KUYANKHULA MPAKA CHONCHO PA MASO PA APULE DR CHAKWELA

  Рет қаралды 78,477

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 173
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 4 ай бұрын
Kkkkkkkkk Koma walankhula mopanda Mantha Kuma kachulungamo kayenda ngt madzi mwakumbukila malemu Bingu achakwera angot ndwiiiiiii
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 4 ай бұрын
Dziko la democracy ndichonchotu anthu saopa
@LuckyChimangeni
@LuckyChimangeni 4 күн бұрын
Ndani angavotere zigawenga zakuphazi
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 күн бұрын
Kulankhula kwachamuna brother ndinu mamuna ❤❤❤❤ Mwalankhula bwino chikangawa akumva ekha
@user-ey2op5gb2g
@user-ey2op5gb2g 4 ай бұрын
APM my vote
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 4 ай бұрын
Kkkkkkk ngat zomwe ana ronjeza paribe or chimozi chomwe wapangapo nde zomwe mkunturirazo apanga km marawi ndi ziko ronvesa chisoni kwambiri
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 3 ай бұрын
Lazalo ali masaya vwapa kutsinkha misokho yathu. Waononga dziko Lazaro.
@DanielJuly-dj2ji
@DanielJuly-dj2ji 4 ай бұрын
Bingu a man of legacy 👏👏👏
@christophergibson72
@christophergibson72 4 ай бұрын
This is good kumpatsa munthu apeleke madandaulo ake direct kwa president dziko litha kusintha sizabwino Kunamiza plesident
@FosterChilumba
@FosterChilumba 4 ай бұрын
Grace Chinga Mofati i quote muzabwera chipani cha magazi Kodi ndi chiti Lazaro anakhetsa mwazi Kuti apezeke mamene Ali clueless presedent
@user-vz8gi8lj1b
@user-vz8gi8lj1b 4 ай бұрын
Ndagwilizana nazo pankhani yapansewu atrafic akunyanyila kuvutisa masewu
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 күн бұрын
a Mwamlima APA MUKUTETA.....😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 4 ай бұрын
Osangomutotola bwanji ndi chipolopolo galu ameneyu
@Owen88887
@Owen88887 4 ай бұрын
Kkkk nsonda wazimvera wekhat😅😅😅 nkhani ndi bingu
@user-vw4vc9xd5z
@user-vw4vc9xd5z 4 ай бұрын
iwe ndi mbuzi ku brantyle yake iti ine kwanthu ndikumeneko ameneyo wapanga chitukuko iwe wabodza kwambili unene Malo amene wapanga chitukuko nosenu ndi mbudzi musamanamize anthu
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 4 ай бұрын
From Don yen mukukhonga chiyani ife sitikumusowa chikwera nkhwangwacho
@ImraanJafali-dk7rg
@ImraanJafali-dk7rg 4 ай бұрын
Kkkkk uyuso waiwala, kuti masakho akubwera zakeyo ndi maplan
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 4 күн бұрын
nde uyu ndi president omva madandaulo a wanthu???😂😂😂😂😂
@CassimCawanga
@CassimCawanga 4 күн бұрын
Apm my vote
@PhillipsbrownBonongwe-ou6ne
@PhillipsbrownBonongwe-ou6ne 4 ай бұрын
Yea yes ndili More more mr present!.
