No video

AFORD AKUPEPHA UTM KUTI APANGE ALLIANCE- ZOMWE ZAYANKHULIDWA KU NSOKHANO

  Рет қаралды 23,062

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 66
@RachelDongolosi
@RachelDongolosi Ай бұрын
Amen 🙏 mawu amphavu Mulungu akutetezeleni azitsogoleli amene mukuimila a Malawi osaopa Mulungu alinafe
@BlessigsChabzola
@BlessigsChabzola Ай бұрын
😊09
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga Ай бұрын
MTAMBO kakhaleni kunyumba...tinatopa nanu.AFORD SIYINGAWINE MWANA WAWUPANDU IWE..UMVE ZIMENEZI KOMWE ULIKO
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu Ай бұрын
ubwino wake simukavota nokha
@user-fl6zc5gz5r
@user-fl6zc5gz5r Ай бұрын
Ndilibe lawyer mkanakuyankha
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 28 күн бұрын
Utm udf my vote
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
That's good l dea God be with you we love you pangani gwilidzano Ife tili pa mbuyo Pano
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
UTM ikuyenera ibwerele ku DPP ndipo Ife angoni a ku Ntcheu tili ready kudzawavotera DPP Pamodzi ndi UTM ngati alliance
@KikaImran
@KikaImran Ай бұрын
You re very right. Sindinavoteko and if DPP coraborate with UTM i ll vote for them though am 100% sure that andale ndi oipa onse, they re there for their empty bellies
@chrispinechirwa2655
@chrispinechirwa2655 Ай бұрын
Vyakuyoghoya vya mtambo ni boza lekha😢😢
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh Ай бұрын
Iwe Mtambo leka bodza unatiputsitsa padzana kulankhula ngt zamzeru kma sitingakhulupilire munthu ngt iwe
@WatipaCawinga
@WatipaCawinga Ай бұрын
Magufuli wathu kupoto
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Alliance tapanga kale ndi UDF musavutike ❤❤❤❤
@marthaphiri3600
@marthaphiri3600 Ай бұрын
Join hands with all the opposition parties, gawani mipando molingana campaign wisely win 2025.
@LuwisKaigwaze-gr6cg
@LuwisKaigwaze-gr6cg Ай бұрын
Musayembekeze kuti mudzalamulira dziko lino aford
@Donnex-gn2sf
@Donnex-gn2sf Ай бұрын
Aford akuwona kuti ku UTM kulibe utsogoleri komabe sizingatheke chifukwa a Aford akufuna mpando and UTM nayo yikufina mpando 🤣🤣🤣🤣
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Ife tapanga kale ndi UDF musavutike 😂😂😂😂😂
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Ай бұрын
Yambani zomwe mukunenazo musanalowe muboma ,kenako Anthu adzakhulupilila Kuti mukufuna kutukula dziko. Anthu Andale inu mumangotizunza,Anthu wovota kumabvutika inu Ana anu akuphunzila kunja
@jamessoko9480
@jamessoko9480 Ай бұрын
Aaaaaaa....,ndimo mukuyowoyela mwa wandyale. Pa mupando khale waka,kujikuzga kwake uko,mwaluwa ivyo mukapangana.
@JumaGadaff
@JumaGadaff Ай бұрын
Mulungu wamakamu kanthani onse omwe adzunza nzimu wa skc lest in peace ndipo chauta langani ndithu
@josephgabriel1016
@josephgabriel1016 Ай бұрын
Timothy sangatinamize for the second time.....
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Ай бұрын
I don't trust NTAMBO ,NTambo vuto nngosamudalila Komanso nkovuta kumukhulupilila uyu . Ife aMalawi mukanakhala Ngati Bingu ,mmali ndi munthu wosavuta ,kungomupangila njira ya chakudya basi ,President ameneyo adzakhala WA muyaya. Ngati dziko Lili ndi chakudya ,ma business amayenda BWINO .Koma aaaaa uyuyu ayi mwina
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Ngakhale banja limayenda bwino ngati chakudya chikupezeka. Zovala ndi zina zimaphweka kugula.
