Nawo Osatira Chipani Cha UTM Akulira

  Рет қаралды 6,206

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Nawo Osatila Chipani Cha A UTM Akulira

Пікірлер: 16
@jamesgama5489
@jamesgama5489 2 ай бұрын
Asangalala bwanji president wawo akuyankha milandu yakuba
@Zerena-le2ds
@Zerena-le2ds 2 ай бұрын
Chidziwitso,Dr Saulos K chilima ndi mfulu pano alibe mulandu chakwera wathesa mulandu,
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Ndipo ngati mukudikira UTM Kuti yisintha zinthu guys yiwarani ndipo ngati kuli njara timwalira zenizeni mulungu wakwiya Si anthu woyenera Awa kuwayika pa mupando guys wake up
@ShukuSh-vi1hk
@ShukuSh-vi1hk 2 ай бұрын
Ife timaesa mwina inu a utm mukumadya katatu pasiku kodi mavutowa tikuona tose sitimaziwa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Mesa ndi Galu wanu yemweyo ammat fertilizer muzagula K495 Kwatcha lero zilikut?
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 ай бұрын
Amanyamula fertiliser paphewa uja ndindani? So chilima emweyo 😂😂😂 amalawi kumvetsa chisoni
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr 2 ай бұрын
Uphawi sizithu
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 ай бұрын
Osauza inuyo a utm muli bomatu ndamene mukuyendetsa boma
@amourvido8027
@amourvido8027 2 ай бұрын
Inu si a UTM zachimidzi basi mukunamiza ndani.
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 2 ай бұрын
Amenewo si a UTM angovala nsalu za UTM. So don't waste time inu mukujambulanu.
@user-sv2vc7ie2m
@user-sv2vc7ie2m 2 ай бұрын
Mukondwetu relo paja mumafuna kuti muone Zina ndiye mwaona nyenkhwetu
@spargomw
@spargomw 2 ай бұрын
Zitsiru izi, mesa inu nd mbuyewanu ndamene mudapangitsa kut dziko lionongeke chonchi? Munya musanati. Kuvala zofiira ngat ozindikira zili mbuzi zenizeni😂😂😂
@lifayohbenson1994
@lifayohbenson1994 2 ай бұрын
Kkkkkk
@RydiaKabowa
@RydiaKabowa 2 ай бұрын
Vitsiluno mukuyakhula mosaganiza Kodi chilimayo adzathetsa mavuto onse mulinayo heee makadavutika 2025 chakwela boma basi pali ndani wina
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 2 ай бұрын
Chekwela bagamoyo ndani havotere zazii
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Koma abale dzino lingoonekamo limodzi NGAT mkamwamo iri ndiyomweyo😂😂😂😂
USAUVER S08E01  CHPS AND EGGS
18:54
Piksy TV
Рет қаралды 64 М.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12
MR JOKES
Рет қаралды 180 М.
Mom's Unique Approach to Teaching Kids Hygiene #shorts
00:16
Fabiosa Stories
Рет қаралды 28 МЛН
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН
I Can't Believe We Did This...
00:38
Stokes Twins
Рет қаралды 133 МЛН
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 161 М.
The Story of Chrissy Luhanga (41)
31:56
Rodwell Lumbe
Рет қаралды 72 М.
MUNAKUMANA BWANJI?..13/05/2024..Mibawa. TV's Content
28:59
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 8 М.
Omwalira apezeka wa moyo
48:05
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 69 М.
Assista na íntegra o Balanço Geral 26/07/2024
Portal FM | Fala Moçambique
Рет қаралды 653
USAUVERS09E01   BOXER
18:16
Piksy TV
Рет қаралды 76 М.
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Zodiak Malawi
Рет қаралды 328 М.
Cruise 5 With General Vincent Nundwe   MDF Commander   Part 2
1:06:01
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 59 М.
Mom's Unique Approach to Teaching Kids Hygiene #shorts
00:16
Fabiosa Stories
Рет қаралды 28 МЛН