A PATRICIA KALIATI KUYANKHAPO ZA MICHAEL USI 21 June 2024

  Рет қаралды 124,226

HOT 265

HOT 265

20 күн бұрын

Пікірлер: 181
@petertaulo8014
@petertaulo8014 18 күн бұрын
We are not fools and we know where this story of Usi coming from, it started the night just before plane crash.
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 17 күн бұрын
Agofuna kupusisa amalawi
@DanielMwandira
@DanielMwandira 15 күн бұрын
Koma why Malawi Mulungu akuloleranji izi Ku Malawi kut mpaka anthu azingoonerera chonchi
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 14 күн бұрын
@@DanielMwandira gwirizano tilibe kaya ku Malawi zinazi magoona waziyamba we all know the history and history is best teacher ever bt wht happen now we bring old vision again in this country
@user-xg5dg7jj4d
@user-xg5dg7jj4d 18 күн бұрын
Kodi sikunali koyenela kuti UTM kusankha yokha amene angakhale mulowa mmalo a chilima
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo 18 күн бұрын
Ali ndimphavu yanji yoposa lamulo sizongoganiza akulu izi.
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 18 күн бұрын
Ayi ndithu manganya anali kale wachiwili kwa saulosi nde mmene adapitila a top awo otengedwa akuyenela kukhala wachiwiliyo basi ndipo amene adasankha manganya anali chilima yemweyo apa Mzimu wake wasangalala komwe aliko ngakhale adachoka imfa yosakhala bwino
@estherkambewa7791
@estherkambewa7791 18 күн бұрын
Constitution imati president asankhe
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 18 күн бұрын
Michael Usi ndi wa MCP ndi kale
@hedgespophiwa
@hedgespophiwa 18 күн бұрын
Is only the black box osati china chilichonse so we r waiting for the voice recorder
@augustMag
@augustMag 17 күн бұрын
Mai Kaliati ayakha bwino Manganya apeza yekha mayakho
@user-lb6ek3ee6d
@user-lb6ek3ee6d 18 күн бұрын
Zachamba Usi azazitenge ngati iye ndiwochenjela mission yawo yatheka koma asayiwale kuti masiku amatha ndikugona tsiku lina tidzalilaso maliro ayiye
@azunguauskay4903
@azunguauskay4903 18 күн бұрын
Iwe ukunena chilungamo
@Certified-Mbudede04
@Certified-Mbudede04 17 күн бұрын
God"s time is always the best.. Not an MCP fan nor UTM but the President apanga zomwe akufuna when it comes to that
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 18 күн бұрын
A utm kuona kwanga akanangojoina zipani zina monga udf,dpp,aford ndi zipani zina,osati mcp ayi ,,koma poti zamumtima ndizawekha iiii kaya
@LamekiSamson
@LamekiSamson 16 күн бұрын
Ndipo ndizoona
@RichardMatandala
@RichardMatandala 18 күн бұрын
U T M idapta ndanuwake bas tivomekeze
@petertaulo8014
@petertaulo8014 18 күн бұрын
UTM is here to stay don't worry
@ulemujumbe8501
@ulemujumbe8501 18 күн бұрын
Basi chidamka mchilima
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 18 күн бұрын
😂😂Zonama basi mwaiwala munatiuza kuti mgwirizano mwayedzeka kaye? Something fishy
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 18 күн бұрын
Ndipo zodabwitsa lero akuwoneka okondwa zedi even mkaka himself 🙌
@thomasmfune5150
@thomasmfune5150 15 күн бұрын
Martha Chizuma analiso ophunzilabwino but she failed to beat the system. Money has special energy.
@LindaKapito
@LindaKapito 18 күн бұрын
Anthu akubwela akafukufukuwo,mwawachuna kale azafotokoze za ziiiiii ,
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 18 күн бұрын
Anthu opanga kafukufuku opezedwa ndi boma sangagwire ntchito mosakomera boma, sizingatheke zachinyengo basi. Ndalama za misonkho ya a Malawi muzingoonongabe choona mukuchiziwa koma kufuna kuwapusisa a Malawi ayi tiyeni nazoni. God is watching.
