Eeeh wachita kutembelera boma lonse andale onse Prophet Mbewe kuti awalange Mulungu

  Рет қаралды 25,475

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

16 күн бұрын

Пікірлер: 99
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 15 күн бұрын
Ndimo mudzina la yesu mau Anu agwile ntchito pa andale okubawa mu dzina la yesu
@user-ro1pl7rv7z
@user-ro1pl7rv7z 9 күн бұрын
Only Young president can do better... Coz they can do it in new model...NOT 60'S MODEL
@MussahIman-cw1cu
@MussahIman-cw1cu 14 күн бұрын
U man of God continue to pray for those bad people to gate pushed from god
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda Күн бұрын
Amen man of God. We are tired wth that thng we call chakwera
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 14 күн бұрын
Mau owoona mulungu atimenyele nkhondo ameeen
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 14 күн бұрын
Mulungu wamatembelelo kkkkk mwayamba zibwana ndimulungu ky pot ndi business yanu ndimulungu wanu
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 15 күн бұрын
Ndipo athu atizuzuza yawa sitizaiwala m, pakana kale kale mmm ndipo asatana
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 14 күн бұрын
Amen mau ishiii ziko lathuli ai zikomo akuluakulu kuntunda mavuto okhaokha bsi.
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 күн бұрын
God bless you man of God
@babranzima8120
@babranzima8120 14 күн бұрын
Perfect said 👏 🙌
@temwarachaelkhonje3733
@temwarachaelkhonje3733 14 күн бұрын
Very bold.....the only Man of God that have told govt the truth
@TheresaKuluwemba
@TheresaKuluwemba 13 күн бұрын
Koma ndipo! Koma nthawi ya APM azibusa ma prophet ansembe palipose kunali kuyakhula zoipa zaboma lija koma pano kuli ziii, palibe akukamba zoipa kapena zabwino za bomali uyuyu ekha basi, ayi zikomo
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 14 күн бұрын
Kodi chakwerayu tu bvuto ndi school komanso mtundu komwe akuchokera mmmmmmmm so shame walephera basi 2025 azipita !!
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne 13 күн бұрын
Tiye prophet awawa mulungu awachose 2025 zikutiwawà .
@AlickBaton
@AlickBaton 14 күн бұрын
This is 2023,, but only God knows
@marryphili5419
@marryphili5419 14 күн бұрын
Oooh yes tatopa ndi boma ili please azibusa lowereranipo ndithu timenyereni nkhondo Kuti kumwamba kuseguke tatopa ndikulira amalawi
@MafunaseKamoto
@MafunaseKamoto 13 күн бұрын
Basi man of God ndalamazo andipatsira ine tikabweze komwe zinabedwa...kkkk
@kennedybanda
@kennedybanda 14 күн бұрын
Matenda ake ena mwa iwo ndi misala.
@YamikanAbubakary-my4ie
@YamikanAbubakary-my4ie 14 күн бұрын
Iwe usankhepo chimodzi pakati PA ubusa ndi Der wamva osamphatikinza za mulungu ndi Zadary 😂😂😂
@julietmussa5103
@julietmussa5103 14 күн бұрын
Alavule ndalama zikenezo in Jesus Name
@PiscaDicksoni
@PiscaDicksoni 14 күн бұрын
Amen man of God
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp 14 күн бұрын
Amen 🙏🙏 power
@PaulKambuzi
@PaulKambuzi 4 күн бұрын
amen aprophert power full
@user-xe5il4cg5d
@user-xe5il4cg5d 15 күн бұрын
Amen prophet
@user-lu8px7td6p
@user-lu8px7td6p 14 күн бұрын
Amen mudzina la yesu
@JohnAsendi
@JohnAsendi 14 күн бұрын
Nkhale Lili LA 2023 akuphempha ndi chimozi mozi tikuyembekezera amipingo ina tinve kunyasidwa kwanu Asilam tiye maduwa
@Dorah-zl9uf
@Dorah-zl9uf 14 күн бұрын
Amen may God bunish them
@user-gj8td8pc4d
@user-gj8td8pc4d 13 күн бұрын
Names nkukhala mommo mundalemo.😂😂
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 14 күн бұрын
May God restore our country
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 14 күн бұрын
Amen zikomo🙏❤️💖
@BrianZenengeya
@BrianZenengeya 14 күн бұрын
Yes 100% truth
@SimeonAbraham-u2j
@SimeonAbraham-u2j 14 күн бұрын
Mulungu akuwonesa ukulu wake sopano mzimu wa Chilima Uli pakati pa Malawi
@michaelsakala8884
@michaelsakala8884 15 күн бұрын
100% true
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 14 күн бұрын
Kkkkkk zamanyazi a prophet m'malo molalika zamulungu mwayamba ndale
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu 14 күн бұрын
Udzimu umaenda bwino anthu akamakhala umoyo wabwino, kuvutika ndi kupemphera siziyenderan, away akuzuzula nchitidwe omwe andale athu oipawa amapanga pozunza aMalawi kuti zao ziyende, ndikupempheranso kwa Mulungu kuti ndalama akubazo zithere kugula ma kidneys, zaoneneni nkhalamba momwe zikuzunzikira kumiziku yet they were promised alot for them to win.
