Limpopo ngozi ya ndege aneba ku Zambia athilapo mulomo kulephela kwa boma la Malawi za manyazi

  Рет қаралды 18,726

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

23 күн бұрын

Пікірлер: 95
@misoMoyo
@misoMoyo 22 күн бұрын
Nkhani zina ukamva kumaona ngati mwina ukulota kuti kma zinachitikadi until NW I dnt believe that SKC is gone
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 22 күн бұрын
😢Koma ndiponso inu hmmm
@lottiempata2487
@lottiempata2487 22 күн бұрын
MCP will never change what I know
@GodrickBarton-e4u
@GodrickBarton-e4u 21 күн бұрын
Malawi dziko lomvetsa chisoni
@user-hj5oq5jm9v
@user-hj5oq5jm9v 22 күн бұрын
Keep it up comrade
@TendekeraniKachingweThenzomale
@TendekeraniKachingweThenzomale 22 күн бұрын
Auzeni mtanyiwa😂😂 we r tired
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 22 күн бұрын
Ndipo kudekha kuli ndi malawi ulendo uno eeeh kukundidabwitsaaa. Koma sanatidyetse khuzumuleee koma
@AngelinaMzowa
@AngelinaMzowa 22 күн бұрын
You can say that again,, Mtambo king of demonstrations adamugulura mano
@YassinAmbali
@YassinAmbali 21 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz 21 күн бұрын
thank you combrade mtanyiwa iappriciete with you continue bring as more facts we are planning proud of u
@user-vw7tj2ss3l
@user-vw7tj2ss3l 22 күн бұрын
Yomwe galu iwe salute sir
@eunicesaiti
@eunicesaiti 22 күн бұрын
Zikomo bwana, following
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b 22 күн бұрын
Am also in Zambia but we need answers guys you Malawi people chkagawa tuzeeni
@user-hu4gu7op7n
@user-hu4gu7op7n 22 күн бұрын
Zitipangisa kuti pobwelela kumalawiko anthu ife tili mumaulendo amayiko ena tinyamule mfuti malawi wayipa kwambili
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x 22 күн бұрын
Things will change 🙏 Buddy Ntanyiwa ulemu wako 🔥🔥
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 22 күн бұрын
Kodi osavomeleza bwanji kwa iye bwanji akuchitisa manyazi
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 21 күн бұрын
Yomweyo galu iwee😂😂😂😂😂
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v 21 күн бұрын
Zoona munthu mmodzi kuzungunza anthu ma miter aaaa koma Malawi ai ndithu mwachaje
@FrankWaresi
@FrankWaresi 21 күн бұрын
Zikomo a comrade
@user-mv1wg2qd6i
@user-mv1wg2qd6i 21 күн бұрын
Following
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 22 күн бұрын
Mulungu akudziwa choonadi chatsiku limene lija ndipo yekhayo oweruza olungama adzaweruza ndikuika zonse pambalambanda. 😢
@umalimaganga
@umalimaganga 21 күн бұрын
SKC SAID THINGS WILL CHANGE AND IT WILL DON'T LOSE HOPE
@FrankMasaka-s7u
@FrankMasaka-s7u 21 күн бұрын
Zambiri tizimva maka tikawachosa maudindo awowo
@VitumbikoJere-h7q
@VitumbikoJere-h7q 21 күн бұрын
Izitu zikungotengera anthu akumabanja oferedwawo ndi achipani Cha utm kukhala patsogolo motero anthu onse azukansio kufikira chilungamo chitaziwika za imfa izi.
@joebrown1158
@joebrown1158 22 күн бұрын
The question is what kind of diffence force is there in Malawi 🇲🇼?
@user-hs2dw7ly2c
@user-hs2dw7ly2c 16 күн бұрын
Boma likanankhala likumva likanamva anthu ayunkhule kwa mtundu bwanji😢
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 21 күн бұрын
Ife a malawi tili ndi mantha wonani panu ku immigration anthu akuvutika kwambiri
@Yaqub-nk4pu
@Yaqub-nk4pu 22 күн бұрын
Yes SKC is no more eish icant believe koma abale munthu chomwe anaika Mulungu mwa munthu zoopsya
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 22 күн бұрын
Ulemu wanu comrade ntanyiwa Mulungu apitilize kukutetezerani
@user-yl3lg5fk8f
@user-yl3lg5fk8f 21 күн бұрын
Gazi lamunthu limayankhula,,mwazi omwe mwaukhesa paamthu omwe sanalakwe kanthu bwana muziziwa kt mmanja mwanu muli magazi okhaokha,,moyo wa ndiolose ndikakutafune
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 21 күн бұрын
Chakwela anapha chilima
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv 22 күн бұрын
Mbuz chakwera mulibemo utsogoleri
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 21 күн бұрын
My brothers from Zambia this chakwera his killer
@EvanceNsomba-j6f
@EvanceNsomba-j6f 22 күн бұрын
These people are very wicked papa eiiiish God knows and will protect Malawi.
