UTM Yasambwaza Peter Mutharika Ndi Mayi Joyce Banda

  Рет қаралды 8,549

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

UTM Yasambwaza Peter Mutharika Ndi Mayi Joyce Banda

Пікірлер: 87
@BridgetZingani-gb8yf
@BridgetZingani-gb8yf 2 ай бұрын
Musiyeni APM mukumuopa .....wait pa 12 May mumva m'bebe
@FaroukMdala
@FaroukMdala 2 ай бұрын
Ngati Pali zitsilu Za anthu Andale ndiopanda nzeru ndiye zili Ku UTM ,tsogolo Lake silimaoneka bwino bwino,mtsogoleri wawo ndiye onama
@superiormoses4802
@superiormoses4802 2 ай бұрын
Ovota ndife kumene zili ndi Ife kma chilima kudzawina iwalani guys
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n 2 ай бұрын
km peter ndie akuopedw chilimba ndi mbava ovota ndi amalaw
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 2 ай бұрын
Malo molimba ndi MCP mukulimba ndi dpp ndinu opanda zrlu
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 2 ай бұрын
Mbudzi za anthu kusiya kukamba za mzeru ntchito ku nyonza adzawo chiiti
@GracianSomola
@GracianSomola 2 ай бұрын
Koma ndiye APM akuwopedwa
@lymonmanda-cd8ol
@lymonmanda-cd8ol 2 ай бұрын
Ana ambava inu
@NedsonIssah
@NedsonIssah 2 ай бұрын
Osazinamiza makape inu a UTM nonse mbava zotheratu
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 2 ай бұрын
Osalimbana ndi omwe akulamula pano bwanji mukumuopa APM ana mwachepa
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 2 ай бұрын
Makape inu izo ndi fundo zotuluka dziko za ziiiiiii mbamva
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 2 ай бұрын
Kodi mesa mukuti ndale zonyozana ndi mulandu?
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
Vuto ndilimenero kupusisa amalawi zinenami zokhuza chipani chanu asiyeni anthu ngati akufuna kubwerera mubuyo ndikuti azibdikira kulakwa kwao komaso aona kupita chisogolo palibe zeru. Yakhulani zaumbava wa mutsogoleri wanu awuzeni anthu kuti mbava yathu ayikhululukikidwa ndi mbava zizake. Musonkhano wanu utm muli busy kuyakhula za munyumba mwaweni mbuzi zenizeni
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 ай бұрын
Utm ndimkayikonda koopswa km moto wamapesi zolamulanso iwalani zimenezo 💙
@EvanceMponda
@EvanceMponda 2 ай бұрын
Mukakhala a UTM mukuvutikiranji kumataya nthawi kumayankhula ngati mulindi mtsogoleri yemwe akukusogolerani? Anthu mukuzitsogolera nokha nkhosa zopanda m'busa
@honourablemcgregorysc97tv
@honourablemcgregorysc97tv 2 ай бұрын
Mukalimbana ndi APM nde I can't support that, limbanani ndi MCP baxi coz pa DPP simungamake ndithu
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 ай бұрын
Komatu azanuwo amatiopsya maonekedwewo ife kkkkk,eeee! Kaya!
@stanleykaludzu-bm4pm
@stanleykaludzu-bm4pm 2 ай бұрын
APM ndi machine I think ndimpase vote tione chomwe anthu akumuopera
@LonelySapanga
@LonelySapanga 2 ай бұрын
Zaziiiiiii musatinyasepo apa aliyese pamalo pache Basi tiona mathero ake
@user-zy9ik7gq2t
@user-zy9ik7gq2t 2 ай бұрын
Mukamati mukukapanga musokhano muzilemba fundo osati zimenezo mukulakhulazo ai , mbava chilima zeze mbava mwagundika kulimbana ndi azanu kupusa
@user-gn3gy5iq5x
@user-gn3gy5iq5x 2 ай бұрын
Izi ndiye zitiso zachibwana basi mukutiona Ngati zinsiru zanu ife... UTM ndi MCP zanu ndizimodzi mwadzuza amalawi Kwa dzaka 4..
@user-xd6hq1pp4d
@user-xd6hq1pp4d 2 ай бұрын
Koma ndiye abwelelatu 2025 mbava yakoyo kwanu komweko
@user-ie4ci3zh7j
@user-ie4ci3zh7j 2 ай бұрын
Ndizisilu izi nde matha amenewo
@mphatsokutama
@mphatsokutama 2 ай бұрын
Tamak ambani fundo zsnu osalimbana ndi ena nde kulephera kumeneko
@MisheckNtanbalika
@MisheckNtanbalika 2 ай бұрын
Nkhani ndiyoti kuziwa kusamala Mano sikusuka kamwa chaka chammawa tizasakhano mwanzelu mujam ambili anali atamwa ambuye ntengen nde samaona ndipo a Peter Tachita kuwapepha sitikufun agalu inuy
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Kkkkkkk ndemwasowa chochita mweee... Nanuso anthu inu mitu yanu imagwira koma...
