ZOMWE AYANKHULA A NAMIWA

  Рет қаралды 47,426

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 98
@StevenMbama
@StevenMbama Ай бұрын
The real son of mother Malawi silvester namiwa keep it up brother plz don't give up
@yusufbanda4980
@yusufbanda4980 Ай бұрын
Lets support him wth anythng
@user-nn9mx5tt6d
@user-nn9mx5tt6d Ай бұрын
Namiwa your the best freedom fighter continue my brother my Allah protecte u
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h Ай бұрын
Namiwa uyu munthu wankulu kwambili kufotokoza mwambemve ndithu keep it up brother tiyamike uli moyo bomali chonde a Malawi tiyeni tichose
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Good Message 2025 Chakwela you go
@KelvinGuta
@KelvinGuta Ай бұрын
A Namiwa,ndakuthokozani zedi.Keep it up,popeza Malswi idakalibe ndi mzika zophunzira koma zoyimbira mmanja zinthu zachabe,mu dzina lokonda chipani ndi.........
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Chonde amalawi tiyeni timuchose Satana ameneyu tikapusa atimpha ndithu
@andrewmtendere3167
@andrewmtendere3167 Ай бұрын
Namiwa uku nde kuyakhula kosanyengerera muthu keep it up😊😊😊
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Inshort , In Malawi we don't have ACB , we have LCB , which means love corruption beurou , under tonse alliance corruption is worse than before . Chakwela him self is a leader of corruption and all the carbinet , We made a mistake to allow 9 parties to rulling Malawi , this time let's change ,
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Timakunyadilani mr.Namiwa, keep it up ❤
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Thanks Mr Namwiwa for talking the truth for the Malawi national keep it up
@lameckmphande-yt4ou
@lameckmphande-yt4ou Ай бұрын
Thanks namiwa gwilani nichito anthu alitolazikoli ngatilawo kuli mlungu kumwambaku azayankha pazomwe akutichila Ife a Malawi siku ndiimozi pitilizani kutimenyela nkhondo anamiwa washing in port Elizabeth South Africa
@mikekhamusi1807
@mikekhamusi1807 Ай бұрын
Koma ikazawinaso MCP ine ndizachokamo dziko mwanu muno
@KestonNGUBO
@KestonNGUBO Ай бұрын
Galu chokerathu iwe
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 Ай бұрын
I would love see if CDEDI works together ndi MALAWI FIRST
@lallanayahyakasakuadam8378
@lallanayahyakasakuadam8378 Ай бұрын
ine ndinachoka koma kungopitilira akapunyanyawa sindizabweranso
@user-mn3ev8rr6f
@user-mn3ev8rr6f Ай бұрын
Keep it up my best friend 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl Ай бұрын
Zoonadiitu aise bomali ndi manjiokhaokha kumkuyu pwalalake asatitenfengatiife ana chakwelaiwe pamako wamva
@user-qg4it7my9n
@user-qg4it7my9n 28 күн бұрын
keep it up i uyo ndi igwee cakwera acoke watikwana watching from cape town
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 Ай бұрын
Mr Namiwa always standing for the truth keep it up
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o Ай бұрын
Kod ndalama ija mmat chakwera abweze zilipat😮
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z Ай бұрын
Katundu wina mu group ya ma president aanthu osauka keep it up
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef Ай бұрын
Anamiwa , Mulungu azikudalitsani mumatiimilila a Malawi
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Mr. Namiwa, mtundu wa a Malawi ukudalila bungwe lanu. Bungwe la mphavu.
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
You good guys
@moyo77777
@moyo77777 Ай бұрын
Koma ndiye chakwera ndimbava Mmmmm osapanga mayazi😂
@BlessingsChitekwe
@BlessingsChitekwe Ай бұрын
Kuyakhula kwapamwamba kwambiri ❤❤❤❤❤❤
@user-gu8fx5gl3g
@user-gu8fx5gl3g Ай бұрын
There is no funding in many government institutions not only ACB.
