Mwaimva ya ma demo akufunatu aletse ma demo anthu aja mwinaso adya mabanzi

  Рет қаралды 4,126

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

5 күн бұрын

Пікірлер: 29
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 2 күн бұрын
Yaaaaaap tidikile kae mayesowa
@user-lu8px7td6p
@user-lu8px7td6p 3 күн бұрын
Apopo ndizowonadi ayimitse kaye alembe
@DavieMaloya
@DavieMaloya 3 күн бұрын
Bola asadyesoo bazi😢😢
@IssahAluba
@IssahAluba 3 күн бұрын
Osasitha Deti ifeso zomwe akuchita zikutiwawa iyaaa pakhale pa 10 July pomwepo
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 3 күн бұрын
Tonse okhudzidwa tikudziwa tsiku lapa 10, osati zimene akunena akambanje zi ai.
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 күн бұрын
Tingodikira 2025 izi zititayisa nthawi aaa
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 3 күн бұрын
Ndizinthu zokhumudwitsa kumene chifukwa tsiku la 10 july silinatchulidwe dzulo ai, tatopa nazo ife zimene likupanga boma limeneli.
@JohnAsendi
@JohnAsendi 3 күн бұрын
Akambanje ndigulu lanu pazakuti zanu musankha nokha pazomwe muzitukwane papa njoka sitimayang'ana zakuti Pali madzira ankhuku kapena Pali m'phika ine ndikukulupirira Pali chaka chomwe Ana sukulu sanalembe mayeso ndiye anamwalira nyamako mapana chibaanzi 🤣🤣🤣🤣🤣 timadabwa man demo amwezi wamawa kulenge PA 1 amwezi inu iyayi mwatisandusa muno opezera chakundya chanu😭😭😭😭😭😭😭
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 4 күн бұрын
Eee eee ai zovutat
@JustinChiwale
@JustinChiwale 3 күн бұрын
Ndizoona cz kulibe ma demo amtendere ana alembe kaye mayeso plz
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 3 күн бұрын
Anthu akumwera inu koma muli ndi kwiyo koma boma lokha sitisintha munya inu mpaka 2030 woooooo
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 3 күн бұрын
Iwe tachoka apa 2030 ndanio machende akowo ndi 2030 yakoyo ukuwona ngat ndi gule kod iweo ndi chakwela wakoyo kupanda kuvota mumwera kuno ku mpoto inuo chigawo chapakati simungawinebe mwamva muzikhala mukuziwa zimenezo ku mwela kuno ndi kumene kuli anthu ochuluka kwambir ndikumapita ku mpoto pakatipo Mesa mwangochuluka ma farm basi ndie mukuona kuti inuyo mungamuwinise chakwelayo inu agalu eti muuzaneso zimenezo ndi kuousa kwanuko
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 күн бұрын
Mademo asachitike chifukwa nthawi yatha ndipo zingabweretse mavuto ena kwa boma lomwe likubweralo
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 4 күн бұрын
Boma likuba osati pang'ono misonkho atipweteka nawo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 4 күн бұрын
Alandila mabazi nawonso ndi achinyengo
@mariezorgen7735
@mariezorgen7735 2 күн бұрын
Can not exam's before?.
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 4 күн бұрын
Anthu abomamu akudya okhaokha
@StevenLemson-wj4dj
@StevenLemson-wj4dj 4 күн бұрын
Date ya mademo asinthe chifukwa,azatsokoneza ana omwe akulemba Mayeso. NOTE: Kupanga mademo ndikofunika kwaaambiri chimene changobvuta,ndi Date basi
@user-ht7vs3dp2u
@user-ht7vs3dp2u 4 күн бұрын
Kom Boma ili mmmmm chazelu balibes chomwe ndikuona ine mulungu atimenyere khondo
@SueWahna
@SueWahna 4 күн бұрын
Anakodza bwanji date asanawunikile
@Standwell78
@Standwell78 4 күн бұрын
Alandila chiseka pakamwa ndekut
@StevenAjusugama
@StevenAjusugama 4 күн бұрын
Asithe tsiku ndizoonadi ayi bola musatalikise after examination then moto
@Robertmkango
@Robertmkango 4 күн бұрын
Algorithm deti km mwezi womwewumo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 4 күн бұрын
Koma Malawi abale 😂😂
@StevenAjusugama
@StevenAjusugama 4 күн бұрын
Zoonadi ayi asithe tsiku
@user-uk3bz1hr5t
@user-uk3bz1hr5t 4 күн бұрын
Ndi zoonadi koma
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 4 күн бұрын
Komano ndikuona kuti mademo sangatithandize tiyeni tikakhile kwa kuya pephelo ndithu ndi chida timulilile chiuta namalenga basi
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 4 күн бұрын
Chauta amafuna athu oziteteza okha
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 3 күн бұрын
@@user-vx5kv8dz3d nanga pepaza oyakhula ayakhula mademo ndi omwe amachititsa kalindo palibe chimasitha nanga tingatani pamenepa
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 28 М.
Alat Seru Penolong untuk Mimpi Indah Bayi!
00:31
Let's GLOW! Indonesian
Рет қаралды 15 МЛН
MEGA BOXES ARE BACK!!!
08:53
Brawl Stars
Рет қаралды 36 МЛН
Heartwarming: Stranger Saves Puppy from Hot Car #shorts
00:22
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 20 МЛН
Raila: Be aware of the WRATH of history
23:42
Herman Manyora
Рет қаралды 33 М.
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 32 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 156 М.
"Wagwa Mtengo" (Soldier Lucius Banda - Tribute) by Pon G (Eugene)
2:32
Pon G On The Beats
Рет қаралды 21 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 91 М.
KAFUKUFUKU PA IMFA YA ACHILIMA
30:18
Jimmy
Рет қаралды 104 М.
Alat Seru Penolong untuk Mimpi Indah Bayi!
00:31
Let's GLOW! Indonesian
Рет қаралды 15 МЛН