Tamvani Zomwe A kuyankhula Za Kondwani Nakhumwa

  Рет қаралды 20,282

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Tamvani Zomwe A kuyankhula Za Kondwani Nakhumwa

Пікірлер: 70
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 2 ай бұрын
Mankhumwa unawononga mbili yako pokhala chete Ku parliament osaimilila a Malawi live from SA Pretoria.Machinjiri my home town Khama..
@user-qf3eo3fo1y
@user-qf3eo3fo1y 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Mavoti onse ndi a Peter Munthalika basi ❤❤❤❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
DPP ndimakina kulibe chipani chomwe Chingazafane ndi DPP mpakana kale
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
DPP ikulowa m'boma wina afune asafune❤❤❤❤❤❤❤
@user-yn4ee1qn2j
@user-yn4ee1qn2j 2 ай бұрын
Nankhumwa ndimwana komatso ndiwandyela
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 2 ай бұрын
Nankhumwa manyaka munthu ngati amakanika kuyankhura ku parliament ndye angasogolere dziko anthu akuvutika chifukwa cha anthu amenewa
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 2 ай бұрын
Nayeso dyera lakurila zimasaya ndipo chipan chimenecho kt anthu achiziwe ndidye paka zaka 20 tsongolomu chizinkhangat chafodi kkkkkkkk
@MusaGande
@MusaGande 2 ай бұрын
My watching from mangochi ❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Munthalika pachiongolero ❤❤❤❤❤❤❤
@user-ji3in4cp3m
@user-ji3in4cp3m 2 ай бұрын
Akufna kusokoneza zisankho ameneyo
@LonelySapanga
@LonelySapanga 2 ай бұрын
Zilo pa ten
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 2 ай бұрын
Luwanda machinjiri fire 🔥
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu 2 ай бұрын
Nankhumwa saganiza bho,kupupuluma Kwake komanso kukula mtima sizingamuthandize
@ElizabethDick-bm4wb
@ElizabethDick-bm4wb 2 ай бұрын
Kupangazithu chifukwa chakupsa ntima sizimayenda.
@user-be3is8rc4r
@user-be3is8rc4r 2 ай бұрын
Mwanamba nakhumwa
@user-tm1fz2qc5z
@user-tm1fz2qc5z 2 ай бұрын
walemba mmadzi mowerenga achule
@h-one2656
@h-one2656 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂@nepman ukuti Chani
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 2 ай бұрын
Apm❤
@dalisoulphiri3094
@dalisoulphiri3094 2 ай бұрын
Tapitaniko mbali yina ya nsewu wo mukafunse ena malo amodzimodzi mpaka kumachita kubweleza anthu aaaaa
@LongiMtimabii
@LongiMtimabii 2 ай бұрын
Fada apm ipondeni nthawi yanu
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Nankhumwa ndi jockey, kulankhula kwa pa Media zimathela popo.vote,ndi chisisi cha, munthu.
@user-pl6it7zc7c
@user-pl6it7zc7c 2 ай бұрын
koma anthu ena ndi mbuli Mesa adathamangitsa kuchipani
@KunokoKaunda-mu6dg
@KunokoKaunda-mu6dg 2 ай бұрын
Nakhumwayo wapenga misala chomwe afuna andalewa ndikuba bas
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e 2 ай бұрын
Nankhumwa apite uko naye akungofuna kusokoneza ifeyo wathu ndi muthalika
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 2 ай бұрын
Mumvere Azimayi wo
@user-jc7qg6cz2k
@user-jc7qg6cz2k 2 ай бұрын
Mpando unali wake umene uja, koma phuma.
@chifundobuledi
@chifundobuledi 2 ай бұрын
Sangawine ndi anyamata a...........
