULUNGU NGATI NDIWE NDANI ? ANAKANIKA MOSE KUCHEZA NDI MUKUNGU IWE NDI NDANI, SAMALANI NDINU AMENE MUKUNYOZETSA DZINA LA MULUNGU CHIFUKWA MUKUBISALIRA MDXINA LA MULUNGU MULI ASATANA, PALIBE CHINGAKUTHANDIZEN. KOMANSO USIYE KUGWIRITSA NTCHITO MAU OTI UMACHEZA NDI MULUNGU,SUNGA CHEZE NDI MULUNGU IWE ANAKANIKA YOSWA WHO IS YOU?
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 3 сағат бұрын
Mutu wanu sugwila ntchito bwino akulu,mwadya ndalama zingati? Zikusonyeza kuti infa ya achilima inakusangalatsani eti.musiye kuseweretsa mulungu coz God will punish you
@user-go5xy3cf1r
@user-go5xy3cf1r 3 сағат бұрын
Yankhulani anthu onse afika nenani munthu wa mulungu
@timothymacheka
@timothymacheka 3 сағат бұрын
Munanena kuti chilima adzakhala president??
@user-ie4ci3zh7j
@user-ie4ci3zh7j 3 сағат бұрын
Uuuuuuuuuu chokani apa mulibeso dzeru
@user-nr2bi5zm9f
@user-nr2bi5zm9f 3 сағат бұрын
Iwe chitsiru kwambr , wasatanic iwe
@GeoffreyNyasulu
@GeoffreyNyasulu 3 сағат бұрын
Kucheza ndi Mulungu??? 😢. Kumbukilani Mneneri Elijah ndi Ahab pa phiri la Caramel.
@hendrixmwangata3452
@hendrixmwangata3452 3 сағат бұрын
Ukufuna kumubera chakwerayo sangawine
@JohnEzelohMagawa-fl8sw
@JohnEzelohMagawa-fl8sw 4 сағат бұрын
I can see that you are nothing but a full
@user-qq3ip1od6i
@user-qq3ip1od6i 4 сағат бұрын
We just lost a true statesman vp,, people are not happy wit Chakwela leaders. If you're true to your calling advice to step aside