Kamlepo anamenyera nawo ufulu wa democracy and timamunvera pa CHANNEL AFRICA, NDIPO zaka za mtsogoleri zinachotsedwa ku choka pa 37year kufika pa 35 years chifukwa cha kuti KAMLEPO anali 35 years, LERO UFULU UJA KULIBE TABWELANSO KONKUJA. CYBER CRIME , TAMUTULUTSANI KAMLEPOYO..he is One of our heroes
@anthonynkhoma426511 күн бұрын
Democracy doesn't mean you should insult others. That's stupidity
@LeendaDeborah20058 күн бұрын
@@anthonynkhoma4265did he even insult?? Don’t accuse someone of being stupid whilst you were too stupid to listen to what he was saying. He just said what the army general said which was very contradictory to what the president said.
@MPHATSOKALUWA-lm2uy12 күн бұрын
In a MBC mtengerepo phunzro this is what we say facts and brilliant discussion osat zanuxo ayiii congratulations 🎉gyz
@amoschataika744012 күн бұрын
Brilliant conversation. Kpt up Guys
@user-ez1kc7zp9m12 күн бұрын
Apezeka bwanji kolumbila a UTM Ngati manganyayo ndi wa UTM,mesa bambo a sikono wo ndi a MCP pamodzi ndi Nakhumwa.mxiiiiii
@Extratremendouszeus12 күн бұрын
Uku nde kulankhula😅😅😅😅
@anthonynkhoma426511 күн бұрын
Ngati zakunyasani muchira.
@LeendaDeborah20058 күн бұрын
@@anthonynkhoma4265inu nde mudwala
@AchinaKellz12 күн бұрын
Good spoke we didn't see him at the funeral, their agreement is for him and mcp, don't allowed devil to intervene
Iwe ukut chn iwe ndi amene ukudya nao Dora uja Ife tizuzike eti fotseki
@user-rk3gq7gd8f12 күн бұрын
Musamalakhule mwamatha usi ndi amene anakoza nao chiwembu chopha chilima
@Pangolinimw12 күн бұрын
Yes
@emmanuelchavula714412 күн бұрын
U have evidence beyond reasonable doubt???
@NgomaRaheem12 күн бұрын
@@emmanuelchavula7144nanu umboni otani ?
@NgomaRaheem12 күн бұрын
Ndipo ndimfiti Manganya
@user-my4gr1pv8h12 күн бұрын
Ndipo adziwapo ngt uli upandu
@leviefeston762612 күн бұрын
TV iyi Bola asayigule iyi kuli anthu anzeru
@JohnmarkNazombe-hi9xd11 күн бұрын
Exactly!!!
@frankiejackzy986212 күн бұрын
Ku UTM ndi zabwino bwino chabe Michael Usi ndi wa MCP Chabe......so Michael Usi asasokoneze chifukwa kunena moona mtima Usi ndi amene adakonza Upandu mogwirizana ndi MCP
@anthonynkhoma426511 күн бұрын
if you are taken to court will provide evidence on what you are talking?
@MPHATSOKALUWA-lm2uy12 күн бұрын
Nice program and akuyankhula ma facts ndithu
@user-jg4xn9dp3p12 күн бұрын
Well spoken Mr ufulu umakhala ndi malire
@user-pv9uk6sc3w12 күн бұрын
A bambo Kaiyatsa mukulankhula chilungamo, a Chakwera ndi MCP yayo afulumilanazo, akufuna kuwophyeza anthu kuti asanene kalikonse pa nkhaniyi. Chakwera ndi achina Chimwendo Banda alakwitsa kobasi. Wamasule anthuwa.
@abrahamzimba672212 күн бұрын
@HOT265 , Achimwene kindly use the language which is favorable to every viewer, try to use english in order to cater for every listener. we your neighbors suffer a lot to get chichewa
@juliusnjerengo261012 күн бұрын
Usi and Nankhumwa they are MCP members by default.