@patsonmtalika1971
@patsonmtalika1971 Ай бұрын
Ndalama zathu amalawi akuwapa anthu akukasiya mwezi uliwonse akumalandila ndalama zosachepela 800 thousand kwacha ngakhale mwana akumalandila kumeneko k
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Keep it up we're tired of this government 🙏🙏
@DannielOnions-fy3dc
@DannielOnions-fy3dc Ай бұрын
Thanks so much keep GOING
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n Ай бұрын
dziko lathu likufunika zimenezi mwina pang'ono pokha zingasinthe. mwangochedwerapo pang'ono cos zinthu zambili zawonongedwa. keep it up aziakulu akulu athu. next time tifufuzilenso kumapasipotiku kut zikuti bwanji . dziko lathu lasakazika
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Mkukuyu ndimbuzi yamundu
@BhekiMavundla-po2bq
@BhekiMavundla-po2bq Ай бұрын
Big up Namiwa,izi ndizomwe timafuna kut tiziziwa mmene boma likupanga mu mphamva yaulamulo wake pothana ndikatangale.I'm fatigue with Chakwela and Tonse alliance regime, stupid!
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Ай бұрын
Apapa ndipamene mukufunika kuuonesa mtundu wa a malawi kuti inu mumaimirira , chomwe chinafunika anamiwa ndi kuyenda pamseu chakwera ndi nduna zake azipita uyu ngati sachoka ife tiuma mtima tikaphulitsa statehouse akafere momo ndi banja lake ndipo afa mozunzika koopsa ngati sasamala basopu chakwera
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo Ай бұрын
Tithandizene ife amalawi tikumvutika kwambiri asakungulenison ayi
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Chakwera ndi Chilima 2025 October akuzakhala kundende wait n c muzandivomereza mau angawa
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Ай бұрын
Anamiwa mumatha kuyankhula momveka bwino ulemu wanu aululen bas
@ForsterThawan
@ForsterThawan Ай бұрын
Agalu awawa ndiopanda nzelu ndipo akutinzunza kwabasi
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
😂😂😂😂 truck 10 million akunamiza ana oro probox siikukwani 😂😂😂😂
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Ай бұрын
Powerful!!!! 💪
@user-kr1tf2tu7s
@user-kr1tf2tu7s Ай бұрын
Mulira kwambiri akanganya simunati macadet
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Ай бұрын
Kukuyu ndichisilu chamunghu
@ChisomoSaiti
@ChisomoSaiti Ай бұрын
Boma la chakwera palibe zomwe likupanga
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Ай бұрын
Ife dzimene lkupanga mcp tatopa nadzo tingo vota mawa basi chakwela achoke machende amako chakwela ndi chilima
@ChristopherBauti
@ChristopherBauti Ай бұрын
Powerful
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Mwana wakwathu ameneyi kukaoichi simasewela ...pitiliza mwana wakwathu
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf Ай бұрын
Kodi onse achita zovundawa Sali Akhrisitu? Kodi kumakhala kukamutukwana Mulungu kapena chiyani? ANAMIWA pitirizani, kumwamba sikudzakhala chete.
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
Mwayakhura bwino
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
God bless you mr namiwa
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
You are true Malawians
@dymonleven7571
@dymonleven7571 Ай бұрын
Nkhani yabho
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Chakwera ndi Chilima ndimbuzi zonse
@nelsonmorris4352
@nelsonmorris4352 Ай бұрын
Ndi zisiru zenizeni ....zisiru zimenezi zaonjeza
@MathewsMynus-ow6no
@MathewsMynus-ow6no Ай бұрын
2025 mbava zichoke bas
@tasmania527
@tasmania527 Ай бұрын
Alomwe mwagundika ndi kulongolola.
@Johnybegood260
@Johnybegood260 Ай бұрын
Nanga ku immigration ?
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq Ай бұрын
Mwauze amabungweo pamtumbo pao,
@OscarPickay
@OscarPickay Ай бұрын
Kkkkkkk
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Ай бұрын
Ife tikufuna tivote may 2025
@Johnybegood260
@Johnybegood260 Ай бұрын
wayaimba bwinotu bola usapange za nthambo ndi nzake trapezi
@fahadmilanzi
@fahadmilanzi Ай бұрын
Morefire sir
@susantembo2076
@susantembo2076 Ай бұрын
You get ideas from someone’s performance. So the performer becomes a hero
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
Nipite ndine
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 Ай бұрын
The first beneficiary of Corruption is himself how can he fight against something he is benefitting from it
@KereeditseMotsetse
@KereeditseMotsetse Ай бұрын
Agalu amenewa amangidwe
@OscarPickay
@OscarPickay Ай бұрын
Mmanja mwanu big
@user-ix7pb6hk2w
@user-ix7pb6hk2w Ай бұрын
Mademo anyoh achitike ndipo amalawi osalora , tiyeni mpasewu
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
Indee bwana ife tilipo
@BosscoNgwira
@BosscoNgwira 21 күн бұрын
Priz do not give Malawi is in fire
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n Ай бұрын
makamaka Moses kumkuyu nde Mmmmmm he is the one amene dziko lathu walisakaza mopanda chisoni. mmene mwanenera kut amalankhula ngat zanzeru Koma ali munthu wopsa kwambili. Amose dziwani kut anthu amaziwa zomwe inu muli. Yahweh wakumwamba ndiyemweso akuziwa kuposa ife anthu Za inu. you don't even fear God maka pakutenga Mbali yakuwononga dziko. Mene Mene tekeli ovasin
@Jongwenyirenda
@Jongwenyirenda Ай бұрын
Chakwera must go (.....
