Imfa la Saulos Chilima. Kulira kwa niece wa Bingu, Abiti Wiliam Dawood.

  Рет қаралды 30,687

Malawi Page

Malawi Page

17 күн бұрын

SUBSCRIBE here for more videos goo.gl/aYvIXK
Malawi videos in English and Chichewa

Пікірлер: 164
@PaulChaleka-lb4vx
@PaulChaleka-lb4vx 15 күн бұрын
Michael usi alibe chilungamo and ndidamuona chilima akuzengedwa mlandu olo tsiku limodzi sadapite
@user-lz5yv4vj6h
@user-lz5yv4vj6h 15 күн бұрын
Even address as the utm VP to address for truth or to stand by him
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 15 күн бұрын
Chilombo manganya
@EmmieZenengeya
@EmmieZenengeya 14 күн бұрын
Akapume Chilima abale😭😭😭
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 15 күн бұрын
Tipemphe anthu aku Chilimba asamupatse manganya vote, munthu ameneyu ndi traitor sure
@laurentchisambi4984
@laurentchisambi4984 12 күн бұрын
Nayeso tsiku lake lizakwana,mulingo womwe umayesa nawo nzako naweso mulungu azakuyesa nawo.
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 15 күн бұрын
GOD bless you Sister power full keep on sharing what ever is coming from our party
@amoschataika7440
@amoschataika7440 15 күн бұрын
Abiti ndi Deal, long live Sis
@elvienyirenda-ln3dm
@elvienyirenda-ln3dm 15 күн бұрын
Mai zoona zokhazokha mukukambazi. I wish you were here, muthandizane ndi Bon Kalindo.
@victorauwana7258
@victorauwana7258 15 күн бұрын
So sad ... Mcp people are not sleeping anymore
@OwamThoko
@OwamThoko 14 күн бұрын
Powerful massage,I'm a man but you make me feel pain like I'm in labour to gv birth to a baby ,100 % I agree with you,GOD protect you from this ng,ona,n bless you,you are the angel of malawians,keep it up❤❤❤❤ 25:47 ❤
@andreabanda7838
@andreabanda7838 15 күн бұрын
Thanx so much madam. This is great for local Malawians. As you keep keep advocating for change. Please factor in the perspectives of the manifesto - such as freedom education, in secondary schools, even in the universities. Eradication of corruption. Change of some elements of sections constitution such as why the VP without real jobs descriptions. Kulira kwanu tonse tikulira. UTM please be strong. It’s only some 13 months to go. People don’t want this MCP thing.
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 15 күн бұрын
Mwazi wa saulos supita pachabe ai..... Ndipo mulungu sangalore kuti mizimu ya anthu 9 isabale zipatso
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 12 күн бұрын
i love the blief dear sis...what a plain tuth ..wow!!i salute u love💥🤝
@ProphetessEzinass-qu4ir
@ProphetessEzinass-qu4ir 14 күн бұрын
Iam not politica but this is the truth and awesome people chose to save gods and no justice . Continue to put sense in malawias God bless you
@user-cy3js1sf2u
@user-cy3js1sf2u 14 күн бұрын
Mcp bolaosamusowetsatu mayi you akulila malilo abwana ake 😢😢😢
@AbuBakrIqrah
@AbuBakrIqrah 14 күн бұрын
😢😢😢 sister indeed you made me cry a lot
@user-sz2wg7ug8i
@user-sz2wg7ug8i 13 күн бұрын
Asis speech yanu it's powerful 👏 🙌 a Malawi 🇲🇼 tiyeni tichose matha amene tili nawo dziwani kuti onena chilungamo adzaona mwayi pamapeto amoyo wake
@user-te3ps3kf2t
@user-te3ps3kf2t 14 күн бұрын
l agree with you sister,your are tolking the truth, Molingana ndimmene mwafotokozelamu musalolere kukhalabe pa mngwilizano ndi mcp chifukwa a Bwanawa Sanali ku chipani cha UTM ,mubwelele ku gwilizano pokhapokha ngati malemu Saulosi chilima angadzuke kumanda kudzapitiliza mngwilizano ndi mcp not Bwana usi chifukwa akuoneka ngati anali a independent, according to your statement.
@HanifMoses
@HanifMoses 15 күн бұрын
MCP singawineso
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 12 күн бұрын
Powerful message mom god bless you indeed it was painful.