@inessmsiyambiri851712 күн бұрын
Urlight
@cynthiakananji160812 күн бұрын
Mai kariat akulira kwambiri, ndi kholo limene lija. Komaso Ali ndi mantha. Action spx louder than words
@user-tn2qg1vs9j11 күн бұрын
Congratulations you guy's ❤❤❤❤
@apostledavismsosa12 күн бұрын
Kaiyatsa apo nde tililimodzi there is no way kumamanga anthu mu nthawi inoyi chifukwa zinsisi za ngoziyi anthu ndamene angafotokoze bwino apa akulakwisa
@temwachaima81712 күн бұрын
Intimidation ndiomwe yakula ndi oppression not in this generation
Mr kaiyasa ndokunyadira kwambili boma likuopseza athu cholinga asaulule ili si boma Ai
@ThomasMunyolowa12 күн бұрын
Keep it up guys
@user-do2cs8nf4b12 күн бұрын
Komanso m'mene zakhalilamu nde kuti ku UTM kulibe president komanso kulibe vice president sinanga usi walowa ku mcpl
@emmanuelchavula714412 күн бұрын
😎😎 alengeza kodi ??
@DarlingtonMaya12 күн бұрын
Wathu wathu Nyamalikiti powerful
@JulietMtsukwa11 күн бұрын
❤
@FrankMafunga11 күн бұрын
Nice programme
@hamiltonsolomon375612 күн бұрын
Following...Nice program .Keep it up Guys❤
@Shire962712 күн бұрын
It would be good for you reporters/journalists to give both sides of the coin in relation to what Mr Kayiyatsa has said in terms of absolute versus relative freedom. Much as it makes sense that arresting people would deter people from giving the information to the investigators, it can also be argued that it should not take someone to talk recklessly on social media to encourage people to talk to the investigators. After all, one doesn’t have to go on social media to provide information to the investigators. If someone is going to be arrested for providing information to the investigators directly, that would be a strong case of human rights violation. Give proper guidance to the people
@HanifiYaumu12 күн бұрын
Manganya ndiwa mcp
@MedsonMzumara12 күн бұрын
ok tavanao
@YohanePatrick-lc2lq12 күн бұрын
Malawi police yoputsa ikungovela dzilidzose tabwelela kwakamuzu ongopha chisawawa ngati khuku popano tawona ku South Africa ayika Ramaphosa zuma ndi dzungu ma DA akuvina amapiano komatu sana mange aliyese ayika koma ikanakhala mbuli ya president yathuya bwezi ikufufudza kuti wapanga dzimwnedzi ndani chakwela mbuli kwabasi
@SamJalie11 күн бұрын
Police is programmed by the ruling party, Morden John Tembo is Kenny Zikhale Ng'oma
@user-mz8nw6nx6p11 күн бұрын
That's true???talking really without fear
@bahatimwakasole489910 күн бұрын
Uyu Michael Usi ayambe asiya kaye za u Manganya. Sitingakhale ndi president amene ali mbali ziwiri. Akhoza kuchita chinachake, pofunsidwa nkudzati anachita zimenezo ndi Manganya osati Michael Usi. We afford that kind of double dealing wit a president
@WanangwaMfune7 күн бұрын
Pazovuta ngati maliro ndipovuta kuyankhula, or kulongosola zinthu mwadongotsoro kwambiri.