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j 22 күн бұрын
Chikangawa chakwera wayiona kkkk mwanzi wa chilima uwona komanso ukufa nawe
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 22 күн бұрын
Mr Chikangawa Chakwera is false and worst president in Malawi history. Shame on him!
@FrankHaruni
@FrankHaruni 22 күн бұрын
Ing,alule tanyiwa umakwan😅😅😅
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v 22 күн бұрын
🔥🔥
@FrankHaruni
@FrankHaruni 22 күн бұрын
Tanyiwa ndiameneyo osati dzinadzi aaa timakukhulupilila iweyo tanyiwa
@FrankHaruni
@FrankHaruni 22 күн бұрын
Munangoti dxiiii.ndimaonangati wachimedza chibadxi bolako apaaa tiliso limodxi
@DysonNakhaphe-bo4dl
@DysonNakhaphe-bo4dl 22 күн бұрын
Limbani ntima man kutiuza zenizeni
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 22 күн бұрын
😢
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf 22 күн бұрын
Ayerekeze kusokoneza misongano yathu tikathanirana konko ku Nsonganoko ena sakabwerako amoyo kumeneko ayerekeze.
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
Ndipo ufunika kuwagwila ndiwapha asatinyase agalu amenewa
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 22 күн бұрын
SKC continue rest in peace sir
@user-hu4gu7op7n
@user-hu4gu7op7n 22 күн бұрын
Kodi anthu amenewa padziko pano akuona ngati anafika basi, akupha azawo ngati nyama yakuthengo,
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 22 күн бұрын
Vuto kusilana basi Malawi,,, salibwino tlibe chinvano.., Chakwera achokeh
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 22 күн бұрын
Ndipo zinthu sizingasinthe opanda umodzi, anthu mantha too much.
@matickosman5316
@matickosman5316 22 күн бұрын
inu mpaka nchenga kukhomela msonkho ufiti chani
@LuundoJohnkabage
@LuundoJohnkabage 22 күн бұрын
😂😂😂😂
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
Zitsilu za wathu za MCP kenako ayambilatu kulipiltsa m,phweya kuti tizlipila
@user-ss9bj5eh6b
@user-ss9bj5eh6b 22 күн бұрын
comrade ntanyiwa machine bambo ing'alureni basi
@rashidadan2533
@rashidadan2533 22 күн бұрын
Zoti amabelalimodzi ndi chakwela mpaka kukhululukikana milanduya katangale tisiyekaye apo , Chilungamo chophana chiyendengati mazi , Chakwela and his evil cabinet are terrorist's .
@imraanJafal
@imraanJafal 22 күн бұрын
Eish koma analoza Malawi analakwa kwambili achoke alipowa
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 22 күн бұрын
Mpaka ovuula nchenga nsonkho dyera la chakwera ndilamtundu wanji kufuna chilichonse chikhale chake kubela anthu ovutika shame on him useless man
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 22 күн бұрын
America said,Trump is not under the law, also here in malawi we say Cahakwera is not under the law paja chilima watisira mawu kuti osaopa,osafooka osatopa,,,,,,,,,mwachidule its triple" O"
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 22 күн бұрын
America simungaifanizire ndi Malawi, they are strict people and zawo anaziika mu system and amatsata. Malawi is too corrupt, Chakwera wapha vice koma palibe chachitika yet evidences are there 😢. Witika anaphedwa ndi Kumkuyu koma pano akadali minister, Malawi aaaaaa
@user-cb5me8wp1k
@user-cb5me8wp1k 22 күн бұрын
​@@user-ww4ei5fb7dkumalawi athu kaya agona kaya sindikudziwa athu angofa ngat khuku koma palibe akudxudxula mmmmm
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 22 күн бұрын
Koma chakwera afa imfa yowawa ngati Mulungu analanga pharaoh chakwera ndi ndani wafika poziona ngati iyeo ndiotilenga eeti asamale
@CatherineMbela
@CatherineMbela 22 күн бұрын
Zoona chakwela azafadi IFA yowawa ngatiso goliati
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
Inu afford mukawagwila anyata ameneo apheni zitsilu za wathu agalu
@DevisonHala
@DevisonHala 22 күн бұрын
Mr chikangawa chakwera forest
@ShaibuBobo
@ShaibuBobo 22 күн бұрын
Xhakwela manyamake amandiyasa ndikamamuva
@franknzerub6644
@franknzerub6644 22 күн бұрын
President ameneyu amayankhula nkhani zongolota basi,mulibe utsogoleri ulionse mwa iye koma bodza basi.very sad to see that our skc is no more with us😢😢
@user-cb5me8wp1k
@user-cb5me8wp1k 22 күн бұрын
Komaso amalembera zolakhulayo ndiolakwa mpaka akut adzafera mbendera ya malawi iiiii koma manyaz alibe
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf 22 күн бұрын
Awa ndiye mabvuto athu ifeyo aMalawi
@user-jj3oo6jh1l
@user-jj3oo6jh1l 22 күн бұрын
Ife ndiolephera km kumanga wanthu ndikumene timakudziwa
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx 22 күн бұрын
Mchengawo wambyache chakwelayo 😂😂😂
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 22 күн бұрын
Chakwera ingotulani udindo pansi
@ChristopherKalumbu
@ChristopherKalumbu 22 күн бұрын
Ine ndimati data yandithela Kusaka KZfaq mtanyiwa osamupeza mmmm bg chiyembekezo chathu chili payinu chomwe mulungu wakoza kut tidziwe zoonadi
@user-uv5rf4zt5q
@user-uv5rf4zt5q 22 күн бұрын
Nkhanza MCP mfiti zokha.
