On Nyasa VoiceBox, A Concerned Citizen, outlines the reason why MCP will not win the Next Election. Pa Nyasa VoiceBox, Mzika Yokhudzidwa, ikufotokoza zifukwa zomwe MCP sichidzapambana pachisankho Chotsatira. #malawi
Пікірлер: 42
@SolomonNjolomole15 күн бұрын
Zoonadi chidule akuluwa ndi kupha apambuyo pawo chomcho sibwino ntchito za satana kumaoneka ngati abusa.
@Homeofpeace32115 күн бұрын
Komatu Iwe Chakwela Mmene Unapha Chilima Muja Usazitenge Opambana Iyayi. Udindo Uliwo Pangafupike Pangatalike Umatha, Iyi Si one Party System. Chitsiru
@Spaw-BTheGogoBoy15 күн бұрын
MCP ku moto 🔥🥵 izikakukuta mano
@PrinceBlessings-bv5bs15 күн бұрын
Koma ndizoona ndithu... Azitolankhan panopa akuopa kwambir, sakuyankhura tchutchu ai... Bodza anthuwatu amayenera achoke mdzina la mulungu please 🙏
@hanifahmponda871115 күн бұрын
Dzowona anthu akudziwa chilungamo pano
@marryphili541915 күн бұрын
Mukunena zoona abro kupanga mugwirizano ndi MCP zikungofanana kuti wuli pa wubwezi ndi mkango mukangosemphana pang' ono basi iwe ndi wulendo
@UTHMAN-WAYA15 күн бұрын
Hahaha izo ndezoona yhoo👀
@JunaKananji15 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤waganisa bho Love you ❤❤
@GoodsonLindani-gf8pn15 күн бұрын
Zoonadi big chakwela akumamvera anthu oipa awa,chimwendo banda, h mkaka, z ng'oma, mkukuyu, gotani hara, ndianthu okupha, oyambisa kusankhana mitundu ndi zonse zonyasaamenewa ndiagalu.
Bakili Muluzi mu 1994, Ndi kamenya kwaya Ana imba nyimbo nthawi imeneyo ndiri kalasi 7.Anati MCP,eeeee, MCP,Anthu aja Ndi akuphààaaà,Abale MCP,eeeee, MCP Anthu aja Ndi A kubaaaa, MCP wakupha Chakwera woyeeeee wakupha aaaaa,aku Phani Nonse kumeneko oooo,thamangisani mimbulu yoooo
@LysonMtalika-tb6fk15 күн бұрын
I salute you big man ❤❤❤
@user-cf9yz3ei5o15 күн бұрын
You are 100 percent right
@dontreybanda27815 күн бұрын
Good massage boss
@user-gg9hw4oj2v15 күн бұрын
That's facts bro
@GeorgePhiri-ub2of15 күн бұрын
Uchitsilu ukabvota wekha ndi tiyana tako ndiwe mbuzi yamunthu
@RCFAKI-mx4dv15 күн бұрын
Hello
@joykhonje11 күн бұрын
U T M please pangani mgwilizano ndi zipanizina
@GeorgePhiri-ub2of15 күн бұрын
Mbuzi yamunthu mbuli yosapita ku school
@ChimwemweKondowe-nj4lx15 күн бұрын
Kumeneko nde kukamba tchutchutchu
@MosesTangwe15 күн бұрын
Ndipo or kumudziko munthu amene Sali pa You tube kumufunsa angoti bola Pete yemweuja chimanga chimkapezeka mu admark. soap timkakwanitsa kugula😢