@kingnavitcha624312 күн бұрын
Mkulu wa police sangalakhule dzimenezo naye akufuna nchere anthu adyera awa ndi okupha awa
Manganya ali ndi masapota? iyaaa nothing to lose pamanganya
@user-je8jm5uy1q12 күн бұрын
Manganya ndi apule amadziwana awa UTM yachita bwino osapitako
@Macrina-vv3us12 күн бұрын
Abhiyeni munawaphera dala dzikoli mutsale nalo a chakwera
@user-cf9yz3ei5o12 күн бұрын
Guys you are really talking but our courts are our last source of hope
@MorganBanda-oc2jx10 күн бұрын
dziko la malawi sasokonekera basi. apolice athu amarrphera kugwira ntchito koma chinyengo
@GraceZumazuma12 күн бұрын
A Utm asiyeni ndipo si jealous but there's something rotten in the city of darkness simungaike bambo anu mmanda lero kungodutsa 2 dys muli ku chisangalaro mkumavina action speaks louder than words
@prettytambala56878 күн бұрын
Anthu akulira ku UTM abale tisawapatse ma pressure osafunikira
@user-ft3qr2gk4y9 күн бұрын
🏀♪𝗧𝗪𝗢 𝗦𝗜𝗫 𝗙𝗜𝗩𝗘♪🏀
@janemanyamba720111 күн бұрын
Apadi pali nkhanza ndithu pomanganapo
@FrankMafunga11 күн бұрын
Michael Usi ndi wa MCP
@colletamwandira-kd5np11 күн бұрын
Apapa npomwe tinkumbukire mayi jane ansa uja ,😢😢😢
@user-ym8zj1zl1e11 күн бұрын
Zapereka picture yoipa A Usi sanaonetse chikondi pa late SKC
@janejali847810 күн бұрын
I like how manganya thinks.Anthu akumutenga ngati nthabwala koma ali ngati Bingu wangokhala kuma stand akudikira kuchinya chigoli
@FestonMpwepwe-zq7hk7 күн бұрын
mmmm Bingu was a brave man. You can't compare him with Manganya
We don't care what you are saying, because us we are mourn our president.
@JustinLipipa12 күн бұрын
Amukonda bwanji M'dani yenwe Ali wa Congress
@user-jv5jy4qy2r12 күн бұрын
Oga you are just talking arrant nonsense here...UTM will never die
@yusufsadic293012 күн бұрын
Nonsenu mukunam manganya adachit kutoledw ndi chilim
@BlessingsLuclus12 күн бұрын
Onse amene akungidwao akutumidwa ndi chakwela
@HenryLaidon-pl9ly12 күн бұрын
Access to Information.........it's not
@EmmanuelGasiten-fo5dr12 күн бұрын
Kaiyatsa wabaya.
@user-rg6hn7mt6w11 күн бұрын
Alipakatiyoo akuafanana ndi chaweratu
@JoshuaNyirongo12 күн бұрын
Mtsogoleri wa chipani si a Usi.....Big story.
@rabisonpias513111 күн бұрын
Program yokoma iyi Yatheranso panjira but why A Zodiak
@dorcasmwale632812 күн бұрын
following
@sherlymhango278512 күн бұрын
Koma pobwera pa camera simukanazela kaye ku saloon mmutu choncho osapesa
@shayrafernandeslatif955612 күн бұрын
Michael Usi olo kunenako ka speech kakang'ono ku maliro olo kuwonesta concerned kuti SKac was close ndi iye,ena onse a UTam thy were very concerned mayi kaliyati was very sincere emotional broken
@chimwemwedulla676012 күн бұрын
Eti inu...kuipa moyo
@user-rf9oe3pb9f10 күн бұрын
Mwina sanapatsidwe mpata woti ayankhule
@CatherineDesire8 күн бұрын
Usi abwelere adzikapanga umanganya 🙄
@CatherineDesire8 күн бұрын
Abare inu mnaonapo mkwati atapita yekha ku ukwati ?maine 🙄🤔🙌koma a Usi ndosankhao dziribwino bwino👉😇😔🙄ayi ndakaika👺👿👹a usi naoso chi😁msaya?kalekale a usi🏃40 kmh🤔
@CalexG12 күн бұрын
Ti anthu tonse tili umu ta DPP... muthu walakhula zopusa afotokoze asasokoneze anthu or ma policy a facebook amati don't miss lead or provide force information... zimenezo mbuzizi sizikudziwa
@thomasmsofi419112 күн бұрын
Panopa tili pa muliro wa v Chipani chamomile tabwelera kumbuyo usually si m'busa ayi atipweteka waiwala must include si 1983 komabe ife Naima mmalo mpakana chakwela boma litasitha apo nde mwinanso akuziwa just azamangidwa mustering a njoy for now azalea anzake onse atamuthawa