kwagwanji wa report lomwe achipatala atulutsa lokhudza Imfa ya Dr Chilima 😢

  Рет қаралды 47,857

VILLAGE CHAMPION

VILLAGE CHAMPION

27 күн бұрын

Пікірлер: 114
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 25 күн бұрын
Kodi ndege ndiyomweso inamvula chilima dzovala ?chilingamo mukufuna inuso ndiye chiti chionadi mukuchidziwa
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 24 күн бұрын
Musavutike umboni tinaupeza kale black box ilikuti nanga maphone alikuti anthu wonse anali ndimaphone ndichifukwa chiyani anali wovulidwa zovala
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 25 күн бұрын
Kumadziwatu kuti Chilima wachita ku phedwa ndi a MCP,paja mwalandira ndalama a wonder
@TheresaKuluwemba
@TheresaKuluwemba 25 күн бұрын
Ine wonder amandionekera wa mcp aaa
@frankjolijo
@frankjolijo 25 күн бұрын
Chilima sangaphedwe chonchija!!🙆🙆🏽🤦.....we have nothing to lose....we are coming
@JiyaWilliam-g8y
@JiyaWilliam-g8y 24 күн бұрын
Odziiwa salankhula zambiri amangoti Insha Allah kutanthauza kuti zonse akudziwa ndi mulungu ndipo ndi mwini zonse
@user-kt5bq2wg6v
@user-kt5bq2wg6v 22 күн бұрын
Zoona mbale moti anthu wose adakaganiza choncho zikanakhala bwino
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 26 күн бұрын
Agalu abodza ife chilungamu tachidziwa muzinamiza ana osati ife amalawi, mwapha anthu afiti inu
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h 25 күн бұрын
Report lachani umboni ife tilinawo jacket anamumvula ndani?? Nsapato anamumvula ndani?? Osawopa chakwela wapha chilima umboni ife tilinawo
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 23 күн бұрын
Ndege yagwera kutali ndi midzi ya anthu yeti it's not far from villegers ndiye iyeyu sanadziwe kuti amanama zosezi ngati alibe choyankhula akhale chete komanso zonsezo zikanati ndi zabwino zokhuza za zosatira za kuchipatala ko bwedzi abanja sanabwere poyera why delay yeti aziti angonenapo izi zokha zinazo azanenabe, presdent wanuyi has something to do ndi imfa ya chilima period
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 26 күн бұрын
Ndipo ine uyuu wandebvuyi amandiyelamo kobs amazimva nzeru kom ndimbuli yothelatu
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 24 күн бұрын
Ine zikundidabwitsa Kuti mchifukwa chani akubanja akuti satulutsa report lonse,akubisa chani????? Apatu zangoonetseratu Kuti zomwe anthu ambiri akulankhula Kuti a Chilima anachita kuphedwa,zomwe akupanga a boma kumamanga anthu chifukwa choti akulankhula molira komaso kufusa mafuso pazodabwitsa zomwe zinachitikaso kutsatira ngozi imeneyi
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 8 күн бұрын
Nose ndinu zinsiru kwambiri amene mukufotokoza maboza anu Chakwera wamupha muzake 😢😢
@user-zo3bf3ec3g
@user-zo3bf3ec3g 26 күн бұрын
Times chichitikileni malilo achilima chinachake pakatipani chachitika ma program anu sakukoma mukuyeneya muzikonze mukuonesa mbali muzochitika zanu Kanakonda ndalamazo mulandile ndipo mudye koma muzima pachilungamo ndipo muzitiuza zoona😔😔
@FionaKhoma
@FionaKhoma 26 күн бұрын
Chakwera anapha chilima musatinyase munachita kuwakhapa
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 26 күн бұрын
Kachilungamo aka ena sakondwa nako kuzolowela kunamizidwa times mwapamba kugwila tchito yeniyeni thanks
@iangondwe6857
@iangondwe6857 25 күн бұрын
thank you for teaching us guys i agree with we must use our brains
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 23 күн бұрын
Nkhan ndyakut chakwera anamupha chilima ndi anzake mcp ndiyakupha kd chakwera chiyambire kulamura kumalawi ndi ngozi zingat,nanga anamuvura zovara chilima ndan samalani mulungu akukanthan nonse muli pambuyo pa chakwera
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 26 күн бұрын
Chachikulu akubanja afotokoza okha zilibwino ndiye makape ena azitengela za ndale chilungamo akubanja achiziwa
@stevezulu2108
@stevezulu2108 26 күн бұрын
Abanja awophyedwa ndi Boma. Zoona zidzadziwika boma likadza sintha.
