Mtsogoleri Oyenela Ndi Chilima Basi - Samuel Lwara

  Рет қаралды 13,666

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

3 ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara says Right the Saulos Chilima Vice President of the Republic of Malawi is the only person qualified to be President of the Country.
Ku Nyasa Voicebox, Samuel Lwara wati Right the Saulos Chilima Vice President of the Republic of Malawi ndi munthu yekhayo amene ali woyenera kukhala mtsogoleri wa dziko.

Пікірлер: 107
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 3 ай бұрын
True, chilima he is intelligent one.from mozambique.
@carlossadimba595
@carlossadimba595 2 ай бұрын
He is the man of the match in this political arena.......and I love his courage yet MCP without CHILIMA they can not carry the day
@PaulNgambi-ep4kt
@PaulNgambi-ep4kt 2 ай бұрын
Exactly Chilima must rule this countly
@user-ic3ps4qd4l
@user-ic3ps4qd4l 2 ай бұрын
Mr lwara mukuyimenyatu nkhondo,, tili mbuyo mwanu
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 3 ай бұрын
That's true SKC my vote ❤❤kungoti anthu mumadana ndi chilungamo nkhani ndi mtima wa nkhwizi basi but Mr Rwara ndi munthu ozindikira❤❤
@user-mv6tn3qv8v
@user-mv6tn3qv8v 2 ай бұрын
I love Chilima and UTM❤
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 3 ай бұрын
Nkulu iwenso Mutu wako sukugwila bwino ayi,chilima ndiye anaika a Malawi pamoto.amalawi si opusa sakumufunanso chilima
@WittinessBeza-cp5kf
@WittinessBeza-cp5kf 3 ай бұрын
Ndiye iweyo bwanji osalamulira ndi chipani chako cha mcp chankhanzachi
@DesmondKanguwe
@DesmondKanguwe Ай бұрын
Akumena zoona ... Malawi ngti dziko singasuthe ndma leaders enawa ndiandale bas koma nzeru zoyendetsera chithu chilima kaya madana naye koma that guy is genius gv him a chance... Enawa mbola
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Ай бұрын
Vote for chilima. He is suitable to run Malawi
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 2 ай бұрын
Amugulatu ameneyo.
@PeterPhiri-di1ux
@PeterPhiri-di1ux 3 ай бұрын
tikuvutika chilima yo ali muboma wtat is he doing 2025 never apm my vote
@MonicatimanyeShaba
@MonicatimanyeShaba 2 ай бұрын
Zoona zake ndizoti SKC amawona mwakuya kwambili Koma AMENE amakhala pachiwongolero amawona mozikundikila nichifukwa Chale zimawa vuta kuwongolelawazelu zikoli NDE osewo poti wakuwona mwakuya azingo khalila kulawa boma kulitaya kulawa boma kulitaya kamba ka mutima woti zosendipanga ndekha pawekha sungakhale munthu vayisi amamutenga Kuti alibe zelunthawizose komandamene angathe kukuwonesa pomwe Pali choipakuti usapitepo
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 3 ай бұрын
Aaaa opusa ndi inu nonse omwe mukunenazo za adad anali kuti?? Komanso agogo ngati amene aja mukufuna muziwapangira zochita lomwe paja ndi akhufu Kumve ndakhulupilira SKC my vote ❤❤❤❤❤
@JoyJere
@JoyJere 3 ай бұрын
Bola adad
@user-mv6tn3qv8v
@user-mv6tn3qv8v 2 ай бұрын
That's true
@KellyHart-pi4hd
@KellyHart-pi4hd 3 ай бұрын
Inu mutirakwitsa kurankhura Ngati mutumo mulibe nzelu ingokharani muzizikanda ndi Chilima wanuyo
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 3 ай бұрын
Mkufuna ya ufa muuzen akupasen bas osataya nthawi yanu kumat chilima chilima
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 3 ай бұрын
Good Message ❤
@NathanielNthala
@NathanielNthala 3 ай бұрын
He is saying the truth.
