MMENE JOE GWALADI ANAPANGIRA MA MILLION AKE

  Рет қаралды 27,105

Hanifa Mw

Hanifa Mw

6 ай бұрын

MMENE JOE GWALADI ANAPANGIRA MA MILLION AKE
Woyimba wapakanthawi Joe Gwaladi ndi mmdzi mwa oyimba womwe ali ndi luso lakutha kupeka nyimbo mwaukadaulo ndipo zomwe amayimba zimadzafanana ndi zomwe anthu pa moyo akukumana nazo. Munanverako nyimbo yotchedwa Chipepeso yomwe amapempha aliyense kuti amupatsiretu chipepeso chake asanamwalire kuti mwina angodyeratu kuwopa kudzapereka atamwalira abale ake mkudzamakanganirana? Nanga ngati simunaimnvere, Tumbocid bwa? Iyi ndi nyimbo yomwe imapempha anthu kuti asalimbane ndi kumwa mankhwala osiyanasiyana akamva kuwawa kwa mthupi ndipo angopita ku chipatala kuti akayesetse magazi awo. Pa nthawi yomwe inatuluka nyimbo mu chaka cha 2012, inafika paliponse mdziko muno ndipo anthu ambiri anayamba kumafalitsa kuti Joe Gwaladi watola chikwama popeza aku unduna wa za umoyo ndi omwe anamutuma kuti ayimbe ndipo amulipira ndalama zambiri.

Пікірлер: 16
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 6 ай бұрын
Uyu ndikatundu chabe sagwiritsa ntchito ndalama moyenera
@giftMalawian-wd8xx
@giftMalawian-wd8xx 5 ай бұрын
Mamilioni akuti nanu akugona mukhitchini uyu aaaaa kwao kwa amai ake
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 5 ай бұрын
😂😂😂 akumwa mowa kwambili Joe
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 5 ай бұрын
Samasunga ikapezeka straight kumowa
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 6 ай бұрын
Now alibe ndalama akuvutika koopsa angakhale Mai ake
@lonnythom
@lonnythom 5 ай бұрын
Ulemu kwa Gwaladi😊
@hananianyirenda
@hananianyirenda 6 ай бұрын
Ali ndi ma million kodi? 🙌
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 6 ай бұрын
Timakota Gwaladi 🤛
@user-fl9xy8bk7e
@user-fl9xy8bk7e 6 ай бұрын
Gwaladi amatha hvy
@jamesbanda3537
@jamesbanda3537 6 ай бұрын
Dolo kwambili Gwaladi
@johnyassin-je8rv
@johnyassin-je8rv 6 ай бұрын
awa ndiwodwala awa😂😮
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 6 ай бұрын
Gwarad ndi dolo
@sokanyabralosa844
@sokanyabralosa844 5 ай бұрын
Gwaladi
@chancymathiwa1998
@chancymathiwa1998 6 ай бұрын
Alibe plan uyu kkkkk
@greatalfredlaijah4474
@greatalfredlaijah4474 6 ай бұрын
gwaladi ndi munthu wankulu
@user-ed4yu9pt3s
@user-ed4yu9pt3s 6 ай бұрын
🥑
Akuchita kusankha anthu omanga; Chilungamo kulibe ku police
10:42
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 7 М.
Mom's Unique Approach to Teaching Kids Hygiene #shorts
00:16
Fabiosa Stories
Рет қаралды 27 МЛН
Happy 4th of July 😂
00:12
Alyssa's Ways
Рет қаралды 67 МЛН
Who has won ?? 😀 #shortvideo #lizzyisaeva
00:24
Lizzy Isaeva
Рет қаралды 64 МЛН
Зачем он туда залез?
00:25
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 3,2 МЛН
IZEKI NDI JAKOBO MALAWI GREAT COMEDIANS
1:41:46
Friends Connect Malawi tv
Рет қаралды 177 М.
Malodza Akuchikangawa A Poem by Sir Michael Benjala
5:00
Clement Thanda
Рет қаралды 4,3 М.
Rudo Ibofu, Dickson And His Older Lady | Issues Pane Nyaya
1:00:59
Ахбори Точикистон Имруз - 25.07.2024 | novosti tajikistana
19:10
ТВ Таджикистан
Рет қаралды 13 М.
Tamvani Zomwe A kuyankhula Za Kondwani Nakhumwa
17:12
Hanifa Mw
Рет қаралды 20 М.
Mom's Unique Approach to Teaching Kids Hygiene #shorts
00:16
Fabiosa Stories
Рет қаралды 27 МЛН