Chakwera Ambuye amuone ndionse omwe anatengapo mbali
@user-xm3zl5cg6xАй бұрын
Yehova amava aliyese apukute misonzi yathu ndi chilungamo
@ruthkundwe7448Ай бұрын
My president suffered with others on that day,oooh God u r the God who never sleeps, THE WICKED WILL NEVER REST
@user-do2cs8nf4bАй бұрын
Zinsinsi ndzayehova, zombvumbuluka ndi za ife ndi ana athu, Mulungu ambvumbulutsa China chilichonse chikhala poyera
@FrynessMoyo-to2duАй бұрын
Chakwera unapedzeka bwanji ndi black box asilikari amalawi ndi manyi chakwera nyini yamako 😢😢😢😢
@PreciousBandah-l2r29 күн бұрын
Mutu sugwela iwe
@cynthiakananji1608Ай бұрын
Mzimu wa chilima sunagone Uzagona chilungamo chikapezeka. Mukazangophaso a nyamata awiriwa, Mizimu ikupengesani misala baba kuvula kulipo chaka chino
@BlacksonKambazawanaАй бұрын
Koma chonde chonde izizi ngati zili chotcho sizabwino .komaso azungu awa atiwuze mwachangu mistake its mistake asibisepo munthu chonde timakukondani koma payizi fulumizitsani chonde ngati zinatelo kungo vomekeza mbili siyiphamunthu panalakwika koma zovotela dpp ayi tizavutika amalawi tisakhe chipani china kupatula ziwilizi ngati ndizowona izi koma ngati ndibodza mcp yomweyo.
@alomuddin8801Ай бұрын
😄😄 CHakwera manyazi bwaaa, amalawi kuwamenyanitsa mitu mmaganinzo Pa ifa ya chilima iwe ukudziwa, apa ndy waonetsa machendeee manyazi bwaaaa
@user-ky4ce9gb6jАй бұрын
Ndipo inu esh
@user-yw7qv3ld5k29 күн бұрын
Mmmhh ayayi imfwa yowawa iyi
@BellaMandalaАй бұрын
Sitingamangoyasa candle for nothing
@RhulaniMukasi3 күн бұрын
Anaminyero ose amatumbwa kumapakira chakweraaja arikut Sono nthawi yakwana DC karindo nkhan ndiimeneyo mmawa kofunika kuilengeza zenizen bakiki muluz osaiwara nkhan ndiimeneyo
@rhodahjere874725 күн бұрын
Galu kamupeni akapangire kwa make,osati a Malawi ndindaniso angamuvotere
@emilynthite6545Ай бұрын
Azimangilila ameneyi chikangawai
@isabelmartin7567Ай бұрын
Mulungu saozela ❤❤❤
@juliusnjerengo2610Ай бұрын
GPS global positioning system.
@yassinn5634Ай бұрын
Anamva akuthama ali Geographical mmalo mwa global
@user-bd5kw8oq1rАй бұрын
Ayi koma mumatha kitumikila satana inu munakachipeza bwanji kumeneko 😅😅 eeeeeeeee kuli ntchito a Malawi amalawi kodi yesu atakupezani mukunena zopanda umboni mungatani osamvako mu mtima kuti ndikunenazi ndili ndi umboni? 😅😅 manyazi mulibe anthu inu work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
@InnocentEdasiАй бұрын
Chilima ause mumtendele
@ChancyJere-pz5svАй бұрын
MCP chomwe yinapanga siyikuchiziwa kom chomwe aziwe misozi yaathu ambiri singapite pachabe muwona mulungu ava kulila kwa malawi
@user-fh7sd6gp3fАй бұрын
Shaaaaa kutamba masana mcp😊
@HaliJana12 күн бұрын
KOMA CHAKWERA NDIWE OLIMBA MTIMA ANTHU 9 UMAGANIZA BWANJI KOMA MIZIMU 9 KUPHA CHAKWERA ULIBE UMUNTHU PANYELA PAKO
Zimenezo nde inu mwazitenga kuti,mu Black box, kapena zabodza zanuzo
@user-ke7ii6ip4sАй бұрын
Baliki muluz ali ku tete ntanyiwa ali ku tazaniya
@AndreaLouis-wd8iv14 күн бұрын
Software which those guys they using l don't even geographic point service it will show 🙄
@user-vu4cz1mt4fАй бұрын
Koma mbuz imenei osangoimika manja bwnj coz zonsetu zingofika poyera
@williamsalexmbongaАй бұрын
Mzosatheka ukunenazo ase iwe Chimphuno chako
@user-oc9vl9xz8eАй бұрын
Zamanyanzi kwambili athawa dziko lokhala lawo
@amoschataika7440Ай бұрын
Yomweyo Chikangawa 😂😂😂
@christiantattoo779Ай бұрын
Paline chinsinsi pa dziko la pansi aziona Mulungu amalanga
@Randy-er2xo3 күн бұрын
Chipulezidenti chakupha
@MariamChipokaАй бұрын
Mulungu amapanga njira popanda njira
@chrispahuwaАй бұрын
Koma chophera anthu ndi chiyani satana iwe wandiliza
@GriffinDelelekaАй бұрын
Masiku ano kuli technology asatengere nthawi ya kamuzu anthu chilungamo amachibisa ndimatha
@Mervic-vm8eoАй бұрын
Chakwera pamtumbo pako galu iwe
@MphatsoIshmaeladamАй бұрын
Yes that's true ndipo akunena zoona koma afufuza bwanji popanda black box
@WilliamBandaWiliАй бұрын
Athakati awa koma ndi abusa assemblies fake
@user-xt2gu9yt9qАй бұрын
Ose paulendo omwe anatengapo gao koma ziliko
@Malani4127 күн бұрын
GPS is global positioning satellite! Don’t get it twisted.
@DanielJuwawoАй бұрын
Mizimu ndi yambiri zedi kuwapha anthu osalakwa zoona mmmmmmm koma mcp ayi ndithu
@ChiukepochakuzgukaMunthali26 күн бұрын
Ukuyankhulawe ndi wa MCP. Apa ukufuna kusokoneza kafukufuku wa German. Chonde khala chete tose tiyang'anile chimene a German atanene, mukachulusa zokambakamba choona chenicheni chisokonekela chifukwa oganilizidwawo alibe pa ulamuliro wa ziko lino