Apolisi ndi nduna achita kumuopseza Queen Kapalamula pa nkhani ya Chithyola

  Рет қаралды 23,879

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Ай бұрын

Пікірлер: 90
@BreezyRoben
@BreezyRoben Ай бұрын
Keep burning my beloved brother you are the one you give us strengt apudent we are appreciate you brother may Allah continue keep you self
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Nthawi zonse ndimakhala active pa Bakili Muluzi Tv 🔥 chifukwa ndipomwe ndimamva choonadi (Long live bro 🙏)
@DennisDonework
@DennisDonework Ай бұрын
Ndipo ineso sindimafuna kuti indiponye ayi
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri Ай бұрын
The biggest pressure that MCP have is from Bakili Mluzi TV than any politician.
@ZaidJafar-kk9be
@ZaidJafar-kk9be Ай бұрын
nde wina azit bakili muluzi tv yathapo aaaah munyela manyi enieni maphwanga🔥🔥🔥😂😂😂😂💪💪💪
@vinmbewe-yr8sr
@vinmbewe-yr8sr Ай бұрын
kma ndye
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Ай бұрын
My tv KZfaq channel here 🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@KwestalanjesAjangale
@KwestalanjesAjangale Ай бұрын
Your the best of best osati zinazi
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 Ай бұрын
Ipondeni fadah ❤❤❤
@user-xs3nj1es1r
@user-xs3nj1es1r Ай бұрын
Ndimayesesa kuti ndikhale ndi Data bundle. Cholinga Bakili Muluzi tv disamuphonye end then ndizisaka chokudya pakhomo log live. My dear brother Bakili Muluzi Tv your the best of the best tv in Malawi l love you 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@VictorPhalula
@VictorPhalula Ай бұрын
No1 Chanel Bakili Muluzi palibenso .Ndimakonda kwambiri
@Moses51
@Moses51 19 күн бұрын
The best TV in Malawi 🇲🇼 📺🔥🔥💯💯
@PeterLemani-jk3mw
@PeterLemani-jk3mw Ай бұрын
You're the best tv in the world
@wilsonfelix6559
@wilsonfelix6559 Ай бұрын
Koma nkhope yandunayo kkkkkkkk bwampini weniweni
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Ай бұрын
I feel proud of you bakili muluzi KZfaq channel!!
@ChejaliChirwa
@ChejaliChirwa Ай бұрын
Don't give up my brother your the best ❤
@robertkamangasadick8012
@robertkamangasadick8012 Ай бұрын
Afufuzidwe basi palibe kuthawa apa 🔥🔥🔥
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 Ай бұрын
Olo asamufufuze Timumanga mtsogolomu
@Justin_Nano
@Justin_Nano Ай бұрын
Best Tv keep up bro 🙏
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 Ай бұрын
Thanks for the update it's for a good of Malawi Also update us on elections olin south Africa who is going to win or government coalition
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p Ай бұрын
Welcome back,,,,usamasowe ase keep it ip❤❤❤
@alinafesalima5597
@alinafesalima5597 Ай бұрын
Yes musamasowedi bro kuteleku inetu nkhawa inandigwira ndimati kodi Bakili TV alimoyo?Bro go and seek asylum any country akakupasa
@BwanaGD
@BwanaGD Ай бұрын
Mukuzitenga ngati madolo komaso kuli madolo kuposa inu pamenepo nde muwone mudziwiletu kuti kuli mulungu zose mukuchita zikugonkhala poyera akuti palibe kobisika komwe mulungu sadzakayika pa mbalambanda big up ❤
@AjeliMw
@AjeliMw Ай бұрын
Ndi TV yokhayo imakamba zinthui zoona ndipo zimakhala zili Ndi umboni wake big up bakili muluzi tv
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Mulungu wathu timemyereni nkhondo musalore satana kuzunza akapolo Anu amen
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 Ай бұрын
Watching from Kenya pa Boma
@georgesmart3791
@georgesmart3791 Ай бұрын
Great TV award goes to .....BAKILI TV!!!!!!❤❤❤❤
@MussaJohn-gt8ep
@MussaJohn-gt8ep Ай бұрын
is only hope of Malawian bakili TV....
