This TV he is a One of the best tv in Malawi we are love you Boss
@chrisboyce227 күн бұрын
Ife Angoni aku Ntcheu tikuti wakumpha Mzake nayeso adzafa popeza wayimapo ndi pamanda pomwe asadalire Nyanga (Continue Rest well Biyeni 💔 SKC )
@user-sk1wj9bw6l27 күн бұрын
Angoni anatitolatu a mcp kumangopha anthu athu ozindikira eish
@user-sd6ri7cp8z27 күн бұрын
I remember video ina munakambako kuti Michael Usi amuuza kuti asayankhule kanthu paza imfa ya Chilima coz amupatsa u VP once Maliro ayikidwa. Lero ndi izi kupherezera zomwe munanena boss, Manganya is a VP.
@user-tk6wf2eg4z27 күн бұрын
Mr pangolini bakili muluzi tv l love soh much this chanel
@JosephJosab27 күн бұрын
Uyu ndkatundu waboma
@user-tk6wf2eg4z27 күн бұрын
Kwambili boss
@webstermbewe839526 күн бұрын
Noted
@user-vl5on2lj8b26 күн бұрын
Dziko lamalawi pomwe lafikapa likufunika chithandizo cha mwini mulungu analenga dziko lamalawi pamodzi ndi anthu komanso udindo waaliyense panthawi yomwe akupemphera azitengapo maminisi angapo kupempha upresidernt wa chakwera usapitilire 2025 chifukwa ambuye mulungu ndi amphavu zonse koma mwaife tokha popanda mulungu sitingakwanise . Amen
@christophermkhize199127 күн бұрын
Pakamwa pa journalist wa bakili muluzi tv sipayankhula zabodza may Allah protect you brother thanks for update
@user-ub1mw7ce5p27 күн бұрын
I always respect you, and praise the Allah who blessed you with this wisdom. We know that you don't do this to get something, but you do this because of your love on voiceless poor Malawians. May God continue blessing you with long live and wisdom.
@richiakina27 күн бұрын
Awa ndi akantundu omanga ndi mawaya❤❤
@BenissoneErnesto-eh6zs27 күн бұрын
Bakili muluzi tv inuyo tivomeleze kt ndinu nkhani Zina watching from Mozambique
@PrinceKachimanga26 күн бұрын
watching from state house ...CHAKWERA must pack and go in 2025
@GodsFavourite127 күн бұрын
Padziko pano palibe wamuyaya, zakuba sizilimba...they will never enjoy that money trust me, ndikulumbila ndithu!
@chifunirochikafumbwa121227 күн бұрын
Keep on informing us dziko muno mukuchitika zambiri zokhumudwisa
@ANUSALAISON-iy7yf27 күн бұрын
This guy delivers good and true points but we malawians don't even consider about it
@user-qq3ip1od6i27 күн бұрын
You always on point,, my question n worries is what's the way forward
@Moses5127 күн бұрын
Keep up update best TV in Malawi 🇲🇼📺🔥💯
@MUSTAPHERMALIDEN27 күн бұрын
Pangolin katundu omanga ndi mawaya bakili muluz tv
@Josephmwangosi27 күн бұрын
You the best and live long big
@tungwaprecious26 күн бұрын
Mwanayo wayamba change umbava, thanks Bakili Muluzi tv for the clear information
@user-xs3nj1es1r27 күн бұрын
Keep it up my dear brother ❤❤❤❤❤🎉 God bless you dear brother
@fahadwalipeya865627 күн бұрын
You the best TV ever bro I respect you👏👏💯
@MussaJohn-gt8ep27 күн бұрын
we here brother. big up my hope all the way
@sharrifmanda804027 күн бұрын
Munthu iwe ndilibe nawe mau ndiwedi katakwe pankhani zofufuza eeee, umandimaliza ❤❤❤
@user-us1qd3zj8m25 күн бұрын
Zikumveka
@yammiejaymakawa506727 күн бұрын
Boss much love always salute
@user-be5fc3ed1i27 күн бұрын
We are here to litsen from you B.M TV ngakhale atabera chotani koma chaka chamawa akuchoka afune asafune
@kenny78326 күн бұрын
Keep up the good work. People's eyes will be opened.
@user-sk1wj9bw6l27 күн бұрын
Kma i think malawi ndi dziko lanthu ogona kwambiri
@RamzyJapanese27 күн бұрын
Chachikulu tizingopempha kut mulungu alowelelepo bas achakwela akuyiwala kut chamoyo chili chose chizalawa ife kanakonda mulungu atatinenyela nkhondo
@NgomaRaheem26 күн бұрын
Pangolin wathu big up bradah
@EmmanuelGasiten-fo5dr27 күн бұрын
Mfumu mumatha, May Good Lord guide you all the time
@martintivalenji32027 күн бұрын
Inuyo matiimilira ndipo mapanga provide nkhani ndi ma umboni ale 🙌🙌🙌🙌🙌
Wapanga ubale ndi nkhalamo , ask him self , where's sidik mia , and where's V'P And wina aliyense akudziwa kuti chakwela ndi nduna zake ndizomwe zapha V'P ndiye mukufuna umboni wina motani
@Eric-gb9ms26 күн бұрын
Ulemu wanu big man
@mufuhtijohn266127 күн бұрын
Tinavomereza kale kale kuti bakili Muluzi TV ndi 1 ndipo imakwanira