Nkasa afinya mwana uyu ndithu anachita kumuyamba ndipo zinali chonchi

  Рет қаралды 17,779

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

8 күн бұрын

Пікірлер: 20
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 7 күн бұрын
Ndikubwe ndizawathandize ankasa kufinya nyamatayo wajayela too much, ine thawi zose ndikaona maposter papeji ndinati Kaya munthu wankhulu mbwanji kuchita tele🛫🛫🏃🏃🏃🏃🏃
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 6 күн бұрын
Aaaa bwana Mkasa zitayeni zikuchedwetsani wakulu tiyeni tirire maliro awa mkulu wathu Lucius ameneyetu kuthawa kokhako wadzipatsa chilango yekha
@AlieInan
@AlieInan 2 күн бұрын
Aphwetekana😂😂😂
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 2 күн бұрын
Ndasala ine mundipeze
@princekaponda
@princekaponda 7 күн бұрын
Adaaah amenewo ndiaku balaka ... Poyambila ndipamenepo mwana akumpelekezeyo ama phudzila pa mapic primary private school, kubalaka komweko .... Tiyeni nayeeee
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 6 күн бұрын
😂😂
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 7 күн бұрын
Iiii mwana wawusilu ameneyo kumabitsala kumbuyo kwa kasa Kkkk nde MCP yake imeneyi yalowa chiwewe ndi mwadzi wa chilima okanamangitsa munthu
@LemSos10
@LemSos10 6 күн бұрын
Kkkkkkk
@FlorahBanda-fl4vf
@FlorahBanda-fl4vf 7 күн бұрын
Kodi ndinu angoni?? 😂😂😂mmayankhula bwanj
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 7 күн бұрын
Amangeso chakwera fiti yamunthu 😢😢
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 7 күн бұрын
Aziona kkkkkkkkk
@IssahAluba
@IssahAluba 6 күн бұрын
Agwidwe bas mwana opusa kwambili
@louismagongwa
@louismagongwa 7 күн бұрын
opoira uyu angamalowe Live osadziwa kkkkkkk😅😅😅😅
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 6 күн бұрын
Mwana wachipongwe
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 7 күн бұрын
zoziyamba dala zina umangoona waziputa
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 7 күн бұрын
La 40 limakwana. Basi ngati wapanga delete page wadziwa kuti amalakwisa and anthu adziwanso kuti anali iye osati Nkasa choncho angomukhululukira azidya chigwada ndi kholowa
@samuzymkwanya8490
@samuzymkwanya8490 7 күн бұрын
Sindikuwonapo vuto ife timaziwa kutisiiye Osayiwala tiliso ndi bakilimuluzi TV nde palibe vuto
@greatalfredlaijah4474
@greatalfredlaijah4474 6 күн бұрын
nde bakili tv ndi bakili elison muludzi zikufanana? ameneyo amumangise ,ndi anthu opusa kwambili
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 6 күн бұрын
Chommangisila kod anatani mwanayu.anamulakwira Chan nkasa
@LemSos10
@LemSos10 6 күн бұрын
Kkkkkkk
Ekedi na Sekuru Kanengo padare kuchiweche akafira pasowe cheshomba part 7
1:26:08
Incredible magic 🤯✨
00:53
America's Got Talent
Рет қаралды 54 МЛН
🌊Насколько Глубокий Океан ? #shorts
00:42
3M❤️ #thankyou #shorts
00:16
ウエスP -Mr Uekusa- Wes-P
Рет қаралды 13 МЛН
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 32 М.
"Wagwa Mtengo" (Soldier Lucius Banda - Tribute) by Pon G (Eugene)
2:32
Pon G On The Beats
Рет қаралды 21 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 156 М.
Nancy vs Che Nkope - Zikhale Ngoma Kapena Drums?
10:46
CHE NKOPE
Рет қаралды 26 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 127 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 91 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19