@josephgabriel5941
@josephgabriel5941 15 күн бұрын
I absolutely agree with you. Nothing to subtract or add. You have said it all
@user-lz5yv4vj6h
@user-lz5yv4vj6h 15 күн бұрын
Exactly
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 15 күн бұрын
You make me cry also ma'am,,, God is watching Malawi and whatever is happening in Malawi God is there 😢
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 15 күн бұрын
You make me cry too 😢
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 15 күн бұрын
Abiti God bless you, zitiyankhulirani plz tikanena ife atimangatu
@dingim1234
@dingim1234 15 күн бұрын
Zodanwitsadi zikuchitika ndi Michael Usi. Money root Of evil. POLITICS is a dirty game. Malawi opposition is wealth. Anankhumwa ankati a Chakwera asiye udvinding, later zoo anagulidwa anatseka pakamwa. But who is fearless to
@MiliamManda
@MiliamManda 14 күн бұрын
Or aphee adadi wioo komabe tivotela My alipo a my Mrs Mary Chilima siazawinaso a Chakwera 2025 UTM yiwinakale takozeka ife kuwapanga sport My Mary Chilima❤❤
@burtonamin5913
@burtonamin5913 15 күн бұрын
Congratulations sister
@WestonGawaza
@WestonGawaza 15 күн бұрын
UTM mwana wake ayimilile u president, mayi chirima akoza kuyima pa president or Brayani Banda to bepresident ku UTM MCP yakupha kuyambira karekale
@LanceLance-mj4kc
@LanceLance-mj4kc Күн бұрын
We are all crying,& others we don't believ that he is gone for gud
@WitnessPhiri-zr9uf
@WitnessPhiri-zr9uf 14 күн бұрын
😢eish zopweteka ndinthu God bless you sister
@user-yc3ik9dq3x
@user-yc3ik9dq3x 15 күн бұрын
TRUE WORDS SISTER 😢
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 15 күн бұрын
Amene muli nchipani cha UTM munvere uthenga uwu mulungu alowelelepo
@LiamTennessee
@LiamTennessee 15 күн бұрын
Komatu nde mwayakhula chilungamo,mwa chapa anthu oyipa mitima ngati ngati awa sinamvepo,
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo 15 күн бұрын
Powerful enough
@TressLuka
@TressLuka 15 күн бұрын
You make me cry tòo Aunt 😢😢😢 . Pipo ayi zikomo chikondi palibeee😢😢😢😢
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne 15 күн бұрын
Chakwera ndi wopusa and misara yake
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 15 күн бұрын
Mzimayi akulira
@user-mf8fi8wt5d
@user-mf8fi8wt5d 15 күн бұрын
Koma Ku UTM Ku Kuli azimayi okongola heavy...SKC ndi idea for sure mama
@MiliamManda
@MiliamManda 14 күн бұрын
Mkunena zowona auntie zikolanthu lili ndimatha kwambiri
@lindamalunjika6581
@lindamalunjika6581 15 күн бұрын
powerful
@MiliamManda
@MiliamManda 14 күн бұрын
Koma atiphera sogolo lanthu kwambiri chifukwa Malawi pano ai siwalibwino ai
@EdnaSiyan
@EdnaSiyan 13 күн бұрын
Very powerful
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft 15 күн бұрын
Zuka malawi
@user-ul5hh3cz8z
@user-ul5hh3cz8z 15 күн бұрын
Powerful massage sister kumalawi kwaza afiti mudzipanimu there not have future anthu anapita school zakamuzu alibwe kuti mawa kubwelanji
@JoyceNkhokwe
@JoyceNkhokwe 15 күн бұрын
Mayi palibe kuloza mukuyankhula bho ndiye poti chilungamo chimapweteka go deeper maah
@arnoldkaikenkayange
@arnoldkaikenkayange 10 күн бұрын
Powerful
@user-tw1jo5xu9r
@user-tw1jo5xu9r 15 күн бұрын
Thats true
@doreenKamwendo
@doreenKamwendo 4 күн бұрын
Facts dear
@Agin2pex-ms3di
@Agin2pex-ms3di 12 күн бұрын
Am touched 😢
@FredKanyerere
@FredKanyerere 15 күн бұрын
Thats true cc.
@user-jn3bg6tj1q
@user-jn3bg6tj1q 12 күн бұрын
Namwera ❤
@dingim1234
@dingim1234 15 күн бұрын
Zodanwitsadi zikuchitika ndi Michael Usi. Money root Of evil.
@EmmanuelZiba-qz6ug
@EmmanuelZiba-qz6ug 11 күн бұрын
😢😢😢😢😢 or Zambian 🇿🇲🇿🇲🇿🇲 we are crying 😭😭😭
@MatemboGondwe
@MatemboGondwe 14 күн бұрын
❤❤
@MichaelWilliamsNyirenda
@MichaelWilliamsNyirenda 15 күн бұрын
Si aphunzitsi okha police, mw Army' ndi Anthu wovutika kwa basi koma pano munthu kuyankhula za boma eti ndikumanga that's nonsense of them
@sakalameck
@sakalameck 15 күн бұрын
Manganya is an opportunist.
