Akugonana ku Nkhotakota malipilo ake kukhala nsomba izi nde nyasi zeni zeni sure

  Рет қаралды 4,376

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

6 күн бұрын

Пікірлер: 20
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 4 күн бұрын
Amenewo ndi mavuto a dziko, ndalama yikusowa, ngakhale kokagwila ganyu sikukupezeka. Zachisoni Malawi.
@abdukarimmponda5698
@abdukarimmponda5698 Күн бұрын
Izi nde za M'mbali mwa nyanja...ku nkhatabay salima mangochi mpaka nkhotakota
@CatherineDesire
@CatherineDesire 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂dzinthu pa malawi
@EyobeAyala
@EyobeAyala 4 күн бұрын
A jami wooooyeee😂😂😂 2025 wooooyeee 😅
@CatherineDesire
@CatherineDesire 4 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Jamison sisomba yodula NDI IJA yamaso angati bilimankhweyi maso pantunda IJA unabwera mwadzuka dzapakatidzi kare kunalibe 🤣🤣🤣🤣🤣p chikaronga amaitcha suhunju pachitonga NDI nthunthumala,imene mnyanja ili ponseponse masiku ano anaponyamo Satana kuyamba kwadzaka dzochepadzi mmene mcheni inadowamu Satana anabisa misheni ndikuponyamo mmadzi Jamison triones of the Jamison🤣🤣🤣🤣kubweretsa uchimo NDI matenda,ameneyo anayamba dzaka dzomwe Satana anapangamatenda a Ezi dzi ,kkkkkkk 😂Jamison pa nyanja ya Malawi🤸🤸🤸🤸🤸
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV 4 күн бұрын
😂Jamison ndi yemwe wavuta😂😂😂
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r 4 күн бұрын
Eeeeh eeh 😂😂😂koma azimayi enawa
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 4 күн бұрын
Koma Malawi taonjeza nyasi MCP mmm
@CatherineDesire
@CatherineDesire 4 күн бұрын
Wavuta Jamison pa Malawi🙄
@KelvinChiwra
@KelvinChiwra 4 күн бұрын
Si ndikuona vuto chifukwa anthu akuvutika mdziko atani awuzeni a boma awapatse tchito asiye zimenezo stupid government
@FlorahBanda-fl4vf
@FlorahBanda-fl4vf 4 күн бұрын
Jamison 😅
@MejarYusuf
@MejarYusuf Күн бұрын
Welenga mkotakota nde wavuta apa ameneyo momunyadila timati asumbaye
@FannyMkumba
@FannyMkumba 4 күн бұрын
Atinyengala nsomba bs
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 4 күн бұрын
Kkkkkk
@PatrickMtira
@PatrickMtira 4 күн бұрын
Sikumveka mawu ( tikozeleni timve nawo
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV 4 күн бұрын
Pepani kwambili. Takonza kunokutu mmene zimayenela kukhalila moti apaso tikudabwa kuti zikukhala bwanji kuti zisamveke. Mwayesa ku kwezako volume kumeneko?
@abdullahikhazum4046
@abdullahikhazum4046 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@IssahAluba
@IssahAluba 4 күн бұрын
😂😂😂 mavuto wavura Ku ,🇲🇼🇲🇼
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 4 күн бұрын
maka maka tachitanso kafukufuku kuti chakwera akumagonana ndi mzimayi wa hijabu uja ku sate house
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 4 күн бұрын
Apolice kugwila tchito ndi chakwela kupha athu basi
KWANUNKHA MWAZI KU MCP.
1:02:17
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 28 М.
TIKUDZIWENI - 13 AUGUST -  ABITI MANICE WILLIAM DAUDI
28:46
Times 360 Malawi
Рет қаралды 40 М.
Can You Draw A PERFECTLY Dotted Line?
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 101 МЛН
1❤️
00:17
Nonomen ノノメン
Рет қаралды 13 МЛН
ОСКАР ИСПОРТИЛ ДЖОНИ ЖИЗНЬ 😢 @lenta_com
01:01
🌊Насколько Глубокий Океан ? #shorts
00:42
Akufuna kupha mafumu a ku Ntcheu; Umboni wa mfuti 400 tili nawo
8:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 32 М.
Atupele Muluzi Chichewa
1:17
Mbcnews Television
Рет қаралды 50 М.
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA USIKU wathawu
42:49
Club Junta
Рет қаралды 10 М.
kumalawi kuno ndani wandale angamake??
1:01:32
Malawian Cameras
Рет қаралды 39 М.
ABDULL..CHIPANI CHOLAMURA UK CHAULUTSA ZISANKHO
12:53
Club Junta
Рет қаралды 8 М.
Gogo finds love at 60: Dickson Speaks out to us finally
33:17
JCTV Africa
Рет қаралды 24 М.
Zikhale ng'oma wamba ndalama zambiri ndipo pano wayamba kutchena
3:04
KU CHIKANGAWA NDIYE KWACHEMA UKU / ZINTHU ZAKE ZOVUTA🙌🙌
17:19
Can You Draw A PERFECTLY Dotted Line?
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 101 МЛН