No video

BLACK BOX YA NDEGE IJA AKUTI ILI KU STATE HOUSE TAMVANI ZOMWE AKUNENA

  Рет қаралды 28,662

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 93
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll Ай бұрын
😅 Lucifer chakwera , 2025 uzikalamulira ku Maula prison
@Mamahashim-xw2bg
@Mamahashim-xw2bg Ай бұрын
Ambuye mulungu wowona zapaziko lapasi ndi kumwamba anthu amenewo awonekere poyera ndithu ayaluke wallah😭😭😭💔
@BrownMulipaa
@BrownMulipaa Ай бұрын
Kkkkkkkk( mbuzi zawanthu amaona ngat abisala
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Fufuzani zonse zibwele poyela, , sakugona Chakwera ndi mizimu , nchifukwa chake wayamba kupemhela lero, wanya.
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 Ай бұрын
May the souls rest in peace,tisasiye imfa yawo ulele,Malawi tuyeni timenyele nkhondo ufulu wathu,ngati anzathu AK kenya
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Kumwamba kuli Yehova palibe chobitsika pansi pathambo
@FloraRonard
@FloraRonard Ай бұрын
Ayi zikomo.Mizimu yawo iwuse ndi mtendere
@AnnieKwisanja
@AnnieKwisanja Ай бұрын
Zobisika zonse zizabwela poyera
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Ай бұрын
Mulungu malungu mulungu wanga chonde chonde chonde titandidzeni ife
@AchinaKellz
@AchinaKellz Ай бұрын
chikangawa party kumwamba kuli mulungu ndithu prison woyeeeeeee😂
@user-zh9kb2sj2i
@user-zh9kb2sj2i Ай бұрын
Ambuye mwatisiyila mikango
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Chakwela you mast go ❤
@user-bd5kw8oq1r
@user-bd5kw8oq1r Ай бұрын
Zilibwino kuti ili ku state house Ndi kumalo otetezeka kwambili musade nkhawa 😅😅😅😅😂😂
@AnthonyMhango-e9q
@AnthonyMhango-e9q Ай бұрын
Thanks for let us known watching in Cape town Athlon
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje Ай бұрын
Ambuye ndiwabwino tiyenazoni
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu Ай бұрын
Chakwera he is very wicked man under the sun
@DavidJoel-l5q
@DavidJoel-l5q Ай бұрын
Mulungu wabwino masiku omaliza za chinsinsi zizaululika
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Chakwera akafera kundende 2025 aafune asafune simeneso sitekanditu musawonaso zicomo
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
@@YasinMusa-ym8lp uyambe ndi iweyo.
@KattieKamangirah
@KattieKamangirah Ай бұрын
Ndipo chilungamo chiyende ngati madzi onse amene anatenga gawo pa imfa za anthu amenenewa ambuye awakathe pansi pompano.
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv Ай бұрын
Mitima itsika pokhapoka chakeraxo afe basi
@user-fd2su4ig1f
@user-fd2su4ig1f Ай бұрын
Saima nawo
@CharityMkandawire-t8u
@CharityMkandawire-t8u Ай бұрын
Pa dziko lapansi palibe chinsinsi, nd tikulira ndi amalawi ambiri mulungu akumva ma dandaulo athu
@Prekkaq
@Prekkaq Ай бұрын
God keep on blessing chakwera
@DevisonHala
@DevisonHala Ай бұрын
Manyazi bwaaaa
@ChristopherChimbalanga-ez5he
@ChristopherChimbalanga-ez5he Ай бұрын
Ayaluka bas
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg Ай бұрын
Oh my God Ambuye achite nanu inu nonse mudampha anthu awaaaa palibe chinsinsi padziko la pansi
@IssahAluba
@IssahAluba Ай бұрын
Uyuyu chakwerayu murandu ukadziwika bwinobwino akuyenera kukhara Ku perisson
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v Ай бұрын
By and by, the truth is being uncovered
@elias.m.chunga
@elias.m.chunga Ай бұрын
Koma mbuli zinazi... GPS? Imatanthauza chani mwati?? 😅😂😅😂
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
😂😂😂😂😂 awuze iweeee
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya Ай бұрын
Tifotokozere inu anzerunu
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 Ай бұрын
Obviously boma la chakwera ndilomwe linapha chilima
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
Iwe udalipo?
