NJIRA ZINA ZOPEZERA UMBONI WA CHOMWE CHINAPANGITSA NGOZI YA NDEGE YOMWE INAPHA DR SAULOS CHILIMA

  Рет қаралды 153,001

Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia

Ай бұрын

NJIRA ZINA ZOPEZERA UMBONI WA CHOMWE CHINAPANGITSA NGOZI YA NDEGE YOMWE INAPHA DR. SAULOS CHILIMA NDI ANTHU ENA 8.

Пікірлер: 273
@campbell8988
@campbell8988 Ай бұрын
This is the type of wisdom we need, ndamva audio yanzeru since i started following this issue. Stay blessed
@evelynnzima1716
@evelynnzima1716 Ай бұрын
My deepest condolences to our beloved sister country of Malawi. As a Zambian citizen I mourn with you. The Lord is your strength!😢
@graciouswasibu5184
@graciouswasibu5184 Ай бұрын
This is so clear
@leonardngala6148
@leonardngala6148 Ай бұрын
Kuyankhura koma kumeneku ithink ndinu munthu wowopa Mulungu. God bless you
@madalitsokalima8533
@madalitsokalima8533 21 күн бұрын
It's not all aircrafts that carry data and voice recorders because the equipment is very expensive in most developed countries only planes that carry above 16 passengers and they are commercial,all planes are mandated to have a transponder which sends a ping that to show position for the air craft.And this aircraft being military less hope it was carrying data and voice recorders and that they were recovered safely for engineers to analyse.On top of that service records, communication between pilots and traffic control also plays a big role in investigation.
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v Ай бұрын
Zikundiwawa kuchiona chichakwera pamwambo umenewu aaa amalawi please 🙏 munthu wationjeza uyu
@ChrissKaswaya
@ChrissKaswaya Ай бұрын
Ose anali kuja amaziwa siku lakwana inuyo mumaona ngati chilima azamfa imfa yodwala yokha kapena ndi wamuyaya mulungu uja mmamulila uja kuti zithu zikudula akumva mapemphelo aja
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Ай бұрын
Usapiteko tisie tiike maliro a president wathu mwaulemu
@user-lz5yv4vj6h
@user-lz5yv4vj6h Ай бұрын
He wasn't suppose to be there
@glorynkhata1185
@glorynkhata1185 Ай бұрын
It's accident you never pridict or know if the pilot loss the control so what ? He was not God chilima
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 Ай бұрын
@@glorynkhata1185the pilot never lost control. The villagers that live near that place said that the plane landed perfectly do not blame the pilot 😑😑
@AaronDungadunga-ff2ny
@AaronDungadunga-ff2ny Ай бұрын
Munthu amene anapanga kuti chilima ayende pa ndege akhale munthu oyamba kupereka umboni chifukwa iyeyo ndiamene ali ndi nkhani yonse ya imfa ya chilima ndipo akuziwa chilichose chomwe chinachitika ndipo ndiyemwe anapanga plan yonse ya mmene chilima amayenera kuyendera
@giftnyirenda5614
@giftnyirenda5614 Ай бұрын
Bwana ndinu munthu wanzeru koopsya. Nkanakonda nkanakudziwani. Your are a matured person, civilized.
@MphatsogiftJerejr
@MphatsogiftJerejr Ай бұрын
Mafana oganiza bho ena ndi amanewa kupeleka upangili ukwanila bwino
@CatherineChalema
@CatherineChalema Ай бұрын
Ndipo kwambiri!
@dominicmphepo-jk8lk
@dominicmphepo-jk8lk Ай бұрын
God bless Malawi with wise and intelligent people like you bro. But such good ideas can't be welcomed now in Malawi we are amongst the weakest people. But you are talking well bro
@speakwellgladys5569
@speakwellgladys5569 Ай бұрын
May the Lord bless you brother for your wise and humane speech may the Lord give you abundant wisdom...
@yahgoshen5815
@yahgoshen5815 Ай бұрын
Thanks brother mwayankhula bwino
@Shereenmustapha
@Shereenmustapha Ай бұрын
Very true. Takumvan abwana
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Ай бұрын
Umbuli these record information no one can stop it... This man is talking something very sensible ❤❤
@loziSteven
@loziSteven Ай бұрын
Well said sir. It's my hope that the two devices were collected from wreckage site, are secure and will be made available during enquiry. May their souls rest in peace.
