MCP Ikuwina Zisankho Mu 2025 - Redson Munlo

  Рет қаралды 3,385

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

12 күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, activist turned politician Redson Munlo, says MCP will win the 2025 Elections. He also explain in this audio why when exercise his political rights as prescribed by section 40 of the constitution of the Republic of Malawi he chose to join MCP instead of any other party in the country.
Pa Nyasa VoiceBox, Redson Munlo yemwe adakhala wandale, wati MCP idzapambana zisankho za 2025. Iye akufotokozanso mu audio iyi chifukwa chake atagwiritsa ntchito ufulu wake wa ndale monga momwe adanenera ndime 40 ya malamulo a dziko la Malawi adasankha kulowa MCP mmalo mwa chipani china chilichonse mdziko muno.
#malawi

Пікірлер: 200
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 11 күн бұрын
Bon Kalindo siukumposa kutali kwambiri. Bon Kalindo ali ndi umunthu komanso amakonda amalawi kwambiri
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 11 күн бұрын
Abambo inu NDINU opusa zedi ndipo MULIBE manyazi polakhula, INUYO zoti mcp ulamuliro wake ukudzuza anthu simukuona? Adpp ukulimbana nawo wo uchedwat chifukwa Iwo mbuli yawo idazizila yateha mbili yoyipa ndiyachipani chakocho chopusa anthu akufa ndinjalat dziko Muno Koma mcp alimomo ndiulamuliro Wanu opusawo mwangokhalira machende anuwo Maloomaudzana dzeru zoyendesera dziko,thawi ya DPP kudali njala? Anthu amadyat ndinu opusa ukumva kuwawa ndi DPP iweyo, chisazo sidaone kutchewu Kuti mcp anthu sakuifuna ? Pm adanyadilidw ndianthu osakhalaso adpp pomwe chakwera adachoka chothawa ndinu opusa MCP ndiyako ndichakwera wamakoyo osat Malawi Ife mwapasidwa zingat? Basi kumvara Panti obooka mkat kulawilira kumatinyasa NDI MCP ? 4yrs MCP yapanga chani ? Mudabwera kuzaononga dziko anamachende inu , bon KALINDO utchulayo amayakhulirat Malawi ndipo ndiwadzeru kuposa iweyo khope Ngat kumimba kwangumbi Mwana wakhumba iwe, malo momenyera ufulu Malawi ukuimisa mbolo kumamenyera ufulu MCP CHOLINGA ukupase ndalama ukagure pantiii wabookayo galu Mwana wahure tikumva kuwawat Malawi ndi m,boma yazitsiru yamcp yosaziwa kuyendesa boma Koma Kuba bass
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 11 күн бұрын
Ndiye ukumukalipira ndani nawenso wamisala iwe. Mukuyiopa DPP ndiyimuyo mmesa. Chifukwa chani munkawapanga chipongwe a DPP komanso Afford kumisonkhano yawo
@user-vw4vc9xd5z
@user-vw4vc9xd5z 11 күн бұрын
aaaaaa mwambo osunga kuti akakuuzani kuti muzipha anthu opus inu kwambili
@MikeKachiwala-ln5vp
@MikeKachiwala-ln5vp 10 күн бұрын
Mmmm a munulo ngati munalephela kulipira ma rentals mpaka kuthawa ku BT mungatiuze chani
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 10 күн бұрын
Gulu la ma activist linalandila ndalama kuchoka kwa chakwera kuti aziyankhula zabwino za mcp lija wina ndi ameneyu. Nde waganiza kuti angojoina chipanicho akuona ngati adya zambiri akatero. Nkulu sungatiputsitse mission yanu tikuidziwa.
@amoscassim8534
@amoscassim8534 10 күн бұрын
Ndimakutengan ngat ndiinu onjenjera ayi ndithu mbuzi yeniyen
@user-dw9zi6bo3o
@user-dw9zi6bo3o 2 күн бұрын
Let's keep the waffle up
@ClifordBwwanali
@ClifordBwwanali 11 күн бұрын
Mmmh money is very dangerous..
