zionetsero Za Polisi Ku Blantyre

  Рет қаралды 12,012

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

lero Kunali zionetsero Za Polisi Ku Blantyre

Пікірлер: 129
@HenryBawah-zc3ss
@HenryBawah-zc3ss 2 ай бұрын
Tikutuluka aise zichani wayikazi kungotithela ma bundle basi
@christophermatemba2241
@christophermatemba2241 2 ай бұрын
please hanif tv tazipangani post zinthu za serious osati masanje mwayambawa
@collingskasanga4257
@collingskasanga4257 2 ай бұрын
Akusowa zochita
@user-zl9vj6hc6y
@user-zl9vj6hc6y 2 ай бұрын
Simungamupeze bakili muluzi t v... apolisi asanduka young pioneer
@usumanidaudi
@usumanidaudi 2 ай бұрын
Akozeke kt akubwera ku south Africa chifukwa kuno a marawi arikuno ndi okwiya ndi chakwera sikumarawi kuno akusakani anyamata kuno maro mosaka wa bakiri tv anyamata akusakani si ku Lilongwe kuno musamare🎉
@user-ll7fy1gz9m
@user-ll7fy1gz9m 2 ай бұрын
Good one❤🔥
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 2 ай бұрын
Kugwa mmanja mwa MULUNGU NDI NGOZI YAYIKULU. Apa ndizomwe Amalawi Anzanga tazionazi. Agule azipita
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 2 ай бұрын
Exactly
@bokaalfan9146
@bokaalfan9146 2 ай бұрын
Inu mwaika zichani izi police amakhala chochi.
@user-cp7hu6xu8h
@user-cp7hu6xu8h 2 ай бұрын
Zimene tikufuna ku malawi ndi zimeneso osamangogona one loom house Chakwera ndi ana Ake there billionare
@FrankKambwani
@FrankKambwani 2 ай бұрын
Phokoso lake limenero munthuyo ndiye sathawa😅😅😅Bakili Muluzi TV is for ever simungamugwire mukhalira kumangoyimba nyimbo dzolawuladzo chomcho kuleka kudzigwira mbava dzenidzeni Chakwera ndi nduna dzake wa😅😅😅😅
@adamusaidih8570
@adamusaidih8570 2 ай бұрын
Malawi ndiziko lotembeleledwa chifukwa cha chakwela
@amoschataika7440
@amoschataika7440 2 ай бұрын
Kokagwila wakuba sitilengedza mmudzi kapena kuchita phokoso. Naye amakhala okonzeka
@user-mw8dq4is6k
@user-mw8dq4is6k 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂Agalu achakwera Inu nyimbo zake .Palibe chomwe mungapange apa kadyeni chinangwacho chifukwa banziso simungakwanitse ndikasalary kanuko.zaziiii
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 2 ай бұрын
Koma mbulizi akachoka pamenepa akagula sugar pa 5 000 mbuzi izi
@PatieKates
@PatieKates 2 ай бұрын
Kkkkkk
@mtumikiJuda
@mtumikiJuda 2 ай бұрын
Poyamba ndinkakusatira nkayesa umakamba zoona koma ndiwe waboza.... Olo munthu opanda ubongoyo angakanike kudziwa kuti this was just a route match😂😂😂😂 Kamba ina ase.... Kwa amene amadziwa apolisi akumalawi, every Wednesday amakhala ndi afternoon run. Ndi sports day.
@mcdonaldgerard9707
@mcdonaldgerard9707 2 ай бұрын
Akupwetekesanipo zazii!!! Musiye mabanja anu nkhani zopusa ngati zimenezi kkkkk koditu oyamba kunenedwa anali Dr Bingu wamuthalika kubwelanso professor peter, palibe anamangidwapo kutanthauza kuti, anthu amenewa ankadziwadi kuti ufulu olankhura ndiofunika.