@PlanzaWisiki-cv2fs
@PlanzaWisiki-cv2fs 2 ай бұрын
Is only atupele muluzi our last hope
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Tikuonerani kuti kodi mudendekeranso matumba pa phewa ulendo uno.
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Chilima nde ndaniso? Agalu inu et Zadziiiiiiiii
@user-gb2rx5bl2o
@user-gb2rx5bl2o 2 ай бұрын
APM My vote
@user-ko3lj7vb2p
@user-ko3lj7vb2p 2 ай бұрын
Tikupita kwa adad aise. Inu ndi amabodza kwambiri. Makamaka uyu nfana oganiza bho yu.
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Zisiru inu prezdent wanu mbava chilima sangawine
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 2 ай бұрын
Ndinu mazoba, MCP yakuzondotsan agaru inu, zowina muiwale, APM my vote
@NelsonKadzakayesa
@NelsonKadzakayesa 2 ай бұрын
Kodi paja ka chipani ka UTM kali ndi ma MP angati paja? Chipani cha UTM chasanduka servant wa MCP womakaperekera madzi kumsonkhano kkkk
@BwanaGD
@BwanaGD 2 ай бұрын
Gulu la amalawi opusa nde ndili anthu amalawi yose yachita kuwadziwa kuti ndi mbava zachita kupulumutsana ku onyolo nde mukutiuza ziti apa kupusatu uku simukuminabe ana anjoka inu
@AmosKalembo
@AmosKalembo 2 ай бұрын
Aaa inunonse mituyanuyosagwila m dalaiwe odwalakwambili chilimawakoyo ndiameneanapangisa kuti McP iloweboma ndiyeuwauzachani pamsanapako
@BernadetterBanda
@BernadetterBanda 2 ай бұрын
Zakuvutani basi muvomekeze inu mukulimbana ndmuthu osapanga zanu bwanj
@JaphyJ
@JaphyJ 2 ай бұрын
Kkkkkk APM uja ndi boma palokha eti, why mantha as if he's in government? Panokha muwina popanda alliance?
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
Muwona zomwe ikupangeni mcp mudziwaso
@YunusBima-ku4qr
@YunusBima-ku4qr 2 ай бұрын
Sizinandiwaze!!!
@user-mi3fw1zg8b
@user-mi3fw1zg8b 2 ай бұрын
Mbuzi za Anthu inu mukuti chani apa mudzakhumudwa muona
@BysonMakalani
@BysonMakalani 2 ай бұрын
Ndiye ku MCP inabwellela ija ndi malilo Kodi mfundolesi
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 ай бұрын
Chilima ndi wokuba ayimanso bwanji
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Ndi agalu nonse ngati muli mboma Mwapanga chiyani
@user-ek9rz5jk5i
@user-ek9rz5jk5i 2 ай бұрын
Mcp inabwelera bwanji ???
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 2 ай бұрын
Peter mmmmmmm akuwopedwa 😂😂😂
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Osamalimbana ndi mcp kuti mulande.boma bwanji mukulimbana ndi apm bwanji
@BridgetZingani-gb8yf
@BridgetZingani-gb8yf 2 ай бұрын
Munatinamiza kale inu musanene za anzanu.....mulibe chonena eti pitani uko
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 2 ай бұрын
Zakunyerani omwe mukuti ndinu anyamatawa
@CalvinBanda-yg1hz
@CalvinBanda-yg1hz 2 ай бұрын
Ana a njoka inu
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 2 ай бұрын
Agulu inu ndiye muvukutika mukulimbana ndi DPP manyi anu
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 2 ай бұрын
Peter ndiye mukumuopa hahahaha
@user-xd6hq1pp4d
@user-xd6hq1pp4d 2 ай бұрын
Mukufuna chilima aziba bwino mukunama chilima mbava
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o 2 ай бұрын
Ulendo uno zakuvutani basi akuba eni eni apite kundende sopano
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Achisulu inu mungalimbane ndi DPP ana mwachepa mudziwona 2025 loko mp simupedza MCP UTM notse chani palibe inu agalu kwabasi wadzudza a malawi
@jeremiahmemmanuel9988
@jeremiahmemmanuel9988 2 ай бұрын
Awa sakudziwa chomwe akupanga
@MajidKasim
@MajidKasim 2 ай бұрын
Machende Anu achilima ndi gululanu
@EnockAckim-lc7ks
@EnockAckim-lc7ks 2 ай бұрын
Mwangopenga
@user-gb2rx5bl2o
@user-gb2rx5bl2o 2 ай бұрын
Sitidya nkhope ya.....
