Bakili Muluzi samala akufuna athane nawe Kunkuyu wachita kunena pa gulu mopanda manyazi nkomwe

  Рет қаралды 18,122

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Ай бұрын

Пікірлер: 94
@user-jy5sl8yr5n
@user-jy5sl8yr5n Ай бұрын
One of the best tv in malawi ❤bakili muluzi tv
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Ameneyi nde akuyabwani mwamuyamba dala, we love ❤️ you bakili muluzi tv God protect him.
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Kunkuyuyo naneso ndikumufuna funa kuti ndimuphe ameneyo wakupha cnanga ma judge akumuikila kumbuyo azafa ifa yowawa ameneo kunkuyuyo ukuona ngat apolice amene umauenda nawo aja sitingathane nawo iwe wa chamba uziyenda naweso mubisala wamva wa bakili muluzi tv sumumanga utamangidwe ndi iweo ndiposo kuphedwa kumene wamva iwe galu
@MuhammadInack
@MuhammadInack 19 күн бұрын
Akunama ameneyo bakili muluzi tv is number one 🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️🏋️‍♀️
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Ай бұрын
Bakili muluzi TV channel never arrested we love this KZfaq channel here 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼✊️✊️✊️✊️✊️
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 16 күн бұрын
Bakili TV number one
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Kumkuyu ukudzitenga ngati iwe ndani iwe ndi mulungu kt anthu adzikuopa pansana pamako wamva uyamba iweyo kumangidwa pakhani yakupha Allan witika bakili muluzi sanaphe munthu mukumusakiranji
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Amene ati amupedze kumkuyu ndikumusaka pamlabdu okupha Allan witika nayenso akufa ndithu
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Kkkkkk wosaka naye kusakidwa kkkkk
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Bakili Tv number one ❤
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Kumkuyu is a criminal , As Malawians we will not afraid of Chakwela , we will still blaming stupid things which Chakwela and tones Aliance do in this country . Enough is enough , Bakili muluzi tv will continue and we will give him a full support ,
@SPAGHETTI313
@SPAGHETTI313 Ай бұрын
Tell mr kunkuyu that nonse mulephera bakili muluz tv ndi oopya kwambili just like Bon kalindo
@AllanChabwela
@AllanChabwela Ай бұрын
Bakili muluzi musiyeni,muyaluka umbava w nboma sitinkaudziwa pano ndipo tayamba kudziwa cheni cheni
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Ай бұрын
Mumuwuze Kunkuyuyo zoti nanetso ndikumufunafuna ndipo ndikamupezamo ndintembo ameneyo anatiphela alan witika
@maskinmsungeni8763
@maskinmsungeni8763 Ай бұрын
Bakili tv Ina ibadwanso Oro mumugwire.
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e Ай бұрын
Moses kunkuyu ndi chitsiru kwambiri akufuna kumugwira bakili muluzi walakwa chan iweyo kunkuyu wakupha ngati iweyo galu iwe musiye bakili muluzi uja ife timamukonda
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Bwanji sakukusaka iweyo ukupha mwankhadza iwe ma chende ako km uziba kunkuyu Mesa nduna imeneyo imangidwe Kaye kmaso iyeyo okuphayo
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm Ай бұрын
Munthu opusa kwabiri kunkuyu,,, ukusowekela school,, galu wamunthu,, ife timakonda munthu woyakhura chilungamo
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Kukuyuo zoti Ali ndi mulandu opha alani wtika waupindila m,thumba yasiya zake
@TsalaniponDan
@TsalaniponDan Ай бұрын
Koma gayz osamaiwala kuti Ali yese ndi ofunika bakili muluzi TV pena umakwera chipan ngat TV ikhale yoima payonkha
@Ishmael376
@Ishmael376 Ай бұрын
Amakwera chipani chanji
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Asowa zochita a boma lake la MCP. Zawakanika basi, ndipo mtola nkhani wa Bakili muluzi tv atiuza chilungamo, akungowonga ndalama za boma a Kunkuyu.
@user-hp4rl8cv3h
@user-hp4rl8cv3h Ай бұрын
Bakili TV yimakwana 🔥🔥🔥
@CarWorld-du9zb
@CarWorld-du9zb Ай бұрын
Yake milandu yakukupha ija ikumudikira kunkuyu angokhala phee,kumwamba kuli Mulungu amaona zonse zobisika,amuonetsa
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Mukuti akufuna akamuwomberenso mkamwa eee! Koma kunkuyu, koma zoona mcp is a bloody party.