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 18 күн бұрын
Abasankhana kma nthawi ikuza nose muzasetera leza sua Mkaka wasangalalano cz Chilima wapita
@momuumro
@momuumro 18 күн бұрын
We are not fools we know everything and we know from where you started your plans So Usi don't be clever here zimene umafuna zatheka komanso zimene amafuna chakwera zathekanso
@Edson-sj8vn
@Edson-sj8vn 18 күн бұрын
Utm tapachika basi Mai kaliati mokupemphani bwelerani ku chisa mbiri yanu isanaonongeke
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 18 күн бұрын
Nanga bwanji munkanena kuti muimanso 2025 ndiye alliance ilipati
@MillyKachepa
@MillyKachepa 18 күн бұрын
za ndale ndzovuta koma manyaz awagwira kusankha usi koma palibe chingayendepo onse opanda nzeru zokha zokha
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 18 күн бұрын
Adzavoterana okha okha😅😅😅😅
@daudaustin7397
@daudaustin7397 16 күн бұрын
Kazitape Michael usi ndichakwera ndamodzi awa
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 18 күн бұрын
Ndipo sitizarira ayi wazifunira dara iyeyu wayifuna ifa uyo ndipo iripafupi ife tikufuna pita mutarika
@RegistermoseskashonKashon
@RegistermoseskashonKashon 18 күн бұрын
Zikomo kwambili mr President nchito yomwe mwagwila kusankha micheil usi kukhala vp mwagwila ntchito yotamandika
@ykzt
@ykzt 18 күн бұрын
Zazii😢😢
@RuthMalani
@RuthMalani 18 күн бұрын
Usi ndi wa mcp asaputsitse amalawi ife sitikupanga nowo zanuzo
@RasheedAssimah
@RasheedAssimah 18 күн бұрын
Mmmmmm malawi ujaaa😢😢
@isahMapemba
@isahMapemba 18 күн бұрын
UTM kuli mavuto bas
@MakandeMpambalika
@MakandeMpambalika 17 күн бұрын
Kaliyati so brief and so wise
@MessiahPitros
@MessiahPitros 13 күн бұрын
God always save him in all situation.
@user-ib6jc4es3s
@user-ib6jc4es3s 18 күн бұрын
Asakudziwa ndindani agalu inu or abwele chilungamo mwagulakale azatiwuza zabodza chimodzi kumbukilani boma simunatenge NDI mavoti munatenga ndimademo ifeso tikusonkhenisa zida zolandila boma lanu osatinamiza agalu wakupha
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 18 күн бұрын
Ayi zovuta zedi
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 18 күн бұрын
Akaliyati asunga ulemu paja 21 day's sidakwane muona adzayamba kutokota ndimunthu wamkulu komanso odziwa uchembere moti akanali kulila mwana wawo ndi ngati zidzukulu vomwe zapita lomodzi nda VP athu tiyeni ta mvetsetse Amai athu a Kaliyati... Mulungu alinafe
@macdonaldkorea2928
@macdonaldkorea2928 11 күн бұрын
Ndikuona choncho nane, kaliati sizikumukonda zakusankhidwa kwa Usi, ndipo masikuwa akatha timvako zinthu ayankhulatu chifukwa ku UTM momwe zatermu kuzafunika kusankhako atsogoleri angakhale Usi anali VP kuchipanicho, koma ndikuona kut sakukhulupilidwa konse UM'THILA KUWIRI MANGANYA
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 11 күн бұрын
Eya adzatokota ameneyu tingiti pheee ...komanso adzapangadi masankho ndipo zidzatelo kumene
@JuuuKomba
@JuuuKomba 18 күн бұрын
Amene akut sanalakwise wakalamba ameneyo iz amayenela kusaka okha a utm zinalo anakalipeleka ku Mcp osat a Mc kusakha zopanda phindi congrats usi
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss 17 күн бұрын
Patricia kaliyati azakhale position next ngat kungazakhale mpata uyu ndi muchine
@flytonenkunika-pi9dn
@flytonenkunika-pi9dn 17 күн бұрын
Usi,,,, tayenderan agreement ya chilima ndi chakwerayo,,, we don't need mcp any more
@alexanderchamgwera-jm1qy
@alexanderchamgwera-jm1qy 18 күн бұрын
Aaaaaa a nkaka lero limenero mesa anati anawezeka??
@user-uc6jk6pr9r
@user-uc6jk6pr9r 13 күн бұрын
Something is wrotten in the city of Denmark
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m 18 күн бұрын
Iye utsi ndiye bwanji kumaliro anamuthamangitsapo ndiye pamenepo adakali Ku UTM chonchi?
