Mkangano olimbirana Nyanja pakati pa dziko la Malawi ndi Tanzania PART 2
Пікірлер: 110
@user-dk6yc8pl2m4 ай бұрын
Kod ka sound ka munakapeza bwanj bro sound nd history zimagwilazana kwambili
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
This is very nice story to hear. Big up
@dalitson35583 жыл бұрын
Ndimakunyadilani braz keep it up
@hamdanmasuku4800 Жыл бұрын
Kamuzu anali wankhaza km pa nkhan iyi anayetsetsa kuonetsa luso lake thank u
@lonelynyirongo15233 жыл бұрын
Tanzania must stay away from our lake pls
@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
Azungu ndi kale anayamba kumenyanisa anthu akuda vuto ndi lakuti wakuda ndi watulo
@Littlefair73 жыл бұрын
You're right but akuluwa all their presentation amalimbana ndi mcp ndi zinthu zakale zomwe sitingazisinthe pano, za ziiii zeni zeni.
@wilsonephraim56062 жыл бұрын
ngati kumalawi kuli nkhani zikulu-zikulu zomwe ndimakhala nazo ndi chidwi kwambri kut ndizidziwa mmene zikuendera imodzi mwa izo nde ndi iyiyi
@chembamisasi69833 жыл бұрын
Tsono Mozambique inatenga bwanji mbali inayo chifukwa zikuoneka kuti nyanyai inali imodzi komanso Likoma ndi Chizumulu Islands zili mkati mwa Mozambique
@alfredbanda169311 ай бұрын
We have a well documented agreement about that but not with you
@richardthera6033 жыл бұрын
Nkhani ili ku court palibenso kuti ma president angakambirane za nkhaniyi. Anapita kukakambirana zina!
@ericbishopjere44943 жыл бұрын
I like watching these videos they r full of information
@haroonharoon19578 ай бұрын
Thanks for your information
@MarkManyowa23 күн бұрын
If Africa is one then why are we fighting one another? 🇹🇿
@boscotonny42733 жыл бұрын
Great work Fam!
@thokokabanda52273 жыл бұрын
Thanks a lot.
@shadreckpatrickmkisi88193 жыл бұрын
Thanks for sharing this
@yusufkassimlumbemajawa71872 жыл бұрын
Inu big ulemu wanu ndinthu Allah be with you
@danielchikota28573 жыл бұрын
Take out this imagenary boundaries is not for us
@user-xp7ig3rk1d2 күн бұрын
Nice
@stanleydamalekani23983 жыл бұрын
Nkhani iyi ndiyovuta kwambili chifukwa pali map awili
@aliuyuli79453 жыл бұрын
Well narrated
@stanleydamalekani23983 жыл бұрын
Kupita ku Tanzania President chakwela sanslakwitse chifukwa kutenga nyanjayo sangatenge popanda zokambilana chifukwa aliyese amaloza chake ndi chikhulupililo.
@HusseinMachemba2 ай бұрын
Kom aide kudikilabetu kt kod zinantha bwanji kapena anatilanda basi
@crosbeygondwe5403 Жыл бұрын
Keep it up broo
@PatrickChilunga-pg4lt2 ай бұрын
Solution is one Africa,or choose to remain puppets.Mzungu divided Africa.