@user-ko1lk3br4r
@user-ko1lk3br4r Ай бұрын
Lobati chasowa ,masambuka nd MCP pena Osamachotsa chitsotso chamzako kusiya chako
@JIMMYWATHONJE
@JIMMYWATHONJE Ай бұрын
Mr killer man munapha witika
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 14 күн бұрын
Mosses kukuyo ndigalu kwabasi ndpo akapitiliz chibwana chimenechi aziwon
@user-oz1ts3yi7d
@user-oz1ts3yi7d Ай бұрын
Ayambe wagwidwa iyeyo (kunkuyuyo) okupha mbuzi yamunthu
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg Ай бұрын
Akukuyu tangopangan zanu musalimbane nd chilungamo lolani zolakwika zibwele poyela chifukwa bakili muluzi amawawuza amalawi omwe amavutika nd misokho please
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Ай бұрын
Awonekera ng'amba akuba tidzudzulabe sitigiva
@user-to6tz6kr5k
@user-to6tz6kr5k Ай бұрын
Mayina amafanana zophana sizabwino ndipo inu si amuyaya komas tili ndi ufulu yolakhura
@alfrednazombe
@alfrednazombe Ай бұрын
Abwele mafamawo asanzikiletu abale awoo mabanja awoo mufela zaenii
@user-mi2xf3sw1i
@user-mi2xf3sw1i Ай бұрын
Kunkunyu mboli ya mako ma arv kumamwa mwa ndondomeko please mufa
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv Ай бұрын
Sazawina achakwera pamodzi ndi mbwezi wawo chilima
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Ай бұрын
Tabweleladi kumbuyo kuja mmmm Apm amanena ngati mukufuna kubwelela kumbuyo sankhani mcp lelo tavomeleza tili ku 1960 hhhhh
@calvinkhonje693
@calvinkhonje693 Ай бұрын
Simunati anyapapi inu mukutuluka boma next year tizizaonana mmakwalalamu
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z Ай бұрын
Nayeso kunkuyuyo nd mbuli kmabe sangakwanitse kumupeza
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y Ай бұрын
Moses usaiwale kuti nthawi yasala yochepa uzakolola zomwe ukudzala
@user-ut5nx5vd6p
@user-ut5nx5vd6p Ай бұрын
Bakili TV for ever
@allimataka6924
@allimataka6924 Ай бұрын
Kodi akukuyuwo metsa ndi muthu okupha
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
abwere awone apita anthu ochepa kumusi
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Ай бұрын
Ndiumunthu ndichikondi chomwe Atcheya alinacho sangakhare busy ndizadxiii ngati idzi .Atcheya ngati sanalisumire boma pakuthetsa mlandu uja kuti alipidwe kapena abwedxeredwe zake koma anakana ponena kuti boma lilibe chilichonse umenewo nde umunthuwo ... and Atcheya amasangarasidwa kwambiri pomamva kuti kuli Bakili Muluzi chanel tv .
@GibsonDamzy-ek8vg
@GibsonDamzy-ek8vg 16 күн бұрын
Its only tv in Malawi give us true story
@QassimuKatsobola
@QassimuKatsobola Ай бұрын
Sangamugwile mudzina la ALLAH
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 19 күн бұрын
We love him wa bakili muluzzz
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 19 күн бұрын
Akuchita maganizo abwino mcp awelengane ndalama zamabokosi zilipo😂
@andrewBwanaisa
@andrewBwanaisa Ай бұрын
Ndi kape uyu
@EmanuelMuotcha
@EmanuelMuotcha Ай бұрын
Osaopa bakili tv more more ayarutse agaru a mcp
@user-ko1lk3br4r
@user-ko1lk3br4r Ай бұрын
Muphetsana ndinu galu
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Kodi iwe kunkuyu, zoti tili mu democracy waiwala kale? Kodi mesa chakwera amacheza ndi atolankhani posachedwapa ndipo amakana kut Boma likuopseza atolankhani ndie iwe ukusutsana naye? Osamusaka bwanji yemwe anapha Witika????? Nonsense.
@AchinaKellz
@AchinaKellz Ай бұрын
Koma ukasiya mulungu ndikuyamba zaziko eshi ndende sauli
@VitumbikoNyirenda-jy3jq
@VitumbikoNyirenda-jy3jq 13 күн бұрын
Kunkuyu ndiwe mwana opusa ndipo usamare
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm Ай бұрын
Atibera kokwana pano mulungu wawaika poyera ndpo amusiye bakili muluzi ife timamukonda kwambiri IYEYO kunkuyu mulungu achita naye kanthu anthu amenewa azunza Malawi mokwanira mmmmm chakwera ndi anzake ndye pano akufuna munthu osalakwa anthu akuba
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Agalu amenewa a MCP ndi zisiru kwambiri chifukwa zawakani kuyendesa dziko ndiye azimanga anthu opanda chifukwa mbamva zopanda chisoni
@ManganiStanley
@ManganiStanley Ай бұрын
Macende ake chakwera ndi mbuzi za nduna zake zitsilu za anthu zogura fertilizer ku butchery zitsilu za anthu
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu Ай бұрын
Nanga wakuphayu amangidwa liti shame on you kumkuyu
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m Ай бұрын
