Pitirizani bwana mpulumusi wa mkulu God bless you all the time big
@vicshyma564415 күн бұрын
Limpopo FM 🎉🎉🎉🎉 we never change that dial !!!
@UsenLashid16 күн бұрын
Kodi asilikali mulikuti bwanji simukuukila president pomwe akupanga nkhaza zika Zanu pangani zachangu kuchotsa chakwela Kodi inu asing'anga mukutani tamumphani chakwela nanuso asatanic mumangodziwa kumwa magazi bas mukumusiya chakwela azizuza azibale Anu zoona zimenezi afiti mulikuti nanuso mumangodziwa kumphuzitsa ana ufiti mukukanika kumilodza chakwela bwanji iyi ndi thawi yanu satanic members asing'anga athakati iyi ndi thawi yanu please please gwilani ntchito yanu akafa chakwela onse ma Israel azathamangisidwa sazapezekaso dZiko lanthu komaso mtendele uzapezeka chifukwa ma Israel awa akufuna Kuti azasokoneze zisakho ndi kukakamiza amalawi katemela wakumpha let's chase out this fuken garvament
@KennedyKanyama-ce8lb16 күн бұрын
Kulibe asilikari kumalawi kuno trust me my brother
@JOHNOlesmasCosmas15 күн бұрын
bola tikadakhala ndima Ninja zikadatithandiza koma zinazi mmmh manyaka eni eni🤣🤣🤣
@harrisbanda589115 күн бұрын
Asilika ake ongoziwa kunyenga azikazi aweni ana asatana 2👺👹👿☻@@KennedyKanyama-ce8lb
@ShakilahMbwanaa16 күн бұрын
We are ready kupanga mademo tipange ngati apangila ku Kenya president waku kenya wathwatu chakweraso ayinthawa Malawi
@MillyKachepa16 күн бұрын
Malawi timaopa sizingatheke izi😢😢😢
@Yusuf-j6c15 күн бұрын
Keep up the good work 👏
@DorrahBanda16 күн бұрын
La 40 chakwela lizamukwanira
@ImanRashidi-so4oo16 күн бұрын
Sangamakambilane zamzeru koma zompha anthu stupid mtanyiwa osaopa wanyamula ndembela pa Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 palibe amene angakumphe
@MabvutoMichaelPanagona16 күн бұрын
Ndi boma lanji lopha anthu
@PreciousHalias16 күн бұрын
Roud n clear from Sandton... Ntanyiwa 💪
@user-nf3ik3ff6y16 күн бұрын
Lipopo FM number one ❤
@victormunthali192415 күн бұрын
2 one bkmtv
@KennedyKanyama-ce8lb16 күн бұрын
Always with u ntanyiwa. U r number 1❤❤❤❤
@zimmekapachika678416 күн бұрын
Boma lanji longopha anthu,tipheni dzikoli mutsale naro...munthu opanga zoipa amafa ngati galu nthawi yako ifika mr Chikangawa C
@inessmsiyambiri851715 күн бұрын
Mr chifunga chakwera
@user-sz6bi3tw5y14 күн бұрын
Tsiku lina mulungu adzatsanjika dzanja lake lamukwiyo pamutu pa Lazalo Chakwera
@FloridaMakwinja-eq2ek15 күн бұрын
Chakwera chikangawa ulibwanji ndi dziko lakolo Munthu wankhanza iwe
@MadalitsoTamayenda-ez5pj16 күн бұрын
😂😂😂 awuzen Ana Arira awa
@MosesKalenge15 күн бұрын
Atimaliza 💔🙌🙌🙌🙌
@RitaKainga16 күн бұрын
Mulungu wathu ndi wamoyo,khutu lake silogontha,mado ake samazinza,with sure awa etetezera ana ake
@FrankWaresi16 күн бұрын
Tiyamika mulungu osaopa kulibe wamuyaya
@PetroJack15 күн бұрын
Boma ladzitsilu ili lagwa basi
@MandalaChaona15 күн бұрын
Like father like son. Chakwera, John Tembo, Kamuzu Banda, killers,evil men. Leaders of Chikangawa Party
@KnowledgecGodwin-xo4pw16 күн бұрын
Big up me Mr Ntanyiwa
@MandalaChaona15 күн бұрын
Ayikeni poyera Brother Mtanyiwa Anthu oyipawa . God is watching
@user-sm8gx4vf1v15 күн бұрын
Mfiti yamunthu chakwela chikangawa from ntcheu kwawo kwa skc
@user-oc9vl9xz8e15 күн бұрын
Koma kaliyati ndi mzimayi osagwedezeka sangapange zopusazo kulandila ndalama ku MCP..ngati ndalamazo mai angakupaseni landilani after nguzangolengeza kuti mwatukuka my ngwilizanowo tizaone ngati azaime poyela kuzaitanisa ndalamazo
@MosesKalenge15 күн бұрын
R.I.P SKC 💔😌😭😭😭😭😭😭😭
@user-artharkkadango15 күн бұрын
Oh my God protect us plz
@PeterMphanza14 күн бұрын
Nice job comred kp it up
@doreenkaliati316616 күн бұрын
Ambuye sakhala chete pa nyengo zathu Mulungu wathu ndi wakumva ndithu sagona turo ai
@DorrahBanda16 күн бұрын
Zoonadi ndipo kwambili
@JaneChimasula15 күн бұрын
A Malawi maso athu ayang'ane kwa mulungu basi chifukwa die amene azatimenyera nkhondo tili chete 😢
@chesterkumwenda15 күн бұрын
Listening from Johannesburg
@CHIWSABINYAMBOSE16 күн бұрын
Izi ndizoona amuhone anatengedwa last week kuchoka kuno kumzimba boma nkupita nawo ku Lilongwe kuja kunali born kalindo 😢😢koma ngati atamuphe mutiva ife kuno achina mzimba
@chrissyamanda551015 күн бұрын
Mmmmmm koma anthuwa ndi asatana eti Nde amawatenga amhone kuti alakwanji mmmmmm ayayayaa atasatu atasa anthuwa
@IsaacMusa-py2jm16 күн бұрын
Loud n clear here in mpumalanga 🙏
@MandalaChaona15 күн бұрын
Koma Mr Lazarus Chikangawa mwaonjeza,muphe anthu onsewo muwaphe akulakwirani Chani, kukana kudzudzulidwa pa kupha anthu 9 eeeeee Koma ndinu Mulungu wachiwiri,mwafikapo 🔨⚒️⛏️
@JefulyPesulo16 күн бұрын
Keep up boss
@frankkaipa892515 күн бұрын
Ndiye tizingokhalila kuphana dziko likubwelela kwa kamuzu ili mmmm
@user-wb3us4pg4b16 күн бұрын
❤❤❤ comrade ntanyiwa
@PaulDaka-dc3re15 күн бұрын
Ndi moto wawa👏👏👏
@RobertChimenya15 күн бұрын
Asilikali akumalawi amalandira ndalama zaulere ndiadyera kwambiri nchifukwa chake Ali mbali ya chipani osat kuteteza nzika tiyeni tizaona ukazatha udindowo
Upo wawo sungapindule chifukwa imfa amaivomeleza ndi Mulungu..I can tell you kut Chakwela mtendele alibe ngakhale kadontho mkat mwa moyo wake..mwadzi wa Munthu ndi ovuta😢😢...dekhani muone zomwe zichitike