@MercyWalani
@MercyWalani Ай бұрын
Keep fire burning
@usumanidaudi
@usumanidaudi Ай бұрын
2025 chakwera ndi rayesi akuchoka murungu aripo wandiwonesera komaso azamangidwa pa murandu wa thirizoni wihawuti thirayo
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 Ай бұрын
Kumenyera ufulu umamangidwa kumene olo kutchuka sikophweka
@user-jy5sl8yr5n
@user-jy5sl8yr5n Ай бұрын
First watch
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Ай бұрын
More 🔥 bakili muluzi
@HoskiesCharley
@HoskiesCharley Ай бұрын
Best tv ever before
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
Kuswa kuswa 💪💪💪💪
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
The best TV ever in Malawi
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Ай бұрын
Apolice alingati ndondocha, akuthandiza kulemeletsa andale mokuba pomwe iwo akukhala mosauka kwambili
@JohnUladi-il6zg
@JohnUladi-il6zg Ай бұрын
Mbambande bro
@augustMag
@augustMag Ай бұрын
Always I like Bakili Muluzi TV 🔥🔥
@CharlesChiyembekezo-fv8lq
@CharlesChiyembekezo-fv8lq Ай бұрын
pitilizan kutiziwisa
@user-mw8dq4is6k
@user-mw8dq4is6k Ай бұрын
Osaopa ayii 💪💪
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 24 күн бұрын
Muwoma queen naye agule phapha lake khalani phe very soon i assume
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Live from Botswana
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga Ай бұрын
Ulemu kwa B muluzi ❤❤
@user-et5nz4vz2v
@user-et5nz4vz2v Ай бұрын
Best TV ever
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Phwala chithyola kmatu iwetu usamadalile asilikali ako wodwaladwala aja titha kukuphelaso limozi machende ako iwe chithyola wuziba ndi kumawawopseza anthu kuti asamayakhule chilungamo ukuwona ngati ndi gule wa mkulu ameneyo mapwala ako chithyola mukufuna muzingowapha anthu akamakufufuzanimo anu nose a mcp ndi agalu mkawona mukutenga zigawenga za ku ruwanda zizizapha anthu kunoko unu agalu kwa basi
@SolomonShaibuh
@SolomonShaibuh Ай бұрын
Live from Capetown
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Mbava zopanda manyazi akulephera ku gona chifukwa cha machimo ambuye akuoneni musiyeni kambanje ananena zoona mukubisana pa nyasi ngati iziii xmiii
@AaronWiniko
@AaronWiniko Ай бұрын
My best tv
@lusolawo73
@lusolawo73 Ай бұрын
Ine ndili pa mbuyo pa bakili Muluzi TV
@WilliamBinali-pl4ci
@WilliamBinali-pl4ci Ай бұрын
Best tv
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f Ай бұрын
Boma ili likapitilira pa 2025 anthu aphedwa ambiri komanso anthu avutika modetsa nkhawa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Ай бұрын
I'm always online cause of BMTV .blaz iweyo ndikupatsa chitetedxo wamva
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms Ай бұрын
Malawia yafika pa umve
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf Ай бұрын
Timadziwa kuti bwampini chithyola ndiwakuba lero ndi izi akuopseza nazo anthu Chakwera nsogoleri opusa kwambiri
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 Ай бұрын
Fadah mumayipondadi and ipondeni fadah sitigona ayi maso amakhala pa bakili muluzi tv ulemu wanu
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Ing'alureni mayi nkhope ya munthu olemera siwoneka chonchi. Nkhope za anthu okhwima izi 😂😂😂
@vytwistthelion98
@vytwistthelion98 Ай бұрын
Abwanyanga sanabiliwirepo
@user-ub7lm5pf9p
@user-ub7lm5pf9p Ай бұрын
Ipondeni fadah❤❤ respect 🫡
@samsonpadiwa9185
@samsonpadiwa9185 Ай бұрын
@KassimIssa-bn3od
@KassimIssa-bn3od Ай бұрын
Bakili muluz tv tili nawenawe ndipo singasekedwe
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Izi ndi zigawenga zomwe zikuyendetsa boma.
