Wa pa kaliyala akuyimba belu; Don't take malawians for granted.

  Рет қаралды 29,401

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Ай бұрын

Пікірлер: 158
@shideshidex5679
@shideshidex5679 Ай бұрын
Apeze Ntchito Kwaamkuno Mbuz Yobhibhira Muchimbudz Iyi Gwape
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Bakili muluzi tv God bless you ❤❤❤
@moyo77777
@moyo77777 Ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣zaziwika Kuti chakwera ndichilima ndimbava zopanda zelu out we don't need them again mbava
@MalakamMillie
@MalakamMillie Ай бұрын
Bakili muluzi umakwanila balewanga God ahead u
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 Ай бұрын
This government has been extremely unsuccessful.
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd Ай бұрын
Exactly
@user-ww2il4wb8o
@user-ww2il4wb8o Ай бұрын
😢malawi ifeyotu kukhanzikaku Koyenda sikufuna
@ZaidJafar-kk9be
@ZaidJafar-kk9be Ай бұрын
kod tima sound tanuti munati tenga kt bigyy timandi waza kwabass🔥🔥🔥🔥 makamaka kena kaja kamandi vetsa kukoma hevyy my best tv 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🙏
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t Ай бұрын
Anayimba nyimboyi ndi a millenium sound checks zinavuta nchala cha 2000
@chimajrbhahat2334
@chimajrbhahat2334 Ай бұрын
Keep informing us bro. Asatana akulamulawa ngolephera
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj Ай бұрын
Ndisamvenso kt mukumusaka wa bakiri muluzi TV mukumva kubomako
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga Ай бұрын
😂😂 eeee ayi ndithu Ulemu wanu brother ❤
@user-et5nz4vz2v
@user-et5nz4vz2v Ай бұрын
Best TV ever
@NoelKhwimba-bh3ts
@NoelKhwimba-bh3ts Ай бұрын
Amene amalandira 35k 2019 amalandira ndalama zambiri kuposa amene alulandira 120k 2024 😢😢
@user-yd7si9ff2h
@user-yd7si9ff2h Ай бұрын
Samadziwa zomwe amayankhula achina chakwerawa amangoziyankhulira🤜👨
@powercharios2087
@powercharios2087 Ай бұрын
Chitsilu ichi akuti chakwerayi akangokambapo atakhuta nsima yomwe imapezeka tikugula fetereza otchipa muthawi ya Peter osati zalerozi ulamulilo wausi one million Job or Jocks
@user-hk1kj9bk7b
@user-hk1kj9bk7b Ай бұрын
Zowona kutinamidza ife akumangochi
@JohnGavinara
@JohnGavinara Ай бұрын
Kkkkk chilungamo ndi mwano m,darayu walepela
@innocentnjoka7014
@innocentnjoka7014 Ай бұрын
Keep it up brother mmakwana❤
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Chikomekome cha nkhuyu mukati Muli Nyerere usogoreli alibe anthu Awa ndi akuba okhaokha
@HassanSinoya-wl3vl
@HassanSinoya-wl3vl Ай бұрын
Ndimomwemo alephela achoke bas ameneyo 😂😂
@chimajrbhahat2334
@chimajrbhahat2334 Ай бұрын
Anthu ankati ayi m'busa apanga chilungamo!! Mbava yeniyeni
@chifundolipenga270
@chifundolipenga270 Ай бұрын
😂😂😂😂😂Malawi ngokoma Odi ine ndipichire kwazizira
@HarryKandani
@HarryKandani Ай бұрын
Aaah nyau alliance zolonjeza thoooo koma yeah abusa a ku bagamoyo
@innocentbwanali7546
@innocentbwanali7546 Ай бұрын
chilima is genius whether one's like it or not
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd Ай бұрын
Because of that mentality that why we are poor......
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t Ай бұрын
Innocent bwanali ndiwe wopembedza mafano kape
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Aksnakhala genius sakanaputsitsidwa ndi MCP. Manifesto amenewa anabera Silvio Berlusconi wa ku Itally. Anachita kukupera ndendende.