@johnussenu2848
@johnussenu2848 Ай бұрын
Utm and udf boma
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Chihana is my vote
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o Ай бұрын
Munthu oyipisitsa mtima Timothy sitingakumvere
@PeterPhiri-u7h
@PeterPhiri-u7h Ай бұрын
MuKufuna alliance mukuopa chani
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 Ай бұрын
Wabodz uyu Mumater mukamafun mavot Mumakhal ngat anthabwino Chilimanso amater Chakweranso amater
@BestonChagala
@BestonChagala Ай бұрын
Regionalism inamkanika chihana ,you can't win the national presidency without people from other regions.Nthawi zina musanayankhula mudzikhala Kaye pansi nkuuzana kuti kodi izi ndizoyenera kudziyankhula pagulu?Mukuti unduna simukuufuna chonsecho mukudziwa kale kuti simungadzawine u president wa 2025.Ngqkhale iwe mtambo pa ticket ya AFORD sungawine kuchitipa u mp ,nthawi imene munali nduna palibe chomwe munawathandidza anthu aku chitipa
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd Ай бұрын
Tiyeni tikavote mwanzeru mcp must go.
@IshmailDukuturu
@IshmailDukuturu Ай бұрын
Mbuzi iyi Timothy
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Utm & UDF Boma 2025 ❤❤❤❤❤❤❤❤
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga Ай бұрын
Mtambo NDI MBUZI...mavuto alipo panowa,anyani akulamulira panowa..mesa anawathandizila kukhala pampando ndi iyeyo😂😂
@BwanaGD
@BwanaGD Ай бұрын
Komatu mtambo munthawi ino ukanankhala chete kaye munalumbwa kwabili nthawi inja ife kukopeka nanu lero munagopita kukamuphetsako chilima inu kumabwerako ndiye muliena nthawi inoyo mukanadenkha kuyamba kulingalira pazomwe munachita aaa
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e Ай бұрын
Amen 🙏
@ntombiunice8637
@ntombiunice8637 Ай бұрын
Mtambo ndikhuluku...u minister unamurephera
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Ай бұрын
Zimenezo2 zithera konko mwene
@user-bv8wo2fn4e
@user-bv8wo2fn4e Ай бұрын
I hope if all mupoto must vote for AFORD
@yassinn5634
@yassinn5634 Ай бұрын
Mtamboyu akunena zoona nthawi Chihana Senior UDF imamunyengerera chifukwa Chihana anali ndi MP ambiri anali ndi mphamvu koma chifukwa chakugawanikana alibenso mphamvu
@BestonChagala
@BestonChagala Ай бұрын
Koma a Enock muchenjere ndi mtambo,mugawana zida 2025 isanafike chifukwa aliyense akuyankhula ngati ndi president payekha.Nanga mmene akuyankhulira mtambomo akuyankhula ngati vice president wa chipani ngati?Akudziwa kuti kupatula Ku hrdc sangayambitsenso gulu lina lotchuka paokha,nchifukwa chake asankha AFORD.Akuti safuna mpando chonsecho amayankhula ndi zodiak kuti afuna Udindo ngati platform yoti adzikhala influential
@user-rg9zc6eo2q
@user-rg9zc6eo2q Ай бұрын
My vote afod
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune Ай бұрын
Join
@yassinn5634
@yassinn5634 Ай бұрын
Chipani cha UTM chija ayamba kuchikanganirana. Chizungu chake SCRAMBLE FOR UTM. Ena apita kwa Aford, DPP ndipo ena atsala ku MCP. Thats my opinion. You got yours take it or leave it.
@Syakinongwa
@Syakinongwa Ай бұрын
Team up and cartel leadership positions within your team. Otherwise forget individual-party leadership as there is no way you can beat MACOPA.
