Tamvani Zomwe MCP ikubweletsa Ndi Kukhazikitsa

  Рет қаралды 4,623

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Tamvani Zomwe MCP ikubweletsa Ndi Kukhazikitsa

Пікірлер: 124
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 2 ай бұрын
Ine ndikusowa kuti ndimutukwane motani ameneyu?
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 2 ай бұрын
Muli Ngati inetu palibe zotipindulira dziko Koma MCP
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 2 ай бұрын
Anthu omwe AKUPHA chilima aja ndi awaaa uyu adali okupha munthawi yakamuzu uja
@abdullalajabu5871
@abdullalajabu5871 2 ай бұрын
Ife pano tikumvela nyimbo zabwino Za jetu ndi chalamanda kutiwalisa zokamba maboza Ngati awa inu tikumana 2025 basi
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 2 ай бұрын
Zaziiiiiiiiiii mmalo mobwera ndi nzeru zabwino komâ ai ndithu kungobwera ndi mbwelera zakezo. Zimenezo ukapangira ku Nyumba kwako Mbudye iwe
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 2 ай бұрын
Zaziiiii, nyansi saphimba, anatero Ben Longwe
@user-iu7gr2hj1j
@user-iu7gr2hj1j 2 ай бұрын
4 years back u never done nothing. So you think in 1 year you will do all that shit ? We are soo disappointed with this government
@samuzymkwanya8490
@samuzymkwanya8490 2 ай бұрын
Awa akuwoneka alindikawudani kenakake ndazawo Komaso kuyankhula kwawo palibe usogoleli kya zanuizo a MCP Ine ngwa DADI
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 ай бұрын
Komatu ndalama zabedwa .. mpaka ndalama kupenga nazo chonchi?
@mussahkachere2332
@mussahkachere2332 2 ай бұрын
Afiti awa akuchita kuzichemelela kut ndine olimba ntima.😊😊
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga 2 ай бұрын
Koma palibe. mulungu alinafe awa ndi agalu
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 2 ай бұрын
Kodi uyu ndi bambo wandani uyu 🙌🙌 no wonder soap wina amangokula alibedi thovu ndaonela👆
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 2 ай бұрын
Mwangokula madala Koma mzeru Zanu sizikusiyana ndi Za mbuzi, malawi mmene ikumvetsela cisoni panomu inu mungamalankhule mwauchitsiru chomcho??? Kuchikwawa!!!!
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Madala ndinu achisiru kwabasi ndipo mulibe nzeru kukamwa kotambalalako 100 years adzidzalamula ana ako osati amalawi ea ife
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Pamtumbo pa bambo uyu, tatopa ndi zimenezi, agalu achabe chabe. Anthu akuba awa, umoyo wa anthu pa ground sulibwino. Kwavuta ku Malawi sizinachitikenso ku Malawi, chitsilu ichi.
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 mcp ndiyabonza
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 2 ай бұрын
I like the confidence and zeal...