@HanifiYaumu
@HanifiYaumu 3 ай бұрын
Iweso machende ako ndichilima wako emweyo iwe sudziwa kuti chilima ndiamene adapangitsa kuti tidzivutika choteke mapazi ako galu wachabechabe
@MuhammadSauzand
@MuhammadSauzand 3 ай бұрын
Umutenge chilimayo akakhale president ku family yakwanuko
@greychizaka4088
@greychizaka4088 3 ай бұрын
SKC vote
@KellyHart-pi4hd
@KellyHart-pi4hd 2 ай бұрын
Izizi ndiye mbwelera zenizeni mtsogoleli samafunika kuyanganira zoputsa Ngati Chilimayi ,Ameneyi ndimanyaka enieni osayesera gys tizalira Ameneyi azizangoramulidwa ndi Azungu Ngati Chakwera emweyi ,Ndiposo iyeyi akanakhara wanzelu sakanalora Kuti pamgwiluzano wawo iyeyi akhale otsatira wachakwera coz iyeyi anakharapo vaice Chakwera palibe chomwe amadziwa chilichonse Koma anakwanitsa kumupugsitsa iyeyi ndikutheka ndiye nzelu zake Za Ameneyi zilipati ?Osayesera mbwelera zimenezi kurankhura amatha Koma kuchita zinthu ndipanja penipeni
@emmanuelmpenda2673
@emmanuelmpenda2673 2 ай бұрын
Massive
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t 3 ай бұрын
Hehede uru kuno , malo mopemphera tikungolalata anzanutu zikavuta amapemphera ife maromopemphera tikungolalata God have mercy on us
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 ай бұрын
Chilima ndi chakwela akumadziwana ,akufuna azitipusitsa ifeyo
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 3 ай бұрын
ntchito ya chilima inatha anali oyitanira bus itazaza ntchito yake inatha musataye nthawi yanu zachilima amene uja watha basi
@andrewchirwa2193
@andrewchirwa2193 2 ай бұрын
Vote saulosi chilima
@Patrickmanyozoproperties
@Patrickmanyozoproperties 2 ай бұрын
Chilima emweyo basi ife taona kuti chilima amaopedwa that's why akumpangira maupo
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 3 ай бұрын
Chilima ndi amene anapangitsa kuti MCP ilowe m'boma tinada nawo kukhosi mukuchemerera yo zao ndi zimozi ndi MCP
@ChristopherPhiri-xq7hv
@ChristopherPhiri-xq7hv 3 ай бұрын
Chilima mukunenayo mesa ndi part of government , and palibe chanzeru chomwe akuyankhula. Palibe chanzeru akuchitapo
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q 2 ай бұрын
Mbava zili mu dpp n mcp sizamasewera chilima akumuchitira nkhanza chonchi cz both mcp n dpp akudziwa kut he is the future of malawians and azawasosola bt aziwe kut mcp n dpp these two sangalowe m'boma without skc izi aziwe n dziwani kut dpp n mcp kwao kwatha
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
Inutu mukunama chilima ndi chakwela onse ndi wolephela balibe mungauze amalawi inunso ndi chitsilunso cha munthu mmulibe manyazi mmutumo mwazaza mamina mbuzi yamunthu mukutitenga ife amalawi ngati opusa agalu amenewa sitikwafuna inuyo pwala lanu chitsilu
@WilfredMathews-yl6ij
@WilfredMathews-yl6ij 3 ай бұрын
Ndipo sukunama chilima alindikuthekera kolamulira coz iye ntchito zake sitidazione
@MatSecurity-gq3hr
@MatSecurity-gq3hr 3 ай бұрын
Timpatse mpata, Zoonadi onse tawayetsa uyu mfundo mzake sizinagwileko Ntchito payenkha, ubwino wake Ndi 5yrs, tizithothola
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 2 ай бұрын
Mufune musafune, Saulos Chilima alamulira. A DPP ambiriwa akuwona kuti Mutharika wakula, akufuna adzidzamubela ngati m'mene mwana akamakhala ndi agogo, amangokwabela nanga simunthu wamkulu. Nawonso a DPP akufuna m'dalayu adzidzangomubela, plz Malawians be careful.