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 Ай бұрын
Ayi, koma iweyo ndi a MCP amzakowo.
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Inuso ndinu achisilu mulindiumboni ​@@cassimyusuf6683
@HoseKatsekera
@HoseKatsekera Ай бұрын
mulungu ndiwachifundo, ziwululika
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Ай бұрын
Mulungu alipo ndipo ifa ya chilima ndiathu ena 8 ziziwika kuti anafa bwanji
@Prekkaq
@Prekkaq Ай бұрын
MCP boma tikayivotelabe
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Chakwera sapuma ndi maliro amenewa, adzazimangilila ameneyu.
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Ай бұрын
Yudasi
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Ай бұрын
Wanya basi galu ameneyi chakwela
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 Ай бұрын
Alibe manyazi ayima
@JasonMailos
@JasonMailos Ай бұрын
Chakwela ndiwakupha
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
Wakupha ndiwe opereka umboni wabodza mbwalo la mlandu
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Anakuphela ambuya ako
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Ай бұрын
Mundege munali zigawenga Ambuye tiyankhulen
@eunicesaiti
@eunicesaiti Ай бұрын
😢😢😢😢😢😢😢
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
Iyeyu adakwera nawo ndegeyo ndi zigawengazo?
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
Inenso ndikuti, Uyu agwidwa posachedwa, pakuti Mulungu adzaulula chilichonse kuphatikiza uyu akudzitcha mboni yu.
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Ай бұрын
@@philemontitusnkhoma7740 angakwere nawo akudziwa kut ndege yo waitchera? Mtsogoleri wathu ndi chigawenga chachikuru. Koma mulungu simunthu. Mzimu wa chilima suzagona mpaka chilombochi chitalangika.. He will never know peace in this world
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Ай бұрын
Apodi ndekt anthu amenewa anali mudege mommo
@Jerry-vm6mo
@Jerry-vm6mo Ай бұрын
Guys olo munene zotani mzanu chilima anapita inuyo muli Moyo nde bola mugosiya nkhani Yii coz palibe chomwe chingatike nde musatinyase so chilima anapita basi zikomo
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Srs ndipo or ayankhule motani kunatha uja basi lasala ndi tsiku lachiukitso ndinthawi yokoza mitima yathu osati mabozawa atichimwisa ulele ndithu anthuwa mumutu mwawo kaya muyenda chani
@michaelamon9691
@michaelamon9691 Ай бұрын
Koma yaaa, papa muli NDI bodza
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Ай бұрын
Iwe ndiye kape kwambili, nkhani yoti ilipalipose.
@MercyChimaliro-fi6mv
@MercyChimaliro-fi6mv Ай бұрын
Ngati ndi bodza ndiye iweyo tiwuze chilungamo chako.