iwowo Ngati akufuna kumugwila bakili muluzi TV mayina abakili alipo ambili Ngati akufuna kumugwila ayambe Kaye anthu akuba ndalama nzaboma
@user-cp7hu6xu8h
@user-cp7hu6xu8h Ай бұрын
Akukhunyu mukuziona Kuti Muli pasana pa njomvu eti muzasika
@mkhokholasamuzonda5094
@mkhokholasamuzonda5094 Ай бұрын
PANYINI PA MOSES KUNKUYU MUNTHU WOYIPA KWAMBIRI ANAPHA ALAN WITIKA
@user-my7sx1qj1d
@user-my7sx1qj1d Ай бұрын
Mulungu amutetezere kumene aliko tidzimupephelera
@Moses51
@Moses51 Ай бұрын
Akunama kwambili achepa
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Chisilu cha munthu ichi chayiwala kuti dziko ili ndi la democracy
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s Ай бұрын
iwesotu ndiwe opusa kwambili
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q Ай бұрын
Agalu anyani awa asowa sochita machende ake
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy Ай бұрын
Mose kunkuyu mumuuze machende ake ndi wakupha infact ngat zili ndi umboni timve mau abakiliwo
@Philemon-dt8il
@Philemon-dt8il Ай бұрын
Sizingatheke
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Kunkuyu mutu wake sumagwila uyu
@HassanSinoya-wl3vl
@HassanSinoya-wl3vl Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂sangamupeze akunama kwambili
@partmaulidiPatrick
@partmaulidiPatrick Ай бұрын
awa yabwadi amenenwa
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e Ай бұрын
Mmmmmmm km akulila maka ya witika anamupha ija
@user-bh4zb7ji3o
@user-bh4zb7ji3o Ай бұрын
Zazii
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l Ай бұрын
Za afit izi za nkhaza
@user-ru1mm7bf4p
@user-ru1mm7bf4p Ай бұрын
2025 ukuyuluka iwe mmalo molimbana ndi kuthetsa umphawi😂😂
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Kulephelatu kumeneko
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Boma lopusa kwambiri
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Ай бұрын
Bolo yako Moses kumkuyu!!
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Dzina ndi moto koma guys musiyeni koma
@josejoaolamissone4195
@josejoaolamissone4195 Ай бұрын
Kunkuyu 😢
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 19 күн бұрын
Wabakili tikumuyadila kwambili
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly Ай бұрын
Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika Witika...........muluzi tv amugwire? Komatu akupitilizabe komanso paja anamulephera kale . Ntchito yoyamba ya Mcp.........kupha sakudziwa ndani
@SwidiqLameck
@SwidiqLameck Ай бұрын
Inuns musakidwa
@user-ko1lk3br4r
@user-ko1lk3br4r Ай бұрын
Gwilani phanani
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 Ай бұрын
Kumalawi kulibe boma pano
@OmegaMussa
@OmegaMussa Ай бұрын
1:25 what bout EEF
@AchinaKellz
@AchinaKellz Ай бұрын
Kkkkkk hahaha 😅
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
Manyazi alibe namamchende ameneyo
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 15 күн бұрын
Sakufuna kuuzidwa chilungamo,,,koma adziwe kuti Iwo ndi athu olengedwa kulibe wamuyaya kuno Ku chalo.
@InnocentDalikiya-tz8go
@InnocentDalikiya-tz8go Ай бұрын
Azitimanga kapena kutipha chfkwa chot akuzuzula boma
@arafatMtyala-bo8ev
@arafatMtyala-bo8ev Ай бұрын
Angasamale ndi kunkuyuyo mbudzi yachabe chabe okhupa Allan witika
@arafatMtyala-bo8ev
@arafatMtyala-bo8ev Ай бұрын
Thanks
@OliverNkhoma
@OliverNkhoma Ай бұрын
Atatha kuononga nawoso adzawonengedwa
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Ай бұрын
Chisilu kukuyu pathako pake iye kukuyu akayakhe mlandu wa witka foseki zake kukuyu
I CAN’T BELIEVE I LOST 😱
00:46
Topper Guild
Рет қаралды 101 МЛН
Khó thế mà cũng làm được || How did the police do that? #shorts
01:00
THEY WANTED TO TAKE ALL HIS GOODIES 🍫🥤🍟😂
00:17
OKUNJATA
Рет қаралды 20 МЛН
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 113 М.
Raila: Be aware of the WRATH of history
23:42
Herman Manyora
Рет қаралды 34 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 156 М.
Times Exclusive featuring Bakili Muluzi - 11 May 2024
58:41
Times 360 Malawi
Рет қаралды 202 М.
BAKILI MULUZI KUCHEZA NDI BRIAN BANDA 11/05/2024.
58:38
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 29 М.
BAITULIE VS FORMER MINISTER SHERIFF ABBA SANYANG 6TH 2024
1:17:26
GAMBIA MEDIA TV
Рет қаралды 4,5 М.
BON KALINDO 8 JULY 2024 BIG MAN WAFIKASO PA MONDAY
15:41
Malawi Trends TV
Рет қаралды 18 М.
Wakatolika uyuyu Amutapa posachedwapa😂😂🤣😂😂
14:40
Malawian Cameras
Рет қаралды 62 М.
I CAN’T BELIEVE I LOST 😱
00:46
Topper Guild
Рет қаралды 101 МЛН