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 ай бұрын
Mumuudze nankhumwa kuti ndiodwala apite akayamwe
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 2 ай бұрын
Galu ameneyo sangawine
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
Kodi Amene mukuwa funsawo Ndi gulu la mbuli zokhazokha,sakuyankha bwino bwino, ndimaesa Ndi nankhumwayo wa pweteketsa amalawi ku nyumba ya mala mulo kungo khala phwii, kusiya MCP iku wononga machende amake mulomwe opanda mzeru ngulu,bulutu munya kumeneko ku Malawi kwanuko muvutika ngati simuganiza bwino
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Amalawi enaa mmmmmmmm mpakana Kumuvotera Nankhumwa???😂😂😂
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 2 ай бұрын
Inu amalawi segurani maso bushiri akukugawirani chimanga chaurere bwanji osamuvotera bushiri bwanji
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 2 ай бұрын
Pempho langa amalawi tazionera tokha tiyeni tizabvote mwamzeru tisazanamizidwe nthawi ya kampeni
@AjeliMw
@AjeliMw 2 ай бұрын
Alore alore akane akane DPP 2025 Boma 🔥🔥🔥🔥🔥
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 2 ай бұрын
Peter muthalika my vote
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Nankhumwa akunama sangawine angotaya nthawi yake pachabe
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 2 ай бұрын
Nepu many wayakjula nwino kupotsa aliyetse
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Nakhumwa anthu sangamukhulupilile anaonga mbili pokhala Chete ku parliament pomwe amalawi akuvutika Akafuse a JB mpinganjila anazola matope alibe mawu
@ChangeChambo
@ChangeChambo 2 ай бұрын
Namachende galu nankhomwa sungakhale president wadziko chifukwa ndiwe mbuzi ya munthu
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 ай бұрын
Chidwi sanaonese ali nsogoleri osusa sanayimire amalawi ayambise chipani chawo akufuna kupusa zenizeni
@SelmoNdoma
@SelmoNdoma 2 ай бұрын
DPP Woeeee
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Nankhumwa azavoteledwa ndi amake ndi banja lake
@hopembendela
@hopembendela 2 ай бұрын
Majority ukuyankhula yokha kumene 2025 vote ikulowela
@AdamAPhiri
@AdamAPhiri 2 ай бұрын
Akunama akamufunse Brown Mpinganjira ndi Uladi Mussah ndi ena omwe anatero
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 ай бұрын
Awo ayamba chipani za zii zimenezo
@user-ko2yv4gi5y
@user-ko2yv4gi5y 2 ай бұрын
Komanso ayina mmene achulukilamu galu ameneyo akuti PDP yasiyana pati ndi DPP
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Nakhumwa ndi chisiru kwambiri ndipo sangawine komanso amalemba maina achipani chifukwa chani sanakane kumuudza kt asibthe dzina lachipani cakecho sanganene kuti dzina la chipani cake ndi dpd pamene akudziwa kuti kuli dpp nakhumwa mbunzi yamunthu
@owenskabazanechiumia3543
@owenskabazanechiumia3543 2 ай бұрын
Nzongopepera basi chofuna nkubalalitsa Amalawi basi ndale zama Gemu pa Malawi kuba basi
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 2 ай бұрын
nonse amene mukulemba comment muliku John simuzavota oziwa owina tikumuziwa ndife
@andrewBwanaisa
@andrewBwanaisa 2 ай бұрын
Ndiwana
@miltonkanyamula9486
@miltonkanyamula9486 2 ай бұрын
A Malawi tili ndi bvuto . Mwina losamvetsetsa funso lomwe likufunsidwa.. poyankha tikuyankha zosiyana ndi funso. I think funso ndi lakuti nkhani ya Nankhumwa youambitsa chipani chawo tachilandila bwanji.. Yankho . Tachilandila kapena sitinachilamdile.. mbali yonse ifotokoze chifukwa.. monga zipangitsa kugawa ma vote a anthu wotsatila DPP. Wochilandila ... Anankhumwa pambuyo pochotsedwa mchipani anali ndi ma choice awiri.. kulowa chipani china chomwe chilipo kale kapena kuyambitsa chawo.. Ndiye poti sanafune kutengeka ndi kukwera bwato woti ukubila Iwo atenga wawo nauyamba ulendo wa ku Kannan Kugawa ma vote a DPP sibvuto la Nankhumwa koma chipani Cha DPP chifukwa chosowa akadaulo a dialogue