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 18 күн бұрын
Siziliko bwino, wanna mene wayankhila kweni? Wayankha mwa miyambitu.
@giftedmshan6779
@giftedmshan6779 18 күн бұрын
Ndikudabwa mkaka akuyankha izi lero koma guys iiiiii
@irridessahmonterosa9943
@irridessahmonterosa9943 16 күн бұрын
Why German yet we have RSA right here?
@MarkManyowa
@MarkManyowa 17 күн бұрын
Mama Kaliati 👏
@user-px5tz4kb5s
@user-px5tz4kb5s 18 күн бұрын
Olo akanapanda kulephereretsa zachikondwerero bwenzi tikundolwerera chani😢 zopusa basi
@user-zl9eq8jw1q
@user-zl9eq8jw1q 17 күн бұрын
We are blind pipo palibe za UTM apa
@KhoBanda
@KhoBanda 16 күн бұрын
Usi ndiwa MCP, anthu awawa akudziwana n UTM ikhala kukhwapa n chakwela Given akuyimSo 2025
@LindaKapito
@LindaKapito 18 күн бұрын
Anthu awa akudziwana,tiyeni pangatalike, pangafupike,chilungamo chidziwika,ka manganyako mkoipa ndipo udindo umenewo anauyamba kuufuna kalekale,anthu oipa ndatitu kuipaaaa
@daudaustin7397
@daudaustin7397 16 күн бұрын
Akatswili ofufuza achani zinthu zooneka ndi maso akazitape a utm amatenga zokambilana kupititsa kwa farao mpaka kumukhonzera chiwembu koma akhumudwa chifukwa samaembekeza kuti solution ikhara njila yakupha
@CholapitsaSamson
@CholapitsaSamson 18 күн бұрын
Man mumangomatula nkhani basi aa zosabeba L
@Tawina0101
@Tawina0101 18 күн бұрын
😮sono mumafuna azipanga bwanji????
@masingatichilumba8263
@masingatichilumba8263 18 күн бұрын
Zofuta sindu sake😢😢
@user-et3il7pi7t
@user-et3il7pi7t 18 күн бұрын
Ndizowona kupanda utm mcp siyikanawina apo musamachosele
@HitSmart-q9o
@HitSmart-q9o 17 күн бұрын
Zaipa😢
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 18 күн бұрын
Ngwirizamo wayambilaso simesa tinayezela Kaye ndale timapanga usiku ok ok
@MakandeMpambalika
@MakandeMpambalika 17 күн бұрын
Kaliyati so brief
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 14 күн бұрын
Frim yao yatheka ife timadziwa koma dzopanda mphindu komabe oooo
@LamieTiger
@LamieTiger 18 күн бұрын
Athu nde mwakula kula koma kumapanga zoputsa m'malo momalapa machimo mulinawowo anyday imfa ikubwera
@BorgeMario-wx5vq
@BorgeMario-wx5vq 17 күн бұрын
Chilima akuona zonsezi.pitilizani ndi ufiti wanuwo.
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 17 күн бұрын
Eeeich athu awa amatipusisa kwambiri amaona ngati amalawi saziwa zithu
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 16 күн бұрын
Lero pano mukumutchula Chilima malemu vice president, Mulungu akupatseni moyo wautali
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 18 күн бұрын
Za ngozi munachita kuzipanga nokha nde musatinyase ofufuza mwachita kuwauza zochita
@AustinKatolika
@AustinKatolika 16 күн бұрын
❤kkkk
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 18 күн бұрын
Funso sono nkhati manganya wasankhidwa pa uvice 2025 azasogoleranso pokhala president chakwera abwelera kukasiya ? Nkhati momwe anapanganirana ndi malemu ?