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n Ай бұрын
Mutu wako sukuyenda bwino, go visit the doctor immediately
@ChildofGod_MjB
@ChildofGod_MjB Ай бұрын
Mulungu wakumwamba akhululukire amalawi tonse chifukwa cha nsanje zomwe tilinazo chifukwa boma lomwe linalipo lija anthu munadana naro opanda chifukwa chokwanira lero tili ndizifukwa zonse zofika pamaso pa Mulungu nkugonja tinachimwa
@BrownMainje-sh7hj
@BrownMainje-sh7hj Ай бұрын
This is great staff
@rexphiri7242
@rexphiri7242 Ай бұрын
Wakuba nd m'bale wake m'busa 😅😅😅😅😅 koma Malawi
@user-vn9or3te9x
@user-vn9or3te9x Ай бұрын
Mmakwana brother ❤❤❤❤
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Olikonda dziko la Malawi asavitere achakwera ndi achilima ,anthu awa asaukisa malawi kwambiri,asayese ngat omwe alikumaiko akunjawo sikuti mkufuna ayi koma kunganiza ndimomwe zithu zilili kuno ku Malawi
@user-th3yy1ku2n
@user-th3yy1ku2n Ай бұрын
Wakuba ameneyo
@user-xu9rh1lm8o
@user-xu9rh1lm8o Ай бұрын
Kuno timangwila ntchito yosatifusa ma pepala aku school
@user-wb3us4pg4b
@user-wb3us4pg4b Ай бұрын
Kkkk kwankuno😂😂😂 koma yaa that's why anasokoneza system yapassport
@IliyasaYusuf
@IliyasaYusuf Ай бұрын
Don't give up bakili muluzi
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Airport mamanga ndiiti imodzi yokha, olo half ya Airport
@AllanChabwela
@AllanChabwela Ай бұрын
Mmmmm awa kulonjeza saxatopa nako
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
phwala lako iwe chakwera ndi chilimayo zitsiru zanthu
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
The grade of MCP government is "Undoubted Failure"=="E".
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Mbuzi ya president
@mrsmoseskita9180
@mrsmoseskita9180 Ай бұрын
Nyau yoputsa galu weniweni chakwera ndiwe mbuzi ya president moyenda bagamoyo watikwana
@ComfortMangochi-gb2su
@ComfortMangochi-gb2su Ай бұрын
Akuba awa
@ashikalam8616
@ashikalam8616 Ай бұрын
Yonse alliance yonse mbuzi za wanthu .
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m Ай бұрын
Anthu away mbuzi dzaanthu asiyeni mulungu atimenyela nkhondo
@user-jy5sl8yr5n
@user-jy5sl8yr5n Ай бұрын
First watch
@ThomasShuga
@ThomasShuga Ай бұрын
Pa mtumbo pake chakwera ndi chilima wakeyo
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l Ай бұрын
Wayambaso kunama chakwera
@abisalomchunga6695
@abisalomchunga6695 Ай бұрын
Good work big
@PatsonFundi-ie2fm
@PatsonFundi-ie2fm Ай бұрын
Big up
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b Ай бұрын
Zintchito lembani anu ndi abale anu ife ndi ana adadi bas palibe zobiza zanuzo zatikwana ife 😂😂😂😂
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias Ай бұрын
Awa liyawo ndithu🤣🤣
@MathewMandutu
@MathewMandutu Ай бұрын
Mapulani amenewa ozachita liti ameneyu kkkkkkkkk
@user-nt9go2fz3k
@user-nt9go2fz3k Ай бұрын
Chisilu cha president
@andrewmtendere3167
@andrewmtendere3167 Ай бұрын
Chakwela kod sangasamuke awone kolowela iya
@user-zw5xq3uc1j
@user-zw5xq3uc1j Ай бұрын
Kkkkkkkkk 😂 ndekwa nkunodi basi mwalephera kapumeni
@VitumbikoKumwenda-sd1uo
@VitumbikoKumwenda-sd1uo Ай бұрын
Best Tv
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv Ай бұрын
The fact is that onsewa alephera a UTM ndi a MCP
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i Ай бұрын
Zonza abwana🙊🙊🙊
@user-ke7ii6ip4s
@user-ke7ii6ip4s Ай бұрын
Bg brother mokupemba tatifufuzileni za hamas ndi israili plz
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Ай бұрын
Kodi achilimawa ATI m,chiyani munthu oyipauyu
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 Ай бұрын
International Airport Ku Nyika😂😂😂
@HamzaAyame-ch3et
@HamzaAyame-ch3et Ай бұрын
Manyaka
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 Ай бұрын
mphamva izi anyapala anjala awa
@Amgwagwa
@Amgwagwa Ай бұрын
Kwankuno
@KennethKadawati-jc1el
@KennethKadawati-jc1el Ай бұрын
Wabodza kwambiri Lazalo
@user-jn3iy5ps6r
@user-jn3iy5ps6r Ай бұрын
Koma ndale siungaivese please mupaseni mupata chilima
@robertthawie3334
@robertthawie3334 Ай бұрын
Malawi sazatheka and we lost our hope
@HedgensChisale
@HedgensChisale Ай бұрын
Koma iweyo chakwela aaaa unatinamizadi feteleza 4000 ndi khathu ai ambuye alowelelepo
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Asatitukwanise galu ameneyi
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f Ай бұрын
President wake kuyankhula modekha ngati zenizeni koma zinazi
@SyilesChebomba
@SyilesChebomba Ай бұрын
Mapwara anuoo
@lusolawo73
@lusolawo73 Ай бұрын
Mi konda u bakili Muluzi TV
@user-wp9js5vu6s
@user-wp9js5vu6s Ай бұрын
chakwela ndiwe galu
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Kkkkk maloto malemba athu 2 million wo
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi Ай бұрын
Mwalephela inu chanu palib
@alfredpindani9045
@alfredpindani9045 Ай бұрын
Nyani okuda kumaso
@xxxrepair
@xxxrepair Ай бұрын
Tikayamba kumanga, airport, tikakhala ndi MA factory, too much promises
@hassanblamu8595
@hassanblamu8595 Ай бұрын
Tikupanga support umakwana iweyo
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Ай бұрын
Chakwera pakamwa nkhati chimbudzi chofulasha chilima imvi nkhati mphaka
@user-nl5nk2wx1q
@user-nl5nk2wx1q Ай бұрын
Koma Malawi 🎉😂🎉😂
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d Ай бұрын
Chimbalangondo cha president ichi
@user-pe8uh6oq8q
@user-pe8uh6oq8q Ай бұрын
Kodi abale Chakwerayu amagwa khunyu kapena?
