UTM YATHETSA MGWILIZANO LIVE LIVE MOTI ZOMWE AYANKHULA NDI IZI

  Рет қаралды 115,588

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

26 күн бұрын

Пікірлер: 453
@ChrissMike-ws9lf
@ChrissMike-ws9lf 25 күн бұрын
Ma followers a UTM tilipo?? Ngat tilipo manja mmwamba 🙋‍♂️
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 24 күн бұрын
Thumb up
@clementmahoka6287
@clementmahoka6287 24 күн бұрын
Tilipo ife
@chimeraJonathan
@chimeraJonathan 24 күн бұрын
Pop L OLo Ok Oi
@chimeraJonathan
@chimeraJonathan 24 күн бұрын
​@@sarahmphande6108 😅ll
@masulasanudi7286
@masulasanudi7286 24 күн бұрын
❤ here
@kettiemkweu4528
@kettiemkweu4528 24 күн бұрын
My UTM fellow let’s gather here. Ndikuti 2025 I will be in Malawi all the way from America just to vote for my UTM UTM you got my Vote ❤
@Littlefair7
@Littlefair7 25 күн бұрын
Great move UTM family. Koma going forward tiyeni tidzipanga ma decision mofulumira, kunjaku nkwa mvula.
@PeterDandaula-ci5un
@PeterDandaula-ci5un 25 күн бұрын
Ndipo live
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 25 күн бұрын
Tiri pa mbuyo panu mama osaopa osatopa osafooka, ine sindinavoteko koma next year ndikavota, viva UTM viva mai kaliyati viva SKC
@user-rx1dj7kg8k
@user-rx1dj7kg8k 25 күн бұрын
Inenso ndukavota🎉
@RachelDongolosi
@RachelDongolosi 25 күн бұрын
Amen 🙏
@user-uf4hp6lu8t
@user-uf4hp6lu8t 24 күн бұрын
Am following you ❤❤
@paulmgombebanda-mr19sate
@paulmgombebanda-mr19sate 24 күн бұрын
Well done
@user-tk6qh9zs7h
@user-tk6qh9zs7h 23 күн бұрын
@@MariamJohn-dg4em palitu kusiyana pakati pa UTM ndi Malemu SKC. CHILIMA anapeza mavote okwana 1 million pomwe UTM ngati Chipani inapeza Aphungu Anayi okha basi.Ngakhale Kaliati anakanidwa kwawo pa Udindo wa u MP kamba koimira utm ndiye kumachangamuka pochita zinthu. Fame ya Malemu SKC si fame ya UTM as a political party.
@petermark6591
@petermark6591 24 күн бұрын
Ifeyo monga a UTM tasangalala kwambiri coz chotuluka mu tonse Kuti mzimu wa president athu achilima ukhale osangalala, glory to Jesus.
@LeganNyirenda
@LeganNyirenda 25 күн бұрын
Applause ❤mama for standing film against this alliance.
@fahadwalipeya8656
@fahadwalipeya8656 25 күн бұрын
Well done ife ndale zanu zopusazo zophanazo ayi UTM in our hearts forever 💕💕💯💪
@user-ri8em6my2e
@user-ri8em6my2e 25 күн бұрын
Boom !🔥🔥inuyo mwabwera ngati coming 💃💃
@ReferendumsWaya-y4q
@ReferendumsWaya-y4q 24 күн бұрын
5
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 25 күн бұрын
Great news,I am so happy you have made an excellent decision
@EvaDzimkambani
@EvaDzimkambani 25 күн бұрын
Well done UTM tili pambuyo panupo
@user-sm8gx4vf1v
@user-sm8gx4vf1v 25 күн бұрын
Amen and Amen kumwamba kulemekeze
@burtonjere-wn3qu
@burtonjere-wn3qu 25 күн бұрын
🔥 🔥 .. well done .. Bravo UTM !! U have my vote
@JenipherRapkani
@JenipherRapkani 24 күн бұрын
Congratulations akweni ambuye azikudalisan ndikulifunila ufulu dziko lanthu ❤❤❤
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 25 күн бұрын
Well done akweni may the almighty God continue to protect you❤❤❤❤❤❤❤❤
@constancemkandawire7378
@constancemkandawire7378 25 күн бұрын
Very good akweni mmakwana, will be waiting from you.May God go before us (UTM)
@louismagongwa
@louismagongwa 25 күн бұрын
mwaitha akwenei mukakamila za tonse allince mutha nose psiti
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 25 күн бұрын
Yehova alemekezake.., Mzimu wa Chilima use mumtendele❤❤❤
@alomuddin8801
@alomuddin8801 24 күн бұрын
A utm mwaganinza bwino 👍👍👍👍 osadya pamodzi ndi fiti ayi
@user-dm2fs6hf1b
@user-dm2fs6hf1b 25 күн бұрын
Well done my sister they is no way to keep on going with these monsters, we the followers shall never give up. UTM wozaaaa munya achule a mcp zombalangondo inu.
