A Mwakasungula Musaletse Anthu Kulankhula - Steven Simsokwe

  Рет қаралды 4,467

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

27 күн бұрын

On 10 July 2024, Concerned Citizens of Malawi are calling for nationwide demonstrations, and renowned Governance and Human Rights Activist Undule Mwakasungula has disapproved of the plans, instead calling for contact and dialogue. However, Steven Simsokwe believes that Mwakasungula is in no position to tell Malawians when they can protest.
Pa 10 July 2024, a Concerned Citizens of Malawi akufuna ziwonetsero m’dziko lonselo, ndipo katswiri wodziwika bwino omenyela ma ufulu a Undule Mwakasungula wakana ndondomekoyi, m’malo mwake wapempha kuti anthu akambirane ndi boma. Komabe a Steven Simsokwe akukhulupirira kuti Mwakasungula sangawuze Amalawi nthawi yomwe angapange ziwonetsero.
#malawi

Пікірлер: 34
@MerryWayson
@MerryWayson 25 күн бұрын
Sitilila wapanseu bas maddemo pa 10
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 25 күн бұрын
Kufa kufa mademo alipo go konko ku state house ko nkukamalizila kwa anthu awa Zikhale Kunkuyu Chimwendo Mkaka Kudzamalizila kwa mbuzi Mwakasungula Osaopa osafooka osatopa!!!
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 25 күн бұрын
Walowa M'maganizo mwanga
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 25 күн бұрын
Ndi Munthu oipa ntima Mwakasungula
@JuaryMbisa
@JuaryMbisa 25 күн бұрын
Ameneyu akalamba asiyeni azingona pakhonde pakepo
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 26 күн бұрын
Powerful 👊
@vincentmalaulo4046
@vincentmalaulo4046 23 күн бұрын
🇲🇼💪💪💪
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 25 күн бұрын
aNyasatimes munasiya kuika maComment lol
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n 25 күн бұрын
go komko kumademoko.. enough is enough. kwakwana kwakwana
@MerryWayson
@MerryWayson 25 күн бұрын
Sitilora ngat akupasa ndalama udye Ife sitinadyenao ndipo sitingadye achoka pa mpando Chakwera Ife wapanseu bas
@RamseyWasi
@RamseyWasi 22 күн бұрын
Honestly. Mademo asakhaleepo. Amene akulamuliilaao mudaachitanso mademo kuti asakhaleepo iwowo kusonyeza kuti amene adaalipoyo ngoofoyira koma uyu .ndye tuudandawulano Chiyani. Tell me more ,tuuganiza kuti wabwino ndindan. Popeza aliyense amakhala akutukwanidwa kapena kulemekezedwa ngati dera lakwathuulo atachtapo kenakake kapena sadachitepo chilichonse. TISANKHENO NDAN??
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 25 күн бұрын
Mandemo alipo achamba basi ifeai ingodya ndalamaso sabomaso ndiposa kuba mademo alipo ndipo ife mtimtulika pa10 July ameaku nena kumti mandemo asachimtike ameneyo machende ake fokof💪💪
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 25 күн бұрын
Amusukwe mkunena zoona akambe iweyo kukupha chifukwa sitiwona mayankho amadrmo amangophesa anthu ndi kuba katundu mmene mnayambila mademo mwapindula chiyani ndiwe chisilu ngati alomwe
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 25 күн бұрын
Meakasungura anagulidwa ndi boma so lilime lake linasitha zochita!!
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 25 күн бұрын
Galu ameneyo azingodya ndalamazo koma asatinyase kulesa mademo mbuzi imeneyo pano amalawi akuvutika kwambili mbuzi imeyo ingalese mademo
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 25 күн бұрын
Awmakasungula pathako pinu
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 15 күн бұрын
Mwakasungulayi akudya zomafuta nde akumasuka kulankhula chifukwa ali boma
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 25 күн бұрын
Kod agalu amenewa MCP sakufa bwanji aaaaaa atopesa bwanji
@anifoiuene6301
@anifoiuene6301 25 күн бұрын
Chakwera chonde liuzeni dziko komwe kuli black box yomwe inali mundege yomwe inanyamula ntsogoleri (vice president) Dr Saulos Chilima pamodzi ndi anthu 9 aChakwera inu ngati kholo ladziko lino la Malawi chonde tiuzeni komwe kuli black box
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 25 күн бұрын
That wizard can't reveal
@user-uf3qh3vn1e
@user-uf3qh3vn1e 15 күн бұрын
Muzangomupangira madewo panyumb
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 26 күн бұрын
Masungula fiti yamunthu pamodz NDI chakwera mademo alipo
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 25 күн бұрын
Masungula ndiwe mbuzi ife sitiimva achoke president wakoyo sitikumufuna ife
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 25 күн бұрын
Ngati akupatsa ndala zitsilu zinzakozo uzingodya ndalamazo usatiuze zochita ndiwe galu kobasi
@JuaryMbisa
@JuaryMbisa 25 күн бұрын
Paja mwakasungula akulandila dollar ku mcp
@user-iv4dj1pi3b
@user-iv4dj1pi3b 26 күн бұрын
Mwakasungula ndi gwape.. Ma demo alipo ndipo tipanga ... osaopa Osatopa Osafooka
@MerryWayson
@MerryWayson 25 күн бұрын
Amalawi tiyeni tizuke Mwasungula amupasa ndalama ameneyo Chakwera waketo
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 25 күн бұрын
Mwakasungula ndi kape kwambiri
@alexsumani6823
@alexsumani6823 25 күн бұрын
And this Mwakasungula guy makes me sick to be frank
@rexnyalugwe4910
@rexnyalugwe4910 25 күн бұрын
compromised
@happymumba2261
@happymumba2261 26 күн бұрын
Mademo achitike basi palibe zolesana
@MasegoModukanele-xg2hj
@MasegoModukanele-xg2hj 25 күн бұрын
Mademo achani mufuna kukabelapo thawi yachisakho yafika kale kapena mukuwopa ?zisakho thawi yatha lale
@petertaulo8014
@petertaulo8014 25 күн бұрын
Iwe pump pumbwa eti!
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 25 күн бұрын
Zisankho zake ziti zomwe ukunena iweyozo?. Mmesa mungolembana kucentral kokha mzigawo zina mukuletsa kulemba anthu, mukuwopa ndinu anyawu a gule kwawo inuu pamt........bo panu . Mademo go komkooo
39kgのガリガリが踊る絵文字ダンス/39kg boney emoji dance#dance #ダンス #にんげんっていいな
00:16
💀Skeleton Ninja🥷【にんげんっていいなチャンネル】
Рет қаралды 8 МЛН
ЧУТЬ НЕ УТОНУЛ #shorts
00:27
Паша Осадчий
Рет қаралды 8 МЛН
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 9 МЛН
Why #RutoMustGo Will Not Materialize~ Robert Alai
39:00
KTN HOME
Рет қаралды 553
LIVE: Donald Trump speaks at MAGA rally in Michigan
1:43:56
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 571 М.
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,8 МЛН
Wina Ndinamuthyola Khosi - Samuel Lwara
14:15
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 42 М.
MBIRI YA DR  MICHAEL USI, KODI USI NDI NDANI?
4:14
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 15 М.