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 25 күн бұрын
@@stevezulu2108 naweso ofoyilatu mene adaliri chilima uja anthu akwawo angaope boma ali ndi masapota ambili adafotokoza chilungamo palibe amene angachite naye matha chilungamo ndichimenecho Mulungu akuziwa chilichose
@RabeccaMpunga
@RabeccaMpunga 25 күн бұрын
Zoona zeni zeni tizaziziwa MCP ikazachoka pampando ndipo sikale.
@AishaChipande
@AishaChipande 26 күн бұрын
Wander ukungonena chakwela mwina kt alindimamina mumutu
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 26 күн бұрын
Ife sitikupanga nawo zinamizanani nokha nokha munamaliza amcp ndi kukhapa
@ZakaliyaAlick
@ZakaliyaAlick 26 күн бұрын
Abusa akudziwawonkha kuti kugwa ndzanja la Yehova ndikowopsa akonda chinyengo asiyeni adzaziwona chimwemwe chawo adyelatu.
@user-hq8yn8tl1h
@user-hq8yn8tl1h 25 күн бұрын
Koma osayiwala Kuti mphekesera ili pawiri; Kukhala yoona Kapena... Kukhala bodza😢😢
@user-hq8yn8tl1h
@user-hq8yn8tl1h 25 күн бұрын
Azanena akazakhumudwisana 😢😢zitapanga xpire😢😢😢😢
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 26 күн бұрын
And mukazilowetsa ndale mukulakwisa because muona ngati lamulo ndi loyipa
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 26 күн бұрын
Anthu kumalawi kuno amasangalala ndimabodza gwelo LA zonsezi ndiumbuli basi
@augustMag
@augustMag 23 күн бұрын
I am waiting 2025 all Malawian tikazavota amene azawineyo ndikukhala president boma limenero ndi lomwe lizachete kafukufuku wa ifa ya anthu amenewa amene anamwalira pa ngozi ya ndege mizimu ya abalewa iunse mumtendere osatha 😭😭😭😭
@Doreen-yl3qm
@Doreen-yl3qm 25 күн бұрын
Mboni yayikulu ndi Mulungu amene anali ku chikangawa amene amawona zonse,la 40 likadzakwana zizaulirika
@AyandaPhungula-bg9ql
@AyandaPhungula-bg9ql 26 күн бұрын
Zawusilutu zoti tidzinamizana 😮😮
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni 25 күн бұрын
Tidzingo koment zachina JB zachina ntanyiwa bakili muluzi TV ndi ena akunjawo bas ife sitidzilemba km ma koment kwaolemba akunjawo bas
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 24 күн бұрын
Andevu zamwayi zanu munadya kale simunganene zoipa za Mcp ayi
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni 25 күн бұрын
Awanda amzanu munalinawo pa program wa sanati waze asadzabwereso mwamva?
@EsnartMartin
@EsnartMartin 23 күн бұрын
Atolankhani achinyengo awa tonse tikudziwa kuti ndalama za magazi zilizonse ponse
@user-bl6km6kx7n
@user-bl6km6kx7n 26 күн бұрын
mafuso ndiye ambiri choti muziwe vuto mphanvu tilibe bs mthaw yanu
@PempheroAlufandika
@PempheroAlufandika 20 күн бұрын
Akukanika bwanji kuulusa .nde mabodzawo azinenambe anthuwotu
@HaliJana
@HaliJana 25 күн бұрын
MUBISE MUNENE IFE TIKUDZIWA KUTI CHAKWERA,ANACHITA PLAN YOPHA CHILIMA MUKUCHWDWA NAWO UMBONI WANU NDIPO CHAKWERA UFA OSANYELA IWE UWONASO
@user-cr6if6tz6d
@user-cr6if6tz6d 25 күн бұрын
Achitsilu chamunthu a ndevu zatsoka mulungu akulangani inu agalu
@user-sz6bi3tw5y
@user-sz6bi3tw5y 20 күн бұрын
Pitani mukatenge black box ya ndege tinve kuti inapanga record zotani pamene ngodzi inkachitika pamenepo ndipu tipenze umboni basi.