@isaacchagwa2917
@isaacchagwa2917 25 күн бұрын
Hono. kaliat you lead this political party,for its survival
@augustMag
@augustMag 25 күн бұрын
Mau amphamvu Mai Kaliati UTM meayitha🔥🔥🔥🔥💪💪♥️♥️
@TressLuka
@TressLuka 25 күн бұрын
Khaaaa UTM kuti buuuu. Wafwaaaa Chakweraaaa !
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 24 күн бұрын
Kkkkk wafwa chakwera mbuzi ya mnthu
@MirriamKambale
@MirriamKambale 25 күн бұрын
ULemu wanu akweni osabwelera mbuyo pa tsogolo ndi Utm keep keeping the SKC manefesto and try hard kukwanilitsa mzimu wa SKC uzausa mumtendere.
@marryphili5419
@marryphili5419 25 күн бұрын
Well done my people wina apenga misara Chaka chake chino
@HarryYottam-ft1bo
@HarryYottam-ft1bo 25 күн бұрын
Keep it up ndazikonda koma ndipemphe nawo Kwa akulu akulu a utm kuti mukamayamba convention, don't forget miyambi mizu yathu inamera pamenepo please
@user-ks3uw8gj8h
@user-ks3uw8gj8h 25 күн бұрын
2025 am going home only to vote for UTM well done guys hope our President Is smiling for the great decision which has been made🎉🎉🎉🎉🎉
@John-to8gl
@John-to8gl 24 күн бұрын
That is what i was waiting to hear from you guys I wish the team all the best and keep going forward 🙏
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo 24 күн бұрын
Mwachitad bwino kuchoka mofulumila mukanatafunidwatu nonse, kuganiza modzama❤❤
@EmmanuelNkosi-ts8bn
@EmmanuelNkosi-ts8bn 24 күн бұрын
Politics will never build Malawi its all about tilowe Boma tikatape basi, listen to Mkasa song very carefully
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 25 күн бұрын
Akweni osayiwala kuti ndalama inapha yesu remember that
@chifundopatrickkamwiyo5784
@chifundopatrickkamwiyo5784 25 күн бұрын
Keep the fire Burning.....utm 🔥
@user-jh8tj5in3y
@user-jh8tj5in3y 25 күн бұрын
Gulu lonse lomwe layima apa munthu ndi Publicity Secretary yekhayo! Ena anthu aphindu ajomba! kutha kwa Chipani!