@zeckbmalawi80178 ай бұрын
We always love you sir
@danielchikota28573 жыл бұрын
We are devided not by our choice
@bestonjoseph21933 жыл бұрын
Where are the records of the boundaries
@oliversichela5657 Жыл бұрын
British are a problem even us here in Zambia we are facing the same problem over one part of our country
@user-uf9mn1du3h2 ай бұрын
Keep it up
@umaliisah69203 жыл бұрын
We follow u
@OustinYusuf4 ай бұрын
But why this President he go there to do what chakwera is very crazy This is lake Malawi
@manessmandebvu58883 жыл бұрын
Taziwa ndithu
@issacdiaton65263 жыл бұрын
Mumakwana brother ulemu wanu koma nanja ndiyathu ife a malawi
@blessingsngwila48582 жыл бұрын
I like ur information my brother ur the best
@LusajoNgabo4 күн бұрын
try us
@PaulMkandawire-oo7by14 күн бұрын
So pali pano ili mumanja mwa ndani
@AminaPhiri-pp9tw2 ай бұрын
Bolaso bakili abale amaziwa story
@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
Chakwera mbola munthu wothawa dzamulungu
@osamabinraden93913 жыл бұрын
💪😎🙏🙏🙏👍👍👍
@leonardjika21004 ай бұрын
AFTER MY ORTH OF THE OFFICE OF PRESIDENT NO ONE WILL CLAIM OUR WATERS SO HELP ME GOD
@hajaleemalinjemuhammad2193 жыл бұрын
We must stand up ✊💪 and to say nyaja ndiyathu chifukwa zikungooneselatu kut nyanjayi ndiyathu our president must know this " if he continue to keep quiet about our lovely Lake Malawi one day it will be ruling by Tanzania for sure, president wathu akuyenela azuke ateteze nyanja imeneyi Tanzania akula ndi maboza basi
@lutufyodixon99973 жыл бұрын
It's a lake of no one. Every country should enjoy richness of natural beauty of africa
@hajaleemalinjemuhammad2193 жыл бұрын
I think your sarvege, you don't know what are you talking or even! Can you look oldest map and then you must look the last map you can find that Lake Malawi is belongs to Malawians not Tanzanians, and if you follow this history properly you can see that all VIPs of Tanzanians was accepted that all parts of Lake Malawi is belongs to Malawians not Tanzanians "so today there is no way to come Tanzanians and craim about our lovely Lake Malawi". And don't say we should keep quiet to allow Tanzanians get profit for our lovely Lake Malawi no! Yes we know that we're neighbours nde asatilowe choncho chifukwa nkhaniyi ikuoneselatu kut nyanjayi ndiyathu look before it's two times that British were used this oldest map for boundaries of Malawi and Tanzania that means Lake Malawi is belongs to Malawians. This Tanzanians they just have a jealous for us because we can get rich easily through this Lake. All and all Tanzania must stop dreaming about our lovely 💗 Lake Malawi.
@jimmyjay99503 жыл бұрын
@@hajaleemalinjemuhammad219 I don't understand when u said u will be rich coz of that lake maybe u forgot one things that Tanzania is richest when it comes naturally resources ..u guys are talking about lake Tanzania as alot of them such as Victoria,manyala , Tanganyika to mention few so stop dreaming my brother
@hajaleemalinjemuhammad2193 жыл бұрын
@@jimmyjay9950 the things that am talking is already documented that Lake Nyasa is belongs to Malawians so you guys your busy to claim the thing that is not for you,. You must stop that and it seems that you don't know history of Lake Nyasa, l quiet you
@luganoessom14643 жыл бұрын
@@hajaleemalinjemuhammad219 probably you are right but there is no water bodies between two countries which are under control of one country,and Tanzania will not control this lake never they have their own part and we have ours but taking it completely from them is a worst idea because we will take it but we will never enjoy it and it's resources. We will be paving the way for terror attacks across the lake.
@Satier4710 ай бұрын
😢 pa chakwera😂😂😂
@MikeSenki-pj3nsАй бұрын
zili pati pano
@richmanjimmy271 Жыл бұрын
KOMAIYAMBA RITI OROINANTHA ZIRIPATI
@richmanjimmy271 Жыл бұрын
ZIRIPATI ZAHISITORE YANYANJI YAMARAWI NDITAZANIYA
@salaam10892 жыл бұрын
Kkķkkk umantha mbare
@isaacmbewe5585 Жыл бұрын
No ya 48 ndi no yomwe ili kumapeto kwa no ya Track driver Jason moyenda yemwe anakwatila mwana wa achemwali anga anamwalila akhala ku Lilongwe ku Likuni ndipo amayigwilitsa ntchito akabwela kuno ku Zambia
@isaacmbewe5585 Жыл бұрын
Komaso iyo no ya 79 ili kumapeto kwa no yomwe ananditumila mkazi wina ndipo dzina lake anandiuza ati ndi charity sinikudziwa komaso nombalayo siyamuno mu Zambia iwoneka inachokela dziko lina
@isaacmbewe5585 Жыл бұрын
No INA ya 48 ku last ndi ya Saulos Ngulube mwana wa akulu apingo opuma kudela kwanthu.