@tapiwakalako-pm1ty
@tapiwakalako-pm1ty Ай бұрын
Well said bravo may the souls of those who were in the plane rest well
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
This massage is open a Malawian eyes let work together to find what cost deaths of our peoples RIP
@chifundomatumula1652
@chifundomatumula1652 Ай бұрын
Well said but kwathu kuno chilungamo chimabisala when people in power, rich and highly trained and educated are involved coz they influence the outcome of the investigations
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 Ай бұрын
Koma this time they will fail miserably
@StiveriaChikonga
@StiveriaChikonga Ай бұрын
Thanks for this massage 🙏
@levisonchimseu2779
@levisonchimseu2779 Ай бұрын
Kulakhula kwa wisdom brother
@BlendaMpinga-fy8dx
@BlendaMpinga-fy8dx Ай бұрын
We have lost our dearest father my your Saul Rest in Everlasting peace my the good lord provide love Mary
@ArthurMzingeni
@ArthurMzingeni Ай бұрын
God bless upangili wabwino
@hendrickbanda5644
@hendrickbanda5644 Ай бұрын
My heartfelt condolences from Zambia
@vascoholland3273
@vascoholland3273 Ай бұрын
Well spoken, keep on giving better and good advice to the nation of Malawi, only God knows what really happened the day our beloved deputy president passed on, let only the investigation reveal the truth May the souls of the deceased rest in eternal peace 😭😭😭😭😭😭
@kachisuzimwale5641
@kachisuzimwale5641 Ай бұрын
Good message
@user-nv5bd4rn8f
@user-nv5bd4rn8f Ай бұрын
Ambuye akudalitseni. Thus strong word
@user-kw7wr4kq9w
@user-kw7wr4kq9w Ай бұрын
We need people like u God bless you ❤❤❤❤❤
@YankhoMAcheso-ee7kw
@YankhoMAcheso-ee7kw Ай бұрын
Not need people like him.... We have to be like him
@EliChitupe
@EliChitupe Ай бұрын
Thank you sir ❤❤
@AnthonyPhiri-bm4vs
@AnthonyPhiri-bm4vs Ай бұрын
Thanks polangiza ndikuphuzisa komwe koma ino ndithawi yoti athu alakhule zakukhos kwao iyi ndi imfa yowawa so do pray with it
@EuniceKalambo
@EuniceKalambo Ай бұрын
God have mercy...
@ireentaombe
@ireentaombe Ай бұрын
Following with interest
@Okalekale
@Okalekale Ай бұрын
Kufotokozela bwino,nzika ya nzeru.Ambiri ndi okhudzidwa koma kulira ndikosiyana-siyana.Tiyeni tilireni,tiyike maliro,then kafukufuku achitidwe mosasiya kanthu mpaka zidziwike zeni-zeni zomwe zinachitika,inali ngozidi kapena umbanda.
@angelmalawiofficial9172
@angelmalawiofficial9172 Ай бұрын
Well impact information Leader
@ThomasMphande-f8d
@ThomasMphande-f8d 22 күн бұрын
Inu abwana mnapitadi ku school mnthu wa school amalankhula motelomo zikomo God bless you.