@BerthaBerhar
@BerthaBerhar Ай бұрын
Following
@MastaraMedisoni
@MastaraMedisoni Ай бұрын
❤❤❤❤❤
@shealtielmajawa8234
@shealtielmajawa8234 Ай бұрын
Athu ambiri mdziko lino alibe nzeru
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Ай бұрын
Mr Nawiwa son of the soil
@user-qp5mu7ui2c
@user-qp5mu7ui2c Ай бұрын
Umakwan kwambiri hot 265
@AffickChaona
@AffickChaona Ай бұрын
Namiwa katundu
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Mkukuyu ndimbuz
@user-nx6dk4bj8v
@user-nx6dk4bj8v Ай бұрын
Iweyo ndikape wanva
@user-qv8sp5cz5x
@user-qv8sp5cz5x Ай бұрын
Iwenso ndi chislu ngt uyo ali kape
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Ndipo ndigaru weniweni kunkuyu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
​@@user-nx6dk4bj8vIwe nditombolombo zedi ndithu
@royGovender-vl9on
@royGovender-vl9on Ай бұрын
Kuwina a chakwela 2025.sindidzabweranso Ku malawiko
@Sophisticate230
@Sophisticate230 Ай бұрын
Kawawa Namiwa❤
@NEBERTMVULA
@NEBERTMVULA Ай бұрын
If Malawians are democratically empowered why NOT dethrone now the poor leadership they voted into power when incompetent? STOP MCP STOP MCP STOP MCP!! this is not a go area in life of Malawians
@LyfordCydseorg
@LyfordCydseorg Ай бұрын
Hope we are still having challenges to fight corruption in this country. Let's just leave this work in the hands of Namiwa but let's all join hands to fight corruption. Malawi will remain poor as it is for ever and it will also very difficult to achieve our 2063 Vision.
@MrChiniko
@MrChiniko Ай бұрын
9. Sw
@GabrielGasiyo
@GabrielGasiyo Ай бұрын
Chakwela 2030 woo!!! Anamiwa aba kwambiri pa msamba parish
@user-on5qq9tg1y
@user-on5qq9tg1y Ай бұрын
Bola namiwayo amaba pa parish koma mbuzi chakwera akutibera misokho yathu
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Kudza mwa coming ❤❤❤
@LovelyGalaxy-rb7yl
@LovelyGalaxy-rb7yl Ай бұрын
Ife tili pano kumvesera kut tiziwe zonad
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Moses Kunkuyu nditombolombo okumwa madzi n'kuthako
@RashidKusum
@RashidKusum 25 күн бұрын
Nkhondo ya ku yukreni iti khuzabwanji a Malawi
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Ай бұрын
Powerful
@IshmaelJambo
@IshmaelJambo Ай бұрын
Koma chakwela atule udindo pansi
Kodwa's resignation a bit of "surprise" - Swana
6:04
Newzroom Afrika
Рет қаралды 7 М.
Double Stacked Pizza @Lionfield @ChefRush
00:33
albert_cancook
Рет қаралды 80 МЛН
Задержи дыхание дольше всех!
00:42
Аришнев
Рет қаралды 2,1 МЛН
Former Comedian, Micheal Usi, Sworn-In As Malawi's Vice President
1:07
TVC News Nigeria
Рет қаралды 26 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 187 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
ZISAKHO ZAKU MANGOCHI ZODABWITSA ANTHU🙌🙌
28:38
HOT 265
Рет қаралды 20 М.
Baba Harare - Vazivi vekumabva Zuva Ep 04
6:25
PSTV Entertainment©
Рет қаралды 171
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
Times 360 Malawi
Рет қаралды 240 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 128 М.
Resignation Of SA Top Minister & ANC Heavyweight Shocks SA
2:43
Hot Current Nduna Yoona Zachitetezo Cha Mdziko Wamukalipira Brian Banda
1:03:23
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 138 М.