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie 14 күн бұрын
Koma pamenepo ine kukhosi mweee😂😂😂
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 14 күн бұрын
Ameeeeeeeeeeeeeeen
@user-po7zs9zd7u
@user-po7zs9zd7u 14 күн бұрын
Amen amen amen amen 🙏🙏🙏❤️❤️❤️
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 12 күн бұрын
Kkkkk 2023 izi Aaaa
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 14 күн бұрын
Gen Z is watching
@user-hg2cw1om1p
@user-hg2cw1om1p 15 күн бұрын
❤❤
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v 14 күн бұрын
Osaopa mbewe chilungamo Nena boma lotopesa ili ipondeni mbewe yomweyo
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 14 күн бұрын
Ifenso tikupemphera mwachinsinsi ndipo mapemphero athu akutheka. MCP mthawi yanu yatha kale. Ndipo MCP yatheratu. Mark my words.
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n 11 күн бұрын
Walankhula munthu wa Mulungu
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 14 күн бұрын
Amen
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 14 күн бұрын
Paja adanena zoti akantheni
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 14 күн бұрын
Amen amen
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 14 күн бұрын
Izizi ndizakalekale,Kodi chifukwa chani mumabweretsa zinthu zoti ndi zakale?
@alicechinyama4155
@alicechinyama4155 14 күн бұрын
Zakale lake liti
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 14 күн бұрын
@@alicechinyama4155 I saw it in 2023, but maybe you didn't see it then
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 14 күн бұрын
The msg was powerful though
@Pangolinimw
@Pangolinimw 14 күн бұрын
Ameen
@cacksygustarf6260
@cacksygustarf6260 15 күн бұрын
Tell dem men💯
@DorrahBanda
@DorrahBanda 14 күн бұрын
Amen❤❤
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 14 күн бұрын
Ameen 🙏🙏🙏🙏🙏
@user-fb6kh2dk1y
@user-fb6kh2dk1y 14 күн бұрын
we are after message not chaka chakacho sungani inu
@AminAbbass-xc4qk
@AminAbbass-xc4qk 14 күн бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉
@WisdomMaseko-fi5sv
@WisdomMaseko-fi5sv 14 күн бұрын
May God also punish fake prophets
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 14 күн бұрын
Anzanuso asanarowe mboma anaringat auzimu ngat inu km anasintha mawanga amarawi osangot amen zirizonse ngat simuziwa mawu bwanji munthu wowopa chauta sankhara busy ndizandare chifukwa kundare kuribe kuopa murungu baibo rimat muthange mwafuna ufumu wake ndipo zonse zizakusatani auzeni zaufumu wakumwamba osat zazikozo ayi panopa amarawi asavoteraso azibusawa ayi asibusa nomwenu ndinu amene mwawononga zikori mawonekedwe achipembezo km mphwnvu yake munaikana kare pezani njira zina zosakira ndarama akuru
@user-gx3xc9lk8x
@user-gx3xc9lk8x 14 күн бұрын
Good point
@MarkManyowa
@MarkManyowa 14 күн бұрын
Amen 😂😂😂
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 14 күн бұрын
Iweso ndiwa bodza mulungu wake UTI
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 14 күн бұрын
Tell them
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 14 күн бұрын
Iweee ukubwera anthuwo ndizako
@GeraldChisokeza-er5cf
@GeraldChisokeza-er5cf 14 күн бұрын
Fire abusa
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 14 күн бұрын
Amen😂
@ruthkundwe7448
@ruthkundwe7448 14 күн бұрын
😮😮😮😮😂😂😂😂😂
@Littlefair7
@Littlefair7 14 күн бұрын
Yes boma ili ndi lolephera koma zoti uyu ndi fake prophet sizisintha.
