TULANI PANSI UDINDO

  Рет қаралды 37,004

Yathu Music Official

Yathu Music Official

Жыл бұрын

Yathu Music Official

Пікірлер: 118
@JohnThomas-fo8jb
@JohnThomas-fo8jb Жыл бұрын
Koma munthu waimba bwino uyu, kip it up, osamaopa pa chilungamo
@stevinmuhone877
@stevinmuhone877 Жыл бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💃💃💃💃 vuto lake anthu awa sizikuwakhunza or tingayankhure motani mmmmmmmmm
@CalistoZidanna-kj2st
@CalistoZidanna-kj2st 11 ай бұрын
Yes !!!this is good music and iyeyo akuyenela ayivere b4 3 hours
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
More 🔥🔥 ndimomwemo basi ananenadi
@user-dn5sf3md5t
@user-dn5sf3md5t 3 ай бұрын
KOMATU WABAYA MWANA WELL DONE APSE NTIMA ZENIZENI GALU KWABASI CHAKWERA ANLONJEZAYEKHA ATULEPANSI UDINDO EYAAAAAAA GALU KWABASI NDI BWEREZASO CHAKWERA NDI GALU MBUZI YA MANU PANSI
@josephncekane4567
@josephncekane4567 Жыл бұрын
He sang the best ever song with sense n strong messege. I'm sorry to say this but this government they all Mbuzi I repeat they all Mbuzi, they have not even single feeling of willing to save the people of Malawi
@IshmaelKamwana-sv6bo
@IshmaelKamwana-sv6bo 9 ай бұрын
This is nice songs agalu amenewa tatopha nawo
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 Жыл бұрын
Tiope ndaninso!!!!Chilima ananenakale #OSAOPA.
@ibrahimatibu8784
@ibrahimatibu8784 Жыл бұрын
Akulu wakulu aku malawi koma kuba katundu wa anthu ovutikanso chakwera ndi mwana sakuziwa kathu bola Peter mutharika uja kusiyana ndi izi mbuzizi
@user-ws1eo3rc7l
@user-ws1eo3rc7l 3 күн бұрын
Yomweyo galu iwe 😅
@MourinhoJabur
@MourinhoJabur 21 күн бұрын
💥💥💥💥💥 chilungamo
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 4 ай бұрын
Koma angatule panopa sakugona kufu funa njila yoti adzabele ma voti koma Muthu mmm ayi ndithu m,busa wa satana
@ayandajack6019
@ayandajack6019 Жыл бұрын
Mmmmmmm muli uthenga munyimbomu I respect u bro .
@user-td5yb3cw7u
@user-td5yb3cw7u Жыл бұрын
Lulululu malawi wanga akumbuse ndithu amati azasiya udindo
@user-qe2lz7mx7u
@user-qe2lz7mx7u 4 ай бұрын
Man muyimbenso lilikuti ziko yalucias bandana kapena life
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes 10 ай бұрын
Yaar nice musice osamuda zinthu Mene zilili
@PeterThomas-lw3io
@PeterThomas-lw3io 24 күн бұрын
Yomweyo kuyipatsa Moto Chakwerayo abowoke mmimba sazawinaso galu wakupha Mpheketsela zake Zamuwonongela Mbili
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon 2 күн бұрын
❤❤❤
@hamidaakimu4188
@hamidaakimu4188 Жыл бұрын
Zomvesa chisoni momwe anthu akuvutikira ndi njala, ambuye chitanipo kathu zithu sizili bwino
@IssahAluba
@IssahAluba 5 күн бұрын
Chimuthu chopanda nzeru koma kugokakamira paphando
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 21 күн бұрын
Good Messnge Chakwela you mast go
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 24 күн бұрын
Ndaimvera mobwerezabwereza😂
@SAULOKANJINGA-fc6ir
@SAULOKANJINGA-fc6ir 4 күн бұрын
👍👍
@rasulmaulidi2224
@rasulmaulidi2224 4 ай бұрын
well done boys..
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 3 ай бұрын
Good music with full of msg tonse did nothing but taking malawi to bagamoyo😢
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
Waimba nyimbo imeneyi mulungu amusogolele ndipo aimbeso nyimbo ina yoposa pamenepa ... Mbuzi zonsezi zimve zenizeni zeni
@enerstntakhala4679
@enerstntakhala4679 Жыл бұрын
Ndithyole dance koma oimba uyu anaganiza
@chimwemwe2
@chimwemwe2 Жыл бұрын
They should not be intimidating you because its the people that gave them power and thy are now abusing the power by mistreating the same people that gave them power. Keep speaking for the voiceless brother 🙏🙏🙏🙏🙏 I love it❤️
@phillipkapata3790
@phillipkapata3790 Жыл бұрын
Kkkkk ndipo ikuvinika guys🤣🤣🤣🤣
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 10 ай бұрын
Nyimboyi ili bwino kwambiri 100% ndipo a Malawi pakufunikanso osaopa, osagona tulo ndikuzunzika chifukwa cha magulu ena a wanthu azinyengo, akuba, ozikonda ndi akupha
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 19 күн бұрын
I'm feeling sorry for people who are in Malawi things are not good on the ground tingotchona mu Capetown
@fridaygonela
@fridaygonela 22 күн бұрын
IZI ndizoona waimba zoona titsatile sadick Mia ndi achilima
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Ай бұрын
Kkkkkkk iwe wayimba bwino wava ndipo usaope ayi pitiriza man
@angellasamuel8186
@angellasamuel8186 Жыл бұрын
Koma guys alusonu tamati fikisilani mauthengo ndipo musamaope akufuna azitiopseza akapolowa mphenvu dyera Ku nthiko
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 17 күн бұрын
Apo wayiska sum iyo
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Жыл бұрын
Powerful!!!! Very nice Song
@IsakyIsak
@IsakyIsak 2 ай бұрын
Nyimbo yayimbiwda bwino zedi
@user-oc8xu5co8y
@user-oc8xu5co8y 6 ай бұрын
mwatiimirira kumuuza m,busa onyengayo komaameneyo amaziwakuti azamwarira
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Жыл бұрын
Ngakhale akukusaka big koma unaimba boo yes
@gizzykondwani865
@gizzykondwani865 23 күн бұрын
Mwaphatu sound makani
@tingoalex6478
@tingoalex6478 Жыл бұрын
Very nice song keep up asakuopseze ai
@AnusaNkhoma
@AnusaNkhoma 13 күн бұрын
100% boy
@user-yo6ql5co1f
@user-yo6ql5co1f 4 ай бұрын
Ipase moto bgy
@moyo77777
@moyo77777 Жыл бұрын
Nice music brother aziva
@imuranmkwanda9669
@imuranmkwanda9669 Жыл бұрын
Very nice song and it has come at a right place and right time this time around not in 2002🔥🔥🔥🔥
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 3 ай бұрын
Chakwera and his mcp dictatorship tonse alliance must go
@Rose-tr6pn
@Rose-tr6pn 3 ай бұрын
Ukuyimba bwino kom upange chako tune, ukuba luso la Billy ndiy akusaka mpakana akuthila dzigwe before aweek
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 Жыл бұрын
Msembe Yanga izakhala apule Kwa Yahweh
@VeronicaMarten
@VeronicaMarten 9 ай бұрын
Muiponye palipose averebe
@martinjames5639
@martinjames5639 Жыл бұрын
Sadalakwitse kuimba nyimbo iyi Zili bho
@HelenMachanya-ip7zv
@HelenMachanya-ip7zv 9 ай бұрын
Nyimboyi si ya Billy kaya anayimba ndindan.....akusiyana mawu
@davidlinerevelation3427
@davidlinerevelation3427 11 ай бұрын
I cried after listening to the song
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
Mbuzi zenizeni zogona kunja ........ Mabongwe
@luciascharles4345
@luciascharles4345 Жыл бұрын
Nice one big up
@preciouseInussah-lh6oz
@preciouseInussah-lh6oz 9 ай бұрын
Ipatse moto
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
Tinasukusula pano amalawife. Makapewa akuona ngati dziko la Malawi ndi la agogo awo kapena la makolo awo, totopa nazo izi
@nellikkmwenda7087
@nellikkmwenda7087 Жыл бұрын
WaaaaaaaaaWoooooooooo zuka malawi atule pansi udindo
@user-bh7ns3rq1v
@user-bh7ns3rq1v 3 ай бұрын
Zilli boh atule basi zamuvuta!
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 14 күн бұрын
Nice song 👍
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
He is best musician in Malawi
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 ай бұрын
Bravo❤❤❤
@NankafumbweJames-cw7vu
@NankafumbweJames-cw7vu 11 ай бұрын
Nyimbo ya mphavu ngati iyi imachedwa pati
@user-ye8tt9tu4t
@user-ye8tt9tu4t Жыл бұрын
Nyimboiyi sanayimbendibilekaunda komasosanayimbebwino
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 19 күн бұрын
Anatule udindowo simuli gondolosi mumpandomo
@kaisimaidankota9023
@kaisimaidankota9023 Жыл бұрын
Anakwera bwino kkkkk azaona zotsatira
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Жыл бұрын
The original song is massive
@adini2919
@adini2919 Жыл бұрын
Very nice song 🌟
@bizwickmbwindinga9751
@bizwickmbwindinga9751 Жыл бұрын
Yomweo waitha kuwakumbusa agaluwa ailtikwana kwambili
@aleksawilliams710
@aleksawilliams710 Жыл бұрын
Odi ndivine ine💃💃💃💃💃💃
@mphatsoyakobe1557
@mphatsoyakobe1557 Жыл бұрын
Ili Mwala eeeeee km ndiye wabayatu iweyo ukufunika kukupasa inayake bas
@ibrahimatibu8784
@ibrahimatibu8784 Жыл бұрын
I like the song
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 4 ай бұрын
Mumantha inuyo
@user-bs5fk5rd2n
@user-bs5fk5rd2n 10 ай бұрын
Nice song 5:48
@stewartgodfrey2336
@stewartgodfrey2336 Жыл бұрын
mbudzi idzi
@user-nd4gh1fi5q
@user-nd4gh1fi5q 5 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉
@user-ye8tt9tu4t
@user-ye8tt9tu4t Жыл бұрын
Waipitsambili yabilekaunda
@gifomusik8241
@gifomusik8241 Жыл бұрын
This voice must be junior k
@mzaminphili8550
@mzaminphili8550 Жыл бұрын
Unaitha udzi bwela bwela.
@happycow1227
@happycow1227 Жыл бұрын
KUSWA KUSWA
@StainGondwe-bq1cg
@StainGondwe-bq1cg Жыл бұрын
Nice
@shadrecknamvula4381
@shadrecknamvula4381 Жыл бұрын
Much respect guys
@grantmphamba6772
@grantmphamba6772 Жыл бұрын
Mr hanifa Nanu wosangoyamikira bwanji tikunven nyimboyi ili boh komanso ndizachidziwikile Kuti si Billy Kaunda yi
@user-ye8tt9tu4t
@user-ye8tt9tu4t Жыл бұрын
Waipitsambili yabilekaunda 6:39
@hassanmussa5205
@hassanmussa5205 Жыл бұрын
Amayichotsa pa chanel pawo aja amaona ngat alinayo okha, nice hit
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 Жыл бұрын
Kkkkkk Koma ndimposooo agwa nayo
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
Ndikupezekaso kuti fertiliser kundulisaso mbuzi zimenezi sukufuna ziphe mtundu wa amalawi
@mlezanyirenda2815
@mlezanyirenda2815 Жыл бұрын
Good song
@robertnkhoma5776
@robertnkhoma5776 Жыл бұрын
Dandaulo limveke😭😭
@alihibrahim
@alihibrahim Жыл бұрын
Obviously
@YusufuUsumani
@YusufuUsumani 24 күн бұрын
apano mutuala udindo
@lewisbonongwe8518
@lewisbonongwe8518 Жыл бұрын
Umatha ayise ndikanakuziwa ndika naku pangira order pa Mukuru 1000 rands
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 24 күн бұрын
Bola akanalonjeza kut tidzamudule mutu akakana kupanga resign Km mutuwo tikanadula ? 😅😅😅😅 MCP WOYEEE😅
@user-zv1so2pd7u
@user-zv1so2pd7u Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂💯
@jagudanicolas5436
@jagudanicolas5436 Жыл бұрын
Or chakwerayo wa ikondaxo atule pansi basi
@africulturetv6498
@africulturetv6498 Жыл бұрын
True cry
@lamulatusaiti7581
@lamulatusaiti7581 Жыл бұрын
Inu zoona chimanga kugula anthu pa mpaka k 25 000 thumba limodz chimanga chomwe chimagudwa k 4000 kapena k 5000
@bilalikamwendo1629
@bilalikamwendo1629 Жыл бұрын
Odiiiiii ndijaze ine 💃💃💃💃💃💃💃💕💓💓💓💓 Chakwela atule pasi udindo waulephela komaso akadulidwe m.jando kut adziganiza dzabwino🤐
@user-ic4qi7yy5l
@user-ic4qi7yy5l 11 ай бұрын
Koma zongo paikana izi kuti aziti nyimbo iyi waimba ndi Billy kaunda pomwe wina wangotenga instrument ya billy yagalatiya koma voice yaleka naso Billy akaimba mau amaveka ngat alindichifine koma awa ati ayesere zawakanikaso!!
@bilalikamwendo1629
@bilalikamwendo1629 Жыл бұрын
Iiiiiii muthuyu waimba bwino kwambili Bola asamusake namabwalayu kut amphe pajatu chipqni ichi chilibe chison ndikupha athu Ndikusavinidwa kwachakwela pamenepo amusaka
@thomasshabalala7999
@thomasshabalala7999 Жыл бұрын
Is true
@omarcharlie5247
@omarcharlie5247 Жыл бұрын
Zoona atule basi mwayitha man mix yanu
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 Жыл бұрын
Bola amva basi chakukhosi chatiphwa ife ndipo nyimbo ikumveka mwauzimuzimu kuli kulira Kwa amphawi 🤐🤐🤐🤐🤐🤐
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 35 М.
Skeffa Chimoto Apresident new Audio Official
8:35
Yathu Music Official
Рет қаралды 167 М.
Самое Романтичное Видео ❤️
00:16
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 4,6 МЛН
Жайдарман | Туған күн 2024 | Алматы
2:22:55
Jaidarman OFFICIAL / JCI
Рет қаралды 1,7 МЛН
ОДИН ДЕНЬ ИЗ ДЕТСТВА❤️ #shorts
00:59
BATEK_OFFICIAL
Рет қаралды 9 МЛН
МАМА И STANDOFF 2 😳 !FAKE GUN! #shorts
00:34
INNA SERG
Рет қаралды 4,7 МЛН
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Billy Kaunda Agalatiya
6:47
stevechikoka
Рет қаралды 155 М.
Zamanyazi mukafukufuku  wanimfa ya saulosi chilima
5:45
Nthambi Malawi
Рет қаралды 14 М.
Dan Lu - Tulani Pansi - Official Music Video
3:27
Dan Lu
Рет қаралды 248 М.
Mbiri ya Dr Bakili Muluzi PART 1
15:16
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 89 М.
UNDIKUMBUKE - Thomas Chibade
4:47
ZAMAKEDZANA
Рет қаралды 51 М.
MR ZEMBANI
11:29
TEAM ENTERTAINERS MW#
Рет қаралды 60 М.
Самое Романтичное Видео ❤️
00:16
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 4,6 МЛН