@micheckphiri5447
@micheckphiri5447 Ай бұрын
This is a good talk
@CynthiaPatel.E.B
@CynthiaPatel.E.B Ай бұрын
A big respect to you sir
@aggieguda8660
@aggieguda8660 Ай бұрын
God bless you Mr
@Yungjoe786
@Yungjoe786 Ай бұрын
Thank you sir
@YamikaniLoya
@YamikaniLoya Ай бұрын
This massage makes a lot of sense
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 28 күн бұрын
May the lord show his grace through our brothers and sisters who lost their lives due to this accident
@user-ul7rb4bn5e
@user-ul7rb4bn5e Ай бұрын
Well said 👏👏
@benchilenje9856
@benchilenje9856 Ай бұрын
Mwayakhula Mr
@Hellenistic109
@Hellenistic109 Ай бұрын
God bless you sir
@PatrickMailos
@PatrickMailos Ай бұрын
Mavuto abwerakale pano Kaya atimanga. Atimange basi chakwera wapha chilima 😭😭😭😭
@John-to8gl
@John-to8gl Ай бұрын
Nice one 👍 bro message yamphamva imeneyi, maka potiziwitsa bwino lomwe dza tizida Tosunga information tamundegeti kuti timakhala malo olimba or Ndege itayaka moto komano tizida timeneti sitikhuzi ndi moto, I hope tizida timeneti tilipo, ambuye alemekezeke
@brightadam110
@brightadam110 Ай бұрын
Awa ndimaganixo womwe ndimaganiza cox ndidavaposo zama devices amenewa kuchoka kwa bwana wanga wa chi China 🇨🇳
@joaquegerman2250
@joaquegerman2250 Ай бұрын
God bless you man
@ImmedGerrard
@ImmedGerrard Ай бұрын
Respect🙏
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Ambuye wakumwamba bwelesani nthenda yamisala pa mbeu yose ya chakwera ndi azake ose achiwembu😢😢😢
@joaquegerman2250
@joaquegerman2250 Ай бұрын
God bless you
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Ай бұрын
Zikuwawa abale 😢😢😢😢😢 taluza anthu dziko Muno
@KenDuweh
@KenDuweh Ай бұрын
Kom Chilungamo chimaziwika nthawi ikakwana ndipo muzachita manyaz kut Amalawi aziwa chilungamo sopano akuteng step ina yot kuyikilaba kumbuyo sizagwira😢
@user-nb1ns6ye1v
@user-nb1ns6ye1v Ай бұрын
Perfect said 😢
@innocentsathasteven4093
@innocentsathasteven4093 Ай бұрын
Sad story to loosing anthu omwe amatipatsa chiyembekezo Pa malawi mizimu yawo iwuse mu myendele
@kayzeesambani7153
@kayzeesambani7153 Ай бұрын
Respect,🙏
@user-qs7nx7wi4j
@user-qs7nx7wi4j Ай бұрын
Loud and clear milandu sorted km funso tizinthu timeneto tilipo
@bensawanga9662
@bensawanga9662 Ай бұрын
Leader par excellence.MHSRIP 🙏
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Ай бұрын
Komanso ma phone a ma passengers can also be used because amongest passengers one might think of recording or eri
@greenwellmponda2363
@greenwellmponda2363 Ай бұрын
Malawi 🇲🇼 my country,mourning together here in Zambia 🇿🇲
@lucassakala3352
@lucassakala3352 Ай бұрын
Too sad rip our brothers and sisters we believe almighty is with your souls Amen
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
aboma azifufuza chani aboma ndi amene apha anthuwa anachoseranji zimenezo nfusen kunkuyu 'chakwera 'zikhale ng'oma ' ndi asilikali ndi apolice achita kuphedwa ndi mcp umboni ndiwuti
@wisdommunthali5202
@wisdommunthali5202 Ай бұрын
Umboni ngati muli nawo tionetseni ugwire ntchito
@jamesjana
@jamesjana Ай бұрын
That's only way to find out the foult of the crach of our plan
@user-lg2ws2ki3d
@user-lg2ws2ki3d Ай бұрын
Respect Sir
@wilsonnoahkadyamaliro1358
@wilsonnoahkadyamaliro1358 Ай бұрын
Well Spoken
@bennyfuratiro8617
@bennyfuratiro8617 Ай бұрын
Eish ndiri kudandaura ini why why mara, forever in our hearts
@georgetwayibu7240
@georgetwayibu7240 Ай бұрын
Live from rustenburge
@SinsamalaWazuwala
@SinsamalaWazuwala Ай бұрын
Kulankhula kwa mkhalapakati❤
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Ай бұрын
Okay following 😢😢😢😢😢😢😢😢
@NedsonKanjira-qj2ig
@NedsonKanjira-qj2ig Ай бұрын
Zimenezo zili Ngati macamera anthu amatha kuzimitsa magesi Chocho camera singajambure Chocho musawanamize anthu , zimenezo kutheka Kuti anazipanga off ndizipanga anthu
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 Ай бұрын
Zidakakhala izizi zachitika ku America bwezi zitapezeka ndithu
@Musafiri529
@Musafiri529 Ай бұрын
Mukamati legend mukutanthauza chani
@user-rm2hr8ps1q
@user-rm2hr8ps1q Ай бұрын
Lord have mercy on us
@eskrecordstv7585
@eskrecordstv7585 Ай бұрын
Its hard
@ArchraphNkhoma
@ArchraphNkhoma Ай бұрын
Iwe Mbuz umafuma azibisa Kut anthu asazione azione kumene oro akanakhala malophyata akanatulutsa coz ngoz siingavule tayi,shat,jekete zose
@user-sz6bi3tw5y
@user-sz6bi3tw5y Ай бұрын
Bambo uyu ali mbali yachakwera angoyenda mbali apa
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Good Messnge koma Chakwela you mast go
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo Ай бұрын
Never give up
@patchipanga8445
@patchipanga8445 Ай бұрын
Amen
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj Ай бұрын
Wich radio station onse ndi anomaly palibe, umboni uziwike maliro asanaikidwe
@DianaMbewe-sj5qb
@DianaMbewe-sj5qb 25 күн бұрын
😢😢😢 Amen 👏👏👏👏
@Furnituremaker-vt8ku
@Furnituremaker-vt8ku Ай бұрын
Rest well ❣️❣️❣️
@SuperStuart1999
@SuperStuart1999 Ай бұрын
Mulungu lowreranipo, tiziwe zoona za ngozi yimeneyi.