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 14 күн бұрын
Simulungu mbewe ndipo tsogolo la muthu sangalidziwe ndindani amewneyu tikusauka chifukwa cha kuba kwa dpp
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 14 күн бұрын
Uli nkati Monday zokubatu
@curtisewilliams8784
@curtisewilliams8784 15 күн бұрын
Cant you see that, the video was recorded in 2023? bloggers be serious
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 14 күн бұрын
Zakale izi akulu
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 14 күн бұрын
Aaaa m'busa wanji olowerera zadziko?? Ufumu wamulungu siuli wadziko lapansi baba, onvera awawa palibe chomwe akutsata
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 14 күн бұрын
Chitsiru iwe mchifukwa chake mwapha chilima
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg 14 күн бұрын
NDE ZOTI DZIKO LAPANSI NDI LA ANTHU OIPA ANANENA NDANI,,MULUNGU SANGAOPE KUYANKHULA ZANDALE CHIFUKWA IYEYO NDE MWINI MPHAVU
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 13 күн бұрын
Ndikanakonda Ndikanakhala ndi number yako kut ndikufotokozere zomwe baible limanena pankhani imeneyi
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 13 күн бұрын
@@CHIFUNDOCHINA-lp9lg ndikanakonda Ndikanakhala ndi number yako kut ndikufotokozere zomwe baible limanena pankhani imeneyi chifundo
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg 10 күн бұрын
ASE UTSOGOLERI WACHIPEMBEZO NDI WOYAMBA KUPOSA U PRESIDENT,,DZIKO LAPANSI LIMADUNIKA LIZIYENDERA MALAMULO AMULUNGU,,TIKAWASIRA ASATANA KUT ALAMULIRE ANTHU AMULUNGU SIYIGWIRA
@user-nr8oq4tr1i
@user-nr8oq4tr1i 14 күн бұрын
Fake prophet, yang'ana za Mulungu, waisted time
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko 14 күн бұрын
Wabodzi
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 14 күн бұрын
Amen pastor
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 14 күн бұрын
Amen ❤
@ellensambo6323
@ellensambo6323 3 күн бұрын
God bless you man of God
@MaryJefry
@MaryJefry 14 күн бұрын
Amen prophet
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 күн бұрын
Amen
@user-pn6ic9yr1t
@user-pn6ic9yr1t 13 күн бұрын
Amen amen
@TalazanGamah
@TalazanGamah 14 күн бұрын
Ameen
@ellenMakoloma
@ellenMakoloma 10 күн бұрын
Amen prophet
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 14 күн бұрын
Amen
@malitajere1609
@malitajere1609 14 күн бұрын
Amen
@user-nv7qt1yp7g
@user-nv7qt1yp7g 14 күн бұрын
Amen
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 14 күн бұрын
Amen
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 14 күн бұрын
Amen
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 14 күн бұрын
Amen
@user-no2sn1fo1h
@user-no2sn1fo1h 14 күн бұрын
Amen
@Twayibu15Chimbama
@Twayibu15Chimbama 14 күн бұрын
Amen
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 9 МЛН
Best father #shorts by Secret Vlog
00:18
Secret Vlog
Рет қаралды 22 МЛН
WHAT’S THAT?
00:27
Natan por Aí
Рет қаралды 13 МЛН
INTERVIEW YA BON KALINDO PA ZODIAK IYI NDIPO CHIKUKHADZULA
59:48
Malawi Trends TV
Рет қаралды 14 М.
I MEET THE GENIUS BEHIND NOMADS' SUPPORT SONGS!
4:01
Che Kalonda
Рет қаралды 18 М.
Limpopo fire nkwiyo wabwela lero pa Limpopo ndi Mr Don’t Trust timve basi
16:36
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,8 МЛН
LIVE: Donald Trump speaks at MAGA rally in Michigan
1:43:56
The Times and The Sunday Times
Рет қаралды 571 М.
CCAPYUM SERVICE
42:33
MVAMA CCAP NKHOMA SYNOD (Rev. Yassin Gammah)
Рет қаралды 188 М.
Best father #shorts by Secret Vlog
00:18
Secret Vlog
Рет қаралды 22 МЛН