@user-dn6eg1xk7f
@user-dn6eg1xk7f 25 күн бұрын
mabodza ayamba osanena moopa ayi anafa ndi mabala ayi
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 25 күн бұрын
Ineso pang'ono ndayambaso kudanwa nazo mmmmm ndalamatu inapha yesu tisaiwale. Athuwa ...........????????
@OscarKJekapu
@OscarKJekapu 2 күн бұрын
Chakwera anyoxedwabe asiye uchigawega
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 25 күн бұрын
Nde akubitsa chifukwa chani! Or asaneneso zilibe tchito so abitsa bwanji kunena uthenga wenweni 😡😡😡
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 25 күн бұрын
Etii angotipwetekatsa mtima
@user-ec4jo9cu4d
@user-ec4jo9cu4d 25 күн бұрын
Mukundisokosera mukanena zotsatira za kuchipatala mmalo monena zakugwa kwa ndege?!!
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 24 күн бұрын
Kodi amene akupanga defend chakwelayi amupasa zingati akuona ngati akunamizatu mwana wakwaotu cz zokhuza ngozi zija msagwilise njira yowaseka pakamwa anthu kuti alankhule, komanso funso ndiloti kodi zomwe amapanga a silikali wo zoti tiyeni tikasake ndege uku osati kwinako amawalangiza ndi ndani komanso potumidza anthu nine akasake ndege zimenedzo ukudziona kuti ndi zazeru komanso kusiisidwa kwa kufufuza ndege basi nkhani zonsezo iweyo ndi ukadaulo wakowo sungaone kuti something was off here, let malawian explain there views malingana ndi momwe a presdent anuwo anapelekera uthenga wao unali osagwira.
@stevezulu2108
@stevezulu2108 26 күн бұрын
Olo ingo zisiyani.
@wonganichakakanyirenda3299
@wonganichakakanyirenda3299 25 күн бұрын
Chilungamo chizaziwika basi
@NdamvaScnp
@NdamvaScnp 25 күн бұрын
Mcp yakumpha
@PeterKayuni-n2r
@PeterKayuni-n2r 25 күн бұрын
Yaaaaa
@user-ml2vw1dc9c
@user-ml2vw1dc9c 25 күн бұрын
Akubanja anena chilungamo ndipo tadziwa basi otukwanawa ndimowa ndifodya
@AufiThera
@AufiThera 25 күн бұрын
Mwapha Munthu
@OscarKJekapu
@OscarKJekapu 2 күн бұрын
Ndinu zitsilu malibe chazeru
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 8 күн бұрын
Chinachitikq ndichan kuti ndege igwe??
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek 25 күн бұрын
Ndichifukwa chani akumanga wina aliyense woyankhura fir the whyy Later kumafufuza
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 26 күн бұрын
Well come dont forget kuti every accident has acause,car ,motor bike,an aeroplane lets just calm we wiil have good answers dont talk things without umboni because its acrime
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 26 күн бұрын
Chakwera anampha chilima ndemukukamba chani nkunkuyu zikhare ngoma nose muzaziona analakwanji chilima
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 25 күн бұрын
Koma mwina achita bwino kusanena iwowo akubanja ndimtaya makoko .