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 Ай бұрын
Tikumva kuwawa my brother koma zikomo mwayankhula bwino pitilizani kutilimbikisa
@MichaelWilliamsNyirenda
@MichaelWilliamsNyirenda Ай бұрын
Good message But impeachment process go ahead
@gracemusuku6645
@gracemusuku6645 Ай бұрын
🙏
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d Ай бұрын
Nkhani ndiyoti zimenezo aboma azibwelese kuti azipange cleare okha
@IsaacDailes
@IsaacDailes Ай бұрын
Mr.. Mulungu akudalitseni poyankhula bwino chonchi no mistake 😢😢
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Kachiduloko nkutheka chakwera anatuma wanthu kuti akachoseko
@jamesbanda6943
@jamesbanda6943 Ай бұрын
Is this type of aircraft fitted with the said gadgets. Remember not all aircraft are fitted with those two devices.
@user-mp9in2bh8d
@user-mp9in2bh8d Ай бұрын
😢😢😢RIP
@DianaNakazwe-bl6oz
@DianaNakazwe-bl6oz Ай бұрын
May their souls rest in peace what a tragic
@user-yd7si9ff2h
@user-yd7si9ff2h Ай бұрын
💪💪💪💪🙏❤️❤️👍
@FletcherMkwailaMkwaila
@FletcherMkwailaMkwaila Ай бұрын
Technology
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
God please give big disease family for chakwera 😢😢😢 mukantheni chonde mulungu wanga napota nanu
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni Ай бұрын
Akutuma kt utikhazike chete ifeyo
@JohnChipeta-wg9cf
@JohnChipeta-wg9cf Ай бұрын
Ambuye atiteteze
@user-cq1sj1bb7e
@user-cq1sj1bb7e Ай бұрын
😢😢😢
@PatrickGamah
@PatrickGamah Ай бұрын
Kuyakhula zthu za nzeru Nd zothandinza kwambr
@brendaMusama-ji4qn
@brendaMusama-ji4qn Ай бұрын
😢😮
@user-qv6vz6hd4m
@user-qv6vz6hd4m Ай бұрын
😢😢
@KingsleyJika
@KingsleyJika Ай бұрын
Mau anzeru ndaku3lani abambo
@KomaniMvula
@KomaniMvula Ай бұрын
Not only Malawi but all maneba mu africa
@lottiemcdonaldsoko8589
@lottiemcdonaldsoko8589 Ай бұрын
I see the same happenings of 1986 when Samora Machel died in the same act
@SueMsukwa
@SueMsukwa Ай бұрын
Its very sad
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Koma ndi zowawa koma eishhhhhhh😭😭😭
KULIRA KWA A MALAWI - MUZAMULIRA BWANJI CHILIMA?
13:44
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 26 М.
Clown takes blame for missing candy 🍬🤣 #shorts
00:49
Yoeslan
Рет қаралды 39 МЛН
НРАВИТСЯ ЭТОТ ФОРМАТ??
00:37
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 2,6 МЛН
NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA
17:06
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 4,8 М.
Chiwembuchi MCP inayamba kukonza 2022. Rest In Peace Dr Saulos Chilima.
12:08
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 186 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 138 М.
LEVITATING MAGIC REVEALED 😱😳
0:18
Milaad K
Рет қаралды 15 МЛН
Slow motion boy #shorts by Tsuriki Show
0:14
Tsuriki Show
Рет қаралды 8 МЛН
Что делать если закрыли на балконе
0:31
Waka Waka 😁 #funnyshorts #rianashow
0:14
RianaShow
Рет қаралды 4,1 МЛН