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 11 күн бұрын
Anyamata amene apha Chilima awa.
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 9 күн бұрын
I respect you Munro you’re honest..ndiufulu wako kusapota boma monga ulinso ufulu wa anthu enawo kutsutsa boma.
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 10 күн бұрын
Mwayamba kusavuka nd ndalama za mwaz mungobwebweta zopanda mutu apa mcp iwine dziko lake lit?
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 11 күн бұрын
Aaaaaaa Ntanyiwa ndi deal Mankkkkkk K😂😂😂 Nkona mukungophanako ku Mcp ko..
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r 10 күн бұрын
Zoonadi ndiwe wanzeru. Koma MCP ilibe mpata kuwina cisankho. Uli ndi mantha. Upokosera kwambiri, ungodikira kupambana kwanu 2025.
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 11 күн бұрын
Mtanyiwa ndiye deal.kape wadyera iwe.
@user-fi9yo9si5k
@user-fi9yo9si5k 10 күн бұрын
A chisiru awa
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 11 күн бұрын
School wulinayo but you dont have respect you like attacking DPP for what.
@homeremedys3748
@homeremedys3748 10 күн бұрын
Ndani angavotele manyi akuyankhulawa kula MP, malawi wake uti
@homeremedys3748
@homeremedys3748 10 күн бұрын
Redson Munlo anamwalira ndichanthohi chikuyankhulachi
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y 10 күн бұрын
MUNLO ndi iwe ngalu kwambiri limodzi ndi mbale wako uja BEN LONGWE ndi inu zisilu umphawi umakukandani kwambiri ndi chifukwa chake mumatisokosera nthawi yandutsa ija mumalilira misokho pamalawi ngalu iwe
@JamesLongwe-qz9fd
@JamesLongwe-qz9fd 11 күн бұрын
Tamatiye uko iwe ukuyankhura za mbwerera apa, aku pasani zindalama zakuba uko, ndiye uzibwera apa ndikuyankhura zopusa. Maganizu anu mwayika pakuba zisankho amalawi akuona chilichose chimene chikuchitika Akakuphe iwe ndiwe ndani?
@ChimwemweHenry-uw1bq
@ChimwemweHenry-uw1bq 10 күн бұрын
Chisilu chamunthu kod ngt uli nd mzelu osamangodya ndalama zomwe akukupasa chakwerayo bwanj.. iweyo ndi zisilu zizakozo mukanangopanga zot anthu awone ntchito zanu.nakha mukumalimbana ndi achina bon kalindo bwanj????? Pangan zachipani osat za anthu èna.
@user-qu5gf7cd5i
@user-qu5gf7cd5i 10 күн бұрын
Umaziwawa wekha ndidyela lakolo ukanabadwila kuchina ndi zako ben longwe mutaphedwa kalekale oloanakuphuzisa sukulu iweyo kukunva zomwe ukulankhulaxo akudandaula mbuli yophunzila ukufuna uwabele anthu akumwanza
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 11 күн бұрын
Redson mhunlo ndi inu munthu opusa kwambiri ngati mulibe chonena osangokhala bwanji mene dzikoli lafikira pano inu ndi munthu opanda nzeru a Malawi akuvutika ndikumadzanena zopusa ngati zimenezi
@GoodmanNzunda
@GoodmanNzunda 10 күн бұрын
Undiolotse ndikakutafune 😊😊😊
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 10 күн бұрын
Koma Munro udakwatira kapena ndiwe batchala .kkk Koma ngati udakwatira akazi Ako Adangosowa zovomere ..ukukwakwakusatu banja kako savegi wamunthu
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 10 күн бұрын
Mesa amanena kut activist ameneyu Tachioneni chikukonda ndalama ngat chikafika nazo kumanda.matembelero akhale pa iwe mpaka tsiku louka mmanda ngat supepesa...kape
@temwachaima817
@temwachaima817 10 күн бұрын
It will never last Bon kalindo woyeee, ntanyiwa all the way Awa a bambowa atichedwesa
@user-ww2il4wb8o
@user-ww2il4wb8o 10 күн бұрын
Mbudz iyi ikumandinyasila
@robenallie6985
@robenallie6985 11 күн бұрын
Anakupatsa chibadzi iwe mbudzi ya muthu
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 10 күн бұрын
Inuyo ndi asizi natole😢
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 11 күн бұрын
Mmaso Ngati kadzidzi Munro ..ukudya ndalama Za magazi
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 10 күн бұрын
Mmutumo mulibe kanthu ataa olo kumvesa chisoni kwakeko
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 10 күн бұрын
Mzimu wa malemu wakuvumbulutsa😢😢
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 10 күн бұрын
Kodi awa akuti chani? Nde inuyo mumalemekeza angodya zanuzo? Anthu opanda chisoni inu mwakhetsa mwazi wa nzanu
@user-oj5ye6bj9q
@user-oj5ye6bj9q 11 күн бұрын
Koma umawerenga ma comment wa kapena ay ??