@user-vi5zx2hk6m
@user-vi5zx2hk6m 2 ай бұрын
Kkkkk Ali ndi chibwana😂😂
@ElliotOrban-th3qn
@ElliotOrban-th3qn 2 ай бұрын
Mbuziii iyiii malotoo achumba dzikoo lawakanikaa kalee
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 2 ай бұрын
Agalu awa ndionama mwakhulupilila bwanji ,muzinamizidwa muzifa ndinjala
@user-nn7sv5yb8h
@user-nn7sv5yb8h 2 ай бұрын
Iwe mdala usiye kusuta chamba upenga nacho misala kodi inu a MCP mwamutola kuti wamisala ameneyu the 😅😅😅
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 2 ай бұрын
Amalawi mukuzimvela nokha chiwanda chikuyankhula kuti MCP ilamulila mpaka 100 years
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 2 ай бұрын
😂😂ndi mawona Ngati achewa mbuzi ndi chakwdla km achewa ndi zisilu zawanthu Bas zangokula milomo wikha nzelo zilibe muzipita kwanu ku zaile agalu inu
@georgesmart3791
@georgesmart3791 2 ай бұрын
Anthu onga olo ataluza zisankho Sangalore bcos zomwe akufuna nzoti tikhale ndi one party system .. anthu oipa mitima..shame
@user-hr2cg3ku1l
@user-hr2cg3ku1l 2 ай бұрын
Bambo iwe ulibe nzeru ndithu ukuona ngati nthawi ya kamuzu ino eti galu
@TheresaNtodwa
@TheresaNtodwa 2 ай бұрын
Mbuzi zamano kusi
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 2 ай бұрын
Paka zaka 100 mene anthu akuzuzikilamu eeeeeeee ndiye malawi asala achewavankhaonkha
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 2 ай бұрын
Mbava za a MCP izi choncho dziko lingatukuke ,Malawi ali moto ngati Boma ili litapitilira ndipo dziko pa Malawi padzakhala umphawi wananu kobasi
@hambalisaeedphiri
@hambalisaeedphiri 2 ай бұрын
Munthu amatero poyankhula akasuta chamba ,mdziko muno muli njala ndi zimene akuganiza apa si misala imeneyo
@user-qp9bn5ed5n
@user-qp9bn5ed5n 2 ай бұрын
Mwaredzera kachaso chani galimoto zachani mmalo momagura chimanga nkumasunga galunso iwe eti nyani
@khalifajalih1960
@khalifajalih1960 2 ай бұрын
Kod mchikumbeyu fodya wake wagulisa?
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 ай бұрын
Ndiye akufuna kugwira ntchito kwanuko ndani zopusa eeeee mwawelengera kale ndalama zopeza pa mwezi kkkkkk
@FelixLivison-eg2hf
@FelixLivison-eg2hf 2 ай бұрын
Zonsezi ndi nkhani yakulephela basi
@YusufuKaifa-fr4wt
@YusufuKaifa-fr4wt 2 ай бұрын
4yers mwapanga palibe mwedzi yokha ndiyo yatsala mungapange zithu zochuluka choncho kkkkkkkkkk ndakayika bodza ili leni leni anthu akufa malawi muno ndi mavuto Akusangalala ndi omwe ali ku boma wo basi ndifukwa chake alindi phavu yoyakhura chonchi akhuta khuta uko ndi kuma phwetsera pa TV is nothing this is funny seriously
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 2 ай бұрын
Think uyu ndimu chewa, chifukwa mtunduwu umaganiza mopoira kwambiri..
@HassanJameskananjie
@HassanJameskananjie 2 ай бұрын
Iwedi ndi olimbantimadi mbuzi ya munthu anthu akufa ndi njala iwe ukufuna kugulila ma quantum a mcp machende ako
@user-yg9rs7tp2x
@user-yg9rs7tp2x 2 ай бұрын
galu ameneyu ndiye ndani?
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy 2 ай бұрын
Nde zopusazo zimenezo inu simungatukule dziko munakanika kale mukapume
@Brandinah-we2dp
@Brandinah-we2dp 2 ай бұрын
Afuna sugar tizizagula pa 20 000 awa 😂😂
@charlesgunda1873
@charlesgunda1873 2 ай бұрын
Kkkkkk this man is dreaming can someone wake him up
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 ай бұрын
Mu anthu 10 kulilongwe 4 mwa iwo amagwa khunyu ... Here is the example 😅
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 2 ай бұрын
😂😂😂 nthawi mkachitsiludi. nanga nthawi yonseyi munali nayoyi mumatani kuzipanga?ntchewa akulira akudziwa kwake kwatha mamama ntima ukumuwawa kut zoonadi Chaka chamawa tikutulukadi m'boma ili tikumadya bwinoli.koma osananama achewa munatasa nazo ndalama zathuzi.koma Aaah kwanu kwatha basi no more mcp next year even mugule anthu you will never get more votes.