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv Ай бұрын
@@michaelamon9691 iwe macende ako ife zikutiwawatu timufuna chilima
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Muthu uyu amakonda kuikila kumbuyo chakwela thawi zose mungutu adzakulangani kwambili chifukwa ifa zimenezija aliyese m,pakana panopa samavetsetse muyaluka mwasala pang,ono
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Ай бұрын
@@petertaulo8014pamtumbo pamako galu iwe, iweyo panga wekha GPS uikepo number ya ndege ija ikupatsa option ya black box nde ufufuze uwone Komwe kuli black box galu iwe
@solomonlapson
@solomonlapson Ай бұрын
Kodi ndindani ameneyu akulankhulayi,, and channel yake ndi yanji
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x Ай бұрын
Ukufuna mukamupheso anthu amcp inu. Manyazi bwa
@patrickscott9086
@patrickscott9086 Ай бұрын
Km ndye kuli kuyesesa kut chilungamo chisawoneke km Only God knows
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Ай бұрын
mbuli zazikulu ndinuyo kulongolora kwanuko mukuwapasa mapulani kuti akataye blac box mmadzi kupusa basi kamene mwva kukamwa mbwembwembwe kharani chete afufuze chomwe cili mkati mwa black box
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 Ай бұрын
Kkkkkk sayimanso ndithu
@lillynhlema9656
@lillynhlema9656 Ай бұрын
Ku statehouse yikutqniko
@FrankSimfukwe-w1s
@FrankSimfukwe-w1s Ай бұрын
Pangani mulimose ife tikufuna zenizeni zibwele poyela
@SandreckBezai
@SandreckBezai Ай бұрын
Iwe ndiopusa udzazindkil okay
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b Ай бұрын
Chakwela you're evil evil
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 Ай бұрын
Galu iwe usaoutsitse a Malawi. Kodi enanu mukungoti ndondondo kwa atolankhani abodza awa moti simudadzukebe kuti uyu angifuna kuononga Malawi? Iweyo umati Achakwera asiye blackbox kuthengo komweko mpaka lero? Amalawi dzukani. Sukusulani. Uyu apezeka posachedwa. Mwana wa mfiti
@user-qn9vc8em6z
@user-qn9vc8em6z Ай бұрын
Kagwere uko akutma et? Tisiye ife ndipo tidakamverabe untill 2025 woooooo ku chonguuuuu
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Ай бұрын
Komano minthu akadziwa chilungamo samakhara ndimantha gyz
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Nkhani ndiyowona
@LimbikaniChirwa
@LimbikaniChirwa Ай бұрын
Inu mkususanu kuti ndizonama tatiuzeni black box yilikuti mitumbo yamanu
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Ubwino wake amako alibe sorry for that 😂
@Prekkaq
@Prekkaq Ай бұрын
😂😂😂 mcp ikukuvetsani kuwawa
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Ndipo akusehula nayo mumimba 😅😅😅
@MariamJaffali
@MariamJaffali Ай бұрын
Ayaluka basi chakwera
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Kkkk munayamba liti nanu apa nthawi yamalilo mumati poyika chilima chakwera nayeso agone apa kuti mukuwona ngati moyo wachakwera uli mumanja mwanu timvomeleze imfa iliko aliyese adzafa ndindani angamulese mulungu zofuna zake
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka Ай бұрын
Mudzakhumudwatu report litatchula zosiyana ndimaganizo anu.Chakwera ine Ndikuona kut Ali innocent sure.
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Ndipo srs akungotekeseka nwini wake aliphee akudziwa choonadi
@EdnaChiumia-h4d
@EdnaChiumia-h4d Ай бұрын
Trading Lie's.... Nawe kumwamba sukalowa....let the truth revealed first b4 judging any one
@FrankBaison
@FrankBaison Ай бұрын
Chakwera amangidwe
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Pita kamumange iweyo
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Ай бұрын
Kut gyz social media simunayizolowelembe stt house yakut?
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Ай бұрын
Panyopa pako iwe ndi Chakwera wakoyo munyera muona simunati
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
​@@Musa1828-l5dkkkkk koma ndiye muli srs tuuu nganti amako alibe
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Ай бұрын
Mulungu yekha ndi amene akudziwa koma chilungamo chidziwika
ULENDO OYENDERA NDEGE YOMWE YAGWA.nkhani za lero
18:37
HOT 265
Рет қаралды 2,8 М.
123 GO! Houseによる偽の舌ドッキリ 😂👅
00:20
123 GO! HOUSE Japanese
Рет қаралды 4,9 МЛН
Вы чего бл….🤣🤣🙏🏽🙏🏽🙏🏽
00:18
Harley Quinn's plan for revenge!!!#Harley Quinn #joker
00:49
Harley Quinn with the Joker
Рет қаралды 32 МЛН
BRIAN BANDA KUWELENGA NKHANI
21:59
HOT 265
Рет қаралды 32 М.
Ndirande candle lighting - Fredo's speech [13th July 202]
5:52
Fredokiss
Рет қаралды 2,6 М.
123 GO! Houseによる偽の舌ドッキリ 😂👅
00:20
123 GO! HOUSE Japanese
Рет қаралды 4,9 МЛН