@mwamibukulu77453 жыл бұрын
if two countries bordered by water bodies the center of the water bodies must be its border!!
@hassanjameskananjie93492 жыл бұрын
What nonsense it is this
@ibrahmdoka7486 Жыл бұрын
The lake belongs to Malawi
@zachariahlungu35772 жыл бұрын
Zikomo bambo
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
A chakwera ngombwambwana sangatenge nyanja
@brightphiri86573 жыл бұрын
tiziti muja anabwera president waku Tz ku malawi ankalamulira ndi chakwerayo? nkhani ya ma neighbours sinyanja yokha.ma president amumbuyomu sanaithense nkhani yanyanjayo mbwanji? musaiwale kuti malawi it's a randlocked country tikumafuna ma neighbours munjira zambili nkhani sinyanja yokha.
@brightphiri86573 жыл бұрын
and palibe anganyamule nyanja, nkhaniyi njongokambilana,
@brightphiri86573 жыл бұрын
iyayi nkhani siimeneyo dziko silingayime kuyenda chifukwa cha nyanja. pali zambili zomwe tanzania ikufuna kumalawi and malawinso chimozi mozi ikufuna zambili ku Tz .that's why mukugona kuti ma president onse akulephera kuyithetsa nkhaniyi koma mayiko akuyendabe.
@brightphiri86573 жыл бұрын
and mundimvetsetse achikulire moti panopa asodzi aku Tz akupha nsomba mnyanjamo full time chimozimozinso asodzi akwathu zawo zikuyenda.
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
Chakwera nchitsiru alibe nzeru
@user-ty7mc9mg1f10 ай бұрын
Britain and German were wrong
@Thewarrior709310 ай бұрын
That entire lake belong to malawi 🇲🇼, that is why it is called lake malawi , Tanzania is just being selfish but i know that the whole lake belongs to malawi and TZ knows it
@MalangaMartin22 күн бұрын
🇹🇿 vs 🇲🇼
@luganoessom14643 жыл бұрын
Hey guys let stop this stupidity ,how do you think is possible for the lake to be under control of one country and our neighbors will be there watching it and it's wave🌊 and fish 🐟, and watching us swimming?🏊🏊😁😁In normal sense that's impossible ,and none of us will be safe .
@thondoyaenterprise3795 Жыл бұрын
Joint ownership is the key 👍
@josephzulu23723 жыл бұрын
Those you think they were against Malawi on the Lake dispute issue, like Chisano, the stance they took was to bring peace between the two countries. What is wrong with sharing? If the lake is shared then the dispute will come to an end.
@cza4212 жыл бұрын
It's more sensible that the lake is shared.Its is not feasible that the shoreline should be the border line.What about the Tanzanians along that lake? Does it mean they are not entitled that lake? Malawi is been selfish on this one
@edwinchimbuto83642 жыл бұрын
@@cza421 tanzania has lake victiria.. its about the possibility of oil. they want a part of it.
@Littlefair73 жыл бұрын
Africa needs to unite and stop talking about mikangano ya nyanja, nothing wrong with Chakwera's visit to Tanzania, there is alot that malawi can learn from tanzania, koma akulu awa anada nayo kukhosi MCP, muphunzire kuyiwala zakale ngati mukufuna kupita chitsogolo, tonse timadziwa kuti Kamuzu anatizuza koma zinachitika and we cannot reverse whatever happened then, muziyankhula zomanga ndi kulimbikitsa osati zobwerera mmbuyo, africa needs unity now than ever before.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
Ndipo ngati simukufuna kumva zakale chomwe mukumakhalira jijirijijiri kumvera ndi chani? Pitani ku ma channel ena chifukwa apa amakambapo history basi. Sangasiye kukamba za MCP chifukwa MCP idapulura mtundu wa amalawi
@@bakilimuluzitv3371 Well said, I've exercised my democratic right and nowhere in my statement did i say our lake should be taken by Tanzania, but we don't need to fuel chaos where there can be a peaceful amd lasting solution, why do you wanna blame chakwera for visiting magufuli? That's wrong, you're wrong, we cannot be enemies with tanzania just bcos of a small lake, a thing that can be discussed and resolved peacefully, we're tired of wars in Africa, don't you see what's happening in DRC? If this lake malawi issue is not handled carefully innocent blood can be shed. Be careful brother.