@Hellenistic109
@Hellenistic109 3 күн бұрын
Chakwela killed his vice
@AceelectricalengineeringAEE
@AceelectricalengineeringAEE 25 күн бұрын
Pa... Pako
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 26 күн бұрын
Komaso apolisi naonso akuyenera kuphunzitsidwa mokwanira,akuyenera kuti lamulo limeneli alimvetse,asangotumidwa ai
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo 20 күн бұрын
Posaikira kumbuyo chipani km malire a ufulu akalankhulidwe ndiofunika kwambri kuyambiri kuzako, makolo , pantchito ngakhale pa mudzi izi ndizofunika koma ndale zikutiyiwalitsa zosezi.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 15 күн бұрын
PALIBE CHANZERU MUKUYANKHULAPO APA NDI ANA OMWE AKUDZIWA KUTI CHAKWERA NDAMENE ANAPHA CHILIMA, OSAMAYANKHULA MOZEMBA KAPENA MUKUOPA KUKUKWEZANI NDEGE NANU IYAAAAAA, MUKAONA KUTI ZOKAMBAZANU NDI ZOZEMBAITSA KUIKIRA KUMBUYO BOMA NDIYE MUTSEKE MA PROGRAM ANUO MUSATINYASENAZO , ANTHU ALI NDI UFULU OYANKHULA TIRI MU DEMOCRACY, MUKAKAMBA ZA POLICE KUMALAWI KULIBE A POLICE KULIBESO ACHITETEZO
@user-dg5pc6rz1b
@user-dg5pc6rz1b 25 күн бұрын
Zao izo or cent sidadyepo nde worries what bisani
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 26 күн бұрын
Inu achina wander dyani ndalamazo ndi chakwera zisiru lnu times palibe chazeru pano
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y 11 күн бұрын
Palibe Cha zelu chomwe mukukamba apa tiziwa kusogoloku a MCP akazagwa m,boma
@Gautengstanzo
@Gautengstanzo 26 күн бұрын
Akuyankhula apapa panya pawo ndithu
@Sophisticate230
@Sophisticate230 26 күн бұрын
Izizi nde ndizopoila kuti tizinamizana
@user-cr6if6tz6d
@user-cr6if6tz6d 25 күн бұрын
Agalu inu ngati simukuziwa chimene mukupanga kuli bwino mungokhala sibwino kuyiyimira MCP chipani chamagazi
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 25 күн бұрын
Palibe chotukwana koma akubanja ndi anzeru siopusa koma wanzeeu sangamasure pano kumbukirani pa bingu anafotokoza chinapha bingu???? anthu amzeru amatero kuti mlungu awamenyere nkhondo popeza zachitika kale
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 14 күн бұрын
Ufulu omwewu anthu akuphilira Za pa Social media in the end akupangidwa scam.
@user-sf7sd1hb4g
@user-sf7sd1hb4g 25 күн бұрын
Uyunso wadya ndalama zaboma
@AshlafHakimi
@AshlafHakimi 25 күн бұрын
Chinyengo ichi agalu inu
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 25 күн бұрын
NDALAMA MDANI WA CHILUNGAMO
@phillipmphanda2163
@phillipmphanda2163 25 күн бұрын
Tizakumana pakachele bola chilungamo tuchidziwa
@stevezulu2108
@stevezulu2108 26 күн бұрын
Zoona zidzadziwika MCP ikadza choka Mboma.
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 25 күн бұрын
Zitsiru Inu mwadya ndarama zochuruka thus why mukuyakhurah zopusaaa
@DafterChitema
@DafterChitema 25 күн бұрын
Kodi anthu Inu atakhara mbale kapena mwana wanu mukhoza kuyankhula zokhuta choncho
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 26 күн бұрын
Paja madolowatu adya za MCP sizodabwisa
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 25 күн бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 24 күн бұрын
Anthu aku ena I inu so kuti mwadya buns ya mcp
@russellsombwa1609
@russellsombwa1609 21 күн бұрын
Mmalawi wina aliyense akudziwa chozachita 2025 sikuti azavota chifukwa cha mayankhulidwe anu koma nkhalidwe
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 25 күн бұрын
koma eee msova a dpp
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 25 күн бұрын
Zitsiru izi zinadya ndalama
@ThokozaniSaiti
@ThokozaniSaiti 25 күн бұрын
All of you one day you will pay one by one for what you did to Chilima and others
@lacfunnytv1251
@lacfunnytv1251 5 күн бұрын
Nonsese
@DiversonChimenya-h2u
@DiversonChimenya-h2u 19 күн бұрын
Khoswe akakhala pa khate sapheka zikanakhala kuti Dr saulosi chilima sanaphedwe bwezi panopa zosatilazo zitawulusidwa kale kale chifukwa black box siyikanasowa koma kusowa ko ndikumwe kukupangisani kuti muziyikila kumbuyo boma limeneri
@BerthThomas-v9l
@BerthThomas-v9l 25 күн бұрын
Munagulidwa Ndi mcp agalu inu
@JTUPHIRI
@JTUPHIRI 26 күн бұрын
Guys Malawi wathapo basi tivomeleze, mpaka wonder kumayankhula moduka mutu chonchi! Ndiye amene angatiimile ndindani?
