Chonde amalawi tisatembelele dziko lathu chonde mau akulu ochokela mkamwa mwa abusa yasini gama amen
@ChikumbutsoTsalangu8 күн бұрын
Awa nde anadalitsika ndinthu
@user-bi6pb5gc8t8 күн бұрын
Nkazi wopusa Ngati Mayi gotani hara
@eliasmpaso29787 күн бұрын
Powerful massage
@SkevaMustapher8 күн бұрын
Amen amen kuying'alula abusa
@LytonMfuni6 күн бұрын
I knew my rev: never go wrong.🇿🇲
@HusseinMoffatt-mi1fl8 күн бұрын
Ayasin ndi mbambandetu ndi weniweni
@user-dg5pc6rz1b8 күн бұрын
Eeeeeee ulaliki ogwila mtima
@MikeMakaww8 күн бұрын
Great great great apstor of the year
@NDIZOTHEKABANDA7 күн бұрын
Amen paste!!!!
@georgealabih89798 күн бұрын
True facts in life, ndaukonda uthengawu
@bernadettechoma8 күн бұрын
Hallelujah!🎉🎉🎉🎉🎉
@Musa1828-l5d7 күн бұрын
Kuyakhula mopanda matha respect abusa a Gama
@mablemathuso39037 күн бұрын
Powerful message
@AtnessBanda10 сағат бұрын
Amen amen
@SanhedrinMasauli5 күн бұрын
M'busa ameneyu ndi wandale, ananyozapo zipani zina ndikuyamikila mcp,
@paulnyondo75725 күн бұрын
Uthenga wabwino koma amaopako pangono a kambiri munthawi ngati iyi anaungalura uthenga .😂😂 a pule osawafunanso kkk.
@MercyMakhala5 күн бұрын
Amen and Amen
@calvinmalinga17746 күн бұрын
kumalawi Kuno kulibe akazi opusa
@StevenBwanausi5 күн бұрын
Ameen Abusa
@LinessStafordsauti5 күн бұрын
Amen man of God
@MarthaChaima2 күн бұрын
Amen
@HendrinaWalani5 күн бұрын
Amen so powerful
@MikeMerecah7 күн бұрын
Shehe uja amatinamiza koma uyu,
@user-kt5bq2wg6v6 күн бұрын
Wuthenga wabwino ambuye akudakitseni.
@FaithDonald-ts2pp8 күн бұрын
Man of God
@augustinechibbalazi88978 күн бұрын
May God bless His Word through you moderator and may He also plant a heart of philanthropy and patriotism in all political,traditional religious, and legal authorities in Malawi to be once again a Godfearing nation. Amen
@RaphaelLudaviko8 күн бұрын
malawi wathu ndipamene takhalapo. Amen abusa
@chifundocharles23488 күн бұрын
Chakwera akuzinyoza yekha aise😂😂 and inuyo mukugwira ntchito yanji if I may ask😂😂😂
@ShidaMfune7 күн бұрын
Amen ❤❤
@user-ec3xh4pc6t8 күн бұрын
Amen 🙏 🙏 🙏
@PempheroAlufandika7 күн бұрын
Ayasini inu ndi munthu wa mulungu ndipo ndinu mlangizi
A malawi sindimakumvetsani koma zowona after all what MCp has done to you in 3 weeks ago mwayiwala kale, kukuyitanani ku msinkhano inu nkupita,, mumati mukamvako chani chatsopano,,a oposition you guys are sleeping to much 😮h munayenela kukana osapezeka nawo pa chikondwelerochi,a MCP akukondelera their successful mission of killing chilima and the other 9, nchifukwa chake lero ali wokondwa,a malawi ndinu anthu osawona,how can you be invited for prayes to pray for the lives lost in chikangawa by the same man who orchestrated their death😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 Malawians are you nomal ⁉️⁉️⁉️⁉️⁉️
@EllinaBitto8 күн бұрын
Ndipo inu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@NatashaBema6 күн бұрын
Zosayenda
@lexsonlanjesi20508 күн бұрын
Nde mwati ABUSA aku 25 eti???😂😂😂😂😂😂😂
@OweniMalokooweni-es9qx7 күн бұрын
Chinyora
@user-km2js5nq9k7 күн бұрын
No the guy knows
@Crysis258 күн бұрын
Koma azungu akumva?
@Musa1828-l5d7 күн бұрын
Aimbileni phone muwafuse
@Creslevison-vj2sl8 күн бұрын
No message at all,this is not gospel ,for have "only and good things in God ,he is good all the time and he is cosistent,this pastor is ignorant that Job was doing all that in ignorance, hence this is jxt a motivational talk not gospel
@chiefmitengo8 күн бұрын
Amene akunyoza Chakwera tsoka Kwa iye.uli ndi tsoka iwe onyoza munthu osalakwa, ngati ndi ulesi wakowo ongofuna kulandira go to page House khalamba yanu ikakupasani za ulele. Agalu inu
@user-re7fo3be2z8 күн бұрын
Iwe ndikape kwambiri
@EsnartGirivin8 күн бұрын
Tikamangosintha sintha ma president dzikoli lidzingosaukabe Mwala oyendayenda siyanga ndele, Zomati kusankha uyu,kenako kubwelela mbuyo, Sizingathandize kulibwino kumusiya yemwe alipo ndikumapemohela kuti Mulungu asinthe dziko lathu, Olo atabwelaso wina tidzati bolaso Achakwela omwe aja Tiyeni timusiile Mulungu adzitisankhila ma president Osati mumzelu zathu Ai
@mablemathuso39037 күн бұрын
Mulibvumbulotso mu ulaliki uwu,tiyeni timvetsere bwino ndi khutu la uzimu.Ambuye apitilize kukugwiritsani ntchito abusa.
@user-rb5dk4cz3m7 күн бұрын
Uwu ndi ulaliki osati zomwe ayankhula look at you anthu okokomeza zaziii koma he's from 49 not 25 a fake journalist