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 25 күн бұрын
Congratulations utm ndi nonse atsogoleri takunyadilani asakunamizeni ndi timaudindo mukachoka maliro kumeneko
@sinoadedza6231
@sinoadedza6231 25 күн бұрын
Pambuyo pachipani Cha utm moto buuuu 🔥🔥🔥🔥🔥
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 25 күн бұрын
Congrats Akweni❤
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 25 күн бұрын
A president akhale madam kaliyati,and tonse takinzeka ku ka vota UTM, burning the fire alive ya SKC MHSRIP 🌹
@mkandawirem610
@mkandawirem610 25 күн бұрын
More fire bravo utm, apa zakhala bwino kwabasi
@dalitson3558
@dalitson3558 24 күн бұрын
I had never voted before but next year a’m definitely going to vote for utm
@user-cn3gi2vf5n
@user-cn3gi2vf5n 25 күн бұрын
That's great mama we are following you
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 25 күн бұрын
Congratulations.Mulungu akuyanganileni.Light and darkness do not stay together
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 25 күн бұрын
Mwakhwana guys uwo ndiye munthu ndipo maganidza booooh ngati Dr Chilima
@SueWahna
@SueWahna 25 күн бұрын
At aliyese osunga ndevu ndi wa UTM anena anena akweni😂
@user-ki1zz7gh5t
@user-ki1zz7gh5t 25 күн бұрын
Kkkkk wazaaa
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 25 күн бұрын
Uyuu sazatheka kkkkkk ndiye kunkuyunso ndiwa UTM kkkk
@ClementinaViola
@ClementinaViola 24 күн бұрын
​@@AlfredNazombe-me2ly ndevu za kunkuyu nzosiyana ndi za a UTM kkkkk
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 25 күн бұрын
AKWENI MOTOOOOO!❤ Mzimayi wathu okondeka olimba mtima wanthabwala ocheza ndi anthu bwino one ku mtima ziiii kumva bwino
@user-gr5zt6kw3s
@user-gr5zt6kw3s 25 күн бұрын
Well done
@UssenNjirinah
@UssenNjirinah 24 күн бұрын
Kkkkkk koma utm ndikawawa kusonyeza kuti manganya asala ndi udindo wokha ngati mulamba utatjawidwa ndimadzi....nambo eeeeeee zandiwopsa kkkk
@Vwalavwata
@Vwalavwata 23 күн бұрын
Indeed ndinayamba kusata za ndale chifukwa Cha Dr SKC may his soul rest in peace
@mabletungande349
@mabletungande349 23 күн бұрын
Am utm n my vote .....Fredo kiss
@RodneySupply-tx3ul
@RodneySupply-tx3ul 25 күн бұрын
Thank you so much elder and akweni for well articulated speeches I am glad for taking this direction, God bless UTM, osatopa, osaopa osafooka!!
@BlessMnyenyembe
@BlessMnyenyembe 25 күн бұрын
Ndanyadila, vote yangso mukhale nayo!!!
@macaleistkanjati-zw6cf
@macaleistkanjati-zw6cf 25 күн бұрын
Akusenda team ija kunooooo. YATHA TEAM!!!!
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 25 күн бұрын
I wish Mai awawa alamule dziko ❤ndale anaziyamba kale
@nafejonga972
@nafejonga972 24 күн бұрын
Me too dear❤❤❤
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 24 күн бұрын
Vuto ndilakuti dziko lililose Lili ndi malamulo oyendetsela dzikolo ndiye munthu akasankhidwa kukhala president amakasainila kuti ndiyendetsa dzikoli malinga ndi malamulo ndiye zoipa amakaziona atasaina kale koma manja awo amakhala omangidwa chifukwa Cha malamulo aja ndiye nthawi zambili munthu amakhaladi wabwino asanakhale pampando koma akakhalapo zimavuta kukwanilitsa zija analonjeza Zina chifukwa Cha malamulo adziko Nde poti lamulo limapangidwa ndi munthu kusinthidwaso ndi munthu koma ndipovuta ndithu kukoza ma mistake omwe adapangidwa zaka 20 zapitazo iweyo ukoze mu zaka 5 zinthuzi nzovuta kuzivetsa nde vutoso akangolawa ndalama anthuwa zose zija amaziiwala ndalama ndi satana ndithu idapeleka mwana wamunthu osalakwa
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 25 күн бұрын
Zimangondisangalasa chifukwa sitimakonda chipani ichichi anthu ake ndi oganiza komanso ndi antendele ❤❤❤
@fannyzimba149
@fannyzimba149 25 күн бұрын
Amen indeed akweni mulungu azikudalitsani ndipo akutsogolereni mzonse
@Jessica-pg6ep
@Jessica-pg6ep 25 күн бұрын
Mwachita bwino well done UTM Members Akweni umunthu mulinawo ❤timakukondani
@SamsonChafulumira-mv7og
@SamsonChafulumira-mv7og 24 күн бұрын
Chikangawa watsala ekha well done mama
@peternashyo9850
@peternashyo9850 25 күн бұрын
Great and wise decision, Viva UTM.