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 11 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 Iwe ndi opusa kwambiri munulo iweyo ndi galu uli ndi minyama
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 10 күн бұрын
Akudandaulani ndani achisilu
@AmiduKachingwe
@AmiduKachingwe 10 күн бұрын
Aledson munilo panyopanu ndi sukulu yanuyo sukulu ndichani Mulindichan kuli azanu ophuxila kuposa iwe koma alibe matama
@ManyowaJeremiah
@ManyowaJeremiah 11 күн бұрын
Adzakuvoteren ndan
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 11 күн бұрын
Kho kho kho amunilo❤❤❤❤
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m 9 күн бұрын
Munlo ndiwe mbuzi nzeru ulibe ndi chifukwa chake unasata opanda nzeru azako achakwera chilima munapha mmamuopa a galu inu chakwera wako fiti ya munthu palibe voti yanu 2025
@joebrown1158
@joebrown1158 11 күн бұрын
Ana asatanic inu
@HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE
@HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE 9 күн бұрын
Where is the brain in this audio 😅😅
@mathewsmbaluko8522
@mathewsmbaluko8522 10 күн бұрын
Eya ndiwe wadyela 😲😲
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 10 күн бұрын
Kodi ndi chipani mcp? Ndimatitu ndi bungwe
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 11 күн бұрын
Amunlo inu kalindo simungafanane naye achisilu inu thokozani chibanzi munalandira simunamuksiyila kalindo kuti 10 million akupasani a udf ilikut siukape umenewo😊
@jonesnezara4294
@jonesnezara4294 8 күн бұрын
Akakuvotera amako ndi family yaki basi, ungotaya nthawi yako pachabe sungawine u MP atapang'ono kalindo and mtanyiwa they are loved guys in malawi, mapwara ako usowa 2015 boma likazasinthu ndipo lisinthadi anthu akupha inu tatopananu
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 11 күн бұрын
Iwe dpp ndimene akufuna anthu.kaseteeeeeeeeee.
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 10 күн бұрын
Inu amunlo ndinu a chitsiru muzikura palibe so amakuopani nanuso ndiye ngati kuli ufulu aredson pangana za ndale mupindula chani mudzabera mukunatu ooooh tiona tu mene musinire
@husseinchikusimbwisa2382
@husseinchikusimbwisa2382 10 күн бұрын
😂😂😂😂😂 iyi ndi mbuzi basi
@TriplejMalawi-cx1vj
@TriplejMalawi-cx1vj 10 күн бұрын
Kalindo ndi Dolo amwene 🤣🥰 ❤
@JumaKachala
@JumaKachala 10 күн бұрын
Comrade iziiii ananena kalee kuti salimbana ndi anthuu ngat inuuu
@user-so7wg6ii5m
@user-so7wg6ii5m 10 күн бұрын
Iwe nkhumba kwabasi dpp yake itiyo ikukamba zaiweyo paja umamwa eeeet waledzedwa iwe
@MrMwambananji-tx8jt
@MrMwambananji-tx8jt 11 күн бұрын
Chitsilu I we!