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 2 ай бұрын
Ndipo inu
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 2 ай бұрын
Bakili muluzi tv never arrested you just wasting you time guys this is home land😂😂😂🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂Mifuti yake Ngati mithiko yophikira paukwatitu😂😂😂😂😂😂😂😂 bwerani kuno ndi Chakwera wanu yemweyo ndi Chilima tizakudyeseni zipolopolo zoyenera
@alinafesalima5597
@alinafesalima5597 2 ай бұрын
Apolice akumalawi matama thoo koma salary ngati ndalama yogulira tomato okathira mundiwo
@user-bb5iy7ry5h
@user-bb5iy7ry5h 2 ай бұрын
Koma zowona amalawi ndalama imakusowesani chirungamo walakwanani munthu😢😢😢
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Mwakuliramo azibambo atatawo mungamaimbe zopusazo ? Waliranayo yolowalowa ndiy zichani? Zopusa bas
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Kuno mubwere ndipo mumutengenso Chilima ndi Chakwera tizakuphereni limodzi
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 2 ай бұрын
What's the meaning of this can you explain what going on??
@louisgolden
@louisgolden 2 ай бұрын
Awa a MCP Wa tilibe nawo ntchito osamaposita Apapa mwatani
@user-jy5sl8yr5n
@user-jy5sl8yr5n 2 ай бұрын
Police machende anu mukamugwira mundiuse just know that mukuyambaso you know president Sterling money
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 2 ай бұрын
Ndipo agalu inu olo manyanzi mulibe agalu zaziiiii
@LongiMtimabii
@LongiMtimabii 2 ай бұрын
Agalu achabe chabe mmalo molimbana ndiakuba omwe akuba m'bomao anyani
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss 2 ай бұрын
Apolisiwa alibe nzeru amangovomereza zili zonse nanga amumanga chifukwa nchiyan eeeesh
@user-gf7nj5cj8x
@user-gf7nj5cj8x 2 ай бұрын
wandithera bundle zopanda phindu zopanda mutu iziiiii
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Mmmm,abale,inu,amachita izi nthawi zonse palibe zoti akukagwila munthu apa, amalawi izi sidzinayambe,lero, ku zomba,olo ku lilongwe area 30 amachita.😂😂😂😂😂😂.boza amalawi linakula
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t 2 ай бұрын
Mfuti ikuchita kuposa nsonkhu wamunthu kunotu kujoni mfuti zimayenda machende sungaiwone
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Anamachende akuba achakwela akapolo adziko
@jameschipula4475
@jameschipula4475 2 ай бұрын
Akunsiya okuba ma billion akufuna wa social media guys be serious
@PrinceMapemba-fn4cw
@PrinceMapemba-fn4cw 2 ай бұрын
Akuti chaniso awa😂😂😂😂tilipo ambili eti
@innocentissah2636
@innocentissah2636 2 ай бұрын
Bola unakaika a police aku Mozambique osati ana ake a Chakwerawa ai
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 2 ай бұрын
Apa ndilinkati kulemba ndikuwona video angotumiza kumene bakili muluziyo agaluwa
@ibrahimatibu8784
@ibrahimatibu8784 2 ай бұрын
Kodi a police amenewa ndi ana eti izi ndi zichaninso izi kkkkkkkkk malawi are you serious to this country
@user-ir8dd8lm1c
@user-ir8dd8lm1c 2 ай бұрын
Zanziii
@MasharPablo
@MasharPablo 2 ай бұрын
naweso wayamba bodza Kodi?
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 2 ай бұрын
Akhuta maungu za ziiii
@mcdonaldgerard9707
@mcdonaldgerard9707 2 ай бұрын
Koma a police aku malawi mukusowadi chochita, mukufuna mumugwire munthu ngati waba, koma ngati musakudziwa tanthauuzo laufulu oyankhula kapena wazipani zambili, nacho chifukwa akungovomeleza / kududukira zilizonse wankulu wa police yo.
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 2 ай бұрын
Bweràni tikuonani kokuno😅😅
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 ай бұрын
Zausiru nga khare ine sanganipeze mumikhukumu kupusabasi
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 2 ай бұрын
Kuno NDE tikuphani straight
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 2 ай бұрын
Zisilu ndi chakwera yemweyo
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 2 ай бұрын
Mukampezera kuti muli naye pomwepo😮
@MundiwaGamuka
@MundiwaGamuka Ай бұрын
#MAHADAR 💪
@jamesgama5489
@jamesgama5489 2 ай бұрын
Zopusa chinangwanso chatani apa mxiii.