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf 22 күн бұрын
Tithawira kuti ifeyo
@VeronicaKondowe-og4zo
@VeronicaKondowe-og4zo 22 күн бұрын
Ngati bozadi kuti saulosi kulibedi, timakunyadilani bwana mumantha kutiyakhulila
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 22 күн бұрын
✊✊✊✊🇲🇼🔥🔥 l don't scared for anyone because mwatikana mukadakha ozidikila mukadatula pasi udindo wau President,mukadakha ndizelu ngat Denes mwana wakumzuzu bweza pano tikusimba lokoma stupid
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 22 күн бұрын
Live from south Africa Durban Pietermaritzburg
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 22 күн бұрын
Vuto lilindi inu azanthu ophuzila, ndiposo osusa boma, simukupangapo chilichose, Apa pakufunika Kuti nonse osusaboma ndiwose ogwila ntchito mupange chimozi, kumalawi kuvute chakwera athule udindo.koma inuyo simuku panga chilichose ndiye Ife osaphuzila tipanga chani? Aliyese ogwila ntchito muboma osapita Ku ntchito, kupaliyamenti ose osusa boma osapitako ,aka khalemo okha a MCP.Ndikupita pa museu kupanga mademo , ndiku pemphera razarus achoke, amene ndifuti munyumba anyamule apolisi akawonbera ifeso tikawombere tinyamuleso zikwanje basi
@RiyemaDomybusiness
@RiyemaDomybusiness 21 күн бұрын
Zoona bro athuwa omenyera ufulu akanakhala kuti tziku lompanga mademo awuzane onse omenyela maufulu awuse amalawi tziku lopitha mpasewu🤝🚛
@user-fr3ge2hf6s
@user-fr3ge2hf6s 22 күн бұрын
Mulungu awalanga osewa ndiokutha athuwa
@karimshaik4485
@karimshaik4485 22 күн бұрын
Chakwela killed chilima
@NedsonKavala
@NedsonKavala 22 күн бұрын
Zomwe zikuchittachipani cha mcp ziachirendo ndimomwe amachitira tikango onamukuvota.
@user-vw7tj2ss3l
@user-vw7tj2ss3l 22 күн бұрын
Amawelenga bable koma abusawa
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d 22 күн бұрын
Palibe kugwira bible, lidatsala kutchalitchi
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 22 күн бұрын
chakwera ndi chigawenga pantumbo pa mache
@IssacMateyo
@IssacMateyo 22 күн бұрын
Kutukwana kumeneko iweyo amay ako koma alindipamtumbo kapena alibe
@IssacMateyo
@IssacMateyo 22 күн бұрын
Kutukwana kumeneko iweyo amay ako koma alindipamtumbo kapena alibe
@InnocentChikhwazaNkhoma
@InnocentChikhwazaNkhoma 22 күн бұрын
Inu chakwera ndi mfiti uyu.
@CatherineMbela
@CatherineMbela 22 күн бұрын
Alinapo Koma pa chakwela ndpamene Pali ponukha ponyasa ndkuona akutukawanapo
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 22 күн бұрын
@@IssacMateyo iwenso kuyankhula kokhako pantumbo pa mbuyako kape mbuzi ya munthu sakhwi iwe ndichigawenga chakwerayo mwayaluka pa dziko lonse anthu akupha ndipo iwe machende ako wanva
@PetroJack
@PetroJack 22 күн бұрын
Useless Chakwera
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 22 күн бұрын
Useless leader
@dontreybanda278
@dontreybanda278 22 күн бұрын
Alephela a chakwera anuwo
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk 22 күн бұрын
Koma chikangawa forest akuzuzika ndi wuchigawenga
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 23 М.
MISS CIRCLE STUDENTS BULLY ME!
00:12
Andreas Eskander
Рет қаралды 19 МЛН
I'm Excited To see If Kelly Can Meet This Challenge!
00:16
Mini Katana
Рет қаралды 17 МЛН
Gym belt !! 😂😂  @kauermtt
00:10
Tibo InShape
Рет қаралды 17 МЛН
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Zodiak Malawi
Рет қаралды 56 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 109 М.
Interview ndi Norman Chisale
1:05:22
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 228 М.
DJ MUNYANANE WABWELASO LERO KUCHOCHOMOLA ANDALE A USILU
31:45
Malawi Trends TV
Рет қаралды 2,4 М.
MISS CIRCLE STUDENTS BULLY ME!
00:12
Andreas Eskander
Рет қаралды 19 МЛН