Iwe umafuna akaombere mmanja agogo?? Kodi zoknda zako zingafanane ndi ena??? Mnzeru zimakuvutani eti????
@user-oq5rg5mz7q2 ай бұрын
MAnyi anu
@MasharPablo2 ай бұрын
Athu oyipa inu
@user-qq1uj7ct6n2 ай бұрын
Kupempha ndalama za ku boma??? 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@MustafaLikaomba2 ай бұрын
Awamanyi achipani walanditu ka 2 pin zopandasogolo
@MAYGOSPELALBUMSChawawa2 ай бұрын
Koma abale anthu enafe ndi omvesa chisoni momwe zinthu zilili ku malawi kuno zoona mungapitenso kumakaombela manja anthu awawa? And a chinyamata kapena mumafunako ndalama? Muyenera kupanga zoti ana anu kusogoloku asazavutike musiye kupanga zapompo pompo.
@user-eh1mg3ww6d2 ай бұрын
Koma ndangosangalala kuti ma komet ose ali apa palibe waikila kumbuyo chakwela ndazikonda kwambili tiyeni tose tisamivotele chakwela