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 4 ай бұрын
Machende ako .iweyo ungayelekeze BINGU ndi NAMACHENDE chakwera
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 4 ай бұрын
😂😂😂😂
@EltonMpira-bv8qc
@EltonMpira-bv8qc 4 ай бұрын
Mukulakwitsa akulu respect our leader 👑
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias 3 ай бұрын
😂😂😂
@JhpiegoMalawi-yj8bm
@JhpiegoMalawi-yj8bm 4 ай бұрын
Atumbuka ndinu omvetsa chisoni wapanga chani chakwera
@user-vq9if2ep5q
@user-vq9if2ep5q 4 ай бұрын
Zapamsewu...wayakhula...bho traffic...imanyanya heavy
@CatherineDesire
@CatherineDesire 7 күн бұрын
Akufuna vote ka kkkkkk
@rashidadan2533
@rashidadan2533 4 ай бұрын
Nothing will change , bcose MCP has come to destroy malawi , Wait DPP on 2025 to continue the development
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 4 ай бұрын
Chakwera anamenya back summer kuyimila ndevu😂😂😂😂
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 20 күн бұрын
Ulemu ukuyenelerani😂 😂
@stanleykaludzu-bm4pm
@stanleykaludzu-bm4pm 4 ай бұрын
Zikakoma kumayamika....Mwayankhula mwanzeru mkulu wa Mavenda udindo ndiwanudi
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 4 ай бұрын
Asonda mpaka Tay kkkkk nthawi yomweyi
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o 4 ай бұрын
Reality wise men
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON 10 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 chitukuko chikuyenda koma kumubisa mmaso muthu tuuuuuuuuuuu
@CatherineDesire
@CatherineDesire 7 күн бұрын
Amakataniko ku mzuzu Lazaro maglass ngati chiwala👺😔
@ayamimustaff-jo2cy
@ayamimustaff-jo2cy 4 ай бұрын
Chakwela ndi mbunzi yeniyeni
@PeterThomas-lw3io
@PeterThomas-lw3io 2 ай бұрын
Atidye nawo ndiyamene amayipitsa zina la president kuti mbiri zide
@user-qs2tx7wt6g
@user-qs2tx7wt6g 3 ай бұрын
Ase uzitipatsa khani zeni zeni nanga apopo chalakwika ndi chani ngat wina watukwanaaa
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 4 ай бұрын
Amsonda mpaka kuyiwara imfa yamzukulu wawo ali bize ku chipani kkkk
@Hendersonspoon
@Hendersonspoon 4 ай бұрын
Pa apolicepo walasa sikokhakuno olo Ku luchenza tikuvutika ndi anthu amenewa Zina aziziona kukugwira mpaka katatu galimoto imozi yomweyo
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 4 ай бұрын
Mkuzeni mmwamba agwemo ekha chifukwa chauchitsilu wake pakuti saatha kuona ekha koma kunamizidwa ndie ,,,,2025 uziona galu iwe!
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 күн бұрын
Wachipewa chofiilayo pansana pake alibe fundo akukamba zinthu zakale
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 20 күн бұрын
Vitukuko vikwenda ,vikwenda kutiko?kumazinamiza pomwe choonadi mukuchodziwa zaziii amalwai ndifedi ombwambwana
@user-ty1vq9lq6w
@user-ty1vq9lq6w 2 күн бұрын
A P M my vote
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 4 ай бұрын
Apm my vote 🗳
@MarthaBango
@MarthaBango 3 күн бұрын
Analedzeratu uyu 😂😂😂😂
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 3 ай бұрын
Nachimutu banda achoke
@sjrecordschannel7687
@sjrecordschannel7687 3 ай бұрын
Mp opusa kwambiri .....ngotukwanitsa kwambiri ndipo anthu sitichedwa kuiwala mphutsi imeneyi yazunza ndipo ikuzunza amalawi kwambiri mpka zoona mp nkuima kumayankhula zopusa chonchi? Kodi or atapanga zitukukozo anthu kutha kufa ndi njala plus kukwera kwa zinthu azapindulire ndani zitukukozo ana opusa kwambir chiuzeni chitsiru chanucho ndi nduna zake zoonandi anyani achabechabe
@GersonKalongonda
@GersonKalongonda 3 ай бұрын
A police amafuna paper pass( ndalama)
@petersoko4283
@petersoko4283 4 ай бұрын
Kodi a chakwera wo bwanji manjawo tatingo'no
@BlessingsNyirenda-kh9rc
@BlessingsNyirenda-kh9rc 4 ай бұрын
Koma ndindani wachipewayo?
@user-yy2kc7tg1r
@user-yy2kc7tg1r 4 ай бұрын
Dziko la Malawi likufunika anthu ngati awa opanda mantha
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 4 ай бұрын
Koma mkuluyo zinthu akuziona kuti zikuvuta mumalawi . Chakwera watitengera ku bagarmoyo.
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 4 ай бұрын
Iwe machende ako bingu anali machine sungafanizile ndi namachende chakwela mbolo yake galu mbuzi
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 4 ай бұрын
Iwe mbudzi azingofika no without notice ndikwawo
@EltonMpira-bv8qc
@EltonMpira-bv8qc 4 ай бұрын
This guy is so wise 🙊
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 4 ай бұрын
Athu akumuzuzu ndinu ozungurila mitu njala ili chiriiii Eshìii koma athufe mavuto sazatha
@user-jc7zq1zr7e
@user-jc7zq1zr7e 4 ай бұрын
Kulankhula uku ikanakhala nthawi ya DPP , ma cadet akanampondaponda munthuyu
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 күн бұрын
a tumbuka kodi munatani????simungamupatse mpata ENOCK CHIHANA koma basi busy ndi nyau z..
