Iyiyi nde yandifikapo ndithu big up Hot current 💪💪
@BwanaGD9 күн бұрын
Tisinthe flag yanthu ilindi mintundu yoyipa ntunduwake mmm ndiwachabe mutundu ya bendera yanthu imagwilitsidwa nthawizabili ndizinthu zakumidima panayenela kuyisintha bas
@Lee-lee-w1r9 күн бұрын
Koma ndipo Simukunama. Taonani flag ya Kenya 🇰🇪 ndi ya malawi 🇲🇼 sizisiyana kwenikweni koma mmene zinthu zilili ku Kenya ndi kuno nzonvetsa chisoni
@RobertCosmas-bo1uo8 күн бұрын
Massive analysis this is good idea and solution zoonad katangale akhoza kutha zkufunika azitsogoleri odana ndizopusa that's right guys.
@IshumaelMbewe-d4t9 күн бұрын
Tidakhala ndi atsogoleri ophunzira angapo koma sitidatukike pa cbuma ndi zitukuko ndiye tidzayese mtsogoleri wa form 4
@PetersenjMwale9 күн бұрын
Mumapanga ma demo abwino not like born kalindo, thanx TTV
@ElizabethMajiga9 күн бұрын
Apa ponkhapa mwawalakhulila amalawi🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@GiftNyirenda-q9d7 күн бұрын
Koma ma decision makers particularly politicians amamva zimenezi? Uthenga nde ndikwabwino and straight forward. Vuto aliyense angofuna iye ndi abale ake akamachoka, zawo zikhale ziyenda. ie alibe chikondi kwa a malawi koma kuzikonda
@user-mh7cc8up4i8 күн бұрын
Apankunku ndi ndevi zamwayi mwayamba bho next time muzapose apa apa ndakayika kuti mudadya chikondamoyo we love you lots ❤
@user-sw6rz4tz3z6 күн бұрын
Suzumilani mu MRA muwone zomwe zikuchitika especially in a hot activities eg boarders kkkk
@PetersenjMwale9 күн бұрын
U guys u talking the really truth
@blessingsfalamenga45756 күн бұрын
Anyamata inu get ready in 2025 boma lina likubwerari tikonze malawi you are good indeed.
@SolokingChimzy-yt7dj6 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂..ati sitidya kwaaaanu eishhhh anyamata anakalowa mu studio ndi mkwiyoo awa...Iman moona mtima ndimopanda mantha ngat Mikaya wa mu Bible yemwe anasutsana ndi mafumu ochuluka pozindikila kut zoyankhula zake ndizo zinali zoona
@louisgolden9 күн бұрын
Mwauzeso kuti akugulileni track trauser kuti yikhale top and down
@user-em3xq2th4g22 сағат бұрын
😢 Apa palibezoti bola baja bandani ni same thing those bantu
@stevephiri10438 күн бұрын
Mmoziyi ndamene amalakwisa program amakonda kuwatchinga azinzakewo kuti asamasuke
@dumisanimoyo31529 күн бұрын
Amati mwanapiye anawonera make kunyera munyumba nde tiphe mayi wakeyooooo
@lastonmasoatenganji-bs5gf7 күн бұрын
Tikadali njira, sindazione munthu wa zaka 60 akukakamira kuyamwa bere la amache. Mkakawo udakoma chotani.
@ChettoSongeah6 күн бұрын
impressive guys Ndevu za mwai umaitha ndi nzako yo 🤞
@Erickasonya-uw8yw6 күн бұрын
Bravo guys mumakwana
@kotking-xg7pp9 күн бұрын
MWALANKHULATU MWAMPHAMVU RELO NDIYAMIKE KWAMBIRI.