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 2 ай бұрын
A Samuel muli ndi misala,yanuyo singawine.
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 3 ай бұрын
Zaziii
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 3 ай бұрын
Chilima ayankhulatu nthawi ilipo paja munamusemera nyau nde akudikira chiweruzo koma ayankhulatu ndipo kwa munthu Wa mnzeru zake kupatula wa nkhwizi ufiti ukhutukumve chilima is a best kuyima utsogoleri wa bwino olo Chakwera amadziwa kuti mwanayu ndi machine komanso first year zinthu zina yenda bwino becoz of that man Mr Rwara never give up ❤❤❤❤❤
@chimwemwegama6143
@chimwemwegama6143 3 ай бұрын
Pantumbo panu nose zikoli lagwa chilimayo ali kuti,minyero zanu agalu,,,tikuzunzikaku ife pa ground pano
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z 2 ай бұрын
Mbava ngati amene
@aubreytiyess
@aubreytiyess 3 ай бұрын
Aaaaa. UTEM2025❌❌❌
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Iwenso agogo kunyumba kwako
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 3 ай бұрын
Uyu ndichophwisi chencheni iyaaaaa mesa akulakwisira limodzi
@WysonMpatama-cv1mc
@WysonMpatama-cv1mc 3 ай бұрын
Eeeti akuononga onse palinso nkhani ap
@mphatsobonongwe8131
@mphatsobonongwe8131 3 ай бұрын
Dzina lanthu lioneni sitiopa , chilima patsogolo
@NelsonNyasulu
@NelsonNyasulu 3 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkk
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba 2 ай бұрын
Misala imayamba chotcho ndiye chonde abale ake amunthu uyu pitanayeni kuchipatala munthuyu ndiwodwala
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 ай бұрын
Zachilimaso pano sitikufuna ochenjela mwautsilu
@user-rj7qv8xk5c
@user-rj7qv8xk5c 2 ай бұрын
😢Osafooka thawi ilipo
@user-zg7iw8kq4r
@user-zg7iw8kq4r 2 ай бұрын
Ngati malawiyi ili ikuona mavuto ali panowa nchifukwa cha ameneyi
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 ай бұрын
Anatiponya pa moto pano wangoti ziii
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 3 ай бұрын
Analikut nthawi Yonsei Mesa anali ku Malawi komweko ndikumaona mmene anthu akufera ndi njara
@andykunyenje529
@andykunyenje529 2 ай бұрын
Lwala umwa chani aise
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 3 ай бұрын
I do understand anthu amene akumamulakhulira chilima ngati iyeyondimwana bwanji if chilima is not happy where's he should come out and speak out himself and I'm not support any of these guys ndikati ndadya ndimayenela ndigwiletchito ndekha
@user-gs9vr1lc9d
@user-gs9vr1lc9d 3 ай бұрын
Wakupatsa zingati chilimayo, galuiwe
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 3 ай бұрын
Kkkkkkk kusauka ndi ukapolo
@arnoldchikopa2611
@arnoldchikopa2611 3 ай бұрын
Chilungamo ichichi
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t 3 ай бұрын
Abale tisalire timatitu zinthu zisinthe oipatu ndi adadi abusa ajanso aipa lero kunokuno kumalawi zationekera kkkkk abusa abale musawatero mumawavotera nokha komanso munampanga chipongwe mwana wayeni komanso munampanga Peter chipongwe Mulungu wakwiya mulape apo bii tidakanzunzika.
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 3 ай бұрын
Ndilipo mulungu akhululukile ndithu
@AustinZidanaNessam
@AustinZidanaNessam 3 ай бұрын
Go to Limbe eeesh town yayipa mikodzo yokhayokha , pple are building in drain filing drainage , minibus parking everywhere aaaaaa zinthu zachita katondo
@WysonMpatama-cv1mc
@WysonMpatama-cv1mc 3 ай бұрын
Alwara kupole moto ndachilima anuwo
@DanielnachanzaBanda
@DanielnachanzaBanda 3 ай бұрын
Ukunena iwe
@user-cf9yz3ei5o
@user-cf9yz3ei5o 3 ай бұрын
Our economy collapsed sometime back I don't know how malawians are failing to see that
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l Ай бұрын
Chilima is right president of Malawi
@charlesdaisi616
@charlesdaisi616 3 ай бұрын
Koma nkulu iwenso kkk ziko lake liti ukuuza anthu okufaa kapena chani?
