No video

Eeeh uyu ogwila ntchito ndi ku Malawi First watumiza uthenga wake wa mphamvu, othokoza ndikudzudzula

  Рет қаралды 14,868

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@ErnestChansa
@ErnestChansa Ай бұрын
Zowona zowona zowona mawu oyanjanisa amenewo more fire 🔥🔥🔥🔥 🔥🔥🔥
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Viva Malawi First 🇲🇼🔥 Big up Brother Salo nthawi zonse mumayima pa chilungamo
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o Ай бұрын
U have said it loud & clear Big up Brother men
@constancemkandawire7378
@constancemkandawire7378 Ай бұрын
United we stand divided we fall tufuna anthu ngati inu ku malawi indeed opposition party Itati imeme ma activists to join forces ku mademo aaaaaaa this ruling party can't stand the heat,enough is enough we are sick and tired of this government. VIva comrades viva
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Ай бұрын
Wachiyao samapanga zatulo more 🔥 Mr kumeneko
@user-dy5bj9ck5e
@user-dy5bj9ck5e Ай бұрын
Well done Mr chidzukulu
@bernardnambwe7753
@bernardnambwe7753 Ай бұрын
more fire mumatha
@cacksygustarf6260
@cacksygustarf6260 Ай бұрын
Malawi first❤
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Ай бұрын
💥💥💥💥
@MustapherLino
@MustapherLino Ай бұрын
Chakwera ndi mbava
@user-mi3fw1zg8b
@user-mi3fw1zg8b Ай бұрын
Fire mabomba
@douglaskamanga7679
@douglaskamanga7679 Ай бұрын
A brother Salo, Kodi aliyense azi Nena za mtundu wake? Ndipamene timalakwitsila zinthu a Malawi. But Malawi first better not mutundu. Mukuona bwanji? Zapa mtundu ndekuti sizatonsetu
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
😂😂kung'aluratu 🔥 🔥 🔥.
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Ай бұрын
Ndipo ankaona azawo mene amamangira ma demo a chakwera ndi mtambo mpaka anawina
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d Ай бұрын
Zoona zoona
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v Ай бұрын
💪💪
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Lets fight together 💪
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Zoona tinayika manyaka muboma
@WilliamBanda-o5r
@WilliamBanda-o5r Ай бұрын
Mwanena chilungamo opposition kugona kwambiri yet akufuna kuzalamulira
@samchibenene4458
@samchibenene4458 Ай бұрын
Mwang,alura bwana wachi yao
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Zikomo malawi ukufuna anthu olimba mtima ngati inu MCP yatikwana zedi awa ndagalu kwabasi
@shepherdkingston
@shepherdkingston Ай бұрын
Umakwana
@Yussuf-b1p
@Yussuf-b1p Ай бұрын
Zoo Zoonad auzeni
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Wasaalile kwereko wachiyao wangalusa😂😂
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h Ай бұрын
Koma nkaz naye wa chakwela ndimbuzi kwabasi sawiza mamuna wake kuti ayi musamuphe chilima
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 Ай бұрын
Kkkkkkk amalawi akutizolesa manyi chakwela kkkkk zonvesati chotson
@GiftNasila
@GiftNasila Ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤😅
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 Ай бұрын
Step down chakwela and anthu ako
@OsmanPatrick
@OsmanPatrick Ай бұрын
Kkkkkk kmtu kulu unyoro baba
@CatherineMbela
@CatherineMbela Ай бұрын
Unyolo sichopyesela Koma ndi chiyambi cha Moyo wasopano osamangoopa amalawi zilizonse
@CatherineDesire
@CatherineDesire 29 күн бұрын
Kupha anthu kuba ndrama
@MerryWayson
@MerryWayson Ай бұрын
Kuswakuswa chilingamo palibe kumuvoteraso chakwera
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Chonde uyu ayenera kumangidwa ayi sikumenyera ufuru uku koma kutukwana munthu sichoncho nde ama khot aziti alibe umbon mene munthu akutukwana president wa ziko kut ndi wakupha nde muziti alibe umboni
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
Mangochi bro imapampadsa makovi or apolice amasiwa kut Mangochi 🙌🙌🙌🙌
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Brother salo zoona ena amangotokota koma akuopanso
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Ichi ndi chitsiru cheni cheni nde uganiza kut president wa ziko angalephere kumanga kanyumba r u serious koma ngat ndi jealous zikomo ,anthu inu akumwera muli ndi nkwiyo waukulu mene anzanu akuyendesera ziko ndipo ngat Pali anthu amene awononga zikoli ndi inuyo anthu akumwera ndi ma president anu ,kamuzu zikoli analisiya pa bwino koma ndi uchitsiru wanu ,munagulisa ma kampani onse a boma pano mukuvutika mwayamba kulila ndipo mulila zenizeni sitingakuvoteleni kut muzabwelelenso ayi takana
@ThomasPeter-zt2ju
@ThomasPeter-zt2ju 29 күн бұрын
Machendeko man Ulibe nzeru
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 Ай бұрын
Chilungamo chokha choka
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Ай бұрын
Zimenezi ndiye anthu nkumayamikira? Zili ndi phindu lanji? Awawa angayendetse dziko? Basi comment, kuma-commentar zopusa ngat izi? Shame on u. Nokha mukuyankhula kut mumayenda pansi mutavala silipansi while president-yo ali ndi ulemerero, ndie onunkha kukhwapa ndindani 😂😂😂😂😂😂 ndiwe munthu onvetsa chisoni aise
@ThomasPeter-zt2ju
@ThomasPeter-zt2ju 29 күн бұрын
U don't know what ur talking mutu wako mwazaza mamina okha oka
WORLD'S SHORTEST WOMAN
00:58
Stokes Twins
Рет қаралды 178 МЛН
哈莉奎因以为小丑不爱她了#joker #cosplay #Harriet Quinn
00:22
佐助与鸣人
Рет қаралды 10 МЛН
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA 14 AUGUST 2024
24:50
Club Junta
Рет қаралды 8 М.
Lyton Mangochi akuti ndinu Mbuzi😂 Koma uyusotu akubwera ndi moto😂😂
4:08
Limpopo FM with comrade ntanyiwa USIKU WAPA 13 AUGUST 2024
24:13
KWAGWANJI LELO PA 10 JULY ON TIMES  🙌 MALAWI!!
36:57
NYANJA MW
Рет қаралды 4,1 М.
WORLD'S SHORTEST WOMAN
00:58
Stokes Twins
Рет қаралды 178 МЛН