@MonicaChirwa-l4b
@MonicaChirwa-l4b 10 күн бұрын
Usilu sagawanadi 😊
@temwachaima817
@temwachaima817 10 күн бұрын
Hehehe God must come down now!!!!! and rescue us
@custommantchombe-rn1oo
@custommantchombe-rn1oo 10 күн бұрын
Aaaaah km ziko Ili ai ndthu,,,,Uzitumikila wekha ai wa MCP iwe
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 11 күн бұрын
Ukatumikile ndani pitakukatumikila akaziako
@user-iu6mr5xu6r
@user-iu6mr5xu6r 10 күн бұрын
Kodi adawina cisankho pakati pa MCP ndi Tonse Alliance? Pazimene unenazo zitsimikiza kuti ndinu akupha?
@UseniMailosi
@UseniMailosi 10 күн бұрын
Inendiimba nyimbo yochemelela agalu a MCP ndipese ndalama sapwekasi
@GoodsonLindani-gf8pn
@GoodsonLindani-gf8pn 10 күн бұрын
Bambo munlo machende anu mwamva. bola ukanangokhala chete ndi dyera lakolo ndiwe mfiti zedi, sungawauze anthu za MCP pamene nthawi yomwei yapha chlima ,Kod sunaone APM kumaliro kuja mphaka iwe.
@user-ni3xw4fv4c
@user-ni3xw4fv4c 10 күн бұрын
Km akwanu alimoyo akunva zomwe mukuyankhulazo😢?
@robertmunthali8521
@robertmunthali8521 10 күн бұрын
Redson ndiwe galu kobasi ndani angamve kuyabwa chifukwa cha iwe
@superiormoses4802
@superiormoses4802 10 күн бұрын
Awanso ndiopepera bwanji kod kuphunzira kochita kuzichemerelako bwanji
@stevietungama9775
@stevietungama9775 10 күн бұрын
Kuwina kovoteredwa kapena kobela ? Ingodyani makobiriwo basi koma musazinyenge ndi chala
@Littlefair7
@Littlefair7 5 күн бұрын
Awa akanangokhala chete basi. Kuwaputa amalawi dala, akakutukwanani ife tizikhala busy kuleletsa?
@HannockMesiwni
@HannockMesiwni Күн бұрын
Munapasidwa bans inu ulendo Uno mukutuluka mwangozichedwesa chipani chakumpha Ife ayi
@robenallie6985
@robenallie6985 11 күн бұрын
Munapha anthu ena wasowa zoyakhula
@joebrown1158
@joebrown1158 11 күн бұрын
Akulu musathe mawu mawa ndi tsiku lina wotoni chirwa sanalamulire dziko ana zuzika ndi Kamuzu wanuyo.
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 8 күн бұрын
Mcp ndikatundu omanga ndi mawaya asiye adpp atulusaso atibela part 22025
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 10 күн бұрын
Mamawa wabwino kwandani ng'azi iwee, amalawi tinakutuluka kalekale fisi wachabechabe iwee
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 10 күн бұрын
Nawenso wanyasa voice box uziwona zoposta papeji yakoyi wamvaa, ukamaposita afisiwa tikutuluka pompano
@chitchohistorical1036
@chitchohistorical1036 7 күн бұрын
Pamtumbo pako iwe ase 😂😂😂
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo 7 күн бұрын
Mudasiya chifukwa chaumphawi inu,tikutero ife abare anu kuno kumwanza.
@DelightfulDalmatianPuppi-fq2cv
@DelightfulDalmatianPuppi-fq2cv 9 сағат бұрын
Ulibe fundo iwe chizilu cha MCP Khala chente iwe ndi chakwera wakoyo nonse agalu
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 10 күн бұрын
Za ziiiiiiii!