@RICHARDENIFANT
@RICHARDENIFANT 3 ай бұрын
Zoonadi
@HurryBeston
@HurryBeston 3 ай бұрын
Icho ndie chilungamo baasi nkhakhale anthu ena saavomereza
@NathanielNthala
@NathanielNthala 2 ай бұрын
Khokhokho
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 3 ай бұрын
Ndiponso mudziwe akulamulira dziko lino si chilima nde akufunika ayesedwe basi
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 3 ай бұрын
Chilimayo akalamulire kunyumba kwa iweyo Lwara
@phirimacdonald8638
@phirimacdonald8638 3 ай бұрын
Akulu awa ndiopusa, wakupasani zingat chilimayo munthu wakuba ngt amenewo lero tili pamoto chifukwa Cha ameneyo chilima,ndiye bola atupeletu kapena peter osati onamayo
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y 3 ай бұрын
You can said that again brother Lerolino anthu akulira chifukwa chaboza la Chilima ndi mzake Chakwera anthu oyipa kwambiri amenewa Ndiponso akufunika adzamangindwe atizumza kwambiri
@homeremedys3748
@homeremedys3748 3 ай бұрын
Born kalindo wayamba mantha kuyankhula koma enafe sitikuopa
@ZelinaKisswell
@ZelinaKisswell 3 ай бұрын
Alankhula bwanji munthu Ali mndende 😮
@UlemuChimembe
@UlemuChimembe 3 ай бұрын
Nonsense
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
alibe funding yet boma likungogawa ndalama ma 150 &700wat nonsense
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
Chilima ndi chakwera wose ndi amodzi ndi mbamva zokhazokha musatipusise ife ngati akupasani ndarama zingodyani Koma mission yanu siyigwira tatopa ndi mbamva zimenezi iesh 🤮🤮
@homeremedys3748
@homeremedys3748 3 ай бұрын
Samuel Lwara Pachiphwisi Pamako Mwana Wa Hule iwe, Chilima wapanga chani? Zomwe analonjeza zikuchitika? Pantumbo pako, Chilimayoso Pantumbo pake, Zitsilu
@WakuMalawi
@WakuMalawi 3 ай бұрын
I have a tough time accepting Chilima as the next guy. He's been a part of Tonse Alliance for years. He is going to continue the mess Chakwera has started.
@carlossadimba595
@carlossadimba595 2 ай бұрын
He is just a sign post .....which shows Lilongwe 20 km but actually it doesn't go to the location .....achina mkaka they are digging holes there for him
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 ай бұрын
bodza chilima yo bola APM bola
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 3 ай бұрын
zaziii chilimayo akawinira kunyumba kwako iwe mbulundi
@PheladiMafologela-ii3vd
@PheladiMafologela-ii3vd 2 ай бұрын
Khala chete ukutisokotsera
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 3 ай бұрын
Zake izo bola ali kunja
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 3 ай бұрын
Keep it up Lwara, boma la chakwera ili latikwana, walepherela.
@EstherJamesChipembere
@EstherJamesChipembere 3 ай бұрын
Achilima tili pambuyo pawo koma aime paokha achoke ku mcp
@arnoldchikopa2611
@arnoldchikopa2611 3 ай бұрын
Skc mote
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t 3 ай бұрын
Hehede bora adadi ikaora modzi zonse zaora onena amati ,not again😅😅😅😅😅 lero tikukanika malo mopita kukanani tikupita kwapharaoh kkkk
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 3 ай бұрын
Nde chilima mukuona ngati angayendetse dziko? Popeza zawo ndi dzimodzi nda pule ngati akuzengedwa mulandu okuba ndalama nde angatsogolere dziko ameneyo? Kaya mwina
@tasmania527
@tasmania527 3 ай бұрын
Ngati kuli mtundu wasankho ku Malawi ndi Alomwe, oh ya. Ali ndi unjustified hatred ndi Chilima for no reason. By the way, Lwara walakwa chani?
