Limpopo kupsa kwa nyumba ya Kaliati zoona zeni zeni izi tamvani bwino bwino

  Рет қаралды 26,412

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

16 күн бұрын

Пікірлер: 59
@MosesKalenge
@MosesKalenge 13 күн бұрын
BEST LEDIO LIMPOPO M'MAKWANA 🙏🙏🙏💪💪💪💪💪❤❤❤
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 14 күн бұрын
Limpopo station is Station of the moment! I listen every day here in Mozambique.
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 14 күн бұрын
Number one radio
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 14 күн бұрын
Ineyo mai kaliati ndimamukonda mai olimba mtima zikomo kwambiri ngati akuti zonse ziri bwino .
@augustMag
@augustMag 14 күн бұрын
The best I Limpopo FM
@MosesKalenge
@MosesKalenge 13 күн бұрын
Ndege kumvula munthu jeket tai pakhotsi mmmmmmmh 🙌🙌🙌🙌😢😢😢😢
@janemvubu7750
@janemvubu7750 14 күн бұрын
Koma abale timazifu tsa mafutso kuti chachitika ndi chiyani zikomo potiwiza chilungangamo
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 14 күн бұрын
Ndimakhurupirira ripompo and bakiri muruzi bas enawa amangokhara kt akhuta mbwanda bad zana romweri atinamiza kt evas mereka wamangidwa chifukwa chanyimbo yomwe anaimba pamariro km guys mmmm ngat mukufuna ku tchuka pezani zina zochita please
@MilwardChanza-mr4yr
@MilwardChanza-mr4yr 13 күн бұрын
That's better kuti Hon P kaliyati sanakhuzidwe ndi ngozi iliyose satana achite manyazi popular khan zabodza ndipo ndi wolephere.
@fannyzimba149
@fannyzimba149 14 күн бұрын
Thanks so much Eeee koma anthu muli pa changu mmmmm koma osamanamizira zinthu ngati zimenezi
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 14 күн бұрын
It's a propaganda aiming to see if Limpopo is fake or real. Apa ndiye auponda
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v 14 күн бұрын
That's great
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 14 күн бұрын
Koma anthu muli patchito yopeka mabodza eeeee ai tiziona
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk 14 күн бұрын
Best radio Malawi never had ❤❤
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 14 күн бұрын
Thanks for the update comrade
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 14 күн бұрын
True info!!
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 14 күн бұрын
Mayankho abwele poyera me from Kzn ❤❤❤
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 14 күн бұрын
More fire Limpopo chilima tidzamulira mpaka kale chakwera ndi Monica Kodi mufalita mukunyasisa dziko
@happymughogho5167
@happymughogho5167 14 күн бұрын
DONT PLAY WITH GOD BECAUSE IT IS YOU WHO MAY DIE BEFORE THESE PEOPLE YOU SEEM TO WANT DEAD
@ThokozaniMaulana-oi5hz
@ThokozaniMaulana-oi5hz 14 күн бұрын
The whole malawi tikuvela
@CeciliaChibwana-lx9dn
@CeciliaChibwana-lx9dn 14 күн бұрын
Best radio ever🙌🙌
@JerseyAlfred
@JerseyAlfred 14 күн бұрын
Umakwana ntanyiwa
@FrankHaruni
@FrankHaruni 14 күн бұрын
Atanyiwa khani ya athu anangwina ku 🇿🇦 dzilipati tiudzen
@LameckBeharry
@LameckBeharry 14 күн бұрын
My best radio
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 14 күн бұрын
Best redio lipompo
@DevisonHala
@DevisonHala 14 күн бұрын
Kodi tikambe kuti tinayiwala bwanji amalawi kuti udf ndi mcp kunali nkhondo tisamale tiuzeni zoona
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx 14 күн бұрын
But wy amalawi 😭
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o 14 күн бұрын
My radio limpopo fm
@yassinn5634
@yassinn5634 14 күн бұрын
Mabodza akutulukawa afunikira kwaoonetsa bwino chifukwatu ine ndikukhulupirira kuti zikhoza kutheka kuti mdani wa a Kaliyati ndi Evance Meleka samene mukumuganizirayo koma alipo wangobisala. Akaliyati ndingowalangiza kuti mdani wanu si MCP ayi mdani wanu ali mkhonde mwanu momwemo
@davidcainoiss2762
@davidcainoiss2762 14 күн бұрын
Viva best TV ever...much love from cape town Western cape
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 14 күн бұрын
NDI A MCP AKUNAMATU KOMA IFE TILI NDI CHIDWI KUYANG'ANIRA KUMVA BODZA LA MCP IFE SITIBALALIKA , MAI KALIYATI OSADANKHAWA MULUNGU ALI KUMBALIYANU , ZIWAVUTA OKHA AGALU AMENEWA,