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 2 ай бұрын
Hanifa mukubowa sopano ndiye osamatihela data ndi Za zii.bolani chiwaya uja amatibwelesela nkhani zenizeni
@user-jx9ij8mr4p
@user-jx9ij8mr4p 2 ай бұрын
Nde mukut zionesero? Police sipanga zionesero musanamizepo anthu apa
@edenngoma8214
@edenngoma8214 2 ай бұрын
Hampton Bundle yanga 😢😢
@fredrickkhebozy6683
@fredrickkhebozy6683 2 ай бұрын
Komanso tuu iwee haniifa usamale usamango wapanga post mavidio opusawa..... Koddii zikukusangalasa issue yofuna kugwila wa channel cha Bakili muluziyooo
@user-cm8ji7im1h
@user-cm8ji7im1h 2 ай бұрын
Kuyambila president ndi omutsatila akee omse amisala mitu yawo siigwila Ntchito aaaa
@user-ev4or2kg4z
@user-ev4or2kg4z 2 ай бұрын
Boli zanu ndi chakwera yomweyo Ndikuuva kuwawa kwambiri mmene dziko langa likuchitira
@joshuachinguwophiri4779
@joshuachinguwophiri4779 2 ай бұрын
Anthu omwe they do publish this page they re all ibencile
@chikagwaharrison389
@chikagwaharrison389 2 ай бұрын
Zaziiii or soda zilibe
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Kusowa zochita a Malawi 😂😂😂😂😂, za chamba basi.
@falukujilani7545
@falukujilani7545 2 ай бұрын
Naweso wa hanifa wasowa zoyika eti tikutayatu
@user-ui6vh1ld4f
@user-ui6vh1ld4f 2 ай бұрын
Mifuti yake yomweyija ya kalekale yoti or munthu sangafe ayi
@chestermajora
@chestermajora 2 ай бұрын
kungomanga ameneyu kuzakhala ma demo a zaoneni
@user-cf7xb6xx5d
@user-cf7xb6xx5d 2 ай бұрын
Zaziii izi,kusowa zochita eti
@SamuerYohane
@SamuerYohane 2 ай бұрын
What happen the
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 2 ай бұрын
Iyi nde misala yeniyeni yosowa mankhwala
@user-xq1wd6wq5h
@user-xq1wd6wq5h 2 ай бұрын
Boma lauchitsilu kudana ndiinena chilingamo
@user-mm4fn8ln4r
@user-mm4fn8ln4r 2 ай бұрын
Zanziiii
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 2 ай бұрын
Hmmm za bodza izi musatibowe
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Zoona zimenezi koma?
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Mbuzi zakumalawi
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 2 ай бұрын
Akapolo achakwe
@IshmaelPatrick-xf7we
@IshmaelPatrick-xf7we 2 ай бұрын
Alondawa amasowa zochita zikalembani ma ganyu olima
@OmegaMussa
@OmegaMussa 2 ай бұрын
Akapolo ophunsa kwambili
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 ай бұрын
Kkkkkk
@Mbalingaplaste
@Mbalingaplaste 2 ай бұрын
Nde amugwira ngat
@samsonmfumu8132
@samsonmfumu8132 2 ай бұрын
Asowa vochita awa
@user-pl3tz1fe5g
@user-pl3tz1fe5g 2 ай бұрын
Ndiye phokoso limenelo akamupezako ? Kkkkkk zibwana zeni zeni
@rechealbracia-vk7np
@rechealbracia-vk7np 2 ай бұрын
Ana opusa dyaa timachenji
@LahimuChalema
@LahimuChalema 2 ай бұрын
Machende Ako iwe wa hanifu wasowa chochita et
@user-bb5iy7ry5h
@user-bb5iy7ry5h 2 ай бұрын
Akapolo inu akupasani ndalama zingati
@fredrickkhebozy6683
@fredrickkhebozy6683 2 ай бұрын
Pachakuti cha awoo pamozii ndi owatumawo
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 2 ай бұрын
Zisilu inu
@user-km5cl9xt2p
@user-km5cl9xt2p 2 ай бұрын
Ugalu bas
@Tawina0101
@Tawina0101 2 ай бұрын
Kom olo ndili ine angandigwile???? ODWALA DWALA NGT AWA
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s 2 ай бұрын
Awa agaluet
@HafizahHarack-bn3bf
@HafizahHarack-bn3bf 2 ай бұрын
Mmmxxxx manyazi bwanji
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 2 ай бұрын
Mtakataka
@franciscomalola9735
@franciscomalola9735 2 ай бұрын
akapolo
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 2 ай бұрын
Akulandila bwino munthawi ya chakwera mpake pitala amangomwa zunza vuto Ra DPP rimatukwana boma zikawavuta amathamangira komweko mupondedwa simunati utsiru wake umenewu anifa akukuonetsani mwina police ya Malawi simuidziwa mumadziwa kadeti yayi police Moyo phunzirani
@Zelinakhisswell
@Zelinakhisswell 2 ай бұрын
Tapitani kae ku xul mukaphuzire kulemba zoveka musanayambe kunyoza DPP
@user-lv8yi7dm1l
@user-lv8yi7dm1l 2 ай бұрын
Mumangidwa nazo zinazi amatelo nanga
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@liki-likiladies---lilongwe6963
@liki-likiladies---lilongwe6963 2 ай бұрын
Kumalawi nkokoma😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂Tikapuma kumwamba tikachita bwino 😂😂
@liki-likiladies---lilongwe6963
@liki-likiladies---lilongwe6963 2 ай бұрын
@@user-uc1pd1tc2x 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@user-cm8ji7im1h
@user-cm8ji7im1h 2 ай бұрын
Kkkkk ku Malawi ngati dziko lotembeleledwaa
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂Dziko ili linatembeleledwa koopsa ndimunthu olimba mtima mmmmmm😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
​@@patriciacraiton-sf5vuUlipo iwe?