@user-pt5wn7nu1d
@user-pt5wn7nu1d Ай бұрын
Okuba okhaokha awa chakwera chilima onse agurukunya
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Ай бұрын
Atitopetsa atose agulu kobass
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Mulungu akukhulukileni ndithu athu oipa inu kutengela boma phuzo mulungu adzakulangani chifukwa mau amanena kuti mulomo.wabodza sudzapuluka chilango
@JoshuaMhango-tf2kh
@JoshuaMhango-tf2kh Ай бұрын
Iwe ndi 1 ase. Sanakugwirebe?
@IliyasaYusuf
@IliyasaYusuf Ай бұрын
Iwe chakwela machende ako mangochi siyimadwa katangale wakoyo
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
DPP woye not much better ApM
@jameskubwalo251
@jameskubwalo251 Ай бұрын
😂😂😂😂😂 kwakuno indeed
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Uzalonjeza abale ako
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Ай бұрын
As ova 2025 wokha
@user-tm8eg3fd1f
@user-tm8eg3fd1f Ай бұрын
🎉🎉
@wysonkomela8223
@wysonkomela8223 Ай бұрын
Tv iyi athu ake oyimila a malawi akunena chilungamo osati ma tv enawa mmmmm
@maxwellchifupa1538
@maxwellchifupa1538 Ай бұрын
Anthu amadziwa kunama, chachikulu polankhula osaseka
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Chakwela walephela
@TinoCharamba-hr9el
@TinoCharamba-hr9el Ай бұрын
Akagwele ku gahena ameneyu ntchitozo zipezeka pano zawu galu bs
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l Ай бұрын
Apa ndipomwe ndimadziwa kuti kumwamba kulibe satana kma ali pansi pano shaaa. Ndizadina kulowa m'manda kma sizapanga mistake yosapota Munthu wandale ayi
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l Ай бұрын
Kodi inu muzalangidwa ndi yehova yemweyu analenga ifeyu kapena wina? Eish anthu inuyo kma mulungu akukhululukireni
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 Ай бұрын
Guys apapa Pali mawu a bakili muluzi tv??? Let's be serious mawu awo agaluwa akuwapweteka okha and because of manyazi they turn in kulimbana ndi anthu aphee tivomerezedi kuti tili mu one party regime
@EnockSaiwa
@EnockSaiwa Ай бұрын
@samphiri9290
@samphiri9290 Ай бұрын
Awawa ngolephela basi koma poti ineyo ndilibe kuthekela kothananawo koma omwe adzalowe 2025 akuyenela kudzawalanda zinthu zonse zomwe atibela mumzakazi
@user-ln5hw7dn9g
@user-ln5hw7dn9g Ай бұрын
Mmmm
@user-ko1lk3br4r
@user-ko1lk3br4r Ай бұрын
Every presence has problem
2024 Elections | EFF leader Julius Malema casts his vote
9:24
SABC News
Рет қаралды 311 М.
Жайдарман | Туған күн 2024 | Алматы
2:22:55
Jaidarman OFFICIAL / JCI
Рет қаралды 1,8 МЛН
1 or 2?🐄
00:12
Kan Andrey
Рет қаралды 58 МЛН
Was ist im Eis versteckt? 🧊 Coole Winter-Gadgets von Amazon
00:37
SMOL German
Рет қаралды 39 МЛН
Tilikonde Dziko Lathu - Billy Banda
17:48
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,4 М.
Intore Mugahinda Zasezeranye Gushyira Maguye ya FPR Hanze/Trump Ntabwo Yahaye Ubutumwa Kagame/
East Africa Daily-Jean Paul Turayishimye
Рет қаралды 870
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 115 М.
Tikuferanji 25 May 2024
26:23
Edson Gunsalu
Рет қаралды 52 М.
Atikumbutsa Samora Machel wa ku Mozambique
10:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 30 М.
KWAGWANJI KUMALAWI
1:43:49
Jimmy
Рет қаралды 44 М.
Times Exclusive featuring Peter Mutharika - 20 April 2024
1:05:34
Times 360 Malawi
Рет қаралды 171 М.
Жайдарман | Туған күн 2024 | Алматы
2:22:55
Jaidarman OFFICIAL / JCI
Рет қаралды 1,8 МЛН