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o 2 ай бұрын
Zikuoneka ngati nkuluyi ankadyetsa ng'ona mthawi yakamuzu
@VictoriaWilly
@VictoriaWilly 2 ай бұрын
Ndangotaya nthawi kumvera mfundo zopepela izi zedi.... Anthu akuvutika zedi ku mizi inu muli busy with your empty promises
@PedroalexandreAlexandre-rz8sz
@PedroalexandreAlexandre-rz8sz 2 ай бұрын
ndiwe chisilu ukusowa chokamba ndiwa galu😂
@PedroalexandreAlexandre-rz8sz
@PedroalexandreAlexandre-rz8sz 2 ай бұрын
Chakwela wachita zosiya.ndiena monga kubweletsa njala komaso mabvuto dziko muno.
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Aaaaaaaa bamboo awa ndiopusa KWAMBIRI Muthu Ngat Sali wa mcp ati samulemba ntchito , this is nonsense palibe chomangapo dziko APA ,mudalonjeza zambiri mudapangapo chani ? Mungodzuzapo Malawi APA Mutu Ngat chiphwete
@MilikaKilion-tn1bn
@MilikaKilion-tn1bn 2 ай бұрын
Kodi malomjezano sanakwane
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 2 ай бұрын
Koma nkhondo ija ilipo chifukwa uyu sangalole kuluzu ndimfiti iyi
@Harlod5566
@Harlod5566 2 ай бұрын
Koma chamba chake n'chomwechi?
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 2 ай бұрын
Tazingobani nthawi yanu muzayaluka kusogolo
@user-dl1dg4yz1j
@user-dl1dg4yz1j 2 ай бұрын
Kusukulu unapita koma nzeru za umunthu ulibe galu iwe
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Mulungu akumva kulira kwa amalawi
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 2 ай бұрын
Kkkkkkkk😂😂😂Maloto achumba
@Johnybegood260
@Johnybegood260 2 ай бұрын
very ambitious
@MasharPablo
@MasharPablo 2 ай бұрын
Ndalama zake zakubazo?
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr 2 ай бұрын
Bava za MCP
@YvonneGerald-rj7lt
@YvonneGerald-rj7lt 2 ай бұрын
Zibani ifika nthawi musanza zikusamwani time will tell
@user-ld8gb9xm7v
@user-ld8gb9xm7v 2 ай бұрын
Kkkkk boza ilo
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 2 ай бұрын
Koma ndinu anthu omvetsa chisoni kwambiri,do you think come 2025 malawians will vote for you again?
@sufiammadi
@sufiammadi 2 ай бұрын
Musanagule ma galimoto wo tapangani zoti sugar azipezeka komanso otchipa🙄🙄
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 2 ай бұрын
Onani ma comment madala pansipo mukuganiza kuti chipani chimodzi chidzathekanso?
@leopolokera8931
@leopolokera8931 2 ай бұрын
Ziwanda zayamba kubwera poyera
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 2 ай бұрын
Boma la chamba, akungofuna kusangalatsa chipani not anthu
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 ай бұрын
Pachitamiro pawopo
@user-lq4mw6kq7t
@user-lq4mw6kq7t 2 ай бұрын
Zaziiii yangali njetesoni
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 2 ай бұрын
Your time is over!!! Mukuyendetsa chipani or dzikoooooo????? Leave our Malawi alone and take your MCP, go!!!!
@JamesMalango
@JamesMalango 2 ай бұрын
Kuchuluka kwa mau mmakhala bodza
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Aaaa achitsi abambowa ndi MCP yawoyo anyanwu
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 2 ай бұрын
Simunawachepesele?
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 ай бұрын
Za mcp zi nsaname zikumandinyasa q
@malvinhusted6245
@malvinhusted6245 2 ай бұрын
Nde mukusuta champhamvutu chamba chake madhala
@fatimaamidu3967
@fatimaamidu3967 2 ай бұрын
Koma madala wa ndi mbudzi yamunthu
@jemasmasimbi8109
@jemasmasimbi8109 2 ай бұрын
uyu ndiye pumbwa weniweni,,,,,,
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 ай бұрын
Mbuzi za anthu remember the time is gone for you guys
@Brandinah-we2dp
@Brandinah-we2dp 2 ай бұрын
Akundisowesa choyankhula awa 🤨aaaah
@chikalabuba9045
@chikalabuba9045 2 ай бұрын
Galu iwe and chakwera yo
@user-ub9on7oj7l
@user-ub9on7oj7l 2 ай бұрын
Pankholo panu nonseku MCP
@robenallie6985
@robenallie6985 2 ай бұрын
Galu ndalama zobela ife anthu ofutika
@PatrickMariko
@PatrickMariko 2 ай бұрын
Koma iwe ndi galu kwabs
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 2 ай бұрын
Ndiyankheni abale ndi alongo kodi mkulu ameneyo ndiwabwinobwino kapena ndi odwala mutu?
