Boma silikwantsa chifukwa apanga ndi iwo pofuna kuti alamulire Dzaka 10 zomwe president akufuna popeza adalengeza kale kuti gwirizano sugwira ntchito
@user-uw7wn9zm6iАй бұрын
Zosakhlatu 😂😂😂
@tamalahmwenera7996Ай бұрын
So sad😭😭😭
@user-qc5hj1gy4sАй бұрын
Ndipati Mulungu anati chilima sadzafa?ufuze iweyo tranpence koma uganize so ngati momwe ukuganiziramo sizinachitike Mulungu akuone mwapaderadera
@AmusedDimSum-hd5ypАй бұрын
mukuyankhura bwanji big mukuziwapo kankhu
@user-mo3zk3fy7dАй бұрын
Zovuta kwambiri😢😢
@FrancisDinalaАй бұрын
DC akuchedwa bwanji kod
@user-lc3sw8iz2gАй бұрын
APM anati Tsikulina choipa chidzalamula Malawi.
@Mwenda-sr9roАй бұрын
Mwamupha chilima
@user-jn7bt1uy5sАй бұрын
Anthu akupha awa inu
@dingdang5209Ай бұрын
Mmmmmmmmm
@BlessJere-jj3ldАй бұрын
Very sad
@GidionJonas-sr4zrАй бұрын
😢😢😢😢
@EliasiChikhau-kf3fwАй бұрын
Zona ifufuzdwe achkta kuphedea
@meeklembemo219Ай бұрын
Boma movement apapa😢
@AmusedDimSum-hd5ypАй бұрын
Dc floor is waiting for you to smoke the cloud
@KhalideNerve-mu1eqАй бұрын
😢😢😢😢😢
@AmusedDimSum-hd5ypАй бұрын
zoona atrapenz mumawagwirila ntchito
@AlickSquareАй бұрын
Basi kufuna kwanu kuchitike
@gabrielmaluwa1038Ай бұрын
Zikuti bwanji
@VictoriaWilliam-ms2ftАй бұрын
Akangokupatsani banzi simulankhula so za kafukufuku inu
@YoungRich-og5luАй бұрын
Very good me l'm Happy
@LeendaDeborah2005Ай бұрын
🙄🙄🙄🙄
@LeendaDeborah2005Ай бұрын
Muzisamala pakamwapo tsiku lina zizalozera kwa inu ambuye akukhudze
@ChristinaLigomekaАй бұрын
Munthu opanda chikondi olo munthu atakuchitila choipa bwanji wamwalila mudziti am very happy atakhala bale wanu kapena mwana wanu mungamve bwanji ifetu munali abale anthu zaziii iwe ndiwamuyaya
@WalesNjaidiАй бұрын
😭😭😭😭😭😭😭
@SamsonKamgusha-gp5fwАй бұрын
😂😂😂
@EvelessNjirazafaАй бұрын
Dziko laluza
@MagabaMike-eu4rnАй бұрын
Sorry! Something happened
@kaykayjella4180Ай бұрын
Ayuba James alipo, timawona ngat anadya baz
@PhillipPhiri-ik3jxАй бұрын
But wy guys you talk good about Chilima wen he has passed on? Bwanji ali moyo simumanena zonsezi kuti timudziwe munthuyu monveka bwino? We are now developing love for him while he is gone.......making us more heartbroken. Don't you think ndivuto la amalawi ili to say good of you once you are gone? Evison Matafale anali oziwa kuyimba eeeeh.......munakamba izi atamwalila. Alimoyo ku show kwake osapitako kukamupanga support.
@tonitohkamarley8335Ай бұрын
Pumani mumtendere
@hanifahmponda8711Ай бұрын
Aaaa mwapha chilima uyi kufuna mudzayimitso 2025 nyengo tsinali bwino nde ndegeyo inanyamuka bwanji ku mzuzu ndinyengo yoyipa yomweyo koma paka inakafika ku LL aaaa MCP yokupha nanga anthu aku Israel amatani kunyumba ya boma kungopha anthu pano apita kwawo iiiii nsonotu ma Israel ndianthu oyipa dzedi chitsadzo ngati anapha yesu what is chilima don't trust chakwela and MCP