@patrickkapinga7091
@patrickkapinga7091 4 ай бұрын
Aaaa mwakumana iwe veendele wabhodza
@PeterBendeka
@PeterBendeka 11 күн бұрын
Galu amuneyu sungamufanizire ndi bingu
@josephmgunda-6123
@josephmgunda-6123 4 ай бұрын
Chakwera my vote🎉
@patrickkapinga7091
@patrickkapinga7091 4 ай бұрын
Palibe chomwe angapange ngati dzomwe analonjedza olo chimodzi ndiye mukungotha mau man
@JohnKayinga
@JohnKayinga 21 күн бұрын
Library ya peter mutharika koma mbuli izi
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 20 күн бұрын
😂😂🤣🙌
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 4 ай бұрын
ATumbuka ndi anthu osokonekera mitu.Chipani cha MCP chinayambitsidwa ndi Atumbuka ku Exile ku Tanzania,AChewa anachita kuchita hijack mkuwapha achina Orton Chirwa,Duduzi chisiza,Masauko Chipembere,Atati m'phakathi.Kuonjezera apo Kamuzu anawathangitsa mzigawo zonse kuti azibwelera ku mpoto.Lero muli busy kusapotera MCP 😂😂😂😂
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 4 ай бұрын
AISE ukuwuza Chiwanda cha munthu, Chakwera tatu, Ndi Chiwanda mzimu woipa Ndi umene umamu lamulira taonani wangoti ndwiii nkhope yake Ngati kanga use, Chitsiru cha munthu Chakwera kusowa chikondi Ndi amzake Munthu womvesa manyazi,mbava Wanthu akufa Njala Dziko lonse la Malawi, chenjerani amalawi musagone muzaliranso Ngati Wanthu A Mu Babeloni
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 4 ай бұрын
Kodi Ken nsonda wafunda skuff
@user-nr2bi5zm9f
@user-nr2bi5zm9f 4 ай бұрын
Ukanangonasula kut kuwapatsa licence yachmanga akut ai akufna 20 pin apolice anyanya
@user-ep2gd4bb8m
@user-ep2gd4bb8m 4 ай бұрын
koma mp uyu ndye kaatu
@gloriambale2277
@gloriambale2277 4 ай бұрын
Iwe wolankhulawe mutu wako iwe,,,,,..........kodi zimeme akuchita chakwera wakoyo sukuona mwina ukufuna ndrama ,...machende ako wamva,umuuzeso muzakayoasabwereso ku mpoto kuno azathawa
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 4 ай бұрын
Kma msonda amavesa chisoni azafela mundale
@wisdommhango
@wisdommhango 4 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@patrickkapinga7091
@patrickkapinga7091 4 ай бұрын
AAA satana uyu iwe wapasidwa badzii kapena chani
@alomuddin8801
@alomuddin8801 4 ай бұрын
Munthu opanda umunthu chakwera, zithu zikukwera mtengo ngt kulibe mtsongoleri akunaminza akulakhulayo chilungamo udzachiona 2025 ngt ukuyesa kt anthu akukondwera nawe
@esthermalixani2244
@esthermalixani2244 4 ай бұрын
Ndipo amatha kurakhula mwazeru kuposa inawa amayakhula zomukomesa purezideti km uyu wayakhula bwino kwambili
@AmujeMwamad
@AmujeMwamad 3 ай бұрын
yah, uyu nde akutolker
@JohnKayinga
@JohnKayinga 21 күн бұрын
Iwe suzawinaso basi kuyamikira zopusa basi wapangako chani chakwera ku mpoto kuno
@user-ym6xu3xt2i
@user-ym6xu3xt2i 4 ай бұрын
Mr msonda kungoti chete chete kuona maso ankhono ndi kudekha kkkk
@user-pf6qw3pv9s
@user-pf6qw3pv9s 4 ай бұрын
Aribe manyazii
@SymonMbuto
@SymonMbuto 4 ай бұрын
kwizakoso kwithu Kono yayi 😌😌😌😌
@user-rc3ze2oi7u
@user-rc3ze2oi7u 4 ай бұрын
Wayankhula bwino kwambiri munthu yu😂😂😂😂
@user-kuluweIconmw
@user-kuluweIconmw 3 ай бұрын
ntchito pali maboma angati angomanga mbali yakwanu komweko
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 4 ай бұрын
Dpp ikulowanso take my word
@JonathanMalimba
@JonathanMalimba 3 ай бұрын
Fake
@user-ci8el1df1b
@user-ci8el1df1b 4 ай бұрын
Wadya fodya wankulu ntumbuka uyu
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 4 ай бұрын