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 14 күн бұрын
Zikomo tayamika kubva kuti Mai Kaliyati ali bhoooo
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 14 күн бұрын
Ameeen ndimadabwa,mayesa asnkhidwa ku ministry of mining??
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 14 күн бұрын
Ndiye inuyo antanyiwa mukuyankhula za ngozi ya mayi kaliyati koma mukubwelaso ndi za imfa yachilima zikukhuzana pati kungoti nanuso mumatenga ngati ife amalawi ndife zinsilu zoti china chilichonse chimene munganene ndizowona koma nanuso zambiri mumanama mukuziwa eni ake amene mukuwamenyela kampeni ndicho chifukwa chake simunena zabwino zimene likuchita boma mumango nena zoipa zokhazokha zina zamaboza koma muziwe mulungu si james ngati wati boma limene liripo lizalamuliraso or mutanyoze chotani lizalamuliraso chifukwa timawona kuti zina zimene mukunena zambiri ndinu onama
@user-ht7vs3dp2u
@user-ht7vs3dp2u 14 күн бұрын
Radio yachoonad ndiyoopa mulungu ndi yopanda chinyengo ndi radio ya Limpopo FM radio osakonda radio iyiyi ndi udasi ndithu
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 14 күн бұрын
Makwanila boss man
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 14 күн бұрын
Awuseni big and ifa ya chiwaya zitidaiwale also
@MecyMalothi
@MecyMalothi 14 күн бұрын
Thank u
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d 14 күн бұрын
N1
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 14 күн бұрын
Bola pamenepo eeeesh
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 14 күн бұрын
Alemekezeke ambuye atetezele onse atsogoleri a utm
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 14 күн бұрын
Alemekezeke wa kumitamboyo
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 14 күн бұрын
Mcp yagwa ndipo,2025 kulowa boma Lina,koma tiyeni tinene zona, nyumba ya mai ili bwino bwino,za mfuti 400 kulibe nkhani imeneyo.tisiye, propaganda.
@user-cp4qt9hs8w
@user-cp4qt9hs8w 14 күн бұрын
Nkhan yabwino kwambili
@DorisChatenga
@DorisChatenga 14 күн бұрын
Zosakhala bwino
@Biath-m4b
@Biath-m4b 14 күн бұрын
No1 radio
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 14 күн бұрын
Mwachita manyazi ndinu zisilu sgalu i u
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 14 күн бұрын
Great 👍
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 14 күн бұрын
Wise man
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 14 күн бұрын
Anakutulukani anthu pano anaziwa kuti ndinu aboza ndinu zisisilu
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 14 күн бұрын
Ngati lipopo imakunyasa usiye kuvela ifeyo timaikonda
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 14 күн бұрын
Ife full time pompano kumvela pompano daily
@LamseyLazarous-dl5qd
@LamseyLazarous-dl5qd 14 күн бұрын
Chisilu ndiweyo
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r 14 күн бұрын
Ndipo zoona munthu wazeru zake sangatengeke ndi izi or ma comments akewo akuwonekaso kuchepa kwake ineyo sindimalizisaso kumvesela mvuuuuu ndadusa zindichedwesa ndi nthawi yolapa ino osati yomvesela mabozawa
@JhdaLifi-vu9sd
@JhdaLifi-vu9sd 14 күн бұрын
Ngati munatuluka inu ife mpaka 2063 wooo
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 14 күн бұрын
Allah Akbar ntima unawawa komanso ntima unafooka mulungu awatetezele kuzoipa zilizonse zomwe zikukonzedwa
Limpopo fire nkwiyo wabwela lero pa Limpopo ndi Mr Don’t Trust timve basi
16:36
INTERVIEW YA BON KALINDO PA ZODIAK IYI NDIPO CHIKUKHADZULA
59:48
Malawi Trends TV
Рет қаралды 17 М.
🤔Какой Орган самый длинный ? #shorts
00:42
WHO LAUGHS LAST LAUGHS BEST 😎 #comedy
00:18
HaHaWhat
Рет қаралды 23 МЛН
Became invisible for one day!  #funny #wednesday #memes
00:25
Watch Me
Рет қаралды 59 МЛН
Malodza Akuchikangawa A Poem by Sir Michael Benjala
5:00
Clement Thanda
Рет қаралды 4,1 М.
РАҲМАТ ҲОҶИ БИБӢ! - ПРОСТО АБУ
16:30
PROSTO ABU 01
Рет қаралды 1,8 М.
Nkhanga Zaona
7:01
Mlaka Maliro
Рет қаралды 12 М.
Tsatane  Tsatane wa Nkhani ya Anthu Amene Akanilirana kwa Wilisoni
17:42
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 131 М.
BON KALINDO 24 JULY 2024 KUSWANYA BASI PA WEDNESDAY
13:14
Malawi Trends TV
Рет қаралды 7 М.