UDF uku kufuna kuthana ndi MCP akuti athetsa zonse ndi Atupele

  Рет қаралды 12,598

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

8 күн бұрын

Пікірлер: 42
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 7 күн бұрын
Ana Amma 2000 za mcp amkangomva lero aziona okha .
@HenryTrevor-nb4ik
@HenryTrevor-nb4ik 6 күн бұрын
Atupele mwai alinaooo Kma santha kuyendera wanthu akumidzi komwe anthu ama vota OK Pali maderawena atupele sanamuonepo.akuyenerakudziwonetsera yenkha ndi kumasuka machezedwee bambo bakili muluzi amadziwa kucheza ndi wina aliyense ndichifukwa pano mulalo alinaooo please hon AA muluzi dzimasukirani anthu anu mwai ulipooo 90%
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 5 күн бұрын
Ndipo ndakunvanananu brother
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 7 күн бұрын
A UDF mumakhumudwisa anthu mumanena zina kupanga zina
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 5 күн бұрын
Dr Bakili Muluzi adanenatu izi kuti musazavotele MCP koma amalawi ukhutu kumve kufuna kuona za nuwani ndiye tikuziwonaditu
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 5 күн бұрын
❤❤❤
@JohnBestMandeule-cr8gp
@JohnBestMandeule-cr8gp 5 күн бұрын
Ndale izi zilipobe? What a shame....
@MaharaWuss-kv8rh
@MaharaWuss-kv8rh 2 күн бұрын
Yomweyo iwe
@user-ft5gp2bo3d
@user-ft5gp2bo3d 7 күн бұрын
Inatha ngati makatani
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 күн бұрын
Ine 2025 ndikudzavotera DPP 💙 Zibwana zanuzi aiiiii
@watchingu-bf2hb
@watchingu-bf2hb 5 күн бұрын
To defeat this arrogant leadership so called MCP make alliance between Dpp,Udf and Afford
@DavidJames-uv1jr
@DavidJames-uv1jr 7 күн бұрын
Chaka cha mawa kwatalika
@usumanidaudi
@usumanidaudi 2 күн бұрын
Ipondeni tiri pa mbuyo panu wachiyawo wangarusa
@user-jq6uh6dg6g
@user-jq6uh6dg6g 4 күн бұрын
Nkhaza za udf zosaiwalika anapha Matafale
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 7 күн бұрын
UDF ITS MY PARTY AND I WIL NEVER ABANDONED THIS PARTY
@user-pw4dv1el3d
@user-pw4dv1el3d 7 күн бұрын
They know what they are doing.
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 5 күн бұрын
zinamizananani mcp is here palibe chochoko mwachepa kwabasi
@user-jq6uh6dg6g
@user-jq6uh6dg6g 4 күн бұрын
Anapha mkulu wa asilikali mankeni chigawa udf imeneyo
@user-bn5om1rv9j
@user-bn5om1rv9j 5 күн бұрын
Kupepera
@TawongaGSMwale-cc2vm
@TawongaGSMwale-cc2vm 6 күн бұрын
Chipani ichi ndichabwino kwambiri Koma mwina wa chipani ichi ali ngat Ras David Chikomen safuna kuzungulira / kupangisa msokhano Muma boma ose aku Malawi Maka chaku Mpoto
@jelsonmlowoka8611
@jelsonmlowoka8611 Күн бұрын
Matafale 😢
@user-jq6uh6dg6g
@user-jq6uh6dg6g 4 күн бұрын
Mwachepa,, mukunama
@user-cp4qt9hs8w
@user-cp4qt9hs8w 6 күн бұрын
Mcp isadzayimeso pachisankho coz 5yrs yakwana bs aononga kale
@Tabithamulundila1
@Tabithamulundila1 7 күн бұрын
Fire 🔥
@chekiamaabdul5083
@chekiamaabdul5083 6 күн бұрын
Atupele he is stingy man
@user-qb1ef1xw5d
@user-qb1ef1xw5d 7 күн бұрын
Ndiyimene wukuyiwonayi
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e 7 күн бұрын
Udf ❤❤❤❤
@mussahchikwenga6194
@mussahchikwenga6194 7 күн бұрын
UDF YOMWEYO❤❤❤❤
@ChikondiKapito-zb8xe
@ChikondiKapito-zb8xe 7 күн бұрын
Muzilankhulako Chiyao mulikwanu uko
@user-ft5gp2bo3d
@user-ft5gp2bo3d 7 күн бұрын
Mukunama bodza ndilanu munatinamiza sapato
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 7 күн бұрын
Tupere umandisangalasa kwambili ngati bambo ako athu abwino
@WisdomMaseko-fi5sv
@WisdomMaseko-fi5sv 6 күн бұрын
Anthu abodza inu
@Standwell78
@Standwell78 7 күн бұрын
Mcp ai bola atupele chifukwa dpp kunkhomelela antho samafuna kut munthu azimasuka pazitukuko or kunthandiza anthu amamanga
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 7 күн бұрын
Tupere ukuyenera iweyo kapena dpp adad awili inu mukuvunika 2025
@AndwatchMambo-gn5bs
@AndwatchMambo-gn5bs 4 күн бұрын
Just brain washing people. Tionera chisankho cha ma khansala chichitike Ku Mangochi posachedwapa ngati UDF yingawine
@ErickTym-u2m
@ErickTym-u2m 7 күн бұрын
2025 Boma
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 7 күн бұрын
Motoooo kuti buuuuuu udf boma ❤❤❤❤❤❤
@OwenMajoni-qv3eg
@OwenMajoni-qv3eg 7 күн бұрын
Kodi udf ikanalipo?
@GeraldChisamba
@GeraldChisamba 7 күн бұрын
Kkkkkk UDF inabesa chipani Bingu anawachangamusa mazoba
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 5 күн бұрын
Adatsala ndimasewela UDF pano ndi DPP mulomwe adakwatila muyao basi sadachedwe adatenga mkazi uthawa naye upita kwao Moti apa aphatikizane basi MCP iwawumbuzi pamodzi a muluzi anaononga chipani kupatsa alomwe samadziwa Kuti alomwe ndiowononga
@GeraldChisamba
@GeraldChisamba 5 күн бұрын
@@JackMvura-ik2td 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 UDF woyeee
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 7 күн бұрын
Fact
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 27 М.
Waxy Kay - Ndikupempha (Official Music Video)
3:55
Waxy Kay
Рет қаралды 126 М.
1❤️
00:17
Nonomen ノノメン
Рет қаралды 13 МЛН
БОЛЬШОЙ ПЕТУШОК #shorts
00:21
Паша Осадчий
Рет қаралды 9 МЛН
Каха и суп
00:39
К-Media
Рет қаралды 1,7 МЛН
MUNTHU WAMULUNGU kuling'alura boma la CHAKWERA...lalephera
4:43
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 24 М.
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
JAI BANDA AND LUCIUS BANDA (RARE MOMENTS)
6:12
TEAM ENTERTAINERS MW#
Рет қаралды 30 М.
JB asambwaza Tygrin, poulula zinsisi Zina za ku America
43:12
Sam Malvitha
Рет қаралды 22 М.
Nkhani ya ku Bisesero ikumukhudza bwanji Zikhale Ng'oma
11:25
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 42 М.
KU HOT CURRENT KWATENTHERATU
25:02
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 155 М.
1❤️
00:17
Nonomen ノノメン
Рет қаралды 13 МЛН