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq Ай бұрын
Chipani ichchi chikazawina chizawina kamba kobela, wallahtu ndichipani choipa kwambiri,
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n Ай бұрын
bakili muluzi tv ndi akamuna
@amiduclement2142
@amiduclement2142 Ай бұрын
Umeneakuone keramo mundudi wakuba
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Ma video a nyuwani sakubwera bwanji?
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 Ай бұрын
komatu munthu ali pa corner yo amadxola mafuta koma 😂😂😂
@allieyusufmtiwiliwi8498
@allieyusufmtiwiliwi8498 Ай бұрын
Koma adhaa akamati palibe chinsisi padziko Pano ankanenatu izi 😂
@user-ci6cj5qq2i
@user-ci6cj5qq2i Ай бұрын
Mumatha bro zambir tizivera kwaizbikakhala zodiac ndiy ili Boma pano
@user-ef2bg2kd4q
@user-ef2bg2kd4q Ай бұрын
Koma fada inuyo ndioopsya kwambiri
@Francis-co4nb
@Francis-co4nb Ай бұрын
Bakili TV moto buuu
@user-lk3ki9hi3k
@user-lk3ki9hi3k Ай бұрын
Kkkkkkkkk Boma lopepela
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q Ай бұрын
Timakunyadila man kwambiri
@user-ky4we4nu2v
@user-ky4we4nu2v Ай бұрын
Komatu Bakili timakunyadira
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Mulungu akudalise
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi Ай бұрын
Anthu oyipa awa
@AbufarihiyyaMussah
@AbufarihiyyaMussah Ай бұрын
Pitilizani osaopayi tilipambuyo panu
@LethubuhleSibanda-ed8oi
@LethubuhleSibanda-ed8oi Ай бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉😢🎉😢
@Benty_Pro
@Benty_Pro Ай бұрын
Umatha Bakili
@user-sb4om5pw2h
@user-sb4om5pw2h Ай бұрын
Eeeeeeeeee kma yah
@FranklinMapira
@FranklinMapira Ай бұрын
Ku Bagamoyo kuno 😂😂😂😂😂
@JonathanZimpita
@JonathanZimpita Ай бұрын
Mmai upusa iwe propaganda yakoyo sikuthandiza
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 Ай бұрын
Chakwera is a devil
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 Ай бұрын
Watching from Kenya pa Boma
@user-ir8dd8lm1c
@user-ir8dd8lm1c Ай бұрын
Choona chenicheni kumachita kuoneka kma anthu tidakayang'anilabe zopusa
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 Ай бұрын
Best tv
@Kay-racle_mw
@Kay-racle_mw Ай бұрын
Best TV
Joe Biden full press conference (July 11, 2024)
58:40
WFAA
Рет қаралды 372 М.
Can You Draw A PERFECTLY Dotted Circle?
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 45 МЛН
I CAN’T BELIEVE I LOST 😱
00:46
Topper Guild
Рет қаралды 120 МЛН
Sigma Kid Hair #funny #sigma #comedy
00:33
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 15 МЛН
Atikumbutsa Samora Machel wa ku Mozambique
10:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 30 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
How to win a argument
9:28
ajaxkmr
Рет қаралды 366 М.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 115 М.
Zina mwa zifukwa zikubweretsa mavuto ku chipani cha DPP
20:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 48 М.
Times Exclusive featuring Shepherd Bushiri - 13 January 2024
1:12:31
Times 360 Malawi
Рет қаралды 401 М.
Can You Draw A PERFECTLY Dotted Circle?
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 45 МЛН