No video

Zomwe ayankhura a mavuto Bamusi madzulo pano pakutulula kwa Dalitso Kabambe ku Dpp

  Рет қаралды 4,923

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 22
@davidwakhokamoto1124
@davidwakhokamoto1124 Ай бұрын
Ku Dpp kulibe zimenezo athuwa akugofuna kukhala atsogoleri mwa fast Mr kabambe akupita ku utm aona kut kulibeko president
@blessbless6929
@blessbless6929 Ай бұрын
Sometimes we die fast zadala just because of befu. Have patience guys, kulamula dziko it's not like kukhala pabanja kapena kutsogolera church. Lekani kutsutsana ndizomwe nyimbo yafuko lathu imakamba. Chotsani msanje paamene ali patsogolo panu ndipo dikirani nthawi yoikika. Owufunitsitsa saupedza. Gwanda Chakuamba, John Tembo, Just Malewezi and many others including Brown Mpinganjira anayetsapo koma sanapange succeed. Let me not mention about Absalom, well deserved to be a successor to be on Peter Muthalika's throne koma phuma lofuna kutsogolera fast anakagwera mudziwe lang'ona imfa inali yomweyo and all his vision was dead. One might come out to proceed his vision but won't match his capacity of leadership and love for his country. Mukachuluka dyera ndi ndalama, ndalama zikuphani. Oyendayendatu sumera ndele izizi muzazindikira bwino patsogolo mawu angawa akazaphelezera. Always remember also kuti pachoka mzako pali malo, as soon as you leave, a replacement is in nthawi yomweyo and you'll be forgotten. Ufumu owukirana okha sumaima. Dekhani enanu lolani mmodzi amene alinawo masomphenya ophula Malawi pamoto atsogole ndipo tigwirane naye manja kuti Malawi wathu akhale okomanso. Nthawi sichedwa kutha, mukanazalamulirabe ngati mukanadekha koma komwe kukupita inuko simuzalamulanso chifukwa muzazindikira bwino patsogolo
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev Ай бұрын
Gogo tsala ndi mpandowo tidzawonana👍
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
Khalamba yopanda mano yangakhala yokha ndi anamalomba basi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo Ай бұрын
Was just a member like me..
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Ай бұрын
Usogoreri ndi mphatso yapadera yomwe imachokera kwanamarenga
@PeterPhiri-di1ux
@PeterPhiri-di1ux Ай бұрын
Takangolowani komŵe mukufuna musaipise mbiri zachipani chomwe chimakusungani ndinu achitsiru
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 Ай бұрын
Welcm to UTM bro
@GoodsonLindani-gf8pn
@GoodsonLindani-gf8pn Ай бұрын
Tazingopitani mukathele komweko, Ndale mwaziyamba liti a kabambe.koma APM mukumutola chifukwa samalankhula mukachita zovunda zanuzo.anzanuso anachoka kukajowinana ndi njoka yawaluma.tiyenazoni.
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
Kabambe has started his end of journey in his political career just like Brown Mpinganjira, Nankhumwa, Jessy Kabwila and others.
@elizasingano
@elizasingano Ай бұрын
Ndipo ayende bwino amafuna afikira pampando waupresident aaaaaaa aphinzire kaye ndale ameneyo
@ClementZintula-wi4tz
@ClementZintula-wi4tz Ай бұрын
Move
@juntoiman
@juntoiman Ай бұрын
Awa asatinyase Ngati akufuna mpando wa President angoyambisa chawo Sizoti azitipwetekesa mutu ku DPP ku
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 Ай бұрын
Cool bro😂😂😂😂😂😂😂uyu akufunika ku camp kwathu.
@jamestembo6724
@jamestembo6724 Ай бұрын
Mwayisiya yokha nkhalamba ku dpp azafera Pampando
@robertkalima874
@robertkalima874 Ай бұрын
Isiyeni nkhalamba yokakamira. Ikufuna idzafere pampando
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Achoke kumene uyu tela kuwili
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx Ай бұрын
Tsalani ndi nkhalamba yopanda manoyo asaaa
@Yoxym
@Yoxym Ай бұрын
Achisilu inu
@joelmakwinjakambalame9652
@joelmakwinjakambalame9652 Ай бұрын
Malawi amadabwitsa mwano umenewu umachokela kuti chonsecho ati ndi dziko la chinkhilisitu komaso iwe unena a Gogo anzako opanda Manu iwe ulibe agogo komaso ukupita komweko Ngati ungadzafikeko
@robertkalima874
@robertkalima874 Ай бұрын
@@joelmakwinjakambalame9652 ndikadzafikako ndidzakhala pansi
Люблю детей 💕💕💕🥰 #aminkavitaminka #aminokka #miminka #дети
00:24
Аминка Витаминка
Рет қаралды 662 М.
Zombie Boy Saved My Life 💚
00:29
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 29 МЛН
白天使选错惹黑天使生气。#天使 #小丑女
00:31
天使夫妇
Рет қаралды 15 МЛН
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 240 М.
Malema addresses Gauteng EFF members
1:25:51
SABC News
Рет қаралды 269 М.
Люблю детей 💕💕💕🥰 #aminkavitaminka #aminokka #miminka #дети
00:24
Аминка Витаминка
Рет қаралды 662 М.