NKHANI ZALERO-KUYANKHULA KWA ADADI

  Рет қаралды 28,918

HOT 265

HOT 265

2 ай бұрын

Пікірлер: 89
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 ай бұрын
Chakwera ndiwopusa Kwambiri bwanji amaleka kuyankhula English kuti America imve koma nkhani ndiyakt ADAD 2025 BOMA!!!💙💙
@user-qt8qe8iu1b
@user-qt8qe8iu1b 2 ай бұрын
Komadi
@Blessingschikadewa-pt6cp
@Blessingschikadewa-pt6cp 2 ай бұрын
Too yomweyo
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 2 ай бұрын
Chitsiru choipitsitsa mdziko la Malawi ndi chimenechi chichakwera, Puppet uyu wa America
@user-xv9en6se4i
@user-xv9en6se4i 2 ай бұрын
APM my vote❤
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
Bon kalindo he must ne the president of malawi hes the true man.
@MphatsoGona-px6bq
@MphatsoGona-px6bq 2 ай бұрын
Chakwera nd wamakani ekha anati Ngati sipatha zaka ziwiri azatula udindo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
APM my vote❤❤❤❤❤
@user-xi7bo8jx8h
@user-xi7bo8jx8h 2 ай бұрын
Apm my vote
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 ай бұрын
Thindwa nthawi zonse amasokoneza zinthu
@NedsonKanjira-qj2ig
@NedsonKanjira-qj2ig 2 ай бұрын
Achita bwino kwambiri Komanso akanabwera akumangeni akulandeninso katundu mukutitenga Ngati zitsiru
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y 2 ай бұрын
Chakwera walozedwa tikuonera 2025
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 ай бұрын
Nde America limazapempha thandizo ngati kumalawi .. .inuyo ndamene muli ndivuto kupempha pempha
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 2 ай бұрын
Ife timadziwa timadziwa kuti chakwera ndi chilima tonse alliance nja bodza mmaonjeza ma promise ma guy APM alowe tione Zina ma khoti akumalawi mu nthawi ya tonse alliance sakugwila nthito yokomera malawi chofunika let's work up malawi tikavote tichotse mbavazi
@patrickkapinga7091
@patrickkapinga7091 2 ай бұрын
Koma chakwera chomwe akuchifuna achipedza ndithu
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 2 ай бұрын
Chakwela ndi mbuzi yamunthu,
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 2 ай бұрын
Akuyankhula ngati ali ndipogwilatu koma koma apure ai zikomo bola munakangokhala chete osayankhulapo moti iwe chakwela sukuona kuti kuyankhula uku ndikuzibeleka mbava ku mbuyo , kdi titamati iwe ndie mbava yaikulu nkulakwa? And ndikakhala ine ndinakuziwa kale ndie president oipa ndie sindikuona chodabwisa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 ай бұрын
Nanuso kharani pasi .. ACB munaimedza ndangati omwe anamangidwa m,boma lanu ..anthu 83 aja chilima yekha nde anakuphwkerani
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 2 ай бұрын
America yangon'alura chilungamo bravo achitsiru apule mudya chani mukanyoza America shut up
@macleanmachamo
@macleanmachamo 2 ай бұрын
America yachita bwino bwanji makhoti akuchedwesa milanduyo
@user-ik8ii8nv1i
@user-ik8ii8nv1i 2 ай бұрын
America yachita bwino powatsekera akubawo
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 2 ай бұрын
American imata kwambili ntati zakuwawa chakwela uwamenye tikuwonele mbava iwe ukuwopa Tanzania kuli bwanji America opusa iwe ndithu
@elishamael-shadai
@elishamael-shadai 2 ай бұрын
Where are the 83 criminals you promised to get arrested including you Chakwera
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 2 ай бұрын
Chakwera m'busa odya chakhumi
@user-td1ll5ge6n
@user-td1ll5ge6n 2 ай бұрын
Mbuzi imene bola awamasula khontiso lachani😊😊😊😊
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa 2 ай бұрын
Mawu awawa akupita kwa American komano American imva nao chichewacho 😂😂😂😂😂😂
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 ай бұрын
Kufoira kmso mantha .😂😂
@ophlexmkondowe8107
@ophlexmkondowe8107 2 ай бұрын
Koma ku bomako kuba kwanyanya mpaka America kulankhulapo,mmati DPP ndiyakuba nanga mwamanga angati,ndale zopusa.
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