@@charlesmuyaya8839 Iweyo ukandiuze kuti ndisamonere, do you own this channel you idiot? Wayidziwa liti this channel? Ndinaymba kupanga follow this channel from its inception, ndimayamikira komanso ndimadzudzula, si ine ombwambwana ngati iweyo, mbuzi.
@nelitopedrofiniasse Жыл бұрын
Espalhados
@jamesmhango2619 Жыл бұрын
Common sense : the border should be in between. Aristotle wrote about the golden mean.
@festongrido81893 жыл бұрын
Ndimbuzi ameneyu ulamuliro wamukanika
@dorikakamwendo69703 жыл бұрын
The lake belongs to Malawi
@wilsonephraim56062 жыл бұрын
exactly !
@aoloathumani10 Жыл бұрын
Go and take it
@anniekhonje78533 жыл бұрын
From my view Tanzania doesn't own it .All who brought this problems us is Britain..
@dastahchikwekwe78643 жыл бұрын
Akuluwa amalongosola bwino nkhani koma ika fika pa Tonse alliance amayiwononga nkhani yonse seems like he doesn't like Tonse alliance for u to be good just explain what u know dont accuse anyone your stories will be good
Uyu amanena za aliyense osati tonse alliance yokha. Umvere ma video ake onse Pena amanena za Bakili Muluzi, Pena za DPP, MCP. Samasankha, musiyeni munthuyu amanena zoona zokhazokha, sali ngati ma wayilesi okonderawa ngati zodisk ndi times
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
But he is right. Chakwera mmene ankabwera kuchokera ku tanzania ananenapo chani zokhudza nyanja? Chakwera is an idiot
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
And mu nkhaniyi wapanga blame peter mutharika, chakwera and even joyce banda. Ndie chomwe waonapo iweyo kuti walakwitsa ndi podzudzula Tonse alliance pokhapo? U must be insane
@peterkondowe92653 жыл бұрын
Nyanja ndi chilengedwe cha Mulungu ili chete yokomela aliyense. Kumbali zose ziwili ngati titamenyane chifukwa cha nyanja ovutika tikhala amphawi ife komanso ndalama za mafutawo zipita mumatumba mwawo nyanja isala yowonongeka. Mwachisanzo kayelekela tapindula nayo chani ngati ziko? ? Kuma wona zokakamila komanso a TZ ndima neighbours anatigawa ndi asamunda a satana osamayiwala kuti kale makola a navuka ndi zisilu anzungu kusiya kwawo kuzagawa ntundu
@brightphiri86573 жыл бұрын
iwe ndi mbora ya reporter.moti siukuziwa kuti malawi ndi tanzania ndima neighbours? ukungoganiza za nyanja yokha bwa, ? kuganiza mopelewera and mopepera
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
Iweyo ulibe nzeru. Munthu wangodabwa kuti Kodi Chakwera athetsa bwanji mkangano umenewu ngati akupita nkumakamwelera nawo limodzi? Chifukwa olo mmene anabwera pa ulendo umenewu sanafotokozepo china chilichonse chokhudza Nyanja. Posachedwa pompa timva kuti Chakwera wapereka Nyanja kudziko la Tanzania. This narrator is 100%right
@danielmaluwa78963 жыл бұрын
Chakwera nchitsiru alibe nzeru sangatenge nyanja.
@kondwanitembo3863 жыл бұрын
@@danielmaluwa7896 pita ukatenge iweyo
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
Ndie tisiye kuteteza Nyanja just because a Tanzania ndi ma neighbours athu? Are you serious? Real president must protect the territory whatever the reason. Zina zonse zikuyenera kubwera pambuyo.
@spencerfweta7333 жыл бұрын
@@charlesmuyaya8839 Any drilling for oil or gas will cause havoc to the beauty of the lake and its flesh sparkling water