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 17 күн бұрын
Aaaa chalaka bakha nkhuku singatole akufuna yes BWANA BWANA yes machine ndiamene mwapha uja anu manganya afela dzayeni uyu wachepa MCP MAGADZI IYI
@AfickDaud
@AfickDaud 18 күн бұрын
Kaliati wayankha mosunga mawu kukhosi
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 18 күн бұрын
U can say it again abro pajatu tikanali kulila wathu nde mpona asunga mau mpaka 21 day's
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 18 күн бұрын
Azikavomera zofoila ngati zimenezo
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 17 күн бұрын
@@inessmsiyambiri8517 Tiyeni tione akatha masiku adanenawa
@FazilaJames
@FazilaJames 18 күн бұрын
Bolani asamupheso
@RuthMalani
@RuthMalani 18 күн бұрын
Olo atamupha ndizawo zimenezo
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 18 күн бұрын
Dzana mwati mgwirizano mwayedzeka lero mukuti tinalowa ngati alliance holaiti
@MveraNambala
@MveraNambala 12 күн бұрын
Utsi hiya afa pompano akuwona ngat wafika sitizakulira ngat chilima zovuna
@manphiri2778
@manphiri2778 12 күн бұрын
Yudas
@RashidKusum
@RashidKusum 10 күн бұрын
Amuphanso ameneyo
@FionaKhoma
@FionaKhoma 17 күн бұрын
Zatinyasa ife sitinakondwere nazo usi kukhara vise zandibowa kwabasi
@ulemujumbe8501
@ulemujumbe8501 18 күн бұрын
WA MCP uyo nthira kuwiri
@victorauwana7258
@victorauwana7258 18 күн бұрын
Koma chakwela uli ndi sambi.. kusunga mgwilizano kwa bwanji uku? Munthu oyipa iwe
@D.RJALLI-qo6yd
@D.RJALLI-qo6yd 18 күн бұрын
Farkas utm ur are the full iwe ausi mbolo yako iwe galu
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 17 күн бұрын
ZAUSIRU USI NDI MUNTHU YEMWE ANALI NGATI SIMONI PETRO ODZIWA MOMWE ANGAPEREKERE YEDU KUTI APHEDWE USI SI WA UTM USI NDI WA MCP NDIPO AMALAWI MUSAONENGATI USI ANGATHANDIZE MAKAWI CHIFUKWA UYU ALI LIMOZI MU MCP ,
@OmegaSanjama
@OmegaSanjama 16 күн бұрын
Mungoononga ndala kutenga anthu akunja kudzafufuza kod kuno kulibe akadauro ogufunza iwo afufunza bwanji dziko lino ndi lanthu t
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 17 күн бұрын
Anthu andale ndi oipa ndipo asamatipusitse koma adziwe naye kuti adzaziwona zomwe Ankawona chilima ndi anzake
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n 18 күн бұрын
Kafukufuku azatiuza chiyani bodza limenelo akafika muwauza zochita. Malawi akudikilira Limpopo Fm ndi Bakili Tv
@fradrickMuvula
@fradrickMuvula 18 күн бұрын
Great
@Certified-Mbudede04
@Certified-Mbudede04 17 күн бұрын
Y'all saying Usi had a plan on this!. Where are your heads. Akanayisiya UTM you could have been talking kuti it was also a plan!.. Tamaganizani pena xina kumangoona. Sizoti mungasithe VP inuyooo aah
@VictoriaPwele
@VictoriaPwele 6 күн бұрын
😮
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 18 күн бұрын
Tiyedzeke kaye
@mkhulukinyata5198
@mkhulukinyata5198 14 күн бұрын
Ine mukamamutchula uyu Ernest Thindwa yu kuti ndi Kaswiri pa ndale" Ayi ndithu ine zimangondiseketsa kuti yaaa ku Malawi yee kkkk.. Munthu wamzeru zake sangamayamikire Chakwera pomusankha Michael Usi kukhala Vp ayi . Ife monga a Malawi " Chomwe tikudziwa ndichoti Michael usi wangosankhidwa ndicholinga choti awaphimbe a Malawi kumaso " Ndicholinga choti tidziti kuti Chilima sanaphedwe ndi iyeyo Chakwera yo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 18 күн бұрын
Kunkuyu datelo ukuti chani iiiiii kuyalukatu uku 22 january kusabvukatu uku
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 17 күн бұрын
Tikudikila mwana wa chilima Sean kuti adzapitilize chipani Cha bambo ake ngati president
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 17 күн бұрын
Germany, France,u.s.a Israel ndi amodzi palibe angapereke zotsatira zabwino komanso akuziwa kale kuti on that day network izakhala ikuvuta believe me komanso guys ndege ija idagudwa ku Germany komweko apapa pilibe chiyembekezo chabwino
@user-wq9ex2sf3b
@user-wq9ex2sf3b 5 күн бұрын
Azafufuza bwanji black box munalibe afiti imwe
@user-ow3tp3vu3c
@user-ow3tp3vu3c 17 күн бұрын
Mmm 6 july mpaka kulepheleka???😮😮😮😮 Hahahaha koma boma iliri mmmm zovutatu
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj 18 күн бұрын
Let's just pray kut kafukufuku kanyende mwachilungamo
@DoYouKnow3838
@DoYouKnow3838 18 күн бұрын
Kafukufuku sangayende mwachilungamo chifukwa akupangidwa influence ndi andale.
