Maliro a Bishop Kapenga mwana wao Waxy kuyankhula zabwino za bambo ake

  Рет қаралды 5,020

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

8 күн бұрын

Пікірлер: 12
@robenmatchilinga604
@robenmatchilinga604 7 күн бұрын
Kulila kwachiyembekezo Ambuye anat tsalire ngat osalawo.mwwna walila mwachiyembekezo uyu amen 🙏
@EsinatMawala
@EsinatMawala 6 күн бұрын
Ine ndimafuna ndive chisoni koma eshi mene akuyakhulila anamalilao ngat akusangalalanazo nde ine ndindani kt ndive chisoni bass ifenso zilibwino pamenepo🎉🎉
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 күн бұрын
Mulungu salakwisa
@lucasmariopaulo5241
@lucasmariopaulo5241 7 күн бұрын
Kusewelesa malilo, atayambe kulila akapitapo masiku atatu
@sonjelaissh8702
@sonjelaissh8702 6 күн бұрын
😢😢😢😢
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p 6 күн бұрын
Ife anthu sitidziwa,,,munthu akamwalila thupi lokha ndilomwe limafa ndipo limawola kusanduka dothi,,koma mzimu siwumafayi umakhala mu mtendele ngati amakhulupila Mulungu m'modzi yekha ndikuchita chifuniro chake,,or titalankhula zabwino bwanji zanthu omwalila,,palibe chomwe chingasinthe pamoyo wake wa m'manda komaso tsiku lomaliza munthu akangomwalila basi zake zapadziko lapansi zimakhala kuti zatha basi zimatsala zapakati pa iye ndi Mulungu wake basi pazintchito amagwila
@Patricia_Chisankha
@Patricia_Chisankha 7 күн бұрын
2 Kings 4: 26
@user-ru1mm7bf4p
@user-ru1mm7bf4p 7 күн бұрын
Aaaa maliro aku Malawi weziwezi mwayamba kuwalowetsa China ana inu
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 6 күн бұрын
Kuyankhula kwanji koyankhula pamaliro? Mwalowetsa dzibwana kwambili.
@kennedychinguwo1640
@kennedychinguwo1640 7 күн бұрын
Kulankhula kopepusa imfa
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 7 күн бұрын
Maliro ndichinthu chodula kwambiri makamaka KUTI analinso bishop koma akukabweta mkuikalposo zazivwana zaziii
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 күн бұрын
Akagudubuka Kodi adzuka aaaaakoma anthu
MUNTHU WAMULUNGU kuling'alura boma la CHAKWERA...lalephera
4:43
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 24 М.
Final muy increíble 😱
00:46
Juan De Dios Pantoja 2
Рет қаралды 50 МЛН
HOW DID HE WIN? 😱
00:33
Topper Guild
Рет қаралды 37 МЛН
Heartwarming: Stranger Saves Puppy from Hot Car #shorts
00:22
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 20 МЛН
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 18 М.
MZIMU WA (SOJA LUCIUS BANDA)UUSE MU NTENDELE
1:45:51
Jimmy
Рет қаралды 9 М.
Johnny Banda kuimba pa Maliro a bambo ake Lucius banda ku balaka
4:48
Bhima Ndalama Official
Рет қаралды 69 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 154 М.
Rev Alexander Kambiri  kupeleka uthenga wachipepeso pa ifa ya Dr  Chilima
28:50
mabena Studio channel
Рет қаралды 21 М.
Peter Sambo feat. Mlakatuli Christon Mbingwani - Tilire Bwanji
6:00
Kacheto Multimedia
Рет қаралды 3,8 М.
Final muy increíble 😱
00:46
Juan De Dios Pantoja 2
Рет қаралды 50 МЛН