@mphatsojuliostandy4918
@mphatsojuliostandy4918 2 ай бұрын
Kusowa mfundo
@user-vn3ty1yg9l
@user-vn3ty1yg9l 2 ай бұрын
UTM yaKuba limbanani ndi congress. Yakuvesani kuwawa
@Hendersonspoon
@Hendersonspoon 2 ай бұрын
Inu ndiye mwalephera Muli Boma ndiye mufunanso chani anthu olephera inu mwapangisa Kuti chakwera alephere shameless
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 ай бұрын
Nawo awa .kachipani kopanda ma Brunch ma Area .mukawinira kuti nanu
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Mbava iwe panga zako ndi mbava mzakoyo chilima amalawi samuvotere
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 2 ай бұрын
Mukunama guys
@thokoJames-gp8mk
@thokoJames-gp8mk 2 ай бұрын
Kusowa mfundo zowauza wanthu
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 2 ай бұрын
Za nzii
@user-ib6jc4es3s
@user-ib6jc4es3s 2 ай бұрын
Wakuba nagakhale wanzelu panyopanu
@moosakananji1879
@moosakananji1879 2 ай бұрын
Inu mmalo moti muzilimbana tose allawas Kaya mati Chan kupusa
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 2 ай бұрын
If Peter is not going to win 2025,Atupele is going to rule Malawi not UTM or MCP your time is over
@OrtonKabbichi
@OrtonKabbichi 2 ай бұрын
Utm no mutu Malawi alipamoto Chifukwa cha makape inu
@maxwellchapita-df4tw
@maxwellchapita-df4tw 2 ай бұрын
Zaziii
@LeahNundwe-wh6vz
@LeahNundwe-wh6vz 2 ай бұрын
Mukutitolatu andale inu Sitidya ndale ifetu tisiyeni osamatinamiza nti miyambi toti "maliro akatuluka mnyumba sabwelera" DPP yalamulira kawiri, MCP yalamulira kawiri nde maliro mukunenawo nde ATI?
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Iyaa president wao okuba awa,peter muthalika,okuba ndalama zathu kazache kumakangowalamula a bank mundipase,ndalama mwa kuti,kutenga ngati boma la nyumba mwao.utm,ndi chilima okuba ndi mwenye zina,lache ati Satan kaya zoputsa, mmalawi muno chasala, munthu akapedzedwa,ndi chamba osamugwila,okuba akagwile okubatso?tawabveni,zisilu pasipo .
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 ай бұрын
Zaziiii
@patriciakenmuir
@patriciakenmuir 2 ай бұрын
Mavuto pa malawi
@ShabanIssa-il6nc
@ShabanIssa-il6nc 2 ай бұрын
Mukanena kuti maliro sabwelera nyumba awondimaliro nanga akaziwa ndan kuti MCP itilamulanso kkkkk kusowa mfundo Achilima o ndi amene akusangalala chifukwa akudya ndlama zaboma ife tiyeni tizingolima bas kapolo sakwiya
@BASHILUMangwetu
@BASHILUMangwetu 2 ай бұрын
Tachoka iwe zachamba basi mulowa kt
@NelsonKadzakayesa
@NelsonKadzakayesa 2 ай бұрын
Nkhope yomangowala koma boma lirilonse kumangokhala kupanidwa ku chitseko sikupusa kumeneko? Vice president wamtundu wanji womangoti sindiri pa chiongolero? Akhungu zimutsatirani popeza wakhungu akatsogola inu nkumamutsatira mumakagwera limodzi. Vice President wosalankhula a Malawi akuzunzika mesa ameneyu ndi uja ankati fetereza tidzagula 4,000 lero muli duuu kubisala chifukwa Cha boza koma umbava basi ndiye ntchito yomwe mumatha
@user-wm2sv8dw5d
@user-wm2sv8dw5d 2 ай бұрын
kayatu😂😂😂
@user-hd7wq2yc6m
@user-hd7wq2yc6m 2 ай бұрын
Chipani cha utm ndi chipani chakuba misonkho ya a Malawi pamodzi ndi chipani cha mcp ,utm musayembekezere kuti mungawine jiiiiiii mwakhululikilana mbava zokhazokha iwe ukuyowoya apo ndiwe wa mahala iwe? Chindere cha munthu kulya katatu kuli nkhuni? Feteleza wa K4495 alikuti ? 1 million jobs ilikuti ? Ivo vikuvina apo navyo vyavyamba vekhavekha uchindere pera munya anthu sakumveranisoni zokamba zanuzo zautsiru ayi mwagwa nayo
@MaxwellKaziputa
@MaxwellKaziputa 2 ай бұрын
Mbuzi zenizeni, rubbish
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 2 ай бұрын
Zaziiii mwakhuta khuta uko mimbagwa nkumakuwa zinthu zopanda mutu apa muzithaima chaka chamawa ndipomwe muzaziwe kt khobwe sinyemba
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 161 М.
Женская драка в Кызылорде
00:53
AIRAN
Рет қаралды 418 М.
Cat Corn?! 🙀 #cat #cute #catlover
00:54
Stocat
Рет қаралды 16 МЛН
Now THIS is entertainment! 🤣
00:59
America's Got Talent
Рет қаралды 39 МЛН
Patriotic Alliance holding its campaign rally in Cape Town
20:50
DRIVING SCHOOL- Episode 166
15:17
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 91 М.
Ching'aning'ani comedy, ft Ngiringande
6:53
Malawi Page
Рет қаралды 305 М.
ZOMWE ZACHITIKA KU ESCOM YAKU BLANTYRE🙌🙌🙌🔥
20:54
HOT 265
Рет қаралды 4,4 М.
Rev Alexander Kambiri preaching at the funeral his uncle in Mitundu- Lilongwe
12:39