@mussafrank-ev6zx
@mussafrank-ev6zx 11 күн бұрын
Cz you growing money that's why your there
@user-em1qi8kj9h
@user-em1qi8kj9h 9 күн бұрын
Kkkk akufuna kupeza nawo ma 5,0000 million komanso anthu alibe nanu program
@hestonsailesinjolomole2318
@hestonsailesinjolomole2318 7 күн бұрын
Za ziiii
@patricktaibu4874
@patricktaibu4874 10 күн бұрын
Iwe ndi munthu wopusa kwambiri ngankhale sindingapitolize kumvera manyi akowo
@AbdulmalikAmanu
@AbdulmalikAmanu 11 күн бұрын
Iwe ndi galu wachabe chabe kwabasi mukuti munapita kukalowa mcp pamene munaonakuti yayamba kuchita bwino kuchita bwino kwake ndiye kulikuti iwe ndinthu opusa kwambiri osangonena kuti uphawi unakupanani galu iwe eti
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 11 күн бұрын
Ndiwe galu kwabasi iwe munolo iwe galu kawuze amayi ako ndi mkazi Wako or Ana ako kappe iwe
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 6 күн бұрын
Asa chisilu munulo
@h-one2656
@h-one2656 10 күн бұрын
After black box wakapasa Chakwera
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s 10 күн бұрын
Manyi ako iwe galu
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 10 күн бұрын
Umphawi unamukwana galu ameneyu, munthu opusa kwambiri machende ako!!!
@kimulaiman8181
@kimulaiman8181 11 күн бұрын
Panyini pa mai ako
@ClementMinyanga
@ClementMinyanga 10 күн бұрын
Munlo iwe ndi kape kwambili,mbolo yakoso.
@alexsumani6823
@alexsumani6823 11 күн бұрын
Satamba koma nkuluyu
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda 10 күн бұрын
Iwe ntanyiwa akulakwira chani galu afiti inu ntanyiwa tsingamupeze wa bakilli mulizi ati chani uku 2025 out panya panu
@aubreytiyess
@aubreytiyess 10 күн бұрын
MCP 2025❌❌❌❌
@marcuswalker2613
@marcuswalker2613 11 күн бұрын
Chitsilu chachabe chabe "tsikutumbila"
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 10 күн бұрын
Kumaona koma comments osangolo ngolola sasi😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v 10 күн бұрын
Mbuli yamunthu kkkkkk iwe nde ndikape bwanji
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 10 күн бұрын
Mwanditera ndata may🤔🤔🤔
@user-fq5kj5ey6f
@user-fq5kj5ey6f 9 күн бұрын
Chete iwe
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 10 күн бұрын
Wasowa sochita kkkkk ineso sindiwopa iweyo kalani nachakwera boma mukushoka mukukalipila ndani 😅😅 yangulani modeka mtikuveni bwino komaso zukuli mumali mbikila sasi😂😂😂mtinakusika akulu 😂😂bon kalindo atenga number 1 zukuli😂😂yolepeela kuyendesa dziko
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v 10 күн бұрын
Kodi ukulimbikila zokuphazo bwanji kkkkkk koma iwe nde ndi kape bwanji
@pidona825
@pidona825 7 күн бұрын
Umamtukwana chakwera emweyo Lero ukut nyonyo kupusa et kape
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 17 М.
Tom & Jerry !! 😂😂
00:59
Tibo InShape
Рет қаралды 67 МЛН
Me: Don't cross there's cars coming
00:16
LOL
Рет қаралды 14 МЛН
ОСКАР ИСПОРТИЛ ДЖОНИ ЖИЗНЬ 😢 @lenta_com
01:01
TIKUDZIWENI - 13 AUGUST -  ABITI MANICE WILLIAM DAUDI
28:46
Times 360 Malawi
Рет қаралды 40 М.
A Mwakasungula Musaletse Anthu Kulankhula - Steven Simsokwe
9:06
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 4,2 М.
Chisankho Sichibeledwa Tsiku Lovota Imakhala Process - Bon Kalindo
15:53
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 27 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 90 М.
Iindaba zesiXhosa @19H00 l 09 July 2024
24:36
SABC Iindaba
Рет қаралды 6 М.
Massive rally in Benin backs Asue Ighodalo amid candidacy disput.
25:49
Tom & Jerry !! 😂😂
00:59
Tibo InShape
Рет қаралды 67 МЛН