President opusa kwambili nde uzikapepha kut galu iwe popeza ndi Baden yemweyo umakamugwadira
@AubreyChiyaya-ty8ge
@AubreyChiyaya-ty8ge 2 ай бұрын
Mwana wa hule chakwela
@homeremedys3748
@homeremedys3748 2 ай бұрын
Ngati bodza kuti wamwalira Nkaka, sleep well Nkaka
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 2 ай бұрын
Chilichonse chabwino chomwe angapange a MCP panopa chifukwa ndi kampeni ili ndi cholinga chofuna kukopa anthu
@user-qp4gk5gx8j
@user-qp4gk5gx8j 2 ай бұрын
Yes but ndizzoonaaa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Ndipo why am alankhula chichewa podzudzula America yo, uyu ndi krook kwambiri mweeee... Inu nonse ndi mbava di zooona zokhazokha..
@LingtonChimutu
@LingtonChimutu 2 ай бұрын
Bomatu iro kazaramurani i
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 2 ай бұрын
Kulakhula kwa apule chimozimozi Mwana weniweni ndalama dzakunja kwake kuti simwati ndiauba paka apule kunena ameleka kuti ndiokuba koma soka lapamalawi ukalodzedwa sunukha
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 2 ай бұрын
Akuyikila kumbuyo anthu akuba uyu
@adamkudzala186
@adamkudzala186 2 ай бұрын
Anangolakwa nayenso osamupanga bar chifukwa nayenso ndiwakuba
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 ай бұрын
Iwe supanga nawo ndiweso mbamva, paka America yakuonelani achakwela
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 2 ай бұрын
Chakwela ndiwee galu wamuthu
@ShadreckNgozo-ng6ll
@ShadreckNgozo-ng6ll 2 ай бұрын
Kodi nkhani imeneyi mudzakamba liti? Idzaweluzidwa liti? Inuyo manyazi mulibe? Nkhani zakatangale zimatha kuno kumalawi? Sheme on you
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 2 ай бұрын
Analowa 2020 boma thawiyosei bwanji samachitapo Kathu padzandalama dzamisokho yaabusawa apanga pano kamba ka kapeni tiyeni mutipedza usogoloko
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Chakwera ndi mfiti guys, nyumba ya zipinda zitatu anthu tiziimanga dzaka 23 mmmmm coz chakudura kwakatundu mmmmm😢😢😢😢😢😢😢
@user-zg9se4rw6v
@user-zg9se4rw6v 2 ай бұрын
Osatukwana, bwanji kodi
@user-xj9uy6wz7b
@user-xj9uy6wz7b 2 ай бұрын
Esh
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 2 ай бұрын
Achakwera nthawi yanu ndiye ikufulumira kuthatu....APM akulowa next year ku sanjika palace....chifukwa chani ukuikira kumbuyo mbava?kodi kapena mumabera limodziiii?
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
APM woyeeeeeee ❤❤❤❤
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 2 ай бұрын
Boma ili ndilakuba America yachitabwino .
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 achakwera njenje aseka ma account awo
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 2 ай бұрын
Ndingaipedze bwanji Vedio imeneyi Kuti ikhale muphone mu
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
America or kukhale zochitika zambiri koma zawo zikuyenda and America palibe chimene ingatenge kuno ku African chauleri imagula. Koma inu apule ndi benja lanu mumapita ku America kukapempha.so dolo ndindani mukukhzikisa zikopa alendo alendo mukufuna azibwera kumalawi wochokera ku America nanga America yingakope alendo kuchoka kumalawi ndakauika
@user-qp5mu7ui2c
@user-qp5mu7ui2c 2 ай бұрын
Uyu akusiwa chilungamo
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 2 ай бұрын
Mbava zimabakiranatu
@WilsonLimited-os1xd
@WilsonLimited-os1xd 2 ай бұрын
2025 bon kalindo Bomaaa ati ngati niseke kkkkkk
@LuteSynos
@LuteSynos 2 ай бұрын
Amangidwe mayiyo
@user-nu8oo6oc4j
@user-nu8oo6oc4j 2 ай бұрын
Mesa iweyo galu papet WA biden
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 2 ай бұрын
Nsonkho kungochotsera abusa okha bwanji komanso mu nthawi ya kampeni kwanji???
@MphatsoGona-px6bq
@MphatsoGona-px6bq 2 ай бұрын
Timakukondani adad Dpp boma 2025.....
@macleanmachamo
@macleanmachamo 2 ай бұрын
Apule mwapupuluma poyankhapo
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 2 ай бұрын