@AmoniNicholas
@AmoniNicholas 3 ай бұрын
Mmmm Abwezi mtsogoleri akhoza kukhala ochilimika, koma ngati ifeyo Amalawi azanga tangokhala manja lere, ukhozakukhala iweyo wazeru ukuyakhulawe koma patsogolo pano uzachititsa manyazi Amalawi ife ngati mmene anachitila bon kalindo iwe, ndiwe wabodza kwambir
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 3 ай бұрын
Chilima ndi Chàkwera ndi olephera okhaokha
@user-ib7ig3xd2h
@user-ib7ig3xd2h 3 ай бұрын
Mukutaya nthaw wakubayi sangawine😢
@ShadreckKusani-vi5ki
@ShadreckKusani-vi5ki 3 ай бұрын
Zoooonazake Dr chilima akufunika bomali atsogolele zisintha,,umboni ndili nawo,tonse italowa chilima anayamba kuyende ekha mdzipatala ku MRA koma zitamveka anamuletsa, atalamulila zitha kusinthadi
@KellyHart-pi4hd
@KellyHart-pi4hd 3 ай бұрын
Inuso inu musamangomvera zilizonse Kuvotera Chilima ndiye bora kumutsiya razalo emweyi ndiagalu awa saziwa chilichonse
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 3 ай бұрын
Kulankhula sikuvota ovata ndi amalawi zachilima wanuyo munyera sua
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 3 ай бұрын
Za nzii
@user-te3ps3kf2t
@user-te3ps3kf2t 3 ай бұрын
What you are talking it's not true ,chilima ndi mmodzi mwaiwo amene Waikato pamavuto malawi chifukwa cha bodza lalikulu,kunamiza mtundu wa a malawi,anakakhala kuti tili ndi mwayi ife amalawi Olira kuno ku south Africa ndinakalanda ndalama zonse za chilima mkugulira chakudya ,mankhwala,komanso kupeleka ndalama kwa mahakazi kuti atsegule ma computer mmene muli information yonse why mukuikila kumbuyo munthu amene Waikato pamavuto amalawi,komanso a Mtambo anthu amene mwathandizila kuika amalwi pamavuto,timakudandaulani kwambiri.
@user-cf9yz3ei5o
@user-cf9yz3ei5o 3 ай бұрын
Yes Peter is just too old let him rest
@AubreyHara-lh9md
@AubreyHara-lh9md 3 ай бұрын
You are talking too much because you were booted from the current government
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 3 ай бұрын
Iwe choka ndi chilima wakoyo ngati wamudyera udzabweza
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 2 ай бұрын
Zaziii
@ShadreckNgozo-ng6ll
@ShadreckNgozo-ng6ll 3 ай бұрын
Kunyumba kwa makotu
Ku Convention Ya DPP Ndikayima Nawo - Country Man & The Uncle
20:18
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 18 М.
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 20 МЛН
MEGA BOXES ARE BACK!!!
08:53
Brawl Stars
Рет қаралды 36 МЛН
ROCK PAPER SCISSOR! (55 MLN SUBS!) feat @PANDAGIRLOFFICIAL #shorts
00:31
Zifukwa Zomwe Zingapangitse MCP Kuchoka M'Boma - Concerned Citizen
11:18
Dziko Lafika Pa Mwana Wakana Phala - Bon Kalindo
14:16
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 13 М.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH JOHN KAPITO
1:09:21
Zodiak Malawi
Рет қаралды 23 М.
KU HOT CURRENT KWATENTHERATU
25:02
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
Alfa Imam gba iyawo Oba ni ilu Ogbomosho
24:24
Tani Olohun
Рет қаралды 1,7 М.
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 20 МЛН