Kkkk boma lakatangele kkk chimanga paka mapepala
@user-zx9zw8yr1n
@user-zx9zw8yr1n 4 ай бұрын
Kuyankhula kwa boh👊
@jamesgama5489
@jamesgama5489 4 ай бұрын
Dziko limafunika anthu ngati amenewa kulankhula mosabisa
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 4 ай бұрын
Koma Chimwendo ndi mbuzi kobasi ati amenewo ndie ma Vendor amafuna zakukhosi zomse zithere2 mutha kuchezera koma Richard Chimwendo ndi mfiti ndithu
@user-nn9bg3ve3g
@user-nn9bg3ve3g 4 ай бұрын
😂😂😂😂 ichi ndicha wise
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 4 ай бұрын
😂😂😂😂
@rashidlamos3403
@rashidlamos3403 4 ай бұрын
Wayankhula za nzeru police Ena ndi odzuza
@MacdonaldMisomali-lt4wu
@MacdonaldMisomali-lt4wu 4 ай бұрын
Iwe gwape kwabas bigu ukayelekeze nd mbuzi yakoyo
@hopeskafumbi2246
@hopeskafumbi2246 4 ай бұрын
anthu ndiovuta mmmmm amangoyamikila zili zonse
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni 13 күн бұрын
UTM my VOTI
@patricgama4788
@patricgama4788 4 ай бұрын
banja la muthalika ndilachitukuko amalawi enieni osati galuyo ayi
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 4 ай бұрын
Apolice amaonjeza palipose atraffic
@user-je8yo3zy3y
@user-je8yo3zy3y 4 ай бұрын
Uyu ndi omanga Malawi
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 4 ай бұрын
Kukhala ngt akumva, koma mbuz yamunthu
@user-qk6if2or2n
@user-qk6if2or2n 4 ай бұрын
Ntumbuka uyu ndiwopepela waiwala kale siwomwewo akadya usipa misika achina chipisi kukwela maminibasi lelo ndiawa alibize ndikugwilagwila tomato wazimayi misika koma iwe siungalankhule ngati vendayo kodi kolelayo wayambila mbado wachakwela
@BriChiozekaV-dp9yt
@BriChiozekaV-dp9yt 4 ай бұрын
Kodi paja mesa iyeyu amkati peter akutha ndalama ndi maulendo ake apandege?lero iyeyu nde wayendele chani? devil on a pulpit.
@Johnybegood260
@Johnybegood260 4 ай бұрын
Ken msonda wango sanduka Hule😂😂😂
@TilekeniLungu
@TilekeniLungu 4 ай бұрын
Akuthoka chilungamo
@misheckchinjala.g
@misheckchinjala.g 4 ай бұрын
DPP my vote from Cape Town Stellenbosch south Africa...ine sindinaluzepo , DPP ikulamulila..... amalaw mwaziyonela yokha zomwe abusa anu akuchita....Alimbe mphatso ya utsogoleli chakwela,Koma
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 3 ай бұрын
Uyu akuyowoya eti 😮
@abdulumali3240
@abdulumali3240 4 ай бұрын
iweyo wamvala zofila galu ukunama chitukukuko chskwera wapangachiyani
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 4 ай бұрын
Mbava chakwela siangawene chilima bomaa
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 4 ай бұрын
Bingu anali chitsiru mesa ankawapasa ndalama mavenda kut agawane angodya koma zinatengera mavendawo anzeru
@user-pb5ou6bs3q
@user-pb5ou6bs3q 4 ай бұрын
Huuuuu koma iwe ndimbuzi kobasi
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 9 МЛН
Despicable Me Fart Blaster
00:51
_vector_
Рет қаралды 25 МЛН
Stay on your way 🛤️✨
00:34
A4
Рет қаралды 5 МЛН
AMANGA MUNTHU OLAKWIKA BON KALINDO LERO PA 25 July 2024
15:14
Trump | Assassination Attempt Minute by Minute: ABC News Special
53:14
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,9 МЛН
JD Vance speaks at Republican National Convention
38:16
NBC4 Columbus
Рет қаралды 67 М.
LIVE: Donald Trump speaks at MAGA rally in Michigan
1:43:56
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 597 М.
President wa mamina mmutu; Amalawi akufuna Franklin Roosevelt wao.
9:21
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 33 М.