Aaaaaa iwe ulibe ulesi kuzilowera kutenga malore ku mcp ko aaaaaaukuona ngati mizimu imeneyi igona owooooo ikusowesani mtenderetu
@LexkasonkanjiАй бұрын
😢😢😢😢 ambuye
@user-xt2gu9yt9qАй бұрын
Iwe ndi chakwela wakoyo nose pa
@chrissyyendayenda4650Ай бұрын
Skc my vote ❤
@user-xz3nz7dy1fАй бұрын
Olo thawi ya yesu ayuda adazindikira kt yesu anali pulumutsi atamupha kale .... Ndiye azindikira kt skc anali pulumutsi wathu ndipo amakondedwa komaso ntendere alibe okuphao
@SolomonMbeweАй бұрын
Welcome to DPP....Tisagone kwambiri coz MCP siikugawa kamba
@EmercianahKasiku-en6hlАй бұрын
Chikwati chatha ndi Manganya asatipusitse
@user-ln5hw7dn9gАй бұрын
Dennis mlowa mmalo wa Chilima
@GeorgePhiri-ub2ofАй бұрын
Koma utm madrama tikuonelani kumene mukathele ife pheeeeee ndi chakwela wathuyu 2025boma kale
@user-qp8kh2hj9oАй бұрын
Aaaa kagwere ndi Chakwera wakoyo iwe mwana Wa anjoka iwe nde ukakhala kuti mfiti
@FanuelMapondaАй бұрын
Uziwona nd nyau zakozo
@user-ml4bl2ll2gАй бұрын
Kuvota ndi ufulu wathu sipafunika kuti munthu akhale ndi Cha unzika kuti akavote, please don't take Malawians for granted, don't block people from voting
@GloriaKaduyaАй бұрын
Kwambiri asatitengere ku dodo ngati ndife maliro anjoka ai it's our rights to vote
@AlexManuelMisomali-sv1vnАй бұрын
😂😂😂😂 m'gwilidzano watha ?
@user-lz4kc5ob1tАй бұрын
UTM yikhodza kupanga kamupeni siku limodzi ndkulowa mboma