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO 26 күн бұрын
Dziko silinathe vuto lilipo ndilakut mumakonda ma negative
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo 25 күн бұрын
Eee
@JacobTMarko
@JacobTMarko 26 күн бұрын
Umbuli ndikufa nanga kumafika pomagenda m'mdipiti wa galimoto zonyamula maliro pali umunthu pamenepo .
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 25 күн бұрын
Imeneyoo timayintcha aggressive ndizinthu zopusa mafunaaa tizisekererah inunso umbuli mulinawo cozi mukufusa funso lopusa kwambiri
@user-hq8yn8tl1h
@user-hq8yn8tl1h 25 күн бұрын
Chibanzi😂😂😂😂😂😂
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj 25 күн бұрын
Taziyayakhurani zanzeruuu ngati ma citizens amalawi bax bzy talking foolish thing yr stupt you tow gys mukuwona ngati mwawinaaa time yovata ikubwerah muzarirah ng,weee😂😂😂😂
@JimsonChisi
@JimsonChisi 25 күн бұрын
Mwaononga kawailesi kanu takasika
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 25 күн бұрын
Indeeee awonongadi Wailesi yawo pano sitikumvetseranso tasiya kuwadalira
@wonganichakakanyirenda3299
@wonganichakakanyirenda3299 25 күн бұрын
Pano akutiuza zina kusongolokuso azatiuza zina akubanjayoo
@ChikondiLikapa
@ChikondiLikapa 25 күн бұрын
Man akubanjawo apasidwa chiseka pakamwa apapa zaoneselatu chifukwa palibe chobisila choona choti chimasule amalawi tathandiza kulila lelo akatibisile alibe chisoni nafe ata ine basi ndazituluka akubanjawo mwina alandila ma banzi
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 25 күн бұрын
Define assassination
@ZakariasintidomathengaMathenga
@ZakariasintidomathengaMathenga 19 күн бұрын
Lie statement isn't true
@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 26 күн бұрын
Don't post this .who a u.
@AchinaKellz
@AchinaKellz 25 күн бұрын
Zopusa chakwera ndiwakupha basi olo Mbiri yake ndinyasa wapha Mia, busa wake reason kufuna mpando
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 25 күн бұрын
MCP ndi yakupha
@iangondwe6857
@iangondwe6857 25 күн бұрын
leave chakwera alone put the matter in the hand of God
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 26 күн бұрын
Zachamba ngozi lmavura zovara lnuso madya mabanzi
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek 25 күн бұрын
Anapha ndi chakwera
@ModicaiChirwa
@ModicaiChirwa 26 күн бұрын
Zitsiru inu mwadya zakukuyu eti,anthu Ali kunja akulankhula chilungamo ndiye mukuti abwere kumalawi mufuna president wanu wazawaphe kumalawi kuli ufulu panopa pathako panu achina wonder
@user-jn2oc3cn3q
@user-jn2oc3cn3q 25 күн бұрын
Kkkkk km anthu muli ndi nkwiyo
Best KFC Homemade For My Son #cooking #shorts
00:58
BANKII
Рет қаралды 58 МЛН
КАК ДУМАЕТЕ КТО ВЫЙГРАЕТ😂
00:29
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 9 МЛН
Женская драка в Кызылорде
00:53
AIRAN
Рет қаралды 374 М.
JD Vance speaks at Republican National Convention
38:16
NBC4 Columbus
Рет қаралды 67 М.
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,9 МЛН
LIVE: Donald Trump speaks at MAGA rally in Michigan
1:43:56
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 597 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 128 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 186 М.
Opening of Parliament at the Cape Town City Hall
4:19:14
SABC News
Рет қаралды 103 М.
Best KFC Homemade For My Son #cooking #shorts
00:58
BANKII
Рет қаралды 58 МЛН