Kalindo is trying his best,chikufunika osusa agwirane manja!,ku UTM apereke mpata kapena position imene Mary chilima angatenge icho chiperekeranso mphanvu ina yapadera muchipani.
@AhmadShariff-bk3rr22 күн бұрын
Tiyeni tiyeni tiyeni Mr DC
@anicakandiado22 күн бұрын
Kulankhula mwachilungamo. UTM tsegulani maso. Tulukani mu tonse alliance monga akunenela Bon Kalindo please. A MCP asakupusitseni ife tili mbali yanu ndi SKC osaopa, osatopa, osafooka 💪
@sydemsamude19022 күн бұрын
the dc
@WestonGawaza22 күн бұрын
Bon kalindo akunena zowona lelo muchoke ku mcp mukapitiliza ndiye kuti mukusangalala ndi ife ya chilima chipani chimene chingawine ndi UTM kampeni wake zikolose lapasi lipanga saport
A UTM uthenga ndiumeneo zili ndiinu kunyalanyaza kapena kutengapo kanthu km mawa pangatalike muzawakumbukira mau a Bon sadutsa pachabe
@ChristopherChimbalanga-ez5he22 күн бұрын
Kmat uyu tiyen Tzimuvela zimene amayankhulaz
@Lazarus-qo1sl22 күн бұрын
Chilungamo ndimwano❤ The DC pick up man
@Shelifibraheem22 күн бұрын
Our freedom fighter ndiwe kawawa ndithu
@khuzenigunya22 күн бұрын
Kalindo good advice
@willardkajalika-m8g21 күн бұрын
😹😹😹 iwe umakwana aaa nilinje mau
@HassaniHassani-yr2rf22 күн бұрын
THE DC PANGOLINI 💪💪💪💪💪
@WestonGawaza22 күн бұрын
Mayi chilima to be president, braund banda,mwana wachilima awa kaliyati, awa musankhemo mumozi ankhale president mwana wa chilima anyamata ose ankhala ndi chidwi
@AgnessMzengo22 күн бұрын
Wise man
@MaxwellumbiriLumbiri22 күн бұрын
Bon kalindo umakamba zoona
@AndreaSignala-hk2yg22 күн бұрын
It's true bwana president woyamba wa anthu osauka muno Malawi
@user-nf3ik3ff6y22 күн бұрын
The Dc bon kalindo ❤
@AnnieMuliya-n5s22 күн бұрын
Mumatha
@PachaloShaba-pf5vw22 күн бұрын
Umakwana winiko
@SolomonMbewe22 күн бұрын
DPP+UTM+UDF+AFORD.... MCP out 2025..
@user-hc8gr4pg4g22 күн бұрын
In short Utm ibwerere ku DDP....tigwetse vinyau tikinze dziko
@user-bf1sz6pu1n22 күн бұрын
What if mrs Chilima is not a politician? Komanso akuti anthu azilowa kuchipinda ndi candle nkumakatchula dzina la Chilima kodi Chilimayo wasandukano mulungu?
@Moses5122 күн бұрын
The Dc bon kalindo 🎉🎉🎉
@MerryWayson22 күн бұрын
Na pa Bone Kalindo palibeso same same Mtanyiwa anthu awa amanena chilungamo chokhachokha
@BlessingsMikeyasi22 күн бұрын
The DC ,lankhula chilungamo bas
@WisikiBlack-gj4gu22 күн бұрын
Musapusisidwe a utm mcp sichipani .muzifunse kuti kodi chilima chamupha ndichani kodi mukugona a utm, tsegulani mumaso
@AndrewMbewe-yp7kg22 күн бұрын
Usazafe kalindo uzangotsowa ngati eliya
@priscillamangata402322 күн бұрын
The DC agogo anga akufuna azakuoneni
@user-fz3gu2ez1o22 күн бұрын
Tidziwe basi. Ma traitor tiwadziwa lero
@Mussa-qs7km22 күн бұрын
Good Good news
@MuhammadSamson-yz1kl22 күн бұрын
A UTM mukapanda unvera za bon kalindo muzalira moyo wanu onse
@MussaAmadu-o9f22 күн бұрын
Very true
@PeterMalizan22 күн бұрын
The DC mulomwe wathuwathu odziwa zinsinsi
@user-qq1uj7ct6n22 күн бұрын
boooooon kalindo!
@OsumaniJaffali22 күн бұрын
Amakwana koma ❤
@user-eh1mg3ww6d22 күн бұрын
Ndipo a mcp ndi athu ochenjela ndi kuipa komwe ndipo chilima amusasa lelo akuyanja otsalao mukapusa akumezani
@chifundobuledi22 күн бұрын
🎉More fire!!!!!!!!!!!
@WestonGawaza22 күн бұрын
Brayani Banda ndimunthu wa chikondi ndi ziko Lake mayi cilima tiwona ngati chilimayo alipo anthu tivota ambiri mwana wachilima anakonda achinyamata ndiye achinyamata ose ali ndi ife
@amfanamane22 күн бұрын
My vote umakwana
@BensonChakalamba-db7uf22 күн бұрын
The problem is anthu akumudz unthengawu suwapeza cz of social media