@nafejonga972
@nafejonga972 24 күн бұрын
UTM FOR REAL😂😂❤❤❤ VAZE VAZE WOYEEE😅😅😅
@dicksonndire1857
@dicksonndire1857 25 күн бұрын
God should be with the family of UTM,
@BlessingsGondwe-v9u
@BlessingsGondwe-v9u 25 күн бұрын
Koma kumeneko,,, 🥳🥳🥳🥳🥳 mwat wina satsegula mmimba kuseli,, go UTM go my vote 🔥🔥🔥🔥🔥
@VungaQueen
@VungaQueen 24 күн бұрын
🔥🔥🔥tili pa mbuyo Panu a utm 🔥🔥
@Mwizaso
@Mwizaso 24 күн бұрын
I've been waiting for this speech yooo🥳🥳🥳 the best decision ever 🥳🥳🥳🔥UTM Boma🥳🥳
@MariaNkhata-i9q
@MariaNkhata-i9q 25 күн бұрын
Weldone mama that's a very good movie ❤
@wizyrastah
@wizyrastah 25 күн бұрын
Tatuluka tatuluka anena anena basi
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 25 күн бұрын
Mwachita bwino akweni mwasiye agalu wokuphawo mbuzi za anthu
@OscarMkandawire-g1z
@OscarMkandawire-g1z 25 күн бұрын
Watching live from Mkwapasi Mbizi- St Augustine Mzuzu
@OsmanBakali-s5x
@OsmanBakali-s5x 25 күн бұрын
Kuzangoti khaaa🔥🔥 akasake ena oti awapatse .... Time over rise up Malawi
@faustascjfronha34
@faustascjfronha34 25 күн бұрын
Zikomo kwambiri UTM mupitireze ntchito za SKC
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 24 күн бұрын
U ar strong woman keep up mah don't afraid God will be with u akufuna moyo wanu ayamba ndiyeyo poti anazolowela kupha koma pano pokha tikumuwona ife aa
@GeorgeLipengaphiri
@GeorgeLipengaphiri 25 күн бұрын
Akweni timakunyadilani keep it up vote yanu ilipo basi
@ErnestChansa
@ErnestChansa 24 күн бұрын
Big point may kaliati ife ma sapota a UTM tizasangalala mugwilizano uthe basi ndi MCP plz ife tizava kukoma
@MercyChimaliro-fi6mv
@MercyChimaliro-fi6mv 24 күн бұрын
We are here for UTM. Let's gather here
@BrianJoe-z7u
@BrianJoe-z7u 25 күн бұрын
Ndakondwa kwabasi
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 25 күн бұрын
Mulungu akutsogolereni a utm akumenyeren nkhondo pamaganiz anu abwin✅❤️❤️❤️❤️❤️❤️🎉🎉🎉🎉
@ViserKabango-jt1hs
@ViserKabango-jt1hs 24 күн бұрын
Moreeee fireeee,go forward akweni, together we stand
@MphatsoPemba
@MphatsoPemba 25 күн бұрын
Uthe ngwilizano umenewo tipiliza kusatila utm
@RaphaelMaunde
@RaphaelMaunde 25 күн бұрын
Viva mama Kaliati viva UTM viva SKC💪💪
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda 25 күн бұрын
Chakwera umamupheranji chilima taona zakuderatu akuthawa Kkkķk. Ovotera mcp panopa sanabadwe mwna coz mbr yanu yanyasa. UTM woyeeee🎉
@yassinn5634
@yassinn5634 25 күн бұрын
Migwirizano ikumapha tizipani ting'ono ting'ono.Mukaona kuti simungapambane imani mwanokha ndi cholinga chakuti mupeze ma MP. Chipani chimalimba ndi ma MP ku parliament. Ndi 50+1 adzakufunani nthawi imeneyo
@Lemankais
@Lemankais 24 күн бұрын
Osaonetsa kufooka... keep going! Gud ting take time
@dalitson3558
@dalitson3558 24 күн бұрын
Akweni must be tsogoleri wa utm because she’s very clever
@margretsandey
@margretsandey 25 күн бұрын
Nkhaaaaa akwene mwabweratu mwa coming, my vote