Chakwera ndi galu iweso
@chrismatemba556
@chrismatemba556 2 ай бұрын
Wasting your time. This country is going no whete with bad reputation of our own making. Do not blame anyone but ourselves. Especially, politicians.
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 2 ай бұрын
Galu mbava yayikulu mumalawi, racist president chiyenda chekha chopanda mwana
@thondoyaenterprise3795
@thondoyaenterprise3795 2 ай бұрын
America has just banned those 4 from entering their nation. I dont see any meddling their.
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
This government is stupid indeed
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w 2 ай бұрын
Chakwara ndi nzibanbo ombwambwana koma nkaziwake samazuzula mamunayi?
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 2 ай бұрын
Kodi chakwera yu akufuna kunama Kuti ACB ikugwira ntchito Malawi Muno?
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 2 ай бұрын
Zakupoila Kwa a pule aliyense akuziwa kale Koma prophet yo amangidwe tisanamugende😡😡
@promixphotography8056
@promixphotography8056 2 ай бұрын
Baga moyo wachakwera
@duncainjimmy
@duncainjimmy 2 ай бұрын
Ngati America amapempha ku Malawi ndie kuti Chakwera is right koma ngati America without Malawi singavutike then Chakwera is wrong
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 2 ай бұрын
Chakwera ndi mbuz
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 2 ай бұрын
Lazaro waumphawi basi bagamoyo 😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 2 ай бұрын
Just translate it into English amarica yo imve bwnobwino .. president opepela uyu watikwana😅😅😅
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 2 ай бұрын
American yachita bwino kuwaletsa koma a chakwera chifukwa cha Kuba kwambiri ndi momwe akuyikira kumbuyo anthuwo
@mussazilingo4544
@mussazilingo4544 2 ай бұрын
Pamenepo akuganiziratu DPP 😅
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
All those you what you talking it can not work dtop down building materials then people then pwople the can manage to build nice houses
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v 2 ай бұрын
Mmm makhoti akuno amatha ntchito ntchito yake iti ziphuphu zomwezo?
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 ай бұрын
Ngat pali nthawi imene mdzika za dziko lino zinataya ma voti awo pa chabe, pamaloto a chumba ndie 2020 povotera Tonse alliance ndi Chakwera, stupid President ever. Mfumu yeniyeni ya katangale.
@hazibatizoni9366
@hazibatizoni9366 2 ай бұрын
Why speech imeneyi osayankhura muchizungu kut dziko la America live😂
@NuradinaAbrahima-rt9ip
@NuradinaAbrahima-rt9ip 2 ай бұрын
Chakwela ndiwe munthu woyipa kwambili stupid ☹☹☹☹
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
Malawian court of the law donsnt work well at all to people of malawi ,because court of malawi they under mcp.
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 2 ай бұрын
Uku ndi kupusitsa Amalawi iwe chakwera ndi mbuye wakoyo America Get out all of you puppets
@WilsonLimited-os1xd
@WilsonLimited-os1xd 2 ай бұрын
Ghetto master munthalika katundu
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 2 ай бұрын
Chakwela ndiwee galu wamuthu
NKHANI ZALERO 9 July 2024.
23:37
HOT 265
Рет қаралды 4 М.
Zohnuai lei khi a chet belh zel.
38:08
Samson ZR Hmar
Рет қаралды 16 М.
Nutella bro sis family Challenge 😋
00:31
Mr. Clabik
Рет қаралды 11 МЛН
🤔Какой Орган самый длинный ? #shorts
00:42
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Raila: Be aware of the WRATH of history
23:42
Herman Manyora
Рет қаралды 38 М.
TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA
10:10
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 174 М.
E361 Navigating the Bible: The Pentateuch
44:18
Saddleback Church
Рет қаралды 138 М.
KUYANKHULA MPAKA CHONCHO PA MASO PA APULE DR CHAKWELA
14:32
Nutella bro sis family Challenge 😋
00:31
Mr. Clabik
Рет қаралды 11 МЛН