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
Mtambo mpaka kumuziwa Mulungu kkkkkkkkk ndale ndizovuta
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Bomo ylo ❤
@HappyAntenna-sf9qx
@HappyAntenna-sf9qx Ай бұрын
iweyo ukumenyela ufulu wako ndalama zakuthela
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 Ай бұрын
Move
@BestonChagala
@BestonChagala Ай бұрын
Vuto ndiloti ena pa imfa ya chilima afuna kutchukirapo.Aford yakhala zaka 30 but no progress koma pano they are claiming to be friends of chilima just to capitalise on the direction less supporters of utm.Ku AFORD kuli ndani odziwa ndale kuposa kaliati?And in terms of popularity utm ili pa mwamba kwambiri kuyerekeza ndi AFORD
@user-wk7ut7ld1x
@user-wk7ut7ld1x Ай бұрын
Mtambo you are Malawian julias malema and your party aford you get 9% of the votes that is my prediction
@BrightNyoni-yd4ip
@BrightNyoni-yd4ip Ай бұрын
Mumakwana a hot 265 watching you from lusaka Zambia twatotela sana
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h Ай бұрын
Koma chaka chino ziliko ndithu.
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Kkkkk mtambo sungatunamize adah ndife a utm we are together with DPP
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
I agree with you 100%❤❤
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h Ай бұрын
Koma a Mtambo akunena zoona kuti samafuna mpando? kkk
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
🫡🫡🫡🫡🫡🫡
@MosesNyalugwe-ll8hh
@MosesNyalugwe-ll8hh Ай бұрын
Maloto achumba
@chrispinechirwa2655
@chrispinechirwa2655 Ай бұрын
Ili ni lirombo yayi 😂😂😂😂
@VungaQueen
@VungaQueen Ай бұрын
Kkkk😂😂😂😂😂
@emmanuelsambo1158
@emmanuelsambo1158 Ай бұрын
It was only SKC
@TiyesNayuma
@TiyesNayuma Ай бұрын
Chitsilu iweyo you failed as a minister
@chrisgremu740
@chrisgremu740 Ай бұрын
Ndiye Chakwera akawinaso 2025 Mutani?
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Ай бұрын
Sangawine mark my words
@user-eh1gn1nj9d
@user-eh1gn1nj9d Ай бұрын
Kodi imfa ya Chilima mukupangira campaign Mulungu akukanthani ndithu
@HappyAntenna-sf9qx
@HappyAntenna-sf9qx Ай бұрын
iweyo ukumenyela ufulu wako ndalama zakuthela
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h Ай бұрын
Koma a Mtambo akunena zoona kuti samafuna mpando? kkk
A RICHARD CHIMWENDO BANDA KUNG'ALULA DPP
25:45
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
ПОМОГЛА НАЗЫВАЕТСЯ😂
00:20
Chapitosiki
Рет қаралды 28 МЛН
My Cheetos🍕PIZZA #cooking #shorts
00:43
BANKII
Рет қаралды 27 МЛН
Logo Matching Challenge with Alfredo Larin Family! 👍
00:36
BigSchool
Рет қаралды 21 МЛН
HOT CURRENT YA LERO 🔥🔥🔥🔥🔥
59:36
HOT 265
Рет қаралды 26 М.
Interview ndi Norman Chisale
1:05:22
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 236 М.
BON KALINDO LERO 🤔🤔22 August 2024
16:09
HOT 265
Рет қаралды 7 М.
CHIPANI CHA UTM CHALIMBA MTIMA.ZILI KU MASINTHA GROUND.
31:24
ZOMWE AYANKHULA KU NDILANDE ATUPERE MULUZI NDI FREDOKISS
24:06
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 24 М.
ПОМОГЛА НАЗЫВАЕТСЯ😂
00:20
Chapitosiki
Рет қаралды 28 МЛН