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 2 ай бұрын
@@user-uc1pd1tc2x ndilipo INE wamoyo kkkkkk
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
@@patriciacraiton-sf5vu Wow!!! Thanks ndithu ndakuona osowa iwe kkkkkkkkkk
@georgeabigailmaseko-ts3fq
@georgeabigailmaseko-ts3fq 2 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣ndakayika kwambil
@MustapherLino
@MustapherLino 2 ай бұрын
Chakwera wa chamba kwa basi mpaka kutuma agaluwa
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 ай бұрын
Bodza ili awawaso angosowa zoika akutithera bundle kaya bro.
@danielsulani8689
@danielsulani8689 2 ай бұрын
😂😂😂🎉
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 2 ай бұрын
Zachamba kusowa zo Post
@stelliamkupa693
@stelliamkupa693 2 ай бұрын
Zauhule basi 😏😏
@user-vl8uw8mc3u
@user-vl8uw8mc3u 2 ай бұрын
Kupusa basi
@user-wd5tw1mz8h
@user-wd5tw1mz8h 2 ай бұрын
Chakwela upwetekesa ana kuno ndiku south Africa R10 yokho munthu amatha kuzima
@BleantSuwed
@BleantSuwed 2 ай бұрын
Fake you bro wangondionongetsa bundle machewo
@collingskasanga4257
@collingskasanga4257 2 ай бұрын
FAkE reporter reporting FAKE news unprofessional reporter cannot be reporting anyhow akuyenera kumasatira zomwe zikuyenera kumachitika and kumapanga report zomwe zachitika dzuro mumati akukusakan lero mukuti akupita kumademo which is which
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Abale mdichanitso kkkk
@AndrewMagombo
@AndrewMagombo 2 ай бұрын
Asowa zochita awa
MFUMUKAZI COMEDY  SERIES 21/12/2022
27:04
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 128 М.
Scary Teacher 3D Nick Troll Squid Game in Brush Teeth White or Black Challenge #shorts
00:47
마시멜로우로 체감되는 요즘 물가
00:20
진영민yeongmin
Рет қаралды 33 МЛН
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
TRAFFIC VIOLATORS CAUGHT RED HANDED BY DMP POLICE
12:40
ELEIÇÕES 2024 | Com Salomão Moiane | MBC TV
24:12
MBC TV
Рет қаралды 79 М.
JORNAL DAS 13 |EDIÇÃO DE SEXTA-FEIRA |26|07|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 27
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Zodiak Malawi
Рет қаралды 328 М.
mbava za ku malawi ndi mozambique zapanga ngozi pochokera kokaba
13:33
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 40 М.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 117 М.
TIMOTHY MTAMBO KUTHAMBITSIDWA NDIMAFUNSO UKU...
59:42
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 78 М.
Oyimba Omwe Amayimba Mosiyana Ndi Ena Onse
7:12
Sam Malvitha
Рет қаралды 25 М.
AMENYEDWA NDI MBAMA YACHIKWANJE KUMALO OBISIKA ndipo zadzetsa ulumari kumaloko.
46:18