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 2 ай бұрын
Akuluakulu dpp basi ithetsa mavuto ngati kale sugar tidzagulatso 700
@mamulemathekga
@mamulemathekga 2 ай бұрын
Kulusa kosayamba kkkkk
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 ай бұрын
Azamvotetera amake ndi abale ake
@yassinn5634
@yassinn5634 2 ай бұрын
Muzitiuzanso kuti tamvani zomwe ayankhula a Namkhumwa osati kumangochulukitsa zomwe anthu akunyonyoza kapena kuyamikira a Namkhumwa tikufuna mfundo za mwini chipanicho tizizimva apa
@TeddySpencerMpezeni
@TeddySpencerMpezeni 2 ай бұрын
DPP 4ever 🥰🥰🥰
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 ай бұрын
Zipani zimene ayambisa anthu amenewa sangawine koma amafuna kuti azikhalabe muboma ndi Zipani zina
@honourablemcgregorysc97tv
@honourablemcgregorysc97tv 2 ай бұрын
DPP ya APM my vote 🥰🔥
@user-ub9on7oj7l
@user-ub9on7oj7l 2 ай бұрын
Sikumveka iy
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
Komanso mudziwe kuti DPP singawine iwina ku mwera komweko basi chipani cha akukhutukumve
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Apo ndiye watha basi nankhumwayo ndi osazamuvoteranso munthu oyipa mtima ndipo kunmulanje centralko osamupatsa mpata wa mp pazimene wakhala akuchita zoipa kumtundu wa amalawi polepherea kusutsa BOMA pamene amalawi akubvutika ndi BOMA LA chakwera iye anangokhala chete
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Kondwani nankhumwa ndi wa Mcp tsegulani maso amalawi mudzakhumudwa chipani chake chikusakanizana ndi chipani cha mcp
@user-sr6hc3pv8o
@user-sr6hc3pv8o 2 ай бұрын
Umbuli ndimatenda amene akuti onsewo ndamoziyo apite kusukulu yakwacha maybe azalankhula zanseru next interview
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
School yakwacha kkkķ
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 2 ай бұрын
Dpp mbava zoka zokaa
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Apo ndiye watha basi nankhumwayo ndi osazamuvoteranso munthu oyipa mtima ndipo kunmulanje centralko osamupatsa mpata wa mp pazimene wakhala akuchita zoipa kumtundu wa amalawi polepherea kusutsa BOMA pamene amalawi akubvutika ndi BOMA LA chakwera iye anangokhala chete
@user-pi2gf5tp2k
@user-pi2gf5tp2k 2 ай бұрын
Balaka wakuti utichititse manyazi apa
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Apo ndiye watha basi nankhumwayo ndi osazamuvoteranso munthu oyipa mtima ndipo kunmulanje centralko osamupatsa mpata wa mp pazimene wakhala akuchita zoipa kumtundu wa amalawi polepherea kusutsa BOMA pamene amalawi akubvutika ndi BOMA LA chakwera iye anangokhala chete
USAUVER S09E03 - UNALI KUTI?
22:37
Piksy TV
Рет қаралды 131 М.
BOY MALICK -SHEILA (video oficial  SDy Pro)
3:34
SDypro Oficial
Рет қаралды 296 М.
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН
I Can't Believe We Did This...
00:38
Stokes Twins
Рет қаралды 129 МЛН
Ching'aning'ani comedy, ft Ngiringande
6:53
Malawi Page
Рет қаралды 305 М.
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 159 М.
DRIVING SCHOOL- Episode 166
15:17
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 90 М.
SIMPLEX CHITHYOLA BANDA ACB YIWAFUFUZE CHIFUKWA CHA CHUMA
20:29
MUNAKUMANA BWANJI?..13/05/2024..Mibawa. TV's Content
28:59
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 8 М.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12
MR JOKES
Рет қаралды 179 М.
TIKUFERANJI 17 DECEMBER 2015
59:37
Edson Gunsalu
Рет қаралды 58 М.
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН