Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu

  Рет қаралды 43,286

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

Zomwe Wayankhura Patricia Kaliyati Zadabwitsa Anthu

Пікірлер: 247
@omarajibu860
@omarajibu860 2 ай бұрын
Pepani mayi, your time is gone. You are all failures. Now is time for DPP, UDF and AFORD. Enanu mukagwere.
@EllenLuwanika-tl5ck
@EllenLuwanika-tl5ck 2 ай бұрын
Dpp uDf AFoRD my vote
@chiluzbandah
@chiluzbandah 2 ай бұрын
Aah thawi ya Dpp inatha
@EllenLuwanika-tl5ck
@EllenLuwanika-tl5ck 2 ай бұрын
@@chiluzbandah mukunama
@chiluzbandah
@chiluzbandah 2 ай бұрын
@@EllenLuwanika-tl5ck tiyeni tidikire
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 2 ай бұрын
Anthu ena anangobadwa opanda manyazi ndikuyankhula.komanso anthu ena timasowekera wisdom from God kumangosatira zilizonse.zoona anthu omwewa ndiomwe anatipusisa leronso tikuwasatilanso bac atimbwititseso?koma aliboma momwemo palibe chomwe akupanga ndiye anthu opanda uzimu akuwatsatilabe komanso adzazivoteranso zitsiluzi.
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Chonde amalawi, amzanga osaononga vote kamba kokuti akukunazani ndi ma ti shet kapena msalu musamale.
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Zatha nfundotu, mungobweleza za kale mumawanamiza amalawi zija. Kuatengela amalawi ku mtoso basi. Olo manyazi mulibe.
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 ай бұрын
Tachionereni chikuyankhula ichochi apa manyaz bwanj isa upusa bas
@JasonJackets
@JasonJackets 2 ай бұрын
Mmzimayi oipa manyazi alibe garu wen wen☝️
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 ай бұрын
Mmmmmm ayamba kunamanso koma amalawi tikamvera izi ndife omvetsa chisoni
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 ай бұрын
Uyu adameza memory card eeeee!!! Wayambapo Zonama zakezija.
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Wazipeza zitsilu Ku chiladzuluko, osakuthamangitsa?
@hmshohagshohag9483
@hmshohagshohag9483 2 ай бұрын
Palibe chanzeru mukukamba inu, Chakwera anakupeperesani kale apa Chilima wanuyo azamuvotera ndi ambuyake .kodi a Amalawife mumatitenga ngati zitsiru eti
@user-hy4el8ov1l
@user-hy4el8ov1l 2 ай бұрын
Muthu wandale ndi satana lero akubwela ndi boza 😂😂😂
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Huleyutu wayamba Tikuthamangitsatu ndi maduka, Usamale hure iwe.
@user-rd8vw1pc4b
@user-rd8vw1pc4b 2 ай бұрын
Chitan manyazi akwen 😂😂😂
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 2 ай бұрын
Zaboza zokhazokha eshii amalawi ndiyeno mukusekelela mmmmm
@omarajibu860
@omarajibu860 2 ай бұрын
Bodza la 2019/2020 lija mwayambiranso? I don't know what you guys gonna say this time. You can't fool a Malawian again, your time is over.
@mustafailanga2585
@mustafailanga2585 2 ай бұрын
Akaliati zauhule basi kuyela kogulako mbudzi yamunthu zausilu basi ndi galu wakoyo chilimayo
@user-hy4el8ov1l
@user-hy4el8ov1l 2 ай бұрын
Akuti nsomba zikaola mundengu nde kuti zonse zaona awa asatimize ayi zisilu zaathu
@user-hy4el8ov1l
@user-hy4el8ov1l 2 ай бұрын
Akwafusa athu kuti kondi simumadya kawili akuti zimene zija zodya kawili zo zinali za UTM akuti kasala kamozi komaso athufe timangosekelela zilizonse
@umalimaganga
@umalimaganga 2 ай бұрын
Chilima 2025 BOMA lanyowani
@umalimaganga
@umalimaganga 2 ай бұрын
Chilima 2025 BOMA lanyowani
@user-rd6zo8ry2d
@user-rd6zo8ry2d 2 ай бұрын
Mai opanda nzeru uyu kuwatenga amalawi ngati opusa eti
@user-pl6it7zc7c
@user-pl6it7zc7c 2 ай бұрын
kuonera live from south Africa mumakwana more fire
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Kodi kaliati uwe ndi munthu kapena chidzukwa muudze chilima anyamule thumba lafertilizer lija ulibe nzeru chilima wakhala akunama pano angamumvere ndani mbavayo okuba ndi sattar
@StanziaElias
@StanziaElias 2 ай бұрын
Mayi mulungu akukhululukileni kwambili koma ndili ndifuso kuti inu mumapemphela?
@MaliGomani
@MaliGomani 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂Koma mbuzi Izi akatero awanamize anthu kena
@user-qe2lv3hs8q
@user-qe2lv3hs8q 2 ай бұрын
anthu andale ndinu oipa inu mulungu azikukhululukilani 100% tikuvutika chifukwa cha anthu andale inu
@HarryRefred
@HarryRefred 2 ай бұрын
😂 zazi palibe chomwe ukukamba pamenepo 😂😂😂😂 kagwele uko
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 2 ай бұрын
Manyaz mulibe mai nd chilima wanuyo kagweleni uko
@user-yk3wc9ei5g
@user-yk3wc9ei5g 2 ай бұрын
Wasowa chonena ameneyi.
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 2 ай бұрын
😂😂😂Sewelo latikufelanji anthu abodza awa
@lloydmalinga1198
@lloydmalinga1198 2 ай бұрын
saulo Ali muboma chipanga iye ndi chani chanzeru.
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 2 ай бұрын
Nzeru ulibe iwe sukuona adayimisidwa ntchito kuti ngwa Kuba, ndipo wakhara asakulamura nawo, pano mwina poti akuti milandu isapitilire umboni alibe siolakwa
@phirimacdonald8638
@phirimacdonald8638 2 ай бұрын
😢tachokani okuba inu ,mumubelenso ndani mmanyamula thumba la fertilizer paphewa palibe mwachita inu
@Ferguson-Mdaka
@Ferguson-Mdaka Ай бұрын
​@@phirimacdonald8638Chilima wasn't given a chance to work. You know, and are a witness, to that. Think
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 2 ай бұрын
Mai opanda nzeru akuwatenga amalawi ngt zisiru,
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n 2 ай бұрын
ife pambuyo pa adadi osati onamawa ,achilimaso ndi kape anali kuti
@samsonphangire1523
@samsonphangire1523 2 ай бұрын
Akweni yokhayi yodya katatuyi Akweni sigwira ataaaaa or pang’ono kkkkkkkkkkk!
@StanfordGoda
@StanfordGoda 2 ай бұрын
🎉bodza bodza bodza koma ulibe manyazi.
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 2 ай бұрын
Takambani zina, ndiye poti amalawi ambiri tinapoila sitimadziwa chomwe timafuna boza la 2024
@FrankKambwani
@FrankKambwani 2 ай бұрын
Ufiti ulipodi ku Malawi 😢😢
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 2 ай бұрын
Manyaka weniweni🥺🥺🥺
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo 2 ай бұрын
Mai oposa iwe wasowa chonena watokhuta
@user-ow3tp3vu3c
@user-ow3tp3vu3c Ай бұрын
Kodi chilima salim'boma penapake akweniwa asamatinamize ndithu aaaa
@ishmaeldama8906
@ishmaeldama8906 2 ай бұрын
Kaliat mulungu akulange😊
@jamesgama5489
@jamesgama5489 2 ай бұрын
Kukamwa konyasako mai iwe osamakayamikira amuna ako bwanji mxiii!
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 ай бұрын
Kupepera zedi uku muuisova DPP ikulowa m'boma itchetcha afiti nonse okubanu
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 so funny the take Malawian for granted. Wht is doing now is in the government mxm
@AlidiNgalande-ou7ig
@AlidiNgalande-ou7ig 2 ай бұрын
You are very correct
@JamesMalango
@JamesMalango 2 ай бұрын
Kuyankhula kwa bwanji uku mukamati munangowalawitsa anthu, kusowatu chonena uku
@Hendersonspoon
@Hendersonspoon 2 ай бұрын
Manyazi mulibe iyayi kkkkk
@user-jp9ip1dl5h
@user-jp9ip1dl5h 2 ай бұрын
Anthu akuyankha mofookatu mphamvu alibe.... Njala Mmmm
@StanziaElias
@StanziaElias 2 ай бұрын
Ulape mulungu akukhululukile
@EdgarBuleya
@EdgarBuleya 2 ай бұрын
Kkk koma malawi eee alibe manyazi akwen inu mwano wake
@francisvisage2705
@francisvisage2705 2 ай бұрын
Musagawe nsalu inu, gawani chimanga ndi kukwanilisa munalonjeza
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 2 ай бұрын
Mbuz yosafunikira kaliat
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Patrisha kawanamidze ana ako osakhala wamkulu ngati ine mmanfesto yanun : mwapanga chani mdiwe chisiru iwe kwabasi koma ndiwe wabodza eeeeeeereee satana
@PleasantMagombo
@PleasantMagombo 2 ай бұрын
Anthu osowa zochita awo.
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 ай бұрын
Mau amati awiri sayenda limodzi asanapangane, inuyo m'mene mumalowa mu alliance munagwirizana lero musayambe kusintha chichewa kamba koti zakuvutani. Zipitani tiyese anzanu, anzeru si inu nokha ndi a Chilima kulinso ena.
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi Ай бұрын
Kodi mwanva speechyi anzanga ine sinkunva mpaka ndaika bluetooth ine 😢
@chikumbutsomarch4484
@chikumbutsomarch4484 2 ай бұрын
Manyazi mulibe
@musamakanjira
@musamakanjira 2 ай бұрын
Wati ma Mp ali ku boma komweko alephera nanga Saulosi si ali ku boma konko
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 2 ай бұрын
Palibe chamzeru chomwe mukunena mayi opusitsitsa inu, a malawi mwawatola
@LinessiTambala
@LinessiTambala 2 ай бұрын
Mwachedwa
@user-iu3bf6oe1x
@user-iu3bf6oe1x 2 ай бұрын
Amp my vote
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 2 ай бұрын
Mayi asazampatsabe mpando,anthu oipa akuononga dziko ndi awa
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 2 ай бұрын
Mbuzi iweee
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 2 ай бұрын
Aaaaaaaa nanunso mwasowatu zokamba wadya katatu ndani inunso anthu ndi omvesa chisoni kwambiri fertiliser wosaka mtengo mwamugula kuti mitu yanu mwaiwala nsanga nsanga
@innocentnjoka7014
@innocentnjoka7014 2 ай бұрын
DPP woyeeeeee❤❤
@GodsonLindan-hn4kp
@GodsonLindan-hn4kp 2 ай бұрын
Akaliati ndinu chitsilu eti, ndinu munthu opanda chisoni.ndichifukwa mumawasiya mai anu akuvutika ndi basiketi ya tomato galu. Ngati chilimayo Ali bwenzi lanu ndie mwauponda.
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 2 ай бұрын
Sopano apa muli muboma bwanji osapanga zosezi agalu inu
@llewellynkhungwa4712
@llewellynkhungwa4712 2 ай бұрын
Kweee is back....💪
@user-pb1yr1jx5g
@user-pb1yr1jx5g Ай бұрын
APM MY VOTE ❤
@HarryRefred
@HarryRefred 2 ай бұрын
Ukuzikolakola wekhatu 😂😂😂😂😂 muziwona katatu😢😢
@TressLuka
@TressLuka 2 ай бұрын
Munatigwilitsa fuwa lamoto Inuuu aaaa😢
@KereeditseMotsetse
@KereeditseMotsetse Ай бұрын
Kalonga ndi chilima machendako nose agalu ndionukha kumatako kaliyati mayi
@user-hy4el8ov1l
@user-hy4el8ov1l 2 ай бұрын
Mayiwa ndi aboza 😂😂😂
@user-lg1bw8fx5m
@user-lg1bw8fx5m 2 ай бұрын
Zakudya katatuzo tazisiyani izo yambani Zina komaso ngat ndale mwatopa nazo muyeseko business ya kaunjika musatichimwitse
@user-vp5mf6bd3o
@user-vp5mf6bd3o 2 ай бұрын
Ndinu mai ovesa chisoni mulungu sakondwera ndi boza ngati limeneli
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 ай бұрын
Zopusa et azakuvotera amako galu Chilima wakoyo azikalamulira kunyumba kwako demet fertilizer K4.595 alikut
@PeterThawi-jc7zl
@PeterThawi-jc7zl Ай бұрын
Kodi fredokiss akutaniko uku😂😅😂😂😂😂😂😂😂
@spargomw
@spargomw 2 ай бұрын
Palibe chanzeru chomwe mwayankhula.Ulendo uno simutinamizaso. Malawi pano adazindikira ndipo zimenezi muziyankhula mnyumba mwanu nd ana anu
@farlenmkorongo
@farlenmkorongo 2 ай бұрын
Vuto simumaziwa kuti vice president ku malawi amachita kutumidwa ndi president, nde ngati president anamuyimisa iyeyo akanatani
@user-ov7yw4bq7y
@user-ov7yw4bq7y 2 ай бұрын
Koma amalawi maona ngati chani? zobvetsa chisoni truck yansalu ithandiza chani pamoyo wa munthu mulungu awone anthu awa
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 2 ай бұрын
Iwe usatitenge ngati ndi chisiru wamva amalawi timazithandidza tokha sitimadadalira prezdent
@user-zv9ud1dx3j
@user-zv9ud1dx3j Ай бұрын
Kodi mulibe manyazi ndithu?
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 2 ай бұрын
Zomvetsa Chisoni kwambili ndipo akamayankhura sachita manyazi
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 2 ай бұрын
Aaaaaaah, musatinamizepo apa, UTM yili mu boma kale mukuchitapo chiani, za bodza basi
@InnocentJavelo
@InnocentJavelo 2 ай бұрын
Olo mayi wakuyandikirayo wakhumudwa nawetu kwambiri😢😂
@user-mi3fw1zg8b
@user-mi3fw1zg8b 2 ай бұрын
Akweni mungobwelera ku DPP komkuja basi zinazi mungotukwanidwapo zamunsalu apa because we are tired of u guys ndi mabodza anuwo fotsek!!!!
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 2 ай бұрын
Panyinipako hele iwe komatso nyiyamako nyiya iviyo
@user-xv3ju8yi9n
@user-xv3ju8yi9n 2 ай бұрын
Ingobwererani ku dpp musowatu cholankhula campaign ikubwerayi.
@user-et3il7pi7t
@user-et3il7pi7t 2 ай бұрын
MAyi. KAyimeni komwe munagwa kuja ngati zomwe munena ndizowona
@user-jr1kq9vc7n
@user-jr1kq9vc7n 2 ай бұрын
UTM my vote
@WitnessKambwiri
@WitnessKambwiri 2 ай бұрын
Hule uyu ali ndikukamwatu kobowoka kkkkk
@user-ee6be5kl5o
@user-ee6be5kl5o 2 ай бұрын
Mwayamba mbava chilima osamuvotelanayi amenewa onse 2025 tikuwagwetsa basi mwatinamiza kokwanila amalawife siianthu opusa
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 2 ай бұрын
Anyani Amenewa akufunika mfuti atikwanapo dzikomuno ndiboza
@user-gx8or3yz9u
@user-gx8or3yz9u 2 ай бұрын
Mzimai oipa uyu za dpp unasunga zija ukabweze kwa eni aka adad mzimai oipa iwe
@isaacchipatala1618
@isaacchipatala1618 2 ай бұрын
SKC my vote
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp Ай бұрын
Amasuleni anthu abwerere ku dpp
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 ай бұрын
Awa ndi mamafiya,,,fundo zao zikuwakola okha,Iwo alikuti panopa? Tonse alliance adapanga ndi ndani? Mwapanga dala kuthesa mulandu kuti mutinyasepo panopano.
@MAPAGASTUDIOS
@MAPAGASTUDIOS 2 ай бұрын
Tentiyo a dpp anakubwerekani yosachapatu komaso zakuti mukutibera misonkho mubomamu zodziwa chilima wanuyotu osangobwerera pambuyo bwanj mpepeseni APM basi
@AngungaThatcherNgoma
@AngungaThatcherNgoma 2 ай бұрын
Onse a ndale ndi a BODZA. DPP, UTM, MCP, e.t.c, e.t.c nga BODZA. Dziko lino likufunika lilamulidwe ndi Asirikali basi. Am tired of the Politicians. Maganizo anga.
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Onse Alliance sopano, eeeeh! Mbuzi zokhazokha.
@isaacchipatala1618
@isaacchipatala1618 2 ай бұрын
UTM for life
@fatsanichibwana9438
@fatsanichibwana9438 2 ай бұрын
DPP WOYEEEE!!!
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 2 ай бұрын
Dpp tatopa nawoo apanga Chali mbili zakale
@KereeditseMotsetse
@KereeditseMotsetse Ай бұрын
Amayi kaliyati pakholopako
@PeterThawi-jc7zl
@PeterThawi-jc7zl Ай бұрын
Ku Malawi kuli zipani ziwiri...osamanamizana ma kape Inu.MCP and DPP basi.enanu mukutaya nthawi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-hn8sr9oc7k
@user-hn8sr9oc7k 2 ай бұрын
Chokani nonse mukulankhula mbwereranu chifukwa chilimatu paja anamuchotsa mphamvu zonse ndiye mukuona ngati angatani?chakwera ankadziwa kuti chilima simunthu wamva ndiye ndimuchotsere kaye mphamvuzo cholinga asamatsutse komanso asamapange kanthu koma akanamusiira mphamvu zonsezija ndiye pano muzikamba zimenezi zikanakhala dzomveka
@robertchitsulo8006
@robertchitsulo8006 2 ай бұрын
Kodi mai uyu mutumu muri ubongo ndithu . Ndikukaika kwambiri .
@andrewchirwa2193
@andrewchirwa2193 Ай бұрын
UTM vote yanga
@MackdonaldMilanzi
@MackdonaldMilanzi 2 ай бұрын
Komaineyo ndikanakhala nfit ndikanayamba ndimayi ameneyi
ZOMWE ZACHITIKA KU ESCOM YAKU BLANTYRE🙌🙌🙌🔥
20:54
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
One moment can change your life ✨🔄
00:32
A4
Рет қаралды 34 МЛН
Cat Corn?! 🙀 #cat #cute #catlover
00:54
Stocat
Рет қаралды 16 МЛН
Does size matter? BEACH EDITION
00:32
Mini Katana
Рет қаралды 20 МЛН
Now THIS is entertainment! 🤣
00:59
America's Got Talent
Рет қаралды 39 МЛН
Lwasa afunye sente bupya,aguze benz ne rangerover
30:52
Kasuku Live
Рет қаралды 40 М.
ZOMWE ZALAKHULIDWA  LELO  POKUMBUKILA  IFA YA DR CHILIMA😢
36:07
VILLAGE CHAMPION
Рет қаралды 26 М.
CHISOMO DAUGHTERS CHOIR ULENDO OYENDA NDI MTIMA OFFICIAL VIDEO
5:20
FAB ONE PICTURES
Рет қаралды 16 М.
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 27 М.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Morton Baghaya
Рет қаралды 118 М.
MUSEVENI TASKS SPEAKER ANITA AMONG TO FIND SIMON ALEPER'S WIDOW A JOB
9:05
UBC Television Uganda
Рет қаралды 1,1 М.
One moment can change your life ✨🔄
00:32
A4
Рет қаралды 34 МЛН