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 2 ай бұрын
Siomuganizila kt ndiwabwino kapena ayi, km kt kod akufunika chipatala chanji cha amisala kut mkuluyu achile, chifukwa misalayake even palibe anadwalapo.
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 2 ай бұрын
@@user-oq5rg5mz7q exactly chief
@ibradaglass8646
@ibradaglass8646 2 ай бұрын
Zaziiiiii mbudzi ya munthu
@Austinnkhula
@Austinnkhula 2 ай бұрын
Iwe usandilankhulise pambali wamva
@Atlanticmusic-4777
@Atlanticmusic-4777 2 ай бұрын
Tachiwonelen mutu
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Wachifufu uyu 😅😅😅😅.
@dannylouischimwala9266
@dannylouischimwala9266 2 ай бұрын
Mutu wanu madala
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 2 ай бұрын
Zazii zopanda mchere
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 2 ай бұрын
Choka kukamwa kwako sataniki iwe
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 2 ай бұрын
70 percent imeneyo uzailira nyooo
@WitinesiJakisone
@WitinesiJakisone 2 ай бұрын
Phatumbo pako
@Allieshaibu8612
@Allieshaibu8612 2 ай бұрын
Munditukwanile kwa galu uyu watumidwa2 uyu
@grantkachingwe7207
@grantkachingwe7207 2 ай бұрын
Akudwala uyu
@MasharPablo
@MasharPablo 2 ай бұрын
Kunyasa khope
@happychimtedza3873
@happychimtedza3873 2 ай бұрын
Satha kuyakhulaso
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 ай бұрын
Uyu ndie satana wen wen
@dontreybanda278
@dontreybanda278 2 ай бұрын
Mbudzi😂
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 ай бұрын
Mxeuii zodabwisa zobweletsa njalazo
@MussaAndreQuenessi
@MussaAndreQuenessi 2 ай бұрын
Uyu ndigaru
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr 2 ай бұрын
Misokho ya anthu
@user-zt7hy5lh4r
@user-zt7hy5lh4r 2 ай бұрын
😢😢😢
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 2 ай бұрын
Ndala iweo ulibe zelu
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr 2 ай бұрын
Athu wa akumba
@user-ux8bc6wy1i
@user-ux8bc6wy1i 2 ай бұрын
Mbuzi za anthu mxiew
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Zopusa et
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
ПРОВЕРИЛ АРБУЗЫ #shorts
00:34
Паша Осадчий
Рет қаралды 6 МЛН
🤔Какой Орган самый длинный ? #shorts
00:42
Lwasa afunye sente bupya,aguze benz ne rangerover
30:52
Kasuku Live
Рет қаралды 38 М.
TRAFFIC VIOLATORS CAUGHT RED HANDED BY DMP POLICE
12:40
NLTV
Рет қаралды 3,8 М.
Misomali Ya Six Inches Yothana Ndi Zipani Zotsutsa - Bon Kalindo
17:18
A Timothy Mtambo Akufuna U President - Country Man & Uncle
16:35
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 6 М.
Makgulong A Matala 05/05/2024❤️❤️❤️
40:16
Motho Wa Modimo
Рет қаралды 7 М.
Ndichikhala Chilima Sindikanalola Kuti Mulandu Ungotha - Bon Kalindo
16:47
Kay G - Agalatiya Ft. Various Artists (Official Music Vídeo)
6:41
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Zodiak Malawi
Рет қаралды 328 М.