@clintonhodda98309 күн бұрын
Koma a Brown mpinganjira mpaka liti osavomeleza kuti Mulungu sanafune kuti akhale president iiiii
@HastingsJonathan8 күн бұрын
Nelson Nelson 🤣🤣ukumaika ma flash et
@jelsonmlowoka861110 күн бұрын
Zoti inali times television yooneledwa ndi anthu ambiri pano ndi history chabe hahaha ndaonela ma viewers ndi kuchuluka kwa ndemanga
@EdwinMakwangwala9 күн бұрын
Ambiri amaonela but they reserve their comments but ndawakonda ma guys
@user-em3xq2th4g22 сағат бұрын
❤😂😢 nkhani yagona pa utsogoleli, kwa anthu amene ukuvoteledwao, tinawavotela pachifukwa chiani?😢 Kd tinawavotela chifukwa choti mwaiwo tikuonamo muzimu wa utsogoleli? Kapena chifukwa choti tikumadyanawo? Apa tiwonepo apa, kwa Ife ngati ovota. Kwa iwo amene akhalapo atsogoleli, ndi iwo amene ali atsogoleli, Asanapange chiganizo chofuna kukhala mtsogoleli anayamba azifufuza okha kuti mwaiwo yilimo mphatso ya utsogoleli kapena ayi? Akulu akulu tisaname apa onse amene tawavotela awa ndi amene tikuwavotela awa akungogweramo chifukwa chokakamizidwa ndi anthu ane amene ali atidyenawo, chifukwa cha mzimu uwu uwu, woti tikamuona munthu ndikumuwuza kuti km inuyo kuti mukhale mtsogoleli anthu akhoza kukuvotelani zaziiii, mawa olira ndifetomwe, muMalawi alimo anthu anzelu ophunzira aliso ndi utsogoleli mkatimwao km chifukwa choti ndi osauka palibe munthu amene angawa votele, pano ndi izi zaka 60+ chifukwa chokonda kusankha bakawalala aba tilindicha zero chosangalasa ndichani kumuvotela munthu maba akukufiya pahoroh 😂 kpn kukumanga ndikukakusekera inside kirikiri😮
@nellybruhan58349 күн бұрын
Ine nde kumalawi kwandikwana😭😭😭😭😭😭 thupi lonse likumachita kuwawa ndikuganiza
@user-ec3xh4pc6t9 күн бұрын
Dear bwelani mbalikuno bas
@nellybruhan58349 күн бұрын
@@user-ec3xh4pc6t kutiko kumeneko saka bag yanga ndapakililatu
Malawi has suffered leaders who kept us in the dark for years. Without water. Leaders that store n cut all rail lines to replace it with mangochi based vehicles. The nation suffered from leaders without teeth who paralized universities for almost a year. If asked, they would go on holiday in the USA. Now, are we promoting such leaders to come back? This is an opposition forum. Not a program that talks reality. None bias reporting is what this nation needs.
@OssmanAbubaker-l5s5 күн бұрын
Zoonadi my brothers osaopa osapepesa zaka 4 palibe chanzeru olo chimodzi chimene achita awa a Tonse
@GraceZumazuma9 күн бұрын
Keep it up times musalore akupatseni ma banz mudzitiimilira chonchi
@dysonmasiye57368 күн бұрын
Za katangalezi tinaluza munthu wofunikira kwambiri amene anali ndi masomphenya pa nkhani iyi....SKC 😢 tidzamlila mpaka kale...koma adaferanji?
@gracemkandawire87698 күн бұрын
Brian alikuti Kodi? Amabebetsa
@christophermukaka74036 күн бұрын
To say the fact ma guys awawa amayankhula zoona koma kumtunda ku mmm
@sparkdymon34299 күн бұрын
Iyi koma mwang,alulandi makosana abwana kutundako azizifusa makamaka achekwela ndimbava ndifukwa akopa ACB
@user-ux8bc6wy1i8 күн бұрын
Iyi ndye hot current yen yen 🔥🔥🔥
@mustafahassan91287 күн бұрын
Koma ndiye mwanena mosanyengeleratu
@user-to5of3ks3g9 күн бұрын
Nice message
@obviouskedson64839 күн бұрын
Ife timamva nanu kukoma chifukwa mumayankhula chilungamo ,ndipo nthawi ya program yanuyo muionjezele mabwana
@user-sw6rz4tz3z6 күн бұрын
Musogoleri akawoneka wa good future kumapha basi
@user-pv9uk6sc3w9 күн бұрын
Yeah! This is hot for sure.
@user-si7po9sd5i9 күн бұрын
The curtain in the temple is about to be torn, we are waiting eagerly
@EdwinMakwangwala9 күн бұрын
The problem of you and us as Malawians we always celebrate when someone fail, this is very bad and ugly kkkkkk
@user-si7po9sd5i9 күн бұрын
Sometimes it's good to understand the message properly,who is celebrating here? If someone is failing to run the affairs of the country,how does that concern me?,he has 23 advisors,What is their job?what are all the advisors doing, this is high level filth,Justice hurts.
@Lee-lee-w1r9 күн бұрын
@@user-si7po9sd5iexactly tell this person the truth
@Lee-lee-w1r9 күн бұрын
@@EdwinMakwangwalait’s not celebrating them. It’s celebration that the truth about them will be coming out
That's why they assassinated malemu mnyamata woganiza boo Adamupha KS and they think we have mastered the crime and they will not be able to be caught and arrested.
@augrinngunga80318 күн бұрын
Mwalakhulako zazerutu, mukamadya ma bazi guys times izakhala Ngati MBC yoonera achakwera okha