@MarthaJonathan-ci8mh
@MarthaJonathan-ci8mh 13 күн бұрын
Bola osapachitikeso ngozi ya ndege
@user-qz5gj3tf2t
@user-qz5gj3tf2t 16 күн бұрын
Oziwa za ndale za ziii palibe chiziwa iwo amenewo
@FionaKhoma
@FionaKhoma 17 күн бұрын
Ofufuzawo akanabwera kudzera kwaamabungwe boran km ngt akubwera chifukwa chot aitanidwa ndiaboma atiyakha bodza chifukwa achunudwa kare auzen abwerere
@hopembendela
@hopembendela 17 күн бұрын
Fuso ndiloti akaswili amenewo amene wawaitana ndi ndani ngati ndi lili boma amalawi musayembekeze chilungamo chilichose apa
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 18 күн бұрын
Chokupha ngat iwe machende ako
@McNeverNjanji
@McNeverNjanji 17 күн бұрын
Mukufuna mupusise aMalawi mwapha bas
@MacmillanMakombe-sz4iy
@MacmillanMakombe-sz4iy 17 күн бұрын
Kodi akulu, simunakangoyika part yokhayo walankhula kaliati yo? Muzitimveresa ndizopusa zomwezo?
@ThomasShuga
@ThomasShuga 17 күн бұрын
Akuluwa alibe talent aaaaaa
@alexsaidi8479
@alexsaidi8479 12 күн бұрын
Wa botza ameneyo anamumpa ndi achakwela ndinthu
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 18 күн бұрын
Aaa akadaulo ake at?mesa osewa ndi akongeresi muti ndife Ana?
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 15 күн бұрын
Kaliati judged it
@mussakapalamula1990
@mussakapalamula1990 18 күн бұрын
Pachoka nzako Pali Malo. Koma Manganya usamale.
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 18 күн бұрын
Koma kaliati ndi mamuna ndi nkazi? Ai munthu uyu amaopsya kumfikila ngati si nkazi ubwino wake amauona ndi kwawo komweko ati amathandiza koma iiiii ai mai owoopsya kwambili
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 18 күн бұрын
Chakupangitsani ndi chani kunena choncho??
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 18 күн бұрын
U t m yathah basi..., Manganya ndiwa M C P
@user-wq9ex2sf3b
@user-wq9ex2sf3b 5 күн бұрын
Miko usi ndi imozi wa fiti zinapha chilima agalu 🐕a MCP
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 18 күн бұрын
Iweyo ku nkuyu panyo pamako
@awezafalesi3873
@awezafalesi3873 14 күн бұрын
Abale chonde musathe za mkamwa kodi si Chilima yomweyo aika amalawi pa moto amati tizidya katatu zinthu zitsika mtengo lero mmmmmmm inde za imfa sitikusangalala ndi mmene afela
@user-lc5nz2lo1n
@user-lc5nz2lo1n 17 күн бұрын
Shit why it's national freedom day so
@KestenMukhwapa-qp2gj
@KestenMukhwapa-qp2gj 17 күн бұрын
Manganya ndi wa MCP kale asatipusise
Vivaan  Tanya once again pranked Papa 🤣😇🤣
00:10
seema lamba
Рет қаралды 33 МЛН
БОЛЬШОЙ ПЕТУШОК #shorts
00:21
Паша Осадчий
Рет қаралды 9 МЛН
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 20 МЛН
NKHANI ZALERO 9 July 2024.
23:37
HOT 265
Рет қаралды 4,9 М.
CRUISE 5 WITH PATRICIA KALIATI
59:03
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 157 М.
ZODIAKTV CRUISE 5 WITH MRS MARY CHILIMA
41:54
Zodiak Malawi
Рет қаралды 92 М.
KU NG'ALULA KWA BON KALINDO LERO PA 8 JULY 2024
16:10
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Vivaan  Tanya once again pranked Papa 🤣😇🤣
00:10
seema lamba
Рет қаралды 33 МЛН