@corretabanda7685
@corretabanda7685 15 күн бұрын
Im really behind you cc. Michael usi aliko okha ku MCP komwe aliko
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 15 күн бұрын
Nai warila uyu mmmmhhhh ndalira
@sayidimisessa
@sayidimisessa 15 күн бұрын
Zoona azimayi nanu onesani nkwiyo
@JoyousDaveson
@JoyousDaveson 14 күн бұрын
Ndipo ife tikulira everyday for SKC kufa imfa yowawa inuuu
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 14 күн бұрын
💯 Dzoona zake izi
@umalimaganga
@umalimaganga 15 күн бұрын
I like you ndinu wolimba mtima Mayi👍🔥
@fairkabambo6386
@fairkabambo6386 15 күн бұрын
zikuveka bwino ndife amasiye
@josiahgarley3824
@josiahgarley3824 14 күн бұрын
Amen
@AliceChitaukali-e5q
@AliceChitaukali-e5q 15 күн бұрын
Why us 😭😭
@user-iz1qi3db2g
@user-iz1qi3db2g 14 күн бұрын
Yes komadi awudzeni amenewo athu avetse
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s 15 күн бұрын
Izo ndiye zoona acc Mcp ndiyankhaza
@MiliamManda
@MiliamManda 14 күн бұрын
Apa bola apesani a my Mrs Chilima u president osalimbanasi ku ku vote ai a my alumbiluseni basi Chakwera achoke wabakwakwana
@JONAHMWALUGHALI
@JONAHMWALUGHALI 14 күн бұрын
koma imfa ya Bingu wa mthalika how did it go?
@Agin2pex-ms3di
@Agin2pex-ms3di 12 күн бұрын
😢so sad
@user-do9of5uo6s
@user-do9of5uo6s 4 күн бұрын
None munjigale mwejiiii kkkkk
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 15 күн бұрын
Sister mukulankhula zowona zokhazokha, mcp alongside usi ndang'azi agule ozola manyi kudambwe. Do me a favour please our beloved sister, mmene mwayamba kubwera chomchimu , pitilizani musasiye ayi , menyani nkhondo imeneyi mothandizana ndi Limpopo FM with comrade Mtanyiwa , Bakili Muluzi tv, Bon Kalindo and others please. Poyamba ndimkawona ngati amalawife ndiofasa koma it's not dat kufasa as such!, amalawi ndife anthu opusa kwambiri , timayang'anila zinthu zikuonongeka pamaso pathu
@chrispinekaludzu864
@chrispinekaludzu864 15 күн бұрын
Ku America mkokoma amai
@user-dm2fs6hf1b
@user-dm2fs6hf1b 13 күн бұрын
What do you mean apa mayiwa akuyankhula za mzeru tsono what does it mean ku America mkokopa please yankhulan za nzeru athu tikulira imfa ya chirima
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 14 күн бұрын
Bwanji a UTM ,asankhe mukazi wa chilima akhale presedent wa UTM , Anthu ife tikamuvotere?
@ZogoZeko
@ZogoZeko Күн бұрын
Pano ndithawi yokonda utm
@user-do9of5uo6s
@user-do9of5uo6s 4 күн бұрын
Kkkkkk wandiwaza kufazafaze kukoko basi
@ELLENKANJERE
@ELLENKANJERE 14 күн бұрын
Tiyeni nazo amayi mwalakhura ndithu sindinu Mai mwatumindwa ndimzimu ghoyera ndiumene ukulakhura zikomo pitilizani
@Franklinclothingcarpentry
@Franklinclothingcarpentry 14 күн бұрын
I cant even believe up yo now that he is nomore
@ZintleSotshange
@ZintleSotshange 12 күн бұрын
Anatigulisa ku mcp ukulele chani iweso unalu momo ziyipe lero sukudya nawo
@PaulChaleka-lb4vx
@PaulChaleka-lb4vx 15 күн бұрын
2025 ndikuona kuchedwa kt tichotse mcp and chakwera
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 15 күн бұрын
Komanso chakwerayo akafere kundende ...he will never be allowed out.komanso Ma boarder onse tidzatseka ...tidzamuvula zovsla adzakhale pa mphepo ngt mmene adapangira chilima
@user-nm8gp1du2m
@user-nm8gp1du2m 14 күн бұрын
MUNTHU OGANIZA BWINO SANGAVOTERE MCP.. AMISALA OKHAOKHA NDI AMENE NGA VOTELE MCP.