@WilliamKude-oj4mi
@WilliamKude-oj4mi 25 күн бұрын
Tilinanu lomodzi mama more fire 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 you open gate please
@OmexAkim-ww9nd
@OmexAkim-ww9nd 25 күн бұрын
Mumakwana inuyo Mesa
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem 22 күн бұрын
Apo ndiye mwapitadadi ngati going muli boh
@SaidyKamala-jj7lo
@SaidyKamala-jj7lo 25 күн бұрын
Yaaaaaaa bola pamenepo mama uvota kulipo guys shuwaka never give up
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 25 күн бұрын
Amen 🙏, mwazunzika enough
@JoshuaMkandawile
@JoshuaMkandawile 24 күн бұрын
Very good news a Malawi 😊
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 25 күн бұрын
Well done uku ndiye kubwela
@rashidadan2533
@rashidadan2533 25 күн бұрын
Mmmh mau amai kaliyati sakundipatsa chilimbikiso , pali china chake chikubisidwa , but it's ok let's look the way forward . But remember l'am not politician .
@AaronChikonde-pk1hg
@AaronChikonde-pk1hg 24 күн бұрын
Kodi Michael usi anabwerapo kapena sizikumukhuza?
@charlesjimu6054
@charlesjimu6054 25 күн бұрын
Yes you need to partways with mcp
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 24 күн бұрын
Beautiful & bold decision!!! Bravo UTM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 25 күн бұрын
Mwachita bwino kutuluka, koma ndikuuzeni kut musamachite kudikira kut pafe munthu kaye then nkumapanga chiganizo. Koma mukanatuluka nthawi yomwe Chilima anali moyo chikanavuta ndichani??? Padakafunda padadyiwitsa galu. I hope a lesson has been drawn.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 25 күн бұрын
100% !, ndiye apa mupabge alliance ndi DPP, AFORD ndi UDF, basi mwamutha Chakwera ndi boma lake la MCP. Watizunza mokwana.
@madalitsochitekwe7786
@madalitsochitekwe7786 25 күн бұрын
Good move my Utm family
@ishmaelMangochi-zo8ks
@ishmaelMangochi-zo8ks 25 күн бұрын
The DC ananena kale kuti mgwirizano wathapo
@Andrew-nz9sh
@Andrew-nz9sh 25 күн бұрын
On by your side UTM 💪💪💪💪💪
@AmosBandula-up4yb
@AmosBandula-up4yb 24 күн бұрын
Nice one pic it up
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj 25 күн бұрын
Tiyiponyele kwakuya utm osaopa
@Tabitha-gs3mt
@Tabitha-gs3mt 19 күн бұрын
United Transform Movement (UTM) 2025 my vote 🔥
@YNOTGEORGE8
@YNOTGEORGE8 25 күн бұрын
❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉UTM woyeeeee
FULL SPEECH: Donald Trump speaks before the NABJ in Chicago
36:28
FOX 32 Chicago
Рет қаралды 369 М.
Fast and Furious: New Zealand 🚗
00:29
How Ridiculous
Рет қаралды 45 МЛН
WORLD'S SHORTEST WOMAN
00:58
Stokes Twins
Рет қаралды 127 МЛН
NKHANGA ZAONA ZIGAWENGA 6 ZABWELA MDZIKO MUNO KUDZAPHA KALINDO
12:03
Malawi Trends TV
Рет қаралды 3,8 М.
Vice President Chilima's visit to the SVTP (Chichewa Interview)
1:47
Shire Valley Transformation Programme
Рет қаралды 47 М.
Fast and Furious: New Zealand 🚗
00:29
How Ridiculous
Рет қаралды 45 МЛН