Ku maliro a Lucius Banda zomwe zalalikidwa ndi izi masanawa olalikayo anaphuzila ndi Lucius

  Рет қаралды 15,509

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

7 күн бұрын

Пікірлер: 20
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV 6 күн бұрын
Pepani akulu akulu audio imadumphadumpha chifukwa cha network. Tinayesetsa kumbali yathu koma za technology zimatelo nthawi zina. Tsiku lopambana
@MikeYasin-pt5ru
@MikeYasin-pt5ru 6 күн бұрын
Rest well soldier
@BennettNjedza
@BennettNjedza 3 күн бұрын
Amen
@DerlickMatengo
@DerlickMatengo 5 күн бұрын
Rest in power fadd
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
Mtsikana wavala mupange wamizele ya black and white'yo ndokongola, ali ndi maso apasa chidwi, she caught my eyes 😂😂😂, ndunena uyo anawelamila pansiyo
@user-ib6jc4es3s
@user-ib6jc4es3s 6 күн бұрын
Kumasangalala IFA ya Bingu lero iye wapita mukuti anali wabwino Kodi inuso mwasanduka mulungu Koti mwayikakale iye Ku mpaladizo???
@user-ib6jc4es3s
@user-ib6jc4es3s 6 күн бұрын
😮😮😮
@FarifahJackson
@FarifahJackson 6 күн бұрын
Will goig to miss him.soon will join u
@MozzyBSaimon
@MozzyBSaimon 6 күн бұрын
Rest in peace Lucius u cant be gud to every one in this world
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
Ma echoes'wo bwanji nanga?, ingochosani video yanuyi, aaaaaaaa
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v 6 күн бұрын
Mulungu wakuti nanunso ingonenani Zina Ngati anali wabwino kwainu Kwa Mulungu akudziwa yekha namalenga osanena Ngati mwapitako muziwerenga bwino bible please
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
Anakakhala kuti amamenyera nkhondo osauka, bwanji anatulusa nyimbo yomalizila yobakila chakwela kuti akuyendesa bwino dziko pomwe zinthu sizikuyenda mmalawi muno?, kumuchemelela ng'azi kuti zitukuko zili paliponse yet anthu akufa akuzumzika ndi njala komanso umphawi, wat a shame!?, ndemukamati anali soldier wamphawi mmmmm , mwina nthawi yabakili koma osati kumapetoku,
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 күн бұрын
Sizikumveka
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
Ali ndi namba ya mzimayi wavala mpango wablak and white'yo alibo kwambiri, alindi maso ngati ampunga , ndunena uyo wawelamila pansiyo 😂😂😂😂
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 6 күн бұрын
😂😂😂
@charitykadama3354
@charitykadama3354 6 күн бұрын
🫢🤣🤣
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
@@gracemaluwa4674mukumuziwa ngati?, mulibe namba yamzimai ameneyu?, she caught my eyes !
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 6 күн бұрын
@@charitykadama3354 ngati mukumudziwa mgaileniko namba yake 😂, even camera man anachedwapotu pamzimayi ameneyu 🤣🤣
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 6 күн бұрын
@@harrisbanda5891 ai ndilibe
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 6 күн бұрын
Soja rest in peace follow eveson matafale
THE POLICE TAKES ME! feat @PANDAGIRLOFFICIAL #shorts
00:31
PANDA BOI
Рет қаралды 24 МЛН
ОСКАР vs БАДАБУМЧИК БОЙ!  УВЕЗЛИ на СКОРОЙ!
13:45
Бадабумчик
Рет қаралды 3,8 МЛН
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 28 М.
MBIRI YA LUCIUS BANDA
6:19
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 5 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 127 М.
Johnny Banda kuimba pa Maliro a bambo ake Lucius banda ku balaka
4:48
Bhima Ndalama Official
Рет қаралды 70 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
THE POLICE TAKES ME! feat @PANDAGIRLOFFICIAL #shorts
00:31
PANDA BOI
Рет қаралды 24 МЛН