@PreciousChisale
@PreciousChisale 10 күн бұрын
pandiwadza ndiapapa eti pa TANZANIA zikuwayendera ndi munthu wamai pachiongolero pamene ife ndi bambo ,malawi vuto ndi chani
@augustMag
@augustMag 15 күн бұрын
Mulungu apitilize kukusogolerani cct Chilungamo chokha chokha ku Malawi matha ndiwo timawayika pasogolo ndi chifukwa dziko lino tikukumana ndi mavuto ufulu tikuugulisa ndi ndalama Usi wapala kwaoko anthu zasankondanso ngati azawine andifuse ndithu
@JoannaMbando
@JoannaMbando 14 күн бұрын
Madam you are talking.
@gaddiemkandawire6436
@gaddiemkandawire6436 15 күн бұрын
Malawi anthu ndia manthandi
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 15 күн бұрын
Tikavotera Apm basi
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 15 күн бұрын
Chilima akanakhala kuti amatikonda ife amalawi bwanji sanachoke ku mcp ataona kuti zimene amafuna sizimachitika personal he was a good guy political zero for me
@KereeditseMotsetse
@KereeditseMotsetse 15 күн бұрын
Muthu akavoteledwe okufa iwe galu eti
@LiamTennessee
@LiamTennessee 15 күн бұрын
Chitukuko ca chakwera ndi kupha anthu basi
@Shadrick-lq6oj
@Shadrick-lq6oj 13 күн бұрын
Mahule awa akulila Poona kuti ntanji wavuta
@ZinawZinawmulu
@ZinawZinawmulu 15 күн бұрын
Ndiopusa ausi
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 14 күн бұрын
Sorry sister , Chakwera galu yeniyeni. Amalawi no vote for MCP.
@JamesZanelo-iv1wb
@JamesZanelo-iv1wb 14 күн бұрын
Usi is an opportunist,he has Never been a member of UTM.
@alubisabili5188
@alubisabili5188 15 күн бұрын
😂
@ZogoZeko
@ZogoZeko Күн бұрын
Manngqnya musiyeni angwa nayo mcp yakupha kuyambiira kale chilima atipwetekesa kugwilizana ndi mcp
@user-jn3bg6tj1q
@user-jn3bg6tj1q 12 күн бұрын
MHSRIP
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 15 күн бұрын
Tiye nazoni andale muziphana ife tili Kuma stand
@kennedybanda
@kennedybanda 15 күн бұрын
Zosakhala bwino
@pierrebanda1176
@pierrebanda1176 2 күн бұрын
Kadzibwerani mudZatule Malawi osamangotukula kaniwake tidzawone luso lanu Mai osangolole kwaniwake
@user-sz2wg7ug8i
@user-sz2wg7ug8i 13 күн бұрын
Mzimu wa SCK uziusa mumtendere
@wonganimwase9881
@wonganimwase9881 15 күн бұрын
Those 9 people were murdered in cold blood.
@floramphinji3771
@floramphinji3771 15 күн бұрын
It breaks my heart mmmm
@CathyKatsokamalanda
@CathyKatsokamalanda 15 күн бұрын
​@@floramphinji3771😢😢😢😢😢😢
@GrinTemboh
@GrinTemboh 11 күн бұрын
Tiyenayo ku fasefaze yachiyawo yeleyo
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 15 күн бұрын
Usi is a hypocrite, ndinthira kuwiri amene anampereka chilima mmanja mwa zigawenga za crocodiles dancer mcp patty and dat we know for sure. I had request sister, i need a capital please, der's no one whom I can ask apart from u sister, zinthu sizilibwino mdziko muno
Eli Njuchi - Tempolale Visualiser
4:23
Eli Njuchi
Рет қаралды 3 МЛН
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 9 МЛН
MISS CIRCLE STUDENTS BULLY ME!
00:12
Andreas Eskander
Рет қаралды 9 МЛН
Trump | Assassination Attempt Minute by Minute: ABC News Special
53:14
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,9 МЛН
Donald Trump speaks at the RNC: FULL SPEECH
1:32:24
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 3,5 МЛН
LIVE: Donald Trump speaks at MAGA rally in Michigan
1:43:56
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 600 М.
TRIBUTE DOCUMENTARY TO LATE DR SAULOS KLAUS CHILIMA
16:04
Malawi Film Unit
Рет қаралды 40 М.
MISS CIRCLE STUDENTS BULLY ME!
00:12
Andreas Eskander
Рет қаралды 9 МЛН