Milandu Yakuba Ya Saulos Chilima Yatha

  Рет қаралды 6,279

Hanifa Mw

Hanifa Mw

2 ай бұрын

CHILIMA ALIBE MLANDU POTI BOMA LATHETSA MLANDU WAKE
Malamulo oyendetsera dziko lino a Constitution, Section 99 (2) imamanena kuti, mkulu woyimira boma pa milandu kapena kuti Director of Public Prosecutions (DPP) ali ndi mphanvu pa mlandu uliwonse umene ukuzengedwa ku mabwalo amdziko muno kuti akhoza kuwuthetsa kapena kuwuyimitsa mmene akufunira, chigamulo chisanaperekedwe. Section 77 (1) yakayendetsedwe ka milandu ku mabwalo kapena kuti Criminal Procedure and Evidence Code imanena kuti pa mlandu uliwonse umene ukuzengdwa mmabwalo amilandu mdziko muno ndipo chigamulo sichinaperekedwe ndi bwalo limene likuzenga mlanduwo, mkulu woyimra boma pa milandu ali ndi mphanvu zonse zoyimitsa mlanduwu kapena kuwuthetsa polembera kalata bwalo limene likuzengalo kuti lichite monga mmene iye afunira. Maamulowo amatinso ngati munthu wozengedwayu anayikidwa mu mndende amayenera kutultsidwa ndipo ngati anali ali pa belo, beloyo imayenera kuthetsedwa. Kuwonjezera apo, Section 99 (3) ya malamulo oyensetsera dziko lino amanena kuti mphanvu zimene mkulu woyimira pa mlamnfuyu ali nazo pa milandu yonse mdziko muno, ndi zake basi ndipo palibe amene angamusokoneze kuti apange zina. Lamulolo likumaliza ndikunena kuti mkulu woyimira boma pa mlanduyu akuyenera kupereka zifukwa zimene wathetsera mlandu uliwonse mdziko muno ku komiti yowona zamalamulo mu nyumba ya malamulo ya Legal Affairs Committee pasanathe masiku okwna khumi.

Пікірлер: 12
@user-pq9mo4om2q
@user-pq9mo4om2q 2 ай бұрын
Signature ina ndi munthu wankulu
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Zoona, ayenela kutelo, chifukwa,akupanga,za mawa kuti nawo,asadzamangidwe.akachoka.president,ndi judge onse mu boma la tonse alliance ndi mbava,apa zikhale kwa ife amalawi kuti tifuna kuti ti votela mbavazi? kapena ayi.ngati,ndi Chocho amalawi tiyenela,kudzatetedza,vote yathu.ndipo,akangobela, chifukwa ife sitiwafuna okuba.wakutsewu.ndipo, tonse alliance izaziwa ndi judge wao okubayo,kuti Malawi ndi ziko la anthu,ndipo police or army ya Malawi sidzawapulumutsa mmanja, mwa thumu.
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 2 ай бұрын
Birds with the same feather flock together,,akufuna kutiveka chijjuzi kumaso,amadziwana chenjezo kwa iwe nzanga wosauka wakumudzi izizo sizosekerera udzimvere chisoni tili ndi zaka zina 5 zoonjezera tidakalira,,zilibwino kwa Iwo amainawo basi.
@user-st6bt5vv9c
@user-st6bt5vv9c 2 ай бұрын
Azimai inuyo musamangovina ai
@munikabambe7625
@munikabambe7625 2 ай бұрын
Mmalemba ngati sukulu inakuvutanitu.. Mulandu wakuba?... Anabeledwa ndani?.. Ndimayesa amati akuganizilidwa kuchita katangale..
@GidionJonas-sr4zr
@GidionJonas-sr4zr 2 ай бұрын
Andale samangana ai
@Litoprincess42
@Litoprincess42 2 ай бұрын
Komaso taphunzilani kuyakhula bwinobwino otherwise zikungomveka mwachitumbuka zomwe mukukambaz
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
Kumalawi katangale sazatha . Anthu ndife ogona kwambiri atsogoleri akuthesa milandu yofunikira kamba koziva kuti kuli ndani anganene kanthu. Ndalama za mphawi zikuononeka chifukwa cha tsogoleri wopanda zeru
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 2 ай бұрын
NO PAIN NO GAIN
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 2 ай бұрын
Yatha pansi pano, koma kumwamba akaipeza milandu imeneyo
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 2 ай бұрын
No evidence no case
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 2 ай бұрын
Mbava inzako imeneyo
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 10 МЛН
Самый Молодой Актёр Без Оскара 😂
00:13
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 10 МЛН
Despicable Me Fart Blaster
00:51
_vector_
Рет қаралды 25 МЛН
50 YouTubers Fight For $1,000,000
41:27
MrBeast
Рет қаралды 193 МЛН
ZOMWE ZIDALI KU BALAKA 🙌🙌🙌🙌25 July 2024
27:52
HOT 265
Рет қаралды 13 М.
Akulu Akulu Achipani Cha UTM Kuyankha Mafunso Pa Hanifa tv
14:18
J.D. Vance addresses RNC crowd: FULL SPEECH
36:00
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 1,9 МЛН
Donald Trump speaks at the RNC: FULL SPEECH
1:32:24
FOX 4 Dallas-Fort Worth
Рет қаралды 3,6 МЛН
Why VPNs are a WASTE of Your Money (usually…)
14:40
Cyberspatial
Рет қаралды 1,4 МЛН
Самый Молодой Актёр Без Оскара 😂